A Thabo Chakaka Mupangitsa Manyazi Dziko La Malawi - Concerned Citizen
HTML-код
- Опубликовано: 6 июн 2024
- On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen says Attorney General Thabo Chakaka Nyirenda is embarrassing the country by giving the President poor legal advice.
Pa Nyasa VoiceBox, mzika yokhudzidwayi yati loya wamkulu wa boma Thabo Chakaka Nyirenda akuchititsa manyazi dziko popereka uphungu wolakwika pa zamalamulo kwa mtsogoleri wa dziko lino.
#malawi
Why did President Chajwera remove Dr chikosa Silungwe? Dr chikosa Silungwe is a competent lawyer who has had worked in the Malawi Government for long long time with vast experience but because he advised the government accordingly.
Mr Thumbo chajaja Nyirenda is an incompetent lawyer he occupied that seat because of political reasons and nothing else. somebody in the MCP had just favoured him yo become the Attorney General of the Malawi Government. Shame on you the president and his politically appointed Attorney General Thabo chajaja Nyirenda. He had never won cases in the Court of law for the RBM and his other clients before.
Therefore the President should now terminate his fake appointment on that post of the Attorney General and give it to the rightful competent lawyers with vast experience. He is as incompetent as the former DPP before Dr Kalua.
Abambo awa akukalipa zoon, Thabo Chakaka sakukwana kulangiza boma, moti akuwononga ndalama za boma pochita zonsezi. Amuchotsepo paudindo.
Chakwerayonso ndi mbuzi yamunthu galu
The problem is ,the president advises the attorney general
Chakwera, ana mchosa silungwe, kadaulo pazamalamulo, ankafuna oti aziba naye, komanso kuphinja Malawi
For sure
Zoona big
Mwapangitsa manyazi atumbuka anzanu ngati anthu osapita kusukilu mbuli zoyendetsa ziko.
Akulu awa ayakhula bwino kwambiri koma vuto lonse ndi Chakwela chifukwa sogoleri azikhala wadzelu ndiwonganiza bho
Chakaka nyirenda chisiru cha munthu akumusochelesa president nkhani ya streight forward then why wasting kumakatenga chileso. Are you pleasing president for wat?? Are you quolified?? Anakutenga kuti??.
Thabo is just an honour's degree holder.
Vuto NDI osewa amwene no sense chakwera 😊
Kulankhula kolankhuliratu 😅😅😅
Ulamuliro ochitisa manyazi mu mbiri ya southern Africa. Embassy ya dziko la kunja kupereka visa pomwe dziko lako kupereka fake passport dzoona?
Eeeeesh 💔💔
Ameneyi si attorney general ndi mbuzi kwabasi tsiku lina pofunika kuzamugenda miyala galu ameneyu
Dr Chakwela akanatha kumayendesa bwino ziko la Malawi koma vuto anthu omwe amuyandikila president ali ndi njiru kuti president azioneka oipa pomwe ndi wabwino.
Komaso ameneyu ndi wa mcp?
Akudxiwana wosewo alilimodxi mmesa adamusakha yekha chakwerayo
Awuze bwana uyu ndi waunsilu
Dzikoli laola kuposa nthawi ya Mutthalika izi ndiye zolopa zenizeni
Experience matters!!!!
They are busy breaking the law
More fire big man you are talking
This is powerful iwe thabo chakaka futsek
We want One Malawi One love, And this iz not Old Malawi, all the malawians know the truth people are crying and suffering Under the rule of MCP, and Chakwera the killer Man fake pastor panyini pa mawo both of them but what they should know is that, this is not Old Malawi, this cruel people must know justice of Malawian people One Day, and justice will come out One Day
Munthu iwe Mulungu akudalise pa masomphenya ako
Wauza bola anve koma ngati sanva tumizani Ina audio apange manyazi
Ndi a Nyirenda akuti wosaphuzira 😢
Athabo chakaka akalowelera bwanji za ku immigration popeza si office yawo komakuti ma guy aku immigration agenda galu mwini wagalu waoneka poti akupangira ma passport kuchipinda munya muona 2925 dpp boma wokavota ndi ife tatopa kulamulidwa ndi gule
Aaaaa MCP simamva zaanthu kuyambila kele mvuto mtima wachipani chimodzi chakaka alibe mvuto mvuto chakwela ndi MCP
Zoona amasureni athabo aaonjeza
Chomwe akuyankhula mkuluyu sindikukuchimvetsa. Who is to blame? Thabo chakaka ndi wabwino kwambiri. Koma anthu omwe amaunikiridwa ndiwo amene Ali ndi vuto. Ask ur president kuti Kodi AG amamuza chani?
