Was Kamuzu Banda a Colonial Imposter?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 ноя 2024

Комментарии • 111

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Год назад +4

    You're doing a good work bro.... keep updating us, please we need new updates on Ukraine War ...

  • @andersonmaster8055
    @andersonmaster8055 Год назад +3

    Ulemu wanu boss, mumayitha timadziwako zambili through your channel

    • @charlesnankumba9991
      @charlesnankumba9991 Год назад

      You are a terrible liar. Find better things to tell Malawians than your big lies from hell. Shame on you and your pay masters. Do you think we are dunderheads to believe your biased and false stories?

  • @ponjekananila6636
    @ponjekananila6636 Год назад +3

    I like these kind of your uploads,osati zinazi za tonse alliance.go deeper bro,Kamuzutu chinali chigawenga 🥺

  • @SamuelNandolo-nc2mo
    @SamuelNandolo-nc2mo Год назад +1

    Salute brother for the update

  • @johnmasangano890
    @johnmasangano890 Год назад +3

    Ngati Malawi umphawi unayamba because of this man

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Год назад

    NO 1bro kamuzud sanali Zika that's why ulamulilowake unali wakhaza KOMA BG TATIFUFUZILENISO ANAMANDWA AKUTILAMULILA PANOWA KUTI NDIZIKASO ZIMENEZII ?????

  • @alfredbanda886
    @alfredbanda886 Год назад +3

    Mbuziiiii za MCP motsogozedwa Ndi Bulutu wawo chakwela mamina thoooooo

  • @ibroxmedia
    @ibroxmedia Год назад +2

    Short story. A dark skinned Kamuzu Banda left Nyasaland in 1915. Came back 43 years after as a coloured/mixed race man who could barely speak his native language.

  • @michellemlalazi7436
    @michellemlalazi7436 Год назад +5

    This is true story for all malawian people thanks for letting us know

  • @AliMagumbo
    @AliMagumbo 2 месяца назад

    Thank you so much Big

  • @ruthtimothy9583
    @ruthtimothy9583 Год назад

    Great job big 🔥🔥💪💪

  • @omegasheibamussa3900
    @omegasheibamussa3900 10 месяцев назад +1

    Alihamdulillah a Malawi ndinzisilu kwambili

  • @Lawrentlboy
    @Lawrentlboy Год назад +6

    I like this guy.he is doing a great job.

  • @jelezulu4707
    @jelezulu4707 Год назад +2

    Akulu inu nga bodza ndipo nkhani yanu yonse ndiyabodza , yes anthu amatha
    Kuloledwa kukhala ndimalo ku Ghana zaka za 1953, kodi iweyo ndiwe muyao komanso mulomwe ungadziwe bwanji zochitika kwa achewa ?

  • @tafadzwamuvhami5841
    @tafadzwamuvhami5841 Месяц назад

    BAKILI TV, I am watching from Zimbabwe. Kindly send me link to video about Worst evil popes. I watched it but cant find it anymore. Please

  • @bishopphiri9286
    @bishopphiri9286 Год назад

    Keep doing great job

  • @salomegondwe1322
    @salomegondwe1322 Год назад +2

    This narrator is a researcher. He investigates and report according to the evidence. Kamuzu was not a malawian indeed

  • @superiormoses4802
    @superiormoses4802 Год назад +2

    Bravo bro mmakwana💪💪

  • @zombagrecian8543
    @zombagrecian8543 Год назад +1

    Good job big man

  • @EllinWatson
    @EllinWatson 9 дней назад

    Nkhani yoona ndiyakuti Kamuzu sanali Malawian amacita kugula mudzi Ku kasunguko. Kodi mwana wa zaka 13 angayende pansi kupita Ku south Africa? Inu tamvani izi, zoona ndizakuti Kodi since anali muno Malawi muno bwanji zamai Wace sizidziwika bwino kunoko

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Год назад +1

    BIG 👍

  • @silajisidze5319
    @silajisidze5319 Год назад

    Sarute big ine mmandisangalasa ndikamanvela,
    Koma kukhla ngat munapanga dismiss nkhani y muhhamad ija coz zindimaipeza ndikamaifuna Gina tipangileni update

  • @RichardGeorge-lg1id
    @RichardGeorge-lg1id 10 месяцев назад

    Anari munthu oipa kwambiri😢

  • @kumbukanismith1461
    @kumbukanismith1461 Год назад +1

    He was a Malawian. osamatchukisa mbiri ya bodza a malawi.

