LIMPOPO FM 05 JULY 2024 NDI COMRADE NTANYIWA, ANTHU OSAZIWIKA BWINO ANAPEZELEDWA MALO OGONA ALENDO

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 190

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 6 дней назад +20

    Koma ntanyiwa. Respect to you May the almighty God protect you wherever you will go

  • @LoydKamtedza
    @LoydKamtedza 6 дней назад +5

    Munandisangalasa yomweo chikangawa❤️❤️❤️🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦 osavera Riiimpopo ndi ndimakhala ngati ndataya kofunikila

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d 6 дней назад +3

    Salute comrade ntanyiwa,we love you and all Limpopo FM

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo 6 дней назад +3

    Limpopo FM live from south Africa Durban Pietermaritzburg auzeni zoona amenewa

  • @yusufbakali
    @yusufbakali 6 дней назад +4

    Panopa ine ndinasiya kuvela ma redio ena panopa ndili limpopo yokha basi

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 6 дней назад +2

    Ulemu wanu big mani mmatimvesa kukoma kwambili god bless you all the time ❤❤❤❤❤❤

  • @bytonalfred5844
    @bytonalfred5844 6 дней назад +2

    Ntanyiwa and your fellow comrades excellent well done, and keep it up for the battle you are fighting for Mw nation

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 6 дней назад +2

    Respect bwana Ntanyiwa 🔥🔥🔥

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 6 дней назад +4

    Ine mchifukwa chake ndinakana ntchito ya usilikali ndiyapolisi coz fans ya madepartiment amenewa ndiyombwambwana kwambiri, zigawenga zaku Israel and Ruanda zikungolowa mdziko mwathu ngat zikulowa mmanyumba mwawo, chomvesa chisoni kwambiri ndichoti asilikali ndi apolisi angoti vyooooo , vyooooo , osapangapo kanthu

  • @Jimmy-m4z
    @Jimmy-m4z 5 дней назад +1

    My brother your number one keep it up

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 6 дней назад +2

    Mtanyiwwa ulemu wanuw mulungu asinkuphasa moyyo wabwinno ndawi sonse I pray for you all the time amalawi tili phamoto 🤲🤲🤲🙏🙏🙏mulungu dalisani Malawi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 6 дней назад +2

    Agape khombe amandibowa bwanjii eish!, i dont feel good wen i heard names like agape, kumkuyu, chimwendo, chakwela, zikhale, yolamu, vetino phiri, pter kalaya, billy malata, layitoni mangochi, ben longwe too many to mention

  • @jamiajafali6619
    @jamiajafali6619 6 дней назад +2

    Antuwo zisilu kwabasi ...Antanyiwa gwilani nchito blo❤

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala 6 дней назад +2

    Chifukwa iyeyu..akupanga zinthu zomwe south African ikhoza kukwiya nanzo.zomwe zingaikidze miyoyo yanthu ife amalawi pa chiswe😢

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 6 дней назад +1

    Tikuziwa zambiri GUYS mmmm Limpopo FM ndikatundu number 1

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 6 дней назад +2

    Mtanyiwwa osawopha mulungu adalise inuyyo mulungu adalise inuyyo nosse

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r 6 дней назад +2

    Limpopo inabwera kuzakhala

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 6 дней назад +2

    May good God knows everything and palibe chingabisike Mulungu ateteze malawians

  • @user-uj9st8zp7v
    @user-uj9st8zp7v 6 дней назад +2

    Ndili pambuyo pako mtanyiwa

  • @ibrahimalex7137
    @ibrahimalex7137 6 дней назад +1

    Ulemu wanu from Limpopo south Africa 🇿🇦

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 6 дней назад +2

    Wailesi yokhayo yomwe ambiri akuikonda kunvera panopa

  • @lottiempata2487
    @lottiempata2487 6 дней назад +1

    God's good always Amen

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 6 дней назад +1

    Mulungu akuulura chinachilichonso ku dziko langa koma vuto dziko langa linasankha kusamva koma limamva china chake chitachitika...Ambuye athandize Malawi