Muthile moto kumene, mwana opusa kwambiri akuwona ngati,,zikoli lawyer alipo yekha mwana opusa kwambiri,,mukalipileni dziko akuliwononga ma guyz watu.
President ndiye akufuna munthu woti atsamulangize ndicho chifukwa anachotsa Chikosa Sulungwe poti akufuna zomwezo
Komanso apule anamuchotseranji lawyer oyamba uja, kuyika Thabo Chaka ka nyirendayo
He is after money not rules nao apresident aganize bwino za advisor wawo failing which mmmm
A Chembe intelligent yake ndiye yotibweresera nkhalambayo.
Osaona kuyendesa dziko mbuzi za anthu izi
Anaphunzira kuzunza anthu basi, asatana achabechabe awa
Pajatu anthunu munkati atumbuka ndiodzindikira kwambiri nanga izi nchiyani ? Anthuwa anasankhidwa ndi Chakwera ndipo amukhaulitsanso Chakwerayo nanga pamenepa a Chakwera zinthu ziwayendera ?
Chiwudzeni chikuwononga dalaa
Osewo ndi zisilu zidude zakuba
Onsewo nzitsiru retired abwelera bwanjinso mboma?
Muuzeni galu ameneyu ndi chitsilu
Noone is above the laws
Manyaka enieni adindo opanda nzeru
Mzowonad tiyamike kulankhula kwa abwanawa.
Ngati ogwira nthito zaboma ziri zitini ofoyira oyamba ndi omusankha .
Madala mwayankhula this is very powerful iwe chakaka futsek 😂
Akulitenga ngati dzikoli ndilambuyake
That Thabbo is the most failed is running away from the truth!
Zangokumana zisilu zokha zokha pamenepo ka awapange abwino kmaso cnanga ndi mbamva anakatani kubelako akubelako limozi ndi mcp 😂😂😂
NKHASA adayimba NYIMBO YONENA KUTI TINASAKHA ORAKWIKA izi lero zikuyikira uboni nyimba imeneyi ya PHUNGU JOSEPH NKHASA
NAWONSO ACHAKWERA NDI UMBULI WAWO AKUGOPITILIZA KUSAKHANSO ORAKWIKA ZOMVETSA CHISONI DZIKO LATHU
Ndiwesilu kwabas apage mayaz kumene puleziditi wo
Kamwana kameneka udindoo wamukulila
Anthu oputsa ,Koditu ine Ngati mmalawi mukamati anthu ambiri akupoto NDI ophunzira ine ndimaletsa Koma chomwe ndimadziwa ndichoti anthuwa amangolowetsana potengera kochokera tribelisim
Thabo Nyirenda ndi kape kwambiri
We need chikosa silungwe back
Ndipo chakwela tizamukumbukila osati ku zabwino ayi koma ku zowawa zomwe chakwela wativetsela kuwawa ndipo sitidzamuiwala
Thabo chakaka ndi Attorney general wa chakwera kalpana wamcp osati wa boma lamawi
Musamuchemerere mdalayu ndiwaganyu uyu.akukoma mkamwa akufuna 1kg ya sugar uyu
Musalimvane ndi Athabo, bwanji mukudusa m'mbali? Kweni kweni muli mbali iti inuyo Apule ndiwo chizete chotheratu inunso mwagudwa timawaxiwa omwe akutimenyera nkhondo tsekani chimbuzicho mukutinunkhitsa kuno
Chisilu cha munthu ichi kaya ndiwakuti munthu wopepela ngati ameneyi ....akuti pamenepa akufuna kusamgalasa president
Zosayenda
If we speak of incompetent means Razarus Chakwera is incompetent.
Nawe iwe chembe tamata kuchimbuzi kwakoko naweso ndiwe kape paja
Kumasiyanitsa Mlangizi wa boma ndi wa banja
Achoke
This guy he called himself atoney General is useless
Kodi munthu ameneyi anakamutenga kuti ......kungotengana zisilu zokhazokha
Zikozakuteka kuti ndi wa udf
Komadimtu Sona🤔
Auze anve
Ndinamva kuti ndi m'bale wawo wa a Chakwera uyu
Wa Monica chakwera cousin wake.
He is not suitable for apresident he must go back to be apastor
Chakwela ndi athabo chakwaka ndi 🐕🦺 kwambili
RUclips yaphweka kumalawi.
Ngakhale ku thyolo kumachoka Bingu komaso Peter koma umphawi osayamba agalu inu
Nanga zugwirizana bwanji ndi main nkhani yomwe ikukambidwa, mesa umphwawi wasefukira chifukwa Cha president wako ongodziwa kugwetsa ndalama ndi kuba moti azilimbikira kupanga zinthu zoti apeze forex
Zomwe zikuonongeka ndi zakuThyolo kapena dziko lonse? Tiyeni tidzuke aMalawi ndikusiya kaganizidwe kodana ndi anzathu
Chichosen pampandopo musazachiyikeso pa mpando uliose chimenecho aaa chandikwana msaname, and
Which pelezideti instead of president you talking about ,not we don't have a leader in malawi,I shall show you a really president of malawi in 2025!!!!
