Fr Nthalika:Yakwana Nthawi, Tiitanitse Mkwiyo wa Mulungu, Pakuti Anthuwa atisinthanitsira Mtsogoleri
HTML-код
- Опубликовано: 4 окт 2024
- Mutu wa Ulaliki: Yakwana Nthawi, Tiitanitse Mkwiyo wa Mulungu, Pakuti Anthuwa atisinthanitsira Mtsogoleri.
Wolalika: Bambo Nthalika.
No comment 🙌🙌 inu munali oyamba osafusa kumwamba mulungu mukuke ife tichepe❤
Amen Father
Thanks for the powerful message be blessed 🙏
😭😭😭 Ambuye bwerani mwachangu mutonthoze dziko la Malawi 😭😭Kam Lord do not delay 😭 Ambuye musakhale chete tikumira
GOD bless you keep on preaching Hard Amen:
Mukulankhula ngati mkwiyowo utabwera mungapulumuketu anthu oyipa a catholic, palibe chimene mungalankhule cha nzeru
Keep on hitting the nail on the Head. Poti ndi satana, sakumva. Keep it up from.
Amen,mau omveka bwino Mulungu apitilize kutilankhula kudzera mwa inu ndi atumiki ena onse olalika kuti anthu adziwe kuti kuli Mulungu ndiye mwini wazinthu zonse .chofunika apa ndikuleka zoipa ,Kuti Mulungu akhululuke ndikupereka madalitso omwe tikuwasowa.
Amen
Amen mumatiyimilila fr yanganso ndachotsa
Amen fr
Amen
Amen pastor!!!! ❤❤❤
Amen father mau achilimbikitso
Uthenga wamphamvu fr
Amen father 🙏🙏🙏
Amen mau amphamvu ❤❤❤
Ambuye kumwambako imvani kulira kwathu.tituluseni mu aiguputumu.
Koma bambo mulungu akudaliseni,,wathu uja siameneyu. ,,inenso Voti yanga ndachosamo
Amen paster
Amen Fr
Anatisinthisila wanthu siameneyu,,inenso Voti yanga ndachosako
amen. farther
Amen and amen father
Uthenga wanu umandisintha fr Kaya Pano mulikuti?
Hallelujah
Great❤❤❤
mumatiimirira father
Mumatimira father
Mawu amphamvu
Mbava izi zikuti langa zenizeni
MCPigs ndi ufiti
Bambo, uthenga wanu umatitsitsimusa
Inde fada,
Wataya njira ya chipulumutso
❤
Mau amphamvu
Ndipo mkwiyo wamulungu uitanisidwed Kwa omwe atimphera Chilima ndi anthu ena Aja akanthidwe ndi mkwiyo wamulungu
Zoonadi atisinthira Mtsogoleri.
Inenso voti yanga ndaichotsa
Amen
Amen Father 🙏
Amen father
Amen Father.
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen