Bingu from Perth & Asia Part 8 - Press Questions 1

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 сен 2024

Комментарии • 207

  • @AffickChaona
    @AffickChaona 3 месяца назад +16

    That time ziko likuyenda bwino,, atola nkhani amasowa chofusa

  • @VesterLuke
    @VesterLuke Месяц назад

    The leader , the greatest

  • @FosterChamowa
    @FosterChamowa 2 месяца назад

    Uyu adali munthu

  • @emmanuelmiropo6366
    @emmanuelmiropo6366 6 месяцев назад

    Mr president ❤❤❤

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 2 месяца назад

    Nthawi imeneyo...atolankhani amasowa chofunsa chifukwa chokhuta kwambiri nsima

    • @GracianJames
      @GracianJames Месяц назад

      Kkkkkk 😂😂😂 uli ndi vuto 😂

  • @aubreymaonga4266
    @aubreymaonga4266 6 месяцев назад

    Journalists opoira munthu azipumako asapite ku holiday

  • @winikomanyenje8190
    @winikomanyenje8190 3 года назад

    A very foolish question,so u want the president to report to you

    • @Napolean45
      @Napolean45 Год назад +1

      You are the one foolish. Anthu ngati Inu ndi amene mumapepeletsa president. President ndi servant wa Anthu osati bwana wawo.

  • @arthurandersenchanya7036
    @arthurandersenchanya7036 3 месяца назад +5

    When MBC was worthy to watch

  • @raphaelkamala69
    @raphaelkamala69 2 года назад +8

    I wish if that question for pirilan from zodiak to ask chakwera now about civil cevants salary as of now

  • @JonesMateusphinifour-b2l
    @JonesMateusphinifour-b2l 3 месяца назад +10

    A man with good leadership, bingu may his soul rest in peace

  • @kamwendoderek6567
    @kamwendoderek6567 Год назад +14

    mmalawi ngati anataya muthu wolemekeza athu onse posatengera ndale , sitizapezaso wina, onse amene anatenga gawo pa imfa ya legend ameneyi adzakayakha ngati sadalape, ine ndinagwirana nawo mzanja atabwera kuzapephera pa nguludi parish ku chiradzulu.mzimu wawo uwuse ndi mtendere.

  • @giftkadzakumanja9308
    @giftkadzakumanja9308 5 лет назад +11

    Big man ameneyu anayenela kukhala life president

  • @JoeyJones-jq8id
    @JoeyJones-jq8id 3 месяца назад +7

    This is time i saw my my parents never struggling to put food on table for me

  • @JamisonElifala
    @JamisonElifala 6 месяцев назад +2

    Pro bingu anar mtsogoleri wamphavu mu ulamuliro democracy anariso okondedwa ndi anthu.

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад +1

    Awa adali machine mu kaganizidwe ndithu... MHSRIP

  • @TheArisingTidzaimbabeGeneratio
    @TheArisingTidzaimbabeGeneratio 3 месяца назад +2

    Bingu anari Genius ❤

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Год назад +4

    This was a heroic speech spoken by the late president of the Republic of Malawi that was a warm heart of Africa before which is now a hell of Africa

  • @ChawanangwaChazily
    @ChawanangwaChazily 5 месяцев назад +4

    We miss you

  • @Chikumbutsojimu
    @Chikumbutsojimu 5 месяцев назад +1

    People love the dead....when alive you hate hi

  • @NyashaNyalugwe-su9sb
    @NyashaNyalugwe-su9sb 4 месяца назад +1

    Mtolankhani koma anakuwidwa😂😂😂

  • @Prolhinga265
    @Prolhinga265 2 месяца назад +1

    Munthu Wamkulu

  • @RasheedBanda
    @RasheedBanda 4 месяца назад +2

    May his soul continue 🤞 rest in peace 🕊️🕊️

  • @ClintonMoffati
    @ClintonMoffati 3 месяца назад +1

    Bingu anali Chawulere chamulungu kumtundu wamalawi

  • @PreciousPhiri-b6j
    @PreciousPhiri-b6j 5 месяцев назад +2

    Bingu,, the greatest president seconded by Kamuzu,

  • @wiseyk1435
    @wiseyk1435 6 лет назад +3

    Uyu nde anali president watsogolo mbili yonse yamalawi

  • @MotivatedI
    @MotivatedI 2 года назад +3

    Continue rest well. We didn’t understand you 🙏🏾

  • @Gifkanjirawaya-fg9ws
    @Gifkanjirawaya-fg9ws 5 месяцев назад +2

    Continue resting in peace Ngwazi

  • @PreciousPhiri-g3d
    @PreciousPhiri-g3d 2 месяца назад

    Nthawi imeneyo sugar ali pa K450 1 kg eeeeh..... RIP Dr Bingu

  • @samluhanga
    @samluhanga 2 месяца назад +1

    Will forever miss this man..may his soul rest in peace😢

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 10 месяцев назад +1

    Madala Bingu munthu wachikulire.tikukusowani ndi ulamuliro wanu.anthu oipa anatisaukitsa.tidzakusowani mpaka kale kale

  • @DanielDuwe-tc9py
    @DanielDuwe-tc9py 3 месяца назад

    Akanakhala kuti nthawi amabweza m'buyo,akanazizwa pamenepo dziko liliri lelo...