Im Garnet J K Phiri, im here to comment on this audio, mzika zokhumudwa they are100% right,to tell our gaverment muli mbuli zosaona zokha zokha paja amati osaona salondolelana njila munthu sungatenge masanzo ndikuwabwezelesa mmimba kachiwiri ,mukutenga munthu wa retired wosanzidwa put back in gaverment Achakwela mutual wanu umagwira bwino ntchito or you are just enforced by some .Nyirenda ,attorney,are you a real qualify loyar?or you are there like a sign post that you don't know what you are doing?Even you Chakwela and your friend Chilima you can't feel shame to how how people are struggling on passports issue? Simuchita manyazi anthu kumabwezedwa pa immigration for sake of fake passport , Chills i thought you're brilliant but you are coward plus Chakwela too
Kkkkkkkkk
Angokumana okhaokha,...ubwino wakenso ma passport wo akuvutika nawo okha.....ife timangoyendatu olo opanda passport ..crossboarder😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
Chakaka Nyirenda very interigent, iwe do you know behind this mess, do you know that Kalumo is fighting corruption at immigration hence this and yet supporting corruption, inu munakhalapo kuti attorney general??¿???
Sakudziwa awa zambiri Ku DPP ndizitsiru zomwe akumazipasa bundle kumangolankhula zopanda mutu agalu awa
Fake passport, fake president, kkkkkkk 🔥🔥🔥🔥boma lofoyila ili
Akuthana ndi corruption? Koma akumapanga ma passport a fake nkhani yochititsa manyaz musamuikile kumbuyo nanu😢😢😢
Fake govement passport fake
Pali zanzeru pa chakaka nyirenda apa? Iwe mbizi eti khoti laweriza bwino bwino iwe nkumanena kuti sizilibwino opanda nzeru iwe khala chete malamulo simuwaziwa Inu boma muziyendetsera unkhungu ,.kuba chitsiru iwe ndi usapota wako wauchitsiru
Thabo chakaka Nyirenda ndi dolo koma zisiru ngati inuyo a DPP ndiamene mukumuona ngati palibe chomwe akudziwa, mwaiwala kuti munali ndi mhango lawyer wa mutharika emwe samadziwa kanthu? Mwaiwala kuti kunali Mai Jane Ansah wa DPP koma Peter anakhala chete? Ndiye nzeru zomwe mulinazo inu Ndiye ziti zotibwelesera nkhalamba kuti izalamulese? Agalu inu zisiru Ku DPP kwanuko musaone ngati akakupasani ma bundle wo a DPP Anthu Ndiye asintha kuvotera nkhalamba? Chitsiru iwe ndi ufulu otengera nkhani Ku court lina mbuzi iwe sudziwa kanthu galu
Anthu ukuwatchurao munthaw Yao zinthu zimayenda ngt Pali zomwe amalakwitsa kma sizinafike ngt apa pokhotesera Dala malamulo Ali clear, ufune usafune 2025 gule kwao abwelere kudambwe
Takhala chete naweso Malawi wavunda naweso ukuyankhula mbwerera
Ndichifukwa chake iwe ukusapota chiboma ichi uli chindere nkhani yachiziwikile iyi iweyu kuyamba kuyamkhula za DPP palizeru apa? Iwe zeru ulije kwali ndiwe wa mcp ulichindere chomene DPP ungafanizire ndi mcp, DPP inayendesa bwino boma kusiyana ndi mcp yakoyo mcp kuba,kulemba nthito pa chibale, kikondera chigawo chimoza, kulembana ntchito pa mpingo wa Assembles of God pama boma ghose agho takhala nagho since democracy 1994 this is the worst of the worst government munthu iyo wakusapota boma ili kulongola kuti mutu wake ngwakufuntha mahala walije chindere foseki
Mwana wanjoka seka pachombuzi pakopo chifukwa suziwa chomwe ukunena
Izizi musazitengere Ku ndale. Time zoona pano Ku Immigration kwaola. You mean you can't see. Kapena inuyo mukapita Ku Immigration, mukuthandizidwa? Tamaganizani osati chifukwa Choti mukudya nawo nde basi kumangotsutsa pomwe Pali chilungamo. SHAME MCP.
Ameneyu anali mulimi sakuziwa za ndale vuto akumasankhilana chibala ndichifukwa akumakanika kuyendesa dziko akumasiya anthu okhala ndi experience ya kuyendesa boma zamanyanzi Malawi