Dziko La Malawi Ndilosauka Kwambili Kuti Tizikhlala Busy Ndi Cybercrime - Samuel Lwara
HTML-код
- Опубликовано: 24 июн 2024
- On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara says, Malawi's level of Socio-econonic development is too low for people and government to be busy with cybercrime laws instead of focusing on development and economic growth.
Pankhani ya Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara wati chitukuko cha dziko la Malawi pa chitukuko cha chikhalidwe cha anthu ndi chochepa kwambiri moti anthu komanso boma limakhala lotanganidwa ndi malamulo okhudza umbava wa pa intaneti m’malo moika maganizo awo pa chitukuko ndi kukweza chuma.
#malawi
Malawi has intellectuals like Lwara ,we need people like Lwara the country can do better
Good Messnge Chakwela you mast go watinyasa
Chilungamo sir great speech
This is powerful speech i ever heard before from anyone who fighting against this useless government. Chakwera ndimbuzi pamozi ndi anthu ake wose galu yamunthu
Powerful message chilima anapanga kale compaign akangolowa kupanda kuganiza zochosa moyo wake koma mau ndi oti chilima sanafe alipo mpaka 2025 MCP isova chipani cha mwazi😢
Sam umalankhula ma points ogwira mtima, keep it up bro, keep on fighting for those whose got a say but they can't talk
Achakwera opusa kwambili wapasako ukuvuna kulimbana ndiandu kusiyakukosa dziko boma lopusa lilibeseluso
kachilungamo2 ulemu wanu ine pheee!!!! ❤❤
This guys impresses me with his naked truth, may god continue keeping this guy for us so that he must continue speaking for those who cant speak.
Samuel Lwara ndiwa nzeru.
Thank you brother, Chilima timulira mpaka tsiku lozavota. Mcp ichoke basi
😅😅😅😅 Lwara ai ndithu lero kulibe Bakili Muluzi TV ndipo sindikanagona bwino kupanda iwe anthu ngat inu mukufunika mMalawi muno kwambiri
From mangochi mumatha kwambiri
Thank you sir
Very nice mr this goverment is felia
Zoona brother
Well facts presented. Well done Mr Samuel
Achape mutu my brother
Good talking brother
Ndimamva Nanu kukoma abambo a Lwara ndipo izizi mmalankhulazi ziziikidwa ku times radio ku mibawa amalawi adzimva kuti atseguke mitu ndipo chilungamo chimawawa. Koma nde Chilima anali mbambande ndipo anali hope yathu RIP
Muwawuzenso kuti social media ndiya azungu, Twitter, Instagram, WhatsApp, facebook, utube it's from European countries, and enu wake azunguwo akumaposita ma video and photos pa social media, ndeinu a mcp muzitilesa kuposita ma video pa social media, who are you?, peter kalaya , who are you? ,daud suleyman, who are you?, kumkuyu and chimwendo who are you?, zikhale ng'oma and yolamu who are you?.
Stop intimidating malawians ok?, mxiem 😡
🙌 powerful achoke basi
Zoona zoona brother kuputsa kwa chakwera
Powerful.!
keep up the good work
Congratulations brother
I salute you sibweni
Zamphavu kwabasi more fire big
Ndipo pafunika kuotcha ma office onse plus magalimoto onse a mcp chitheretu chipani chimenechi mmalawi
Tell dem bro, they don't know de definition of the word CIBER CRIME 😂😂😂😂😂😂
Cybercrime kunyumba kwako ndi family Yako chakwera,,not Kwa ife amalawi
Inuyo comrade ndinu mafia Mutha kulowa Malo mwa chilimat inu chilungamo chomwe mukulakhula ZOMWE chilima amafuna zimu wawo SKC uziutsa mumtendere taluzat muthu UJA wapita wamala kwabasaaaaa mwatililisa mcp pachilima ndianthu 9 onse ujatalirat
Uku ndiye kulankhula Kwa mzuru bwana Lwara
Chakwela ngat uli wa mzelu unakangochoka wenkha pampandopo because watikwana ndikuti Nyasa kwambili.
Ndipo izi nane ndinali wodabwa komaso chikudabwisa a police omanga anthuwo akuchokera ku LILONGWE Kodi ku BT ndi ku mzuzu a police kulibeko? MCP government is falling apart koma zomanganazo zikapitilira zitha kubwelesa kusamvana mziko
inetu sindimakuteengerani a lwara pazoyankhula zanu koma ngati zoyankhaula zanu ndi izi nde kuyambira lero ndizikusatani chifukwa umu mwayankhula chilungamo komaso za nzeru kwambiri
Shaaaa!!!!!
