I can tell you Muthalika family brought brilliant leaders ,Malawi rise up my vote on the Dpp ,I give to.all my heart ,ngati anthunu mumaona ngati ime mmene ndimaonera focus on wjat i say we wont regret
Can somebody take bingu speach serios and rule malawi eith his ideas pls,can someone became 2nd moses for malawi pls,we need a leader like bingu not politicians
Aliyense anali wabwino munthawi yake komanso woipa munthawi yake sakhala wabwino mu zonse. Mwachitsanzo bingu amene mukumunena kuti ndi wabwino, alipo ena amkamunyoza Ali mmoyo
Amayiwa ndi amene anapangisa kuti a Malawi asakhulupilire azimayi pa maudindo osiyanasiyana Makamaka pa udindo wa pulezidenti Kumavera za azungu, Kuba ndalama za ndege a Malawi ali duuuuu..osafusako Kaya a Malawi anapangilidwa mankhwala Kaya?
He is the very first thief of a president of Malawi 🇲🇼 he went to London to donate money from Indians who were kicked out of Malawi 🇲🇼 by Kamuzu Banda because of corruption. He told them to give him £2,000 each to come back to Malawi 🇲🇼
Bingu ws great leader our country ever since continued rest in peace I respect n we'll never forget ur jobs.
Bingu was a great leader followed by his brother Peter, the family is blessed
The blessing family ❤❤❤
Mutharika's family is blessed with good leadership
Yeah their bless 🙌🙏 ❤
Boza mafana
The best of all Bakili Muluzi.
Achalume, Atcheya, Kuchitekete. The king of self rule, the Fearless Father.
Live long Bakili Muluzi
Bingu anali tate wafuko❤❤❤❤❤
Best of all the time Mutharika's 🇲🇼🇹🇿
Adad inutu munali abwino kma anthu zolankhula zanu saamamva🙏🙏🙏🙏
Bingu n Peter mutharika I respect you guys❤❤
Bingu ndi Peter sadzapezekaso
I really agree with you ❤❤
💪💪I support late Bimgu wamntharika only. Enawo nde kaya I don't know them
Number 1
Bingu was a leader not a politician
I can tell you Muthalika family brought brilliant leaders ,Malawi rise up my vote on the Dpp ,I give to.all my heart ,ngati anthunu mumaona ngati ime mmene ndimaonera focus on wjat i say we wont regret
Bakili mulizi is namba 1
Muluzi munapangisa chimanga chonse kukhala cha yellow😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂Ndipo inu Kaya amachitenga kuti
Best family..Mutharika
Abale tamabelani nzelu zabingu zinaliza mphavu ❤❤
Bingu a dali atate,,,,, siizi
Munthalika family ur blessed.
awa ndie adali amuna awa 👏
Bakilli ndiwe Galu kwabasi 😂😂
Wawo wachiyao
Amai munali ndi fundo kma anthu amakujelasilani😂😂😂😂
Can somebody take bingu speach serios and rule malawi eith his ideas pls,can someone became 2nd moses for malawi pls,we need a leader like bingu not politicians
😂😁😁😁 bingu muthalika super speech💪💪😁😁😁😁
Bingu and Peter good speechs
Bakili mbakatundu kwenitu
Bakili love you
Big man kuchitekete😅😅😅😅
Kuchitekete, machine
Keep resting in peace bingu❤❤✝️✝️🙏🙏🙏😭
He was a great man bingu
Powerful 👊
MHSRIP Late President Bingu Wa Mutharika. You were indeed a good president Malawi lost a lion.
Aliyense anali wabwino munthawi yake komanso woipa munthawi yake sakhala wabwino mu zonse.
Mwachitsanzo bingu amene mukumunena kuti ndi wabwino, alipo ena amkamunyoza Ali mmoyo
Abwana kunena zoona munapasa pando muthuoyenela lest in peace bingu
Banja la Mr and Mrs Munthalika linabeleka ana anzelu. Mizimu yao iziusa muntendere
Amayiwa ndi amene anapangisa kuti a Malawi asakhulupilire azimayi pa maudindo osiyanasiyana Makamaka pa udindo wa pulezidenti Kumavera za azungu, Kuba ndalama za ndege a Malawi ali duuuuu..osafusako Kaya a Malawi anapangilidwa mankhwala Kaya?
Bingu wayankhula mbwelera.. ma boma ambuyo akunenawo mafuta sakamvuta
Bingu alwayz waz be legend
The same applies to the current leadership
Madala madala , we will remember you for ever RIP
What does the four rings on your fingers Bakili muluzi means?
Bingu anali anthu
Kutunda kumeneko Bakili Muluzi
Wachiyawo wangalusa bulasa
Muluzi super
Hehehe pitala wake uti aaa nenani za Bingu osati pitala hiyaaaa musatinyase ana anjoka inu
😂 our presidents ...making history ...😂😂😂
I support late Mr bingu wamutalika
Haya
Nice Bingu speech
Mawu chair amenewo 😂😂😂
Kkkkkkkk 😂😂😂😂😂I miss home
Pa osewa walankhulapo za chitukuko nd Bingu mh koma zinazi
Bakili muluzi bodza lokha lokha,😂😂
Bingu adali machine
Rest in peace bingu wamuthalika
Bakili anasokoneza mitu yamakolo athu
Bingu adali amuna awa.
Zinakukanikani 😂😂😂😂
Unali mwana sukudziwa chomwe ukuyankhula
Bingu was a politician..the rest just power hungry people..Peter it was his brother’s dream so had no details..but apparently second best..
A chair ntchito munagwila , koma anthu sayamika
Ayao ngakombola basi 😂😂😂
Kkkkkkkkkkk asogoleli anthu amenewa munayika mathaki
l like chair koma bingu anali katundu
zoona bingu anali amuna omanga nd ma wire
Koma bingu ndi amene anamanga anthu
koma atcheya wa ndi machine
I like your voice chair😂😂😂
He is the very first thief of a president of Malawi 🇲🇼 he went to London to donate money from Indians who were kicked out of Malawi 🇲🇼 by Kamuzu Banda because of corruption. He told them to give him £2,000 each to come back to Malawi 🇲🇼
Bingu ndi peter inuyo mulungu anachedwapo
Mulungu sachedwa, amapanga zinthu munthawi yake
Azitsogoreri anarakhura mau abwino
Munthu wankulu adayankhula uyu a Malawi a m'nzanga!,,,
Bingu anali adala
Kkkkkk malawi ndimene imakhalira BINGU
Acheya sopano zinali nthawi izo!!
Bakili muluzi ali munthu wankulu amatha kukankhula
Ngwazi😂😂
Bingu was a man indeed
Mmmmmm dziko lasoka
Bingu was great leader bakili ndikayani
Bakili
Peter munthalika amathaso
Bingu uja sadali kape
Bingu, Muthalika munali doro
This last one send him back to school his chewa isnt right.
Bingu rest well
kkkkk kuba ma billion ndikopanda ntchito? koma awa andi opoila kkkkkk
Mcp yakupaku mene lelo apachilima
Bingu he was a leader others looters
Anali akamuna
Mawu omveka bwino ndithu koma anthu kusamva Brooo
Koma muti bakili zimayend
King behavior detected
Mbava zakumalawi kulankhula Ngati anjelo sorry
Super yao
Bingu was great president 😍🥰
Mutharikas family
At list bingu amaganiza guyz
Apule bwaaa
Zonse ndi thawi
Bingu anali akatundu.
Chitsilu unawononga dziko
Mayi uyu alibe zeru
Wasalile wee ayao
Unali mbava iwe
Zoona