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 6 дней назад +2

    Mulungu wayitenga nkhondo imeneyi kukhala yake ndipo palibe yemwe angamenyane ndi MULUNGU.
    OKHA OKHA A MCP AMENYANA NDIPONSO AWULULANA POSACHEDWAPA. IFE TINGOTI PHEEEEEE KUDIKIRA

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 6 дней назад +1

    Tafika ndithu kuzamvera our very own limpopo Fm

  • @LoydKamtedza
    @LoydKamtedza 6 дней назад +1

    Comrade ntanyiwa mulungu azikupasa moyo wautali azikusogolera ndipo mupitiliza kuti pasila choona chamalawi Allah azikuteteza kulikose ukuyenda Limpopo FM ndimanyoya nayo ndikamavera

  • @HanaNyasulu
    @HanaNyasulu 6 дней назад +1

    Mumatiimirira acomrade timakunyadilani❤

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 6 дней назад +1

    I salute you comrade, you are genius

  • @charlesjimu6054
    @charlesjimu6054 6 дней назад +1

    God bless you ❤

  • @Angolnanjilayusufu
    @Angolnanjilayusufu 5 дней назад

    God bless you comrade

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x 6 дней назад

    Buddy Ntanyiwa ‼️
    Always proud of you ♥️🔥

  • @yusufbakali
    @yusufbakali 6 дней назад +1

    It's only champion station in limpopo fm

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN 6 дней назад +2

    Musalimbane ndi manyi woo aaaa muti asilikali alikuti??
    Agalu osaziwa ntchitowo? ntchito zigololo bas.
    ife tiibe ma ninja mmalawi muno aaaa

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 6 дней назад +1

    🔥🔥🔥🔥Ana Wachepa awa Zina amangoziyambadi...

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 6 дней назад +1

    Tinakusowan Mr Mtanyiwa muli bwanji kumeneko kuno tili bwino ndithu

  • @MaxwellManual
    @MaxwellManual 6 дней назад +4

    Chakwela sawina wapangila ena kapeni

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 6 дней назад +2

    boma la zitsiru apolice army chakwera mitumbo ya chamanu

  • @MervisYobe
    @MervisYobe 6 дней назад +2

    Chikangawa Ali madzi😅😅😅

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o 6 дней назад +1

    Mutitumizire zithunzi za anthu omwe agwidwa ku South Africa.

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 6 дней назад +2

    Mcp ikupanga zinthu zoopsyeza kwambiri ndipo zamdikwana mmmh

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 6 дней назад +1

    LIMPOPO FM PALIBESO IFE TINGOTI NYADU

  • @FaressPatel
    @FaressPatel 6 дней назад +2

    Kkkkkkkkkk yomwe mwaiputayo chakwera ikuphulikikani

  • @StevenFombe
    @StevenFombe 5 дней назад

    Even Tv,Radio stations in Malawi are getting lessons though they are silent bravo

  • @user-vw7tj2ss3l
    @user-vw7tj2ss3l 6 дней назад +1

    Yomwey gulu iwe

  • @user-iv4dj1pi3b
    @user-iv4dj1pi3b 6 дней назад +2

    Pangolin ..ntanyiwa ....