Zoonadi Big
Amasuleni kuti boma likupita ili kkkkkkk koma Lwara kkkkk anthu osamva awa boma lililamulidwa ndi nduna president of ofoyila kkkk
Wakumva wave koma agaluwa Chakwera ndi azinzake samba chifukwa ndi ana asatana
Kkkkkkk inu Mmayankhula bwino kwambiri🔥🔥🔥🔥reality..
😅😅😅😅koma chilungamo chitipha
Zowona
Chilungamo brother
25 mini zoyakhula za nzeru zokha zokha
Kkkkk wawo wa mcp akuti uza yekha a tavala nsalu yawo amangetu
Fire dem
Zoona zokhazokha mbambande
💪💪💪💪💪
Kkkkkk chakwera watikwana kwambiri nichifukwa ni lazar wa zironda
Aaaa kwathu kumzimba no chitukuko Kayama mps aliko ndkukaika, mzimba to eswazini, mzalangwe, kafukule upto ekwendeni mseu unayamba mnthawi ya bingu mpaka pano sunatheee ndikunena pano mcp government inachotsa contractor, mwachidule tinene kuti anasiya kumanga since chakwera anatenga boma mu 2020 ndiye ine ndikudabwa kuti mafumu amuboma lamuzimba akulephera bwanji kumuuza chakwera zamuseu imeneu chifukwa ena mwa mafumuwa ndikwawo kumeneku komaso akugwiritsa ntchito mseu omweu eeeeee abale kumzimba anthu akuvutika nthawi ya mvula mayendedwe,,
Mr lwara you are genuine comrade may God continue to bless you! Tell these idiots the truth.
Imwe muli wa chindele imwe, nzeru kuchuluka.
Samuel from the bible tiyeni nazo osamakhala ndimantha ngati ndinu obwela tell them truth mantha satithandiza
Ndipo live chilungamo kuwawa chakwera watiphera msogoleri wathu
Ndipo live sukunama chakwera saziwa kanthu ndipo ndale saziziwa ata 😂😂😂😂
Nde mwati mwazi wachilima utani big
Iwe nde akumanga..
Awuze kuti onse ndamphawi tikuvutika
S
Tell them boss Lwara
😮😮😮😮
Zoona apange resign onse felliar minister
Live talk ulemu wanu
Chilungamo biggy
Lwala iwe ndi wazelu kobas ulemu wako
Waying'alura momveka bwino aseh 😂😂😂
Amakambilana zaupandu afiti awa
Sumapita kuchimbuzi ukadya question 😅😅😅😅
Presdent uyuyu nde ayi panja penipeni Chakwela lazalo
Kapen asimti usachaniso agaluwa
Komatu ndiemwayankhulabwino bolamusasinthekusogoloku pajatu kunali laitoni mangochi
Why u were quiet for the whole last month bro?
Bingu came with helicopters from China, where are these helicopters ?
Mnthu kuchoka ku church kukankhara mutsogoleri wadziku kkkkkkk malawi ife kumbwambwana kukatsankha nkhumba
😂😂😂😂😂🎉🎉🎉 mtumbuka iyoo
Cybèrspace 😢
Kkkk apatu apatu watokota dziedi lwala ti amva pena pake akuti a boma akupasini bazi ayiiii bodza anthu ngati inu ndimene mulungu adzikupatsani moyo wawutali anthu ankhadza mulungu adziwachepetsela moyo wawo chifukwa ngati a MCP akumanga anthu ndiboma lopaaidwa ndi malemu chilima mwalo mothokodza ndikumuphatso ufiti wanji abale nde awine 2025 malawi tafa basi chuma chiwakanika kukodza nsono akufuna amalawi adzatiiani kodi iiii mulungu simunthu achite nanu a MCP
Another freedom fighter is here guys 😂😂😂😂
Guyz!, sam rwala is here kkkkkk😂😂😂😂😂
MCP rest in peace
Kkkkkkkk keep it up
ipaseni moto fada empty head chakwera
Olira sitimamutseka pakamwa chakwera bomaaa sanje akulu awa akalamba mwachangu kuipa mtima zedii utopa ndikulankhula chakwera sudzamuona kuyankhapo zopusa ngati izi very stupid massage to Malawians tikuuze tsono chakwera adzawina with landslide ukuonanso dikira
😢😂😂😂❤
😂😂😂 koma yeah
😂😂😂❤❤
😂😂😂😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Is dat true that you recieved the money from dis cruel and useless crocodile party?
Ii
Kkkkkkkkkkk
kkkkkkk