BON KALINDO LERO PA 18 NOVEMBER WASEKA MWA MWANO ONSE OMWE ALUZA KU UTM CONVENTION AKUTI ZAMANYAZI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 ноя 2024

Комментарии • 146

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 20 часов назад +10

    Akabambe mtengeni mai kaliati pa vice pls pls chonde chipanichi chayima ndi mayiyu nthawi yaitali

    • @MaureenMollen
      @MaureenMollen 20 часов назад

      Ndipo Mai kaliat she's a strong woman.

    • @JackMizimbe
      @JackMizimbe 2 часа назад

      😊😊😅😊😊😊😊😊q

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 22 часа назад +5

    INE NGATI M MALAWI NDAPHUNZILA ZEDI UTM yapanga Exactly imene Ili Democracy. Ndipo Chipani Ichi chikapitiliza Bwino ndi Mngwiriza kudinda Mfundo pa ground Tsikulina Chiyendetsa Boma this is real Democracy Very Good UTM. Chinsinsi Mukamanena zo bwezeletsa Dziko Yambani kupanga Zokoma Kuma member onse Akamapita Mtundu worse Wa Malawi Anthu aziloza kuti YES these Will Deliver, One of Exposing the Party moove
    Congratulations UTM We Are Following.

    • @ChisomoYosefe
      @ChisomoYosefe 22 часа назад +1

      @@johnnyirenda5848 exactly ndipo chidzalamuliradi

    • @DoreenMuhota
      @DoreenMuhota 22 часа назад

      Akabambe chonde musamuiwale Patricia kaliati 😢😢 u vp okhaa chonde

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 18 часов назад

      ​@@DoreenMuhotandipo shonde shonde strong woman kaliati

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 18 часов назад +2

    More fire 🔥 kalindo ena anyera manyi ziliko 2025 uyo woooyeee❤❤❤❤

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku 6 часов назад +1

    Bon Lero ndiye wandisangalasa zeeeed kkkkkkkk kmano yakwiya ndi mizimu 😂😂😂😂😂😂

  • @ChisomoYosefe
    @ChisomoYosefe 23 часа назад +31

    Akabambe plz kaliati muonen u VP coz chipanichi wachisunga nthawi yaitali musamutaye ndithu

  • @HijkkFjkffj
    @HijkkFjkffj 18 часов назад +3

    🤣🤣🤣🤣Conena cagwera nkati inuo Bon Kalindo inuo ndi 1 ndipo mumandivetsa kukoma Mmalawi muno💞💞💞✨✨✨✨

  • @abcdefghichgvhbffjbv
    @abcdefghichgvhbffjbv 20 часов назад +1

    wayankhula za nzeru kwabasi.Chonde mai Kaliati osawasiya.She has been loyal enough.

  • @chifundobuledi
    @chifundobuledi 21 час назад +1

    Musathe mawu a kalindo, simukudziwa chobwera mawa, mwini chipani ndi kaliati, enawa mmmm ndalama zomwezo

  • @Imrandaniel683
    @Imrandaniel683 2 часа назад

    Koma kungomutaya kweni nanenso utm ndituluka iya 😊😊😊

  • @TesefayeAdise
    @TesefayeAdise 48 минут назад

    Kkkkkk bon kalindo amandisangalasa koma deriket alibe chisoni 😂😂

  • @tamanikumposha3908
    @tamanikumposha3908 15 часов назад +4

    Bwana kabambe mayi kaliyati musayiwale plz

  • @JamiraMzungu
    @JamiraMzungu 22 часа назад

    Koma akangomusiya kaliyati ndiye kuti dzikodi lilibe chikondi koma akalindo mupole moto komabe mumkanena ndithu ❤

  • @Esa-u3t
    @Esa-u3t 6 часов назад

    ABWANA KABAMBE PLEASE OSAMUTSIA MAI KALIATI PLEASE😢 PA VP CHONDEEEE IFE TILIPAMBUYO PANU.....🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @hanifazuwaja1300
    @hanifazuwaja1300 14 часов назад +2

    Akweni asawasiye ayende nawo limodzi achisunga chipanichi muyende nawo limodzi ku utm

