I manage to proceed my Education in time of bakili muluzi because of free education contribution of exercise book pen and porridge the situation of my family waz very poor may Almighty God bless you achair
you are matured man and you spoke that leadership type of malawian we need bravo Dr Bakili muluzi THAT IS WHY I HAVE BEEN VOTED FOR YOU IN YOUR ALL TERMS WE ARE ONE MALAWINA AND ONE NATION NOT AWA ASABWERE THAT KUGANIZA MOPEREWERA MU UBONGO
I am not a UDF member but your speech surpluses all speeches U have heard.You are a true democratic.If all parties emulated what you have spoken,malawi would have a better place for politics.There are other people who are busy formulating false information which only incites division ,anger and hatrage. LATE US BE A PEACEMFUL COUNTRY THAT DIES NOT SPREAD FALSE INFORMATION FOR POLITICAL GAINS
Ndipo ana timanjoya nthawi imeneyo ana sitimavutika ma text book makope aulele zolembera aaa miss my malawi those days was endeed good for everyone not awa achikangawa ntchito kupha anthu kudzikonda
Well said mr president former deserved even your voice shows that you were chosen to be our leader words of unity may Allah keep you alive may you live longer insha Allah
I will never trust politicians Kuteroku muitenge bwino speach ya atcheya,then take kamphekesera kanamveka kaja kut udf ndi mcp ali limodzi,mupeza mayankho onena kut this people ali limodzi.ndipo tizavote mwanzeru,apo ayi tivotera magazi njala ndithu.
This is the speech that we need to hear from our leaders. To unite us, to conglomerate not to divide us. That's the speech of the wise old man president retired
There was a time i loved this man so much, the reason i hate DPP forever! It breaks my heart the time bingu left udf nnachiona ngati chipongwe chachikulu for this gentleman
Malawians, the chair still looks charismatic and Speaks with a sense of humor. Let’s keep watching at the depth of his speech. We may not see the reasoning behind his sense of humour now but rather things will unfold for the better Malawi or not. My hope is that all is well and there is no sinister move
Very comforting speech a Chair , may the Lord God continue to bless you Sir!
So wat about Chakwela brah? ❤
I manage to proceed my Education in time of bakili muluzi because of free education contribution of exercise book pen and porridge the situation of my family waz very poor may Almighty God bless you achair
Exactly property of Malawi government
Thank you chief
@@Mustafafrodrickabdudullahiz a father ov the nation ndipo munthu uyu amakondedwa
you are matured man and you spoke that leadership type of malawian we need bravo Dr Bakili muluzi THAT IS WHY I HAVE BEEN VOTED FOR YOU IN YOUR ALL TERMS WE ARE ONE MALAWINA AND ONE NATION NOT AWA ASABWERE THAT KUGANIZA MOPEREWERA MU UBONGO
uku ndiye kuyankhula kwa muthu wankulu, ulemu wanu
osati kwa anthu enawa mpaka kumati wakutiwakuti asabwere mmmmm
Wow! Ndawakumbukila a chair,, anabwera pa school yakwathu awa ,, President wozichepetsa,, voice yokhayo yaaaa
the most beautiful speech I have ever heard..Atcheya our very own Mandela..🤝
Amasangalasa gogo wathuy ndpo ndiwacifundo
so nice, a speech worthy praising.......a man among men indeed
ACHEYA Is Still Energetic. God Be With Your Good Health Bigy.
Peaceful person, I am proud of you, may God give you a long life
Perfectly said Your Excellency ❤ receive your flowers 🌹 🌹 🌹 🌹 whilst still alive Bwana Chair 😅😅😅
Machine 🎉🎉🎉🎉
Atcheya Kuchitekete!!!! Katundu bambo, proud of you Atcheya
A chair ngati akugulani mupita ndiinuyo chipani sichikupita ku mcp mufune musafune we fight for our freedom long live a chair
Hahah 😂😅
Zoonadi aaa
That's great thing the formal president we love you 😍 💜 ❤ so much & it's good speak
I am not a UDF member but your speech surpluses all speeches U have heard.You are a true democratic.If all parties emulated what you have spoken,malawi would have a better place for politics.There are other people who are busy formulating false information which only incites division ,anger and hatrage.
LATE US BE A PEACEMFUL COUNTRY THAT DIES NOT SPREAD FALSE INFORMATION FOR POLITICAL GAINS
😂😂😂thank you so much Atcheya. Mawu Anu ndi okoma kuwamva❤❤❤
Nanga chakwela?
God bless you a chair, man kindness, most malawians we are so helpless, we need's people like you.