  • @charlesjimu6054
    @charlesjimu6054 6 дней назад +1

    Tchimo limayitana Lin,zache

  • @user-vw7tj2ss3l
    @user-vw7tj2ss3l 6 дней назад +1

    Yomwey galu iwe umakwan

  • @ThoccoKakowa
    @ThoccoKakowa 6 дней назад +1

    Osasiya kunena zowona

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel 6 дней назад +1

    Zigawenga zosadziw dziko akadziwe munthu ali kudimba zoon

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 6 дней назад +2

    Achita bwino 😂😂😂arirata😂😂

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 6 дней назад +1

    Guz Malawi ndiwatu if anyone ali okudzidwa ndikulephera kwa Chakwera tiyen paunsewu tonse pa 10 July

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 6 дней назад +1

    Zoonadi brother mtanyiwa ifetinapanga mistake kuvotera Chakwera ndigululake komano chakwera aziwekuti wasalandi madzi amodzi

  • @StellaCharles-dq8db
    @StellaCharles-dq8db 6 дней назад +1

    Mcp mulungu walange ndinthu ndipo apange kanthu mudzina layesu akutitenga ngat chisiru ndinthu

  • @AlinafeChimoto-pp7wp
    @AlinafeChimoto-pp7wp 6 дней назад +1

    Pa 10 akuchoka bas

  • @gifthara2460
    @gifthara2460 6 дней назад +1

    Koma braz mumakwana athawa a mcp

  • @SindawaPelekamoyo
    @SindawaPelekamoyo 6 дней назад

    Respect to you bro nthanyiwa keep the 🔥 buuuuuu

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x 6 дней назад +1

    Ndipo anapa chilima ndi ameneyo lelo chikuza mawu ndi iyeyo aziwona ndithu atule pasi udindo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 6 дней назад

    God bless you mr ntanyuwa ❤❤❤

  • @mikephiri4092
    @mikephiri4092 6 дней назад +1

    Amalawi let’s gather together and fight like our fell Kenya’s bakili tv and Limpopo fm thy are doing there parts ife tonse tikutani kapena yathu ija ya Ulemu???

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 6 дней назад +1

      Not ulemu as such bro, amalawife ndombwambwana kwambiri man, mtanyiwa and bakili muluzi tv alongside bon Kalindo are doing their part for sure

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 6 дней назад

    We need some more teachings brother man !!

  • @user-yi2fg1lh8x
    @user-yi2fg1lh8x 6 дней назад

    Be blessed

  • @philonampha
    @philonampha 6 дней назад +1

    27:11 ❤❤❤❤❤

  • @user-yu4np2wq4s
    @user-yu4np2wq4s 6 дней назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂musandikomole antanyiwa ine lero Koma kulizithuuuu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 6 дней назад +1

    Kodi agapeyu ndindani nanga tundu wanji wamunthu ku malawi kuno agalu kwabasi ndi MCP yawoyo