  • @rooneymaster4861
    @rooneymaster4861 6 лет назад +5

    mulungu amudalitse bingu

  • @ShobimaKalima
    @ShobimaKalima 3 месяца назад

    Hamble president pano tingomangidwa tikalankhula zakukhosi

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 14 дней назад

    Awa adali katundu wabwino kudziko laMalawi koma pokhala Mulungu salakwitsa, tizingoti rest in peace mfumu

  • @labanrodrick4224
    @labanrodrick4224 2 года назад +2

    Anapulumutsa a Malawi for 9 years

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude 3 месяца назад

    Dickson Kashoti wa congress😂😂

  • @InnocentKapesi-gx7yf
    @InnocentKapesi-gx7yf 2 месяца назад

    Bwana pumani mumtendere dziko munaliyendetsa bwino heavy

  • @HellingsMughogho
    @HellingsMughogho 5 месяцев назад +1

    Bingu was just lucky economy padziko lapansi inali bwino. Koma anali wakuba just like ma president ena. Anayambitsaso tsankho mmalawi muno. Komaso anapha anyamata 20plus mu jully. Plus Robert Chasowa. May their soul rest in peace❤

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 5 месяцев назад

      Ngati ankaba koma mumakhuta,Bakili anapeza economy ili bwino kwambiri koma anapanga chiyani chanzeru.

  • @QochiweNkhoma
    @QochiweNkhoma 4 месяца назад

    Bingu anali president wamphamvu ndipo amathandiza amphawi aliyense nthawi yake anali ndichakudya pakhomo. Otsati awatikuwaona pano

  • @pyjames5627
    @pyjames5627 5 месяцев назад +2

    For the love of late Bingu

  • @edisonnyasulu9568
    @edisonnyasulu9568 5 лет назад +2

    Kunena zoona umbuli wathu wakumalawi ndagoma nawo kumangokuwa zilizose

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 2 месяца назад

    Mulungu tatidzutsireni uyi ife tikupasani chakwera

  • @BoscoKalua
    @BoscoKalua 10 месяцев назад +2

    The right President ❤

  • @trustmakawa5432
    @trustmakawa5432 4 года назад +4

    rest in peace Dad

  • @WilfredYekha
    @WilfredYekha 3 месяца назад +1

    Big hand to the late Bingu wa Mutharika

  • @ThokozaniPiyo
    @ThokozaniPiyo 29 дней назад

    This man was having charismatic power

  • @Andule-v4n
    @Andule-v4n 3 месяца назад

    This was not right intimidating the journalists

  • @VioletZakwanira
    @VioletZakwanira 3 месяца назад +1

    I loved this guy since and nothing has changed up to date

  • @gearardphiri6904
    @gearardphiri6904 3 месяца назад

    Ndakunyandilani koma mudzimuwanu wupumemumtendele

  • @BobJade-hq8qj
    @BobJade-hq8qj 5 месяцев назад +1

    True meaning of leadership

  • @SirNanjalaMw
    @SirNanjalaMw 3 месяца назад

    Pamene lero atola nkhani akuchita kuopa Galu uyu alipoyi

  • @michaelmperembe6872
    @michaelmperembe6872 2 месяца назад

    Media freedom was suppressed 😢

  • @PeterMajawa-dx4sb
    @PeterMajawa-dx4sb 10 месяцев назад +1

    This man was indeed ordained by God to lead us, when God is in control no wonder hunger, outbreaks are nowhere.

  • @kotking-jn5us
    @kotking-jn5us 4 месяца назад +1

    the great leader and we miss you Dad may your soul rest in peace.