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 7 месяцев назад

    Ntchito yabwino makili muluzi tv

  • @kenslinchikwenga1277
    @kenslinchikwenga1277 Год назад +4

    Kamuzu adali oyipa mtima

    • @Syakinongwa
      @Syakinongwa Год назад

      Mfiti. Chakupha anthu osalakwa

  • @StanelyMangani
    @StanelyMangani 8 месяцев назад

    Still listening

  • @michellemlalazi7436
    @michellemlalazi7436 Год назад +2

    Kamuzu was a devil may his soul be in Gehena

  • @owennyangu360
    @owennyangu360 Год назад +1

    Zopusa zitipindulila chani zimenezi pakuti munthu adamwalira kare.

    • @amisichiphiri8227
      @amisichiphiri8227 Год назад

      Chifukwa chake sudziwa history, kukonda kutsutsa basi.history amakamba za munthu wamoyo yokha?

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm 6 месяцев назад

      Nawe achitsiru usatinyatse sukuva kut ndi history bwanji kusowa makhutu ngadwa iwe

  • @samsfrankle4921
    @samsfrankle4921 Год назад

    Salute

  • @emmanuelthom5793
    @emmanuelthom5793 Год назад +1

    Deep history

  • @hassanhappy9300
    @hassanhappy9300 Год назад

    Following

  • @enockthomasloyidi4914
    @enockthomasloyidi4914 Год назад +1

    👍👍

  • @frankntembenuzah2884
    @frankntembenuzah2884 Год назад +2

    Kamuzu anali phwala

  • @sheila5812
    @sheila5812 Год назад

    Chibodza,Kamuzu anali waku Malawi kuno.

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel 4 месяца назад

    Ghanaian 😢😢we sleep too much i wonder how he was very dangerous to Malawians mmxie

  • @hamdanmasuku4800
    @hamdanmasuku4800 Год назад +1

    Big inu mumakwana pls ulendo wna mutifufudzile mbiri ya #smith_jaden fana wa kwa American uja

  • @petermitambo9257
    @petermitambo9257 Год назад

    Koma kamuzu ameneyu ukhla masiku wano eehee ameneyu akadafinyidwa. Ndipo munthu Meneyi. Asaaaa. Nsilibe nae mawu koma amangobweletsa ululu basi. Koma i don't evn know kut why some people are still supporting him.

  • @kondwanichiweza4101
    @kondwanichiweza4101 Год назад

    za ziii.
    you cant change history

  • @alinafesalima5597
    @alinafesalima5597 Год назад

    Keep up bro,komano tatifufuzireni nkhani ya John chilembwe kuti ndi zoona zoti sanaphedwe koma anathawila ku america? Plz tisakireni

  • @AliMagumbo
    @AliMagumbo 2 месяца назад

    Zoona abwana

  • @isaacfesani2357
    @isaacfesani2357 Год назад

    Thanks for uploading

  • @bkelly3053
    @bkelly3053 Год назад

    Here we are 💥♥️♥️

  • @issufojoao5607
    @issufojoao5607 Год назад +1

    100%sure

  • @kenslinchikwenga1277
    @kenslinchikwenga1277 Год назад

    Mcp inamatikwila kwambiri chifukwa choona chake amachidziwa,
    Tsiku lina choonadi chizadziwika.

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w 10 дней назад

    Izi ndzoona

  • @WisemanCathy
    @WisemanCathy Месяц назад

    True story

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Год назад

    uyu simmalawi chilungamo ndichomwe akunena captain yu

  • @sandraissah1161
    @sandraissah1161 Год назад +1

    Dr. Banda was a true statesman...always proud of him

  • @AliMagumbo
    @AliMagumbo 2 месяца назад +1

    Kamuzu inali mbuzi yamuthu

  • @victormaulika6523
    @victormaulika6523 Год назад

    Mumatisegula maso akulu

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Год назад

    Ku Israel kuli mpungwepungwe ,tithandizeni kudziwa zambiri za zomwe zikuchitika kumeneko

  • @gelitofernandojose6654
    @gelitofernandojose6654 Год назад

    Koma Big nkhani yaku Ucrânia ili pati pano ? Timakunyadilani Big.