  • @AngelaGraysham
    @AngelaGraysham 20 часов назад +5

    Kabambe woyee uku ndiye kusankha mwa nzelu UTM my vote

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji 18 часов назад

    Well said Mai kaliate ndi Newton Kambala osakwiya

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 20 часов назад +4

    Kalindo kkkkkkkkk ulilisa kaliyati chifukwa akaliyati mwano kwambiri kuderera

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 22 часа назад +1

    Mulungu simunthu, next year UTM will rule the country believe me, kampen yakabambe achite sitikumudziwa 😂

  • @PatrickKazilala
    @PatrickKazilala 20 часов назад +3

    Asomva amenewo kupusa mungamuthamangitse manganya

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 20 часов назад +1

    Kalindo yoweee lero lokha ndikunena Kuti watokota zazeru

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 21 час назад +1

    😂😂😂😂😂 deligate mmmmm ndilibe mau pano munthu kumawina 21,28 ai zikom deligate iweyo anakonza

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 18 часов назад

      Kodi delegate mkanyama kanji 😂😂😂😂😂😂 koma mkoyipa kanyama kameneko

  • @ZainabHajj-q9d
    @ZainabHajj-q9d 17 часов назад +1

    😂😂😂ķuseka kwa bwanji uku😂😂😂😂

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja 15 часов назад

    Ubwino wake ife tinagwilizana kuti tiike Kabambe as president ife zomwe tinagwilizana zatheka ENANU simukudziwa kanthu even kweni knows this and Ali free minded

  • @RuthKaledzera
    @RuthKaledzera 13 часов назад

    Mai kaliyati aganizilidwe coz chipanichi ndiye achigwila mosanama

  • @LauraNtala
    @LauraNtala 21 час назад +1

    Deligate ndi munthu owopsya hvy eish !!!!!

  • @EmmanuelHarrisonTembo-k4t
    @EmmanuelHarrisonTembo-k4t 20 часов назад

    Dr kabambe osamutaya mai kaliati,wasunga chipani cha UTM

  • @BesterWilliam-y3y
    @BesterWilliam-y3y 19 часов назад

    Katundu wathu uyu🎉

  • @AnnieChipofya
    @AnnieChipofya 23 часа назад +4

    Kaliyati asakhaleso paudindo Ali ndi pakamwa

  • @jamesFoster-dx4ur
    @jamesFoster-dx4ur 21 час назад +1

    Delegate angakuphe half past 12 ndithu eeeee kkkkk

  • @Lipengabuildingconstruction
    @Lipengabuildingconstruction 14 часов назад +1

    Zoona bwana

  • @Chikumbutsomwale-to1qz
    @Chikumbutsomwale-to1qz 18 часов назад +1

    Iwetu umatumidwa ndi a DPP adyere kaye amenewo akukupatsa zambiri jama yawo bora zitsakutsamwe.

  • @SophieShawa
    @SophieShawa 22 часа назад

    Esh kalindo mmmmm anakoza lne mau athela mkati 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @YohaneStevenMhone
    @YohaneStevenMhone 15 часов назад

    Ngakhaleso masankho a general election.Wina aliyense alinaye kale mmutu mwake ndyeno zoperekapereka ndalamazo ku anthu mzalila ngati momwe zawachitikila azanuwa. Ma twenty million+ alowa mmanzi ndyeno kwasala kt tmve kut komwe mnakongolako aktengeran kkhot

  • @jarraeohll.s.bwanali1537
    @jarraeohll.s.bwanali1537 22 часа назад +1

    Moti anthunu simukudziwa kuti inali plan kale kuti Kabambe alamulire?

    • @PAULMOSES-y3e
      @PAULMOSES-y3e 21 час назад

      It was a plan indeed coz iwo samafuna usi komanso ntunbuka

  • @AngelineDumha-ec5le
    @AngelineDumha-ec5le 16 часов назад

    Kaliati alibe ntchito ndi mayi otsokoneza kwambiri leave Kabambe alone anthu asankha kale vp

  • @nelsonkholomana1909
    @nelsonkholomana1909 13 часов назад

    Chonde mai Kaliati musamutaye chipanichi wachigwila bwino kwanthawi yaitali

  • @TinaSaeed-t7x
    @TinaSaeed-t7x 16 часов назад

    Kma kalindo muwakomola anthu kkkk

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 19 часов назад

    Mai Kaliati Vp fukwa she's the one who introduced Kabambe to delegates,she Baby seated Kabambe all way longkomaso it was a move kuti apange nawo compete awabalalise anthu cholinga awine kabambe iwowo vice president,muonaso