  • @DeezoWrld
    @DeezoWrld 5 месяцев назад

    Bingu anali omvesesana ndi anthu ake

  • @DuncanMbulo
    @DuncanMbulo 2 месяца назад

    Uyu analiphuradi zikoli pa moto😢

  • @silvesternyirenda5211
    @silvesternyirenda5211 3 месяца назад

    DPP inali ndi mbuli za ma supporter

  • @Skipton-ox5zp
    @Skipton-ox5zp 3 месяца назад

    Mkuluyu amkakondedwa hvy eeeeee😂

  • @VesterLuke
    @VesterLuke Месяц назад

    The presidential

  • @jamesonmzungu
    @jamesonmzungu 8 месяцев назад +1

    A leader very humble....May your soul keep resting in peace

  • @LoydChata
    @LoydChata 4 месяца назад

    Eeeee km akulu awa tidzawasowa ndithu

  • @WardsonMadalitso
    @WardsonMadalitso Месяц назад

    RIP BINGU

  • @GustarLafisha
    @GustarLafisha 3 месяца назад

    Osati zisilu zili lerozi aaaaa mbala zenizeni

  • @EliasKawuwa
    @EliasKawuwa 3 месяца назад

    Munthu wamkulu ,mzimu wake uuse mu mtendere

  • @GoodKavisika
    @GoodKavisika 5 дней назад

    Gk

  • @josephcalisto
    @josephcalisto 5 месяцев назад

    Munthu wankulu kwambili tidzakusowani😢

  • @jackmuhura1797
    @jackmuhura1797 5 месяцев назад

    Chonchi nk
    unali ulamuliro wamtendere, koma atolankhani apa sanagwire ntchito yawo mwamtendere.

  • @declarembukwa
    @declarembukwa Месяц назад

    Visionary Leader

  • @LukasMackion
    @LukasMackion 2 месяца назад

    Sitinamuvetsetse BINGU

  • @PidoMaganga
    @PidoMaganga 6 месяцев назад +1

    Continue resting in peace Dad ❤❤❤

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli 2 месяца назад

    Anali Amfumu AWA osapha Anthu ai

  • @users-girroblonce
    @users-girroblonce 2 месяца назад

    Awawa anali machine a three phase😢

  • @ManuelJohn-p3m
    @ManuelJohn-p3m 3 дня назад

    anali wakulu

  • @VesterLuke
    @VesterLuke Месяц назад

    Ameneu an2 amachta manyaz

  • @WalikoMsutu
    @WalikoMsutu 5 месяцев назад +1

    Wina adaiwonera patali kungoyankhula chingerezi onse ziii

  • @BinaliCharles
    @BinaliCharles Месяц назад

    My vote

  • @miovekanola2780
    @miovekanola2780 3 месяца назад

    Eeee mn

  • @PatienceMafeni
    @PatienceMafeni Месяц назад

    Hahahaha

  • @timothymollen7823
    @timothymollen7823 4 месяца назад +1

    Great speech

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 8 месяцев назад +1

    he was wise man and may his soul rest in peace.

  • @PatienceMafeni
    @PatienceMafeni Месяц назад

    Kkkkkk

  • @SpencerKadewere-cd5ok
    @SpencerKadewere-cd5ok 4 месяца назад +1

    We're still missing this great man

  • @Prescottmathewe
    @Prescottmathewe 2 месяца назад

    GOAT

  • @JosenMhangomlowoka-og9es
    @JosenMhangomlowoka-og9es 25 дней назад

    Koma zidaliko

  • @ThoccoKapito-ds7cj
    @ThoccoKapito-ds7cj 3 месяца назад

    Mathers

  • @SirNanjalaMw
    @SirNanjalaMw 3 месяца назад

    uyu anali Munthu guys

  • @YusufJames-f5f
    @YusufJames-f5f 3 месяца назад

    Kmkmm

  • @vincentsayenda3946
    @vincentsayenda3946 2 месяца назад

    Shasha kwambiri ❤

  • @AaronChiwasa-qr9be
    @AaronChiwasa-qr9be 9 месяцев назад +1

    He was a great leader

  • @MaxwellMisanjo-xw9rl
    @MaxwellMisanjo-xw9rl 5 месяцев назад

    Mzimu wake uwuse mundendere

  • @Telezachinokongulube
    @Telezachinokongulube 3 месяца назад

    Muimaso madala

  • @idrissahsabit4007
    @idrissahsabit4007 5 месяцев назад +1

    Legend never die

  • @EmmanuelManiya
    @EmmanuelManiya Месяц назад

    Mumakwana dad

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 3 года назад +1

    Uku kunali kuntunda osati zibwana

  • @declarembukwa
    @declarembukwa 5 месяцев назад +1

    Legends never Died

  • @NumeriJohn
    @NumeriJohn 2 месяца назад

    M'makwana

  • @gabrielkalonga1113
    @gabrielkalonga1113 2 месяца назад

    Bingu

  • @alfredpindani9045
    @alfredpindani9045 2 месяца назад

    Bingu

  • @DanMwatchipitsa
    @DanMwatchipitsa 3 месяца назад

    Bingu😢😢

  • @isaacknyakwechilembwe-lw6lp
    @isaacknyakwechilembwe-lw6lp 3 месяца назад

    kugaya