Atsogoleri tikuyamikireni koma nkhani zanu simukumaliza mukaziyamba ngati mukunena kuti ntchito zomwe akugwira anthuwa ndi malipiro pa zomwe achita powotcha wa police ku Nsanje kutanthauza kuti anatumidwa ndi abomawo, ndiye a bomawo akuuzani chilungamo chotani? Inu mukadaulula zifukwa zomwe adamuwotchera wa police kuti womutumawo adziwe kuti abisala mmbatata musamangochulukisa kuseka ndi kamangoyimba nyimbo ayi, ifeyo timamvetsera ndi chidwi kuti nkhanga zaonanji tidziwe koma mumango nena molumpha lumpha ngati kuti zomwe mukuwulusa ndi zongopeka so please help us we love you
Mwaswela bwanji nonse amene mumamvela pa nkhanga zaona.ngati mulibwino dzikomo
Taswela bwino kainu kumeneko bas dzikomo kwambili
Mwaswela bwanji abale anga pa nkhanga zaona,ineyo kuno ndilibwino
More fire broo osaopaaaa kunena chilungamo.
Limpopo FM more fire
More fire 🔥
More fire Limpopo
More fire kt Buuuuuuu!!!
Also were waiting for bakili tv thanks you guys
Limpopo FM radio ndi one 🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪
Zoona koma lipopo mbambande
More fire no fear comrade go go go!!!!!!
Atsogoleri tikuyamikireni koma nkhani zanu simukumaliza mukaziyamba ngati mukunena kuti ntchito zomwe akugwira anthuwa ndi malipiro pa zomwe achita powotcha wa police ku Nsanje kutanthauza kuti anatumidwa ndi abomawo, ndiye a bomawo akuuzani chilungamo chotani? Inu mukadaulula zifukwa zomwe adamuwotchera wa police kuti womutumawo adziwe kuti abisala mmbatata musamangochulukisa kuseka ndi kamangoyimba nyimbo ayi, ifeyo timamvetsera ndi chidwi kuti nkhanga zaonanji tidziwe koma mumango nena molumpha lumpha ngati kuti zomwe mukuwulusa ndi zongopeka so please help us we love you
Ndipo message yomwe imasowa muno ndeiyiyi kkk kumatambasula bobo ngati muja apangila DC Kalindo, otherwise zikumavuta kuzitsatatu. Love you ❤❤
That's true muzimalizisa nkhanizo kut tiziziwa zoona zenizeni wr real love you mr Comrade
Iipopo fm mukutiimilira keep it up to
Mukutiyimirira kumred go go go km ndikufuna nyimboyi yoti chakwera watipweteka anayimba ND ndan
Ine ndili pheeeee vela limpopo fm
Mbambande nkhanga zaona❤️🔥
Mumatilankhulira mukukhonza ndithu Limpopo
Keep giving us updates
Live from south Africa
Muyaluka chaka chake ndi chino
Auzeni
Nice song
Tikuthokozeni ntciito ndi yayikulu mukugwila more fire mulungu aikepo zanja tione mphumulo mumalawi
Zana amayi asanka chifanti malunga ngati vice koma pano ndi opposite ndi zambiri zomwe amalankhula za boza
Online from Pretoria
Tiyenazoni ,ife tilipambuyopa tidziwe
Ndipo musasiye mukutisegula maso❤
Never give up
Lipopo mo faya
Antanyiwa ndakusowani
Sikuti nkuopa bill ya mkadzi ati nkukhwimila anamunamidza Kwa sing'anga akabiba mu toilet apenga a Vaya 😇🤣🤣🤣
Mwadza bwanji
timakunyadilila big man .mtiuzilekoso wa bakili Muluzi tv tawasowa mau ake😢😢😢 guys timakunyadilan
Yomweyo galu iwe Nankhumwa😅😅😅😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅
Limpopo fm moto buuuuuu
Apa ndiye mwangarula zenizeni😂😂😂
Zoona big man
Timanyadila Limpopo fm
Limpopo moto kuti buuu
Mtaniwa uma kwana
Timayikonda wayiresi imeneyi.
Umakwan iweyo
Osafoka osatopa osawopa
Bola bon kalindo ndi bakili mukuzi tv amafufuza mokuya kwambiri
Mumakwna alimpompo fm
Kkkkk koma eeeee
Mulungu azizikuteteza nthawi zonse.
❤ big up brother
Awa ndaboza awa
Uyu ngwa maboza saziwa kufufuza nkhani zoona
Ndizzkho zimenezo ife tikumudalira anatiuza kuti onse amu ndege amwalira zinali zoona
Ndikufuna kanyimbo Ako please send kamandivesa kukoma heavy ka nyimbo ka zisakho ako
Morefire
Timakudyadirani our comrade!!
😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅kwagwanji bambo
Kulonjedza nde analonjeza ndikalephela kusitha dzithu kwa dzaka wilili ndizatula pasi udndo Kodi pana pano sanavomeleza kuti alephela kukweza Malawi pano Malawi alipamoto kuposa alamulilo wa muthalika
Zomaotchazi zisiyike chifukwa tsiku lina mudzagwidwa ndiye tidzaona
Go deeper comrade, proud of you always 🔥🔥🔥🔥
Mumakwana bwana
Yah tamudziwa.....uja ali ndi bukula azibambo
Lipopo fm Palibeso ai
fire fire
dyimboyi iilibwinowo😂😂😂😂😂
Wanunkha malawi
Kkkkkkkkkkkk Sevethday
Eisj where are you brah Malawi first we're confused ryt niw so brah plz tell us the truth
Lovely song🎉🎉🎉
😂😂😂😂😂 Limpopo fm
Koma comrede indipha ndi phwete😂😂😂😂😂😂😂
kunoku moyo wake ndi osiphina omwewu basi. Malawi zikuoneka kut m'manja mwa atsamunda sitinachokemo ayi
Osaopa mulipa bill yanga 😂😂😂
Mundifunsilenso chipatala chakumangochi chimawotchedwa chakandichaka zikukhalabwanji?
Tilinawe limodzi limpopo Fm mumatiimilila
Koma ambuye kumwambako musatipitirire ku Malawi 😢😢😢
Akut anapengapo Misara kkkkkk amawona ngt amalawi angagwrinse ntchito Misara yakeyo
Limpopo fm ndimainyadila kwambli simabisa zigawenge 😂😂😂 more fire nkhanga zaona ife nde malawi olilawo
Mumakwana Limpopo mumatiimirira Ife a malawi potidziwitsa zonunkha za afisi a nkhaza awa tikudziwanao zambiri 😂😂😂
Kwan
Auze ngozi
Achimwene mumanikwana
Auzeni apite kumangochi aone
Osapa todze ndi amalawi fredom c_to_
Mulipo angt,
Opusa iwee ukusochelesa amalawi koma amalawi anapenya zidya drama za muthalikazo ife tikupitax chisogolo ndi mcp bas
Zikachitika timvera kwainu
avomele zavuta ayimikemaja
Kkkkkkkk 😂😂😂😂😂
😊
😂😂 amangonyera mplastic
Zamphanvu
Koma nyimbo zachuluka
Koma Patricia unaziyamba wenkha kkkkk
Osafooka osatopa osagonja
😂😂😂
😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Zifukule zose zidziwike❤
Network problem ashh
Limpopo fm moto buuuuuu
😂😂😂😂😂😂
Limpopo fm moto buuuuuu
Limpopo fm moto buuuuuu