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa 22 часа назад

    Kkkkk koma chakwera mumuuze kuti ph7ziro ndiili

  • @80yami
    @80yami 20 часов назад

    Ishiiiii kumvetsa chisoni UTM

  • @AndrewCosmasmpama
    @AndrewCosmasmpama 22 часа назад +1

    Convention imeneyi taphunzira zinthu zambiri panopa a Malawi akungoima pa chilungamo

  • @GoodsonMtambo
    @GoodsonMtambo 22 часа назад

    Umutenge Patricia kaliat akhale running ment wako upanga bwino

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 23 часа назад +3

    Kkkkkkk the DC number One kkkkk

  • @YohaneStevenMhone
    @YohaneStevenMhone 15 часов назад

    Mzatiuza ndnuso akalindo kt ena awatengera kukhot kamba kolephera kubweza ngongole yomwe agawira ma delegates(akalindo mphesa azanu nd BP

  • @YusufJames-f5f
    @YusufJames-f5f 23 часа назад +2

    😢😢😢ok mwaveka

  • @PatricePhiri-r3w
    @PatricePhiri-r3w 23 часа назад

    Amakangana okhaokha nde kuwaona amene watenge udindowo

  • @HamzahBenson
    @HamzahBenson 22 часа назад

    Eeee ndale ndi njuga. Koma akaliati asamusiye chifukwa ndi munthu olimba mtima

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 20 часов назад

    Wina wake mavote Ake ngat Zaka zanga 😂😂😂😂

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 21 час назад

    😂😂😂😂😂😂 kalindo iwe ase 😅😅😅

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa 16 часов назад

    Mtengeni kaliat akhale vp plz plz

  • @BubaAubi-m3l
    @BubaAubi-m3l 12 часов назад

    Kalindo lnuyo mulungu anankotsa lnuyo umakwana

  • @PatrickKazilala
    @PatrickKazilala 20 часов назад +1

    Zovuta kwabasi mumayesa manganya wamasewera eti!!

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze 22 часа назад

    Kma kaliyati asamusiye chonde cfukwa chpani chija wachisung ndiyeyo plz

  • @PatrickKazilala
    @PatrickKazilala 20 часов назад

    He he he he de! Kaliati

  • @GribetaBongis
    @GribetaBongis 22 часа назад

    Likhale phunziro kwa zipani zonse pachisankho chikubwerachi chifukwa delegate ndi ooopsa

  • @mirriamphiri-ln2lk
    @mirriamphiri-ln2lk 21 час назад

    UTM my vote next year

  • @PatrickKazilala
    @PatrickKazilala 20 часов назад +1

    Kodi secretary mwatenga mpandowanji

  • @davieabel5631
    @davieabel5631 22 часа назад

    Kabambe please kaliyati usamusiye game ndimene ija kusiyadi amene uja athu sabwerako

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 23 часа назад +4

    This universe and the earth will.remain but the creation will be vanished so be kind to everyone may good Lord bless us all

  • @lindadzaoneni
    @lindadzaoneni 22 часа назад +1

    Deligate ujayo😂

  • @JaneHunga
    @JaneHunga 21 час назад

    Chonena chagwera mkati😮

  • @RebeccaKudimba
    @RebeccaKudimba 23 часа назад +1

    Kkkkkkkk DC umakwana aise

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb 23 часа назад +3

    Kabambe usamutaye kaliyati wayezesa kusunga chinichi mumuike akhale VP or mzimu wachilima uzakodwa