  • @SankhaniHarawaMtungambera
    @SankhaniHarawaMtungambera 11 месяцев назад

    We are good at other African history than our own land it's so bad, genuinely Banda wasn't aMalawian

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 Год назад

    🤝🤝♥️♥️👍💪

  • @FatimahKaliyes
    @FatimahKaliyes Год назад

    Chifukwa chake chinali chingawe chika mudzuchi

  • @blessingsmaulid8776
    @blessingsmaulid8776 Год назад

    Ulemu

  • @habibuburhani6688
    @habibuburhani6688 Год назад

    Rero ndine woyamba kuwonela

  • @janenkhoma6447
    @janenkhoma6447 Год назад

    Ukuitha

  • @abumussah9766
    @abumussah9766 Год назад

    Hmm kamuzu was bad guy

  • @kelzkelz4133
    @kelzkelz4133 Год назад +1

    This is false History,Visit Kasungu your books are misleading you and quench your a hatred for Kamuzu

  • @Nilakay07
    @Nilakay07 Год назад

    Kamuzu anali dolo

  • @Malani41
    @Malani41 Год назад +9

    There are videos of Kamuzu publicly speaking Tumbuka than most people. No Ghanaian can pull that off even after leaving in Malawi for a 100 years. Look that up where he was telling pastors how to pronounce words and expressions. There are also public videos where Kamuzu speaks fluent chewa. I respect your channel because you bring a lot of illuminating and interesting political stuff concerning Malawi but sometimes you are completely off dude. You seem to be obsessed with Kamuzu for all the wrong reasons.

    • @bakilimuluzitv3371
      @bakilimuluzitv3371  Год назад +12

      Kamuzu was reading tumbuka and even Chichewa. But he never spoke for himself. We have seen Sir Gyln Jones reading fluently Chichewa at Domasi teachers college but that doesn't mean he was speaking. Even yourself, you can read Swahili or Bemba language but that does not mean you know how to speak. Kamuzu Banda has never used to speak chichewa like the way we used to; but the truth was that we saw him reading tumbuka and chichewa in some govt functions.

    • @lucaslumbani2771
      @lucaslumbani2771 Год назад +1

      @@bakilimuluzitv3371 fact

    • @jelezulu4707
      @jelezulu4707 Год назад

      @@bakilimuluzitv3371 akulu mukungofuna kumapanga ndalama pa RUclips mudzina la kamuzu nkhani yonse mwafotokoza ndi yabodza ndipo ilibepo umboni

    • @bakilimuluzitv3371
      @bakilimuluzitv3371  Год назад +6

      @@jelezulu4707 tell me, ndi zabodza motani? Ndakuuza mabukhu, ndakuuza monse mmene zinayambira; ndakutchuliranso mayina a anthu amene adapanga claim kuti Kamuzu was a foreigner. Ndie ukamati ndi bodza ukutanthauza chani poti nanenso am just following the event of the past?

    • @molicieeosama8877
      @molicieeosama8877 Год назад +1

      Inu ngakhale zowelengazo akamawelenga sizim'kaveka zowerenga zakezo. Osamamukila kumbuyo kachidazi

  • @jelezulu4707
    @jelezulu4707 Год назад +2

    Hahaha bakha iwe, palibepo umboni wakut kamuzu Banda anali wa Ghana ndipo kulibeko amene anachoka ku Ghana ndikumati ndi wa chibale wa kamuzu Banda, pathako pamako sasamba iwe.... history yake ya bodzayo?

    • @giftbanda8027
      @giftbanda8027 Год назад

      Chitsiru iwe ngat sizinakusangalatse ukanangosiya osat uzinyoza muthu did he force u to listen or comment???? Ulibe mtima ofuna kuphunzira ndwe kape usazapangeso comment

    • @jelezulu4707
      @jelezulu4707 Год назад

      @@giftbanda8027 ndikaphuzile history yake ya bodzayi , manyi ako wamva ? Iweyo ndiwe mulomwe kaya mu yao ndie zochitikwa kwa achewa ungazidziwe?

