KU PARLIAMENT KWAVUTA AYIMITSA NYUMBAYI MPAKA MAWA - MALAWI PARLIAMENT 50th SESSION AFTERNOON

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 дек 2024

Комментарии • 75

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 8 дней назад +14

    Andale inu mitu yanu koma imagwira kapena nonse ndinu amisala komanso a Satana? Zoona mmene tikuvutikira a Malawi moyo ukulimba komanso misonkho ikutifinya. Zoona kukula mitu yanuyo mkumaseweletsa misonkho choncho? Nkhani iyi si ya otsutsa kapena olamula koma ndi mu malawi aliyense. Feel shame. Tidzabwera kumeneko kudzakuumbudzani nonse kumeneko. Mwachulutsa chibwana 🤮

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 8 дней назад +5

    I love you my sister,,so brave and Intelligent,am behind. Youu ,,ashoshe a Mcp. Mbava izi

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 6 дней назад

    You are powerful woman , you stand for Malawians

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 8 дней назад +6

    Madam don't withdraw the statement Chimwendo hinself is involved in fuel deal.

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 8 дней назад +6

    Chimwendo Banda akuyitenga Parliament ngati ndi nyumba yake ndi MCP ndichifukwa chake amadelela wina aliyense. Kikanakhala kuno ku RSA akanawombeledwa ndi futi.

  • @HaroldFodya
    @HaroldFodya 7 дней назад +1

    Well spoken madame proud of u

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 8 дней назад +1

    Ayiboo 😂😂chauluka chizatera madam speaker 🔊❤

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 8 дней назад +3

    Mama we silute you ❤❤

  • @Jamilahchinyama-y9b
    @Jamilahchinyama-y9b 7 дней назад +1

    Malawi wathu wabwino uja akupita kuti ambuye😢😢

  • @MacWilliamKaunda
    @MacWilliamKaunda 8 дней назад +3

    Anakubala enieni... salute 🫡

  • @MuluMishamo
    @MuluMishamo 8 дней назад +1

    Madamu l love your speech ❤

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 7 дней назад +1

    Very powerful words udf mp

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 8 дней назад +2

    Mzimayi wanzeru,,adabwitse akuba awo

  • @stevenbanda6665
    @stevenbanda6665 7 дней назад +2

    Thank u my sster

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 8 дней назад +3

    Mai jolobala mumatiyimilira kudela lathu, ndipo chimwendo ngati siukumudziwa Mai ameneyo umufuse DC wamachinga akuwuza bwino bwino ataba ndalama yogulira chisulo

  • @KetrinaMandiwa
    @KetrinaMandiwa 7 дней назад +2

    I wish if I could shake hands with that madam only represent me here at Phalombe

  • @ABDULEasha
    @ABDULEasha 5 дней назад

    Chimeendo banda. mutu wake waukulu ngati chisomba koma mmmm mzeru alibe poti sukulu mulibemo mutumo angoba ndalama za m,boma ndi abusa man lazalo limodzi 😭😭😭😭😭😭😭ife amalawi 😭😭😭

  • @BernaChauluka
    @BernaChauluka 8 дней назад +5

    English ilibe kanthu bola tamva mfundo zake mai uyu , komanso sindimaona chifukwa chomwe amalankhula English coz amaimilira ifeyo a Malawi kaya okhala ntauni komanso kumuzi

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 8 дней назад +3

    Mama umatiyimilila ife timangokupemphelelan kt mulungu zikhala nanu inuyo kwanthu Kuja ngt ku kusitha nkhani ndinu bc

  • @EdenBrigadia
    @EdenBrigadia 8 дней назад +3

    Mama openga mugodya ndalama palibe chimene mpangako kumeneko ma mp

  • @PhiriVictor-e9l
    @PhiriVictor-e9l 7 дней назад +2

    Mai wanzelu woposa achimwendo ndi amatola koma.mukamapanga ziganizo unyolo .2025 yizakupezani mwatafuna Chuma cha dziko mokwana

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 7 дней назад +1

    Let God expose them

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 8 дней назад +3

    Pajatu DPP imafuna manual. Auzeni iziimika zala mmwamba they are good at it.

  • @andymasingajunior
    @andymasingajunior 8 дней назад +1

    Madam 2nd deputy speaker utsogoleri wa Nyumbayi unawakulira today

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 8 дней назад +2

    Very shameful MCP and Chakwela government

  • @IsaackFrank
    @IsaackFrank 7 дней назад

    Zoona mama iuzeni paliyament

  • @LoyceshadShad
    @LoyceshadShad 8 дней назад +2

    Awa ndiwo azimai tifuna kumalawi osati izi mucita mai yolamu Ku police

  • @juliusmateyu
    @juliusmateyu 8 дней назад +2

    More fire mum

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 8 дней назад +2

    Mwanenepa ndi milomo yomwe

  • @PatrickMaluwah-bx9or
    @PatrickMaluwah-bx9or 8 дней назад +3

    Here is another woman representing poor Malawians out there,we need more of them.