  • @PatrickMulangala-os4by
    @PatrickMulangala-os4by 6 дней назад +1

    Walemphela udindo

  • @ShafieIdrissah
    @ShafieIdrissah 6 дней назад +1

    Chakwera wamupa chilima kuvuna akhale president galu kwabas

  • @JefulyPesulo
    @JefulyPesulo 6 дней назад +1

    Mumakwana ntanyiwa

  • @PatrickMulangala-os4by
    @PatrickMulangala-os4by 6 дней назад

    Respect for you

  • @user-vl9se5bl9s
    @user-vl9se5bl9s 6 дней назад

    Limpopo FM is number one

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 6 дней назад +1

    Bambo mu mtanyiwa ulemu ndi wanu mulungu apitirize kukuyang'anirani

  • @EmanMiles
    @EmanMiles 6 дней назад

    🎉🎉🎉 to Limpopo FM

  • @ZondoChirwa
    @ZondoChirwa 6 дней назад

    Ntanyiwa more 🔥🔥🔥🔥🔥 fire

  • @LatiffKadyamawuseni
    @LatiffKadyamawuseni 6 дней назад

    Mumakwana ❤

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z 6 дней назад +1

    Koma athu aku mcp mulungu achitepo kathu

  • @CatherineNkhala
    @CatherineNkhala 6 дней назад

    Be protected sir

  • @ChiefJustin-cl8jl
    @ChiefJustin-cl8jl 6 дней назад

    Limpopo fm ❤

  • @LoveKhobiri
    @LoveKhobiri 5 дней назад

    God be with u brother

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 6 дней назад

    Ulemu wanu Comrade ❤

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili1362 6 дней назад

    Great Job Ntanyiwa

  • @MosesLackson-l4f
    @MosesLackson-l4f 6 дней назад

    Comrade umakwana bigup

  • @PetroJack
    @PetroJack 6 дней назад +1

    Limpopo ndi katundu uyu😂😂😂😂

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg 6 дней назад +1

    Eyetu ameneyo nde mulungu inuyo ngati mukukwanitsa kutseka anthu pakamwa ndindalama ndiomwewo opusa osusuka achina yudasi Ana anjoka inuuuuu
    Malawi mizimu yambiri ikuzunzika kusowa chisamaliro zinthu zinakwera kuli okalamba Ana amasiye nzipatala kundende ndi anthu onseee mdzikomu ofuna zabwino koma ayi zikuvuta kwacha mwagwetsa mwagwetsanso ma million mukukhonyolera m'matumba mwanu kukhutisa mimba zanu
    Nde pemphero la olira ovutika Mulungu samalisiya amayankha mwachangu nde anthu ayamba kugwidwawa nchiyambi chowululika zinsisi zanu
    I'm repeating all most each and every day kuti you will pay one by one
    I'm not just taking this is prophetic word
    Mulungu ndiokwiya nanuuuuuu anthu amagazi m'manja inu

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 6 дней назад +1

    Komatu ndiye nyama ya malemu Chilima mwasavuka nayo afiti inu muyaluka simunati akanyimbi

  • @marthablessings1314
    @marthablessings1314 6 дней назад

    Inde bwana wathu❤❤❤

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala 6 дней назад

    Ife kuno ku South Africa kungochotsedwa chifukwa Cha zomwe akupanga chakwela😢azaona konko ku Malawiko zomwe tizapange

  • @GeorgeChakuamba
    @GeorgeChakuamba 6 дней назад +2

    Auze zoona a Malawi iwe umakwana ndipo ndimachita kukuika PA Bluetooth kut maneba amve nawo kkkkkk

  • @user-vb5dh8ip6g
    @user-vb5dh8ip6g 6 дней назад

    Our channel Malawian channel we love you comrade together with your people ❤❤❤

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 6 дней назад

    Namu bwana mumata ❤

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 6 дней назад +1

    Koma a mcp dzikoli ndiye mwalipezelera bwanji pasana panu nonse a mcp ndi masapota anu nonse zitsiru za anthu inu

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 6 дней назад

      @@EdwardMathuwa Ndipo mbalame zokhazokha

  • @martinaustin-qm9yp
    @martinaustin-qm9yp 6 дней назад +1

    Kkk koma ntanyiwa usazamwalire uzangosowa mumat tsegula maso ndikutichosa khawa ndikavera mtima kut miyaaah

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 дней назад +1

    My channel ❤❤❤

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 6 дней назад

    South Africa ikangomuphulisa wagule uja basi, walowa mkati mwana wang'ona ameneyu

  • @JafaliLysani-nb6bq
    @JafaliLysani-nb6bq 6 дней назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 6 дней назад

    Chakwera woyeeeeeee! Mutu waima, ndipo a Malawi tisalole zopusa

  • @EsnartMalewa
    @EsnartMalewa 4 дня назад +2

    😂😂😂

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 6 дней назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 6 дней назад

    Amuchita bwino kumuthyola msagwadazo on top of dat mapwala ake , atilakwisapo apaa kafucheche ameneyuu eish

  • @user-mo5od8cy3n
    @user-mo5od8cy3n 6 дней назад

    No matter anyone to hate but the truth i talk.

  • @user-gq6nj6yo6f
    @user-gq6nj6yo6f 6 дней назад

    Yomweyo chikangawa

  • @MecyMalothi
    @MecyMalothi 5 дней назад

    Inuyotu mumakwana palibenso