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm 6 месяцев назад

      Mbuzi iwe palibe chomwe ukuziwa galu wachabe chabe ndichimfukwa chake ukuvutika kusapota MCP nyama yapatumbo pakopo galuiwe

  • @jelezulu4707
    @jelezulu4707 Год назад +1

    Kamuzu banda was true malawian, some of you uneducated fools claim that kamuzu Bandah came from Ghana some say he was American but truth it's that nobody came from Ghana or USA claim that he's/she's related to kamuzu banda ,,kamuzu Banda don't have relatives in Ghana or USA stop spreading fake news..it's not even truth to say that kamuzu Bandah spoke Ghanaian language..yes in 1950,s foreigners were allowed to buy land in Ghana..many people Sierra Leone , Liberia and ivory coast used to buy land in Ghana..,zaka zomwe mukunenazi ndi zaka zomwe maiko aku Africa anayamba kudzilamulira paokha ndipo Ghana linali dziko loyamba kukhala independent , lodzilamulira palokha ..it's not even true to say that kamuzu Bandah bought relatives in kasungu .,iweyo unalipo pomwe kamuzu ankagula anthu ku kasungu kuti anali abale ake ? Chief mwase anakakumana ndi kamuzu banda ku England ndipo anamuitana kuti abwelele ku nyasaland.

    • @greenedkalichero4528
      @greenedkalichero4528 Год назад

      Iwe wabodza history yakoyi kataye kuchimbudzi, ubwere ndikuyimbire nyimbo yomwe kamuzu amakonda kuyimba mu nchiyankhulo cha chichewa. Kamuzu anali wa kumalawi kuno koma moyo wake unali wama principles samafuna zachibwana ndipo dziko ili amkalikonda komaso anthu ife, 4 example ndinamuonako ine akukalowa munda wa chimanga kukaona mmera atavala jombo, izi amazichita every seasons ndi president utiso anapangako zimenezo.lero ndikuwuze uzinamiza ana anzako amma 1995 mpaka pano ife ayi, wapitako misonkhano ingati ya kamuzu iwe? Ndipo usadzayelekezeso kutamandila atsamunda mizimu ya azigogo athu idzakukwiyira seriously.

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm 6 месяцев назад

      Nanga iwey unalipo pamene mapwala kamudzuyo akagula Malo ku Ghana kwakoko

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm 6 месяцев назад

      Ndichimfukwa chake ukutsuzika paka pano muphunomo mwangozaza mamina oka oka iyeyo ngat anali Malawi bwanji akapanga nkhaza zotero

  • @JaneDzanjalimodzi-o4k
    @JaneDzanjalimodzi-o4k 11 дней назад

    The story is not true. Please make time to do proper investigation
    Write a true story even if you hate this man. Be properly informed.
    You are lying you hate Kamuzu.

  • @bornfacephiri
    @bornfacephiri Год назад

    Ulemu wanu pitilizani utsakula mitu wanthu

  • @thegreens9075
    @thegreens9075 Год назад

    I don't buy the story.

  • @alexanderchingati-phiri1172
    @alexanderchingati-phiri1172 Год назад +3

    Typical lies made by Bakili Muluzi TV. Once you become a member of a royal family, you become protected. I know every member of the president family, but since ascending to power, I have never been able to see them, this is normal.
    Kamuzu was a doctor in Scotland, he then moved to Ghana on his way to Malawi. He was hosted by Kwame Nkrumah. Hence why he was living in Ghana. He was waiting for the right time to move to Malawi. Kamuzu was invited to come home by the Late Orton Chirwa, Vera Chirwa is still alive and has spoken so many times about Kamuzu. The information you are providing is FAKE. RUBBISH.

    • @africulturetv6498
      @africulturetv6498 Год назад +1

      Why he was failing to speak Chewa we have see Peter and bingu stayed out of Malawi but never forget there mother tongue

    • @mastersubiri7934
      @mastersubiri7934 Год назад

      @@africulturetv6498 true that bra Kamuzu was not a Malawian

  • @arthurtakondwantandika3306
    @arthurtakondwantandika3306 Год назад +1

    Fake news. Kamuzu to speak Fluent Chewa with the Kasungu accent. He also spoke fluent Tumbuka. When he met Samora Machel they greeted each other in a south African language. Stop spreading lies and misleading ignorant people

  • @kondwanichiweza4101
    @kondwanichiweza4101 Год назад

    Mbuzi ya reporter.
    You think people are foolish to be alive you.