Thank you Achair we still remember your great achievements
We will never have a people president like him, may u live Long a chair athu..
Wow that's amazing
Adala asyeene ulumu wawo❤❤❤
😅😊😊
Well said speach komano it abit late cz zinthu izi monga kholo la matipaty amayenera kuyankhula izi since pomwe zipanizi zinayamba kudana osati kukhala pa convention komabe zamveka ndipo ndikhulupilira kuti boma komanso osusa boma aphudzilapo
No wonder you became the first democratic president of this nation.
This country needs more of you atcheya.
Great speech ❤
Akuluakulu ndi mdambo mozimila Moto achair ndi achair bas 💪💪💪 very meaningful and powerful speech to the Malawian people
This man was truly a political giant
When i was listening i remembered that time when Malawi was peaceful country,l end up forgotten that i am with Chikangawa now😢😢😢
Powerful speech. Congratulations former HE 🙏
Bakili Muluzi is a true STATES MAN
Live live
we miss those days free education free notebooks free.......
DR Bakali Muluzi palibeso wina
Ndipo inu😢
We love you a chair,, you introduced democracy in this country and free primary school,,live long a chair
Mbambande Achair,Nice speach
Every lmppressive Dr Bakili Muluz❤️🩹
Malawi needs such people what a wonderful speech
Apm my Vote❤❤❤❤❤
So powerful speech from a chair Dr Bakili muluzi ,the former president of Malawi ❤❤
one of the best public speaker,i have ever seen
May God give you a long life,Peaceful speech
Adha awawa muli voice💯💯
Words of wisdom I really appreciate our former president atchaya ❤
My vote Dpp
Ulemu wanu a Chair, tinakusowani ndipo tidzakusowani masiku onse. Mukamayankhula, uyo anali ndi nkhawa zimachoka, matenda amachira, maudani amabalalika. Akulu ndi mdambo mozimira moto. Adzikusungani Mulungu. ❤❤❤❤🎉🎉🎉
I just like this man. His charisma 🎉
A chair ndimakusowani. i enjoyed my secondary school time with Gable, iyiyi atsikana tinkanjoya nayo
Thank you big man
Ndalandilapo makope ine ambirimbir osat tuonaz machine awa zovuta sizlephela kma salute Mr muluz
Mwana mmodz ma kope 10
ndipo makope amachita kukumana sukulu ya ulere ija idali ya chair yonkha,,Ambuye aziwapasa moyo ochuluka
Allah wape Umi welewu Insha Allah ❤❤❤
Mayi patel mzimayi osatekeseka opanda dyela loduphadupha zipani.imvani kukondedwa from me
Nyc speach Dr muluzi we like you
Ndipo ana timanjoya nthawi imeneyo ana sitimavutika ma text book makope aulele zolembera aaa miss my malawi those days was endeed good for everyone not awa achikangawa ntchito kupha anthu kudzikonda
Good speech from Dr bakili muluzi
Well said mr president former deserved even your voice shows that you were chosen to be our leader words of unity may Allah keep you alive may you live longer insha Allah
Ameen
Kulakhula kwabwino .....kwambili A chair......makwana inuyo ndinu munthu wamkuludi.... respect mr Chair❤🔥
He was deserved to be president indeed mr chair we really appreciating you together with your administration ❤❤
May Almighty God bless you and give you long life we love you
I will never trust politicians
Kuteroku muitenge bwino speach ya atcheya,then take kamphekesera kanamveka kaja kut udf ndi mcp ali limodzi,mupeza mayankho onena kut this people ali limodzi.ndipo tizavote mwanzeru,apo ayi tivotera magazi njala ndithu.
I agree with you
You're right my brother but mcp itimaliza kwambiri.
This is the speech that we need to hear from our leaders. To unite us, to conglomerate not to divide us. That's the speech of the wise old man president retired
Aliyense ndi bussiness party yake tiyeni tisapote dennis mahata and utm plzzz
Kuyankhula kwa true Democratic man kumeneko. A chair long live!!!
May Allah bless bakili muluzi and give him more and more years l like achair
we love him ❤
Chair born to be a leader keep on
Democratic leadership
To be honest Atcheya Ambuye anakupatsani mawu achikako .... Long live atcheya!!