  • @planmalawi-sm2cw
    @planmalawi-sm2cw 23 часа назад +4

    Kabambe mutenge kaliati pa VP chifukwa chipanichi wachisunga ndi iyeyu

  • @EstherMalewela-d8r
    @EstherMalewela-d8r 22 часа назад

    Koma iwe ndi one 😂😂😂

  • @PiliranChimalizen
    @PiliranChimalizen 10 часов назад

    Kkkk osaitsula dpp et kkkk

  • @BesterWilliam-y3y
    @BesterWilliam-y3y 19 часов назад

    Wamisala anaona khondo 😅😅😅😅

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 22 часа назад

    Usi sanakawina or anakapita ku conversation anawona kuti angozivuta

  • @samsonmisomali6799
    @samsonmisomali6799 15 часов назад

    😂😂😂Aaaa winnie

  • @StaffordNgoleka
    @StaffordNgoleka 23 часа назад +1

    😂😂😂 akt chalakwe

  • @PiqueShafik
    @PiqueShafik 17 часов назад

    Musical musician musicians

  • @marthakamanga8879
    @marthakamanga8879 22 часа назад

    Deligate simunthu wambatu😂😂😂😂

  • @alekaphiri6017
    @alekaphiri6017 13 часов назад

    Delegate wa UTM waposa delegate aliyense eeeeee

  • @IreenMwachande
    @IreenMwachande 21 час назад

    Akabambe mukumbukeni mai kaliati

  • @kingsleyChisenga-i8g
    @kingsleyChisenga-i8g 18 часов назад +1

    Kkkk koma ichi

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 17 часов назад

    Koma Bon kalindo 😂😂😂

  • @FidesChandama
    @FidesChandama 23 часа назад

    Zowona zeni zeni mukunenazo anthu awa asawataye zangovuta kuluza koma nanga titani musakhumudwe

  • @kapitowiskies432
    @kapitowiskies432 23 часа назад

    Koooooooooooma kalindo upha munthu

  • @AlexanderBilliat
    @AlexanderBilliat 22 часа назад

    Kulankhula mophuza nyoo ulibe ulemu ayi kkkkkkk

  • @MadalitsoSalanje-e1h
    @MadalitsoSalanje-e1h 16 часов назад

    Nkhalidwe ndi chuma

  • @DANIELSimwaba-f5p
    @DANIELSimwaba-f5p 20 часов назад

    Kalindo ying'alule mwana wa may

  • @HappyBanda-g2t
    @HappyBanda-g2t 18 часов назад

    Ulendo waku DPP UTM ndi DPP pano

  • @MadalitsoSalanje-e1h
    @MadalitsoSalanje-e1h 16 часов назад

    Ili likhale mphudzilo kwa athu ena

  • @TadalaBirsonkanjanga
    @TadalaBirsonkanjanga 21 час назад

    Mutenge kaliyati chonde chonde

  • @petrosmunthali5562
    @petrosmunthali5562 22 часа назад

    Mukamakokana chingwe chikaduka nonse mmagwa

  • @PatricePhiri-r3w
    @PatricePhiri-r3w 23 часа назад

    Km Mr kalindo iiiiiiiiiiiiiii kkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkk

  • @MadaMpaya
    @MadaMpaya 20 часов назад

    Deliget udyayo😂😂😂😂😂

  • @Maxwell-b6q
    @Maxwell-b6q 22 часа назад

    Malangizo omveka bwino kwambili kupita ku utm, mafuwa akale amagwila bwino pophikila. The DCccccccc

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 19 часов назад

    Kodi njawala wawina!?

  • @MicyThobve
    @MicyThobve 19 часов назад

    Haye haye

  • @chimwemwebanda9939
    @chimwemwebanda9939 23 часа назад

    Koma iwe😂😂😂😂

  • @marychavula698
    @marychavula698 19 часов назад

    Koma winiko

  • @collengoma6542
    @collengoma6542 22 часа назад

    machine okha ayi sakufunika

  • @ObvinessKBanda
    @ObvinessKBanda 20 часов назад

    Kusankha kwa bwino kwambiri

  • @lyfordpreciousloti2989
    @lyfordpreciousloti2989 22 часа назад

    Powerful

  • @MenasKaliati
    @MenasKaliati 22 часа назад

    Kom iwe ase kkkkk

  • @Mayamikophiri-pg7zt
    @Mayamikophiri-pg7zt 22 часа назад

    Deligate sakalowa kumwamba ndithu iiii

  • @O1d2a3l4a5
    @O1d2a3l4a5 18 часов назад

    😅😅😅 soka mwaiwe unasamba mankhwala 😂😂😂

  • @LindahBandah
    @LindahBandah 18 часов назад

    Deliget ola moto

  • @ruthkaipa1457
    @ruthkaipa1457 22 часа назад

    Koma deli😂