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 8 дней назад +3

    We need MP like this one,she has spoken on behalf of many MALAWIANS who voted for CHAKWERA, today are crying bcoz of his leadership style that has pushed us into an inconsolable state due to the high price of local products, forex crisis,alot of aliases which are not addressed,pationias

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 8 дней назад

    More fire 🔥 🔥 🔥 🔥

  • @ZaoMaster-c7v
    @ZaoMaster-c7v 7 дней назад

    Olo muja anaberamutu kumkapita chinamtondi

  • @MalamaMithi
    @MalamaMithi 7 дней назад +1

    Yeremiah Chihana ndi akatundu

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 8 дней назад +1

    Woow 50billion dollars 💰💰 fuel 🤔🤔

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 6 дней назад

    Chifukwa chani chimwendo akumangoima osaloledwa kuderera?

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 7 дней назад +1

    Mukumva kukoma nonsenu muli mweee inu a MCP.
    Tikuonani 2025

  • @wisekanyinji5377
    @wisekanyinji5377 6 дней назад

    Chimwendo amadelera ngati mawa kulibe, muzalira inu, timavota ndife, ndipo uku mukusewera kwambiri

  • @PhiriVictor-e9l
    @PhiriVictor-e9l 7 дней назад

    Mwakanika kuyendetsa zinthu meazinenepetsa muli see ndi mphuno zomwa

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 7 дней назад +1

    But why mcp is killing Malawi?

  • @Jamilahchinyama-y9b
    @Jamilahchinyama-y9b 7 дней назад +1

    Achimwendo kunja kungade bwanji kuzacha basi

  • @Georgekalipinde
    @Georgekalipinde 7 дней назад +1

    Kusaukitsa dzikotu uku mwadala. Anthu oipa, atsoka,zigawenga izi

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 7 дней назад

    What is madam second deputy speaker madam means what?

  • @dytonkaphwanya5167
    @dytonkaphwanya5167 7 дней назад

    time to tell

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 8 дней назад

    Parliament ya Chimwendo ndi MCP yomvesa chisoni

  • @MocambiqueMocambique
    @MocambiqueMocambique 7 дней назад

    Kumkuyu akumuuzila chimwendo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 8 дней назад +1

    misonkho ya amphawi ija kuno...................

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 8 дней назад +1

    Its not denting,,chilungamo

  • @HaroldFodya
    @HaroldFodya 7 дней назад

    Some of u wl not make it to parliament again ths is u last time there

  • @Georgekalipinde
    @Georgekalipinde 7 дней назад

    Anthu akuba awa

  • @Thokozani-n6d
    @Thokozani-n6d 8 дней назад +2

    Am understand for mother arankhura bwino kut mitini ipitirire mawa akaiganinzire bwino amkuru akuruwa kuti nziyende bwino

  • @SteveSolomon-m7f
    @SteveSolomon-m7f 7 дней назад

    Athu akuopa paja akabweresa umboni mukumawapha MCP kupha,khaza , ndipo simuuona mpando agalu inu a MCP mbuzi inu sikulina tizafika nkoko order yake iti iwe chimwendo ndiposo osati chimwendo koma chimimba umandibowa kwambiri

  • @AlexNjovu-j4z
    @AlexNjovu-j4z 7 дней назад

    Ayizikomo

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 8 дней назад

    Chimwendo Banda ufiira Maso sudati uziona wayamba zosayamba

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 8 дней назад +2

    Mcp icoke kumene ikuba kwambiri ndipo cikangawa panyoo pako ndi mcp yako yonse 4tsake

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r 8 дней назад

    Ma mp wose palibe akuchitako ku parliament wonse akungowononga misonkho mutawafinsa kuti ma 200 million mumalandira every year mwapanga po chani ku constituency kwani akuwonetsani chimbuzi cha million, bwanji zinazo kutsegulilako minda, kuti ikakukwapulani mudzikatengako nkumapatsa akudya kalongonda wo? Malawi heyiii dzukani

  • @PatriciaTikhiwa
    @PatriciaTikhiwa 7 дней назад

    Judgement day will come u wanna see

  • @phillimonmaila4269
    @phillimonmaila4269 8 дней назад +3

    Parliamentary Members pls polish up ur English

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 6 дней назад

    Chenjerani pano koma siku lina muzayankha pafupi fupi ziko lonse LA Malawi kumawadandaula anthu amozi mozi omwewo apambana bwanji achakwera ndi boma lanu LA mcp mwalionesa ziko LA Malawi zosaona muzachita ligileti siku likubwera

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow 8 дней назад

    osathawa ngongole zomwe tinaziputa tibweze basi iya

  • @lindakankhwani
    @lindakankhwani 8 дней назад

    Poor English in parliament 😅😅😅😅 alimo ambiri

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 8 дней назад +1

    Aphungu ambiri ndiosazindikira kulephera kugwiritsa ntchito computer ndi kukumva ambiri ndi aDPP. POFUNIKA KU PARLIAMENT MINIMUM QUALIFICATIONS IDZIKHALA DEGREE IZITU ZOCHITITSA MANYAZI

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 8 дней назад +2

    Kamtonga ko kangotha kulankhula apako ndiwausilu,sitose atonga ndife ausilu koma yekhayo mp wa MCP ndiwausilu

  • @ChicoBanda-kq7py
    @ChicoBanda-kq7py 8 дней назад

    Motor

  • @PatriciaMkwenda-xc4mh
    @PatriciaMkwenda-xc4mh 8 дней назад +1

    People are suffering with hunger but your busy talking nonsense.

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 8 дней назад +1

    Try not talk with hands