Munthu wamkulu tsopano kuyankhula kogwira mtima timakunyadirani a Chair Ambuye wathu wakumwamba azikudalitsani nthawi zonse ndikukupatsani moyo wautali, 👏👏👏
I love Udf I love Bakili muluzi
Am happy to see my president kale likanati lidzibwerera mmmm
Nthawi yaulamuliro wa bakili ndimatha kutola ndalama panjira . Which means kudali ndalama ❤❤😂😂 UDF 2025 bomaaa 👋🤲🤲
😂😂😂
Ndalama zotola😂
Chomwe nimakondera akuluwa kuzichepesa sazikutumula peaceful no 1
There was a time i loved this man so much, the reason i hate DPP forever! It breaks my heart the time bingu left udf nnachiona ngati chipongwe chachikulu for this gentleman
He might have his own flaws but Atcheya is one of the most loved former presidents, Malawi will ever have.
Thats the true meaning of wise leader chosen by God
😂🎉😂😂😂😂😂Kkkkkkkkkkk 🎉🎉🎉🎉🎉 big boss kulankhula kokhako ma speaker onse akunjenjemera
I love UDF since i was young❤❤❤
God bless you a chair timakunyadira kwambiri
Kd anthu munangozolowera kutukwana? DPP ndi UTM yalakwa chan pamenepa mukamaika macoment opusa?? Zankutu,osaitchura MCp Bwanji akungogawa ndrama kwaoimba anthu akufa ndi njalao
Akutukana DPP ndi UTM zisilu za anthu
Sakupuma nayo bwino DPP awa alekeni akutayitsani nthawi @@SliviaJosephy
Ndizitsilu zimakhala kuti zalandila bundle ya Mcp kuti izitikwana dpp munya muona ndipo simunati zitukwanani ndi bundle ya magaziyo mbuziii
Za kumwezi zimenezo ndizimene a chair sakuzifunazo. He wants one people one Malawi. Zamanyi a DPP zo ndizimene akukanazo, fotsek
Nthawi imeneyo maluwa soap tikugula 5 tambala ,kazinga cooking oil pure aaaaa nthawi kachitsilu may god keep you self mr Tchair
Thanks a chair mwayankhula monga munthu wankulu komaso a promoter of unity
Very powerful speech we need such kind of leadership
This is a powerful message from Chair Muluzi. Agalu a DPP ndi amene akuononga democracy muno Malawi. Mwachita manyazi lero chairman wakumasulani
Awuzeni a DPP avetse chifukwa democracy samayidziwa mult party democracy
Agalu ndi congress!!Chipani chokupha! Afiti.
The kind of leadership we need to build Malawi 🇲🇼
This is our special cheir for us may God bless you
I remember president muluzi he did the best in his time but these president of today not good .
Acheya woooye ngakhale munatinamiza sapato tikudikilabetu Ife 😂😂😂😂😂😂😂
Tikuzifunadi sitinaiwale awuzeni😂😂😂
😂😂😂
Km ndipoo
Kkkkkkk nkhani izitha
Koditu sanatinamize.,kungoti ma size athu sakuwaziwa kkkkkk
Thanks so much atcheya mumakwana inuyo ulemu wanu
Muthu wakulu.bakili good voice
😂😂speech Kumasekako koma chikwiyilenicho mpaka kutha kkkkk bravo chair
Malawians, the chair still looks charismatic and
Speaks with a sense of humor. Let’s keep watching at the depth of his speech.
We may not see the reasoning behind his sense of humour now but rather things will unfold for the better Malawi or not. My hope is that all is well and there is no sinister move
And very good speech...yomanga Malawi
Exactly
Mwandisangalatsa ANchea chifukwa chakuvomereza kuti mwakura pachokhacho ambuye akudalitseni koposa ❤❤
DR Bakili Muluzi palibeso wina ❤❤❤❤
Elder always gives great words mbambande Achair anyamata apa town 😂😂
Wise words from a wise man ❤
He never changed though ,how he speaks.
We proud for you
I love a Chair.
A chair ndi a chair forever hold peace ❤❤ 🙌🙌🙌
Acheya i wish long life
Dziko la Malawi langokhala lovuta , koma achair analidi president wa Malawi
Chair my president
Kwambiri, God bless you a chair.
Ndimakukondani a chair. Free exercise book ndi ma pen ❤
Exactly bro
Ife taphunzila nthawi ya a chair .ku school makope osasowa
Timalandira aulele
Zoona❤
Ndinayamba sukulu ya ulere std 4 /1994, tinkalipila K4.00 komatu kuti ipezeke eeeh anali mavuto.
Zikomo Ambuye Yesu
Zikomo a Chair
Zikomo UDF ( free primary school)
We thank God 🙏🙏🙏 a chair is so energetic but chikangawa is still not welcomed ku UDF convention power to the pipo
We love you Acheya
If this guy can come back to be a prisedent will win
Achir sadzakulaso bas tivomereze🙏🔥