ZA NGONGOLE YA NEEF TINAYAMBA NDIFE ASANATIBELE BOMA - MAI MARY NAVITCHA A DPP AINGALURA LERO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 116

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama 2 месяца назад +15

    Dzikomo my sister u b next president in malawi your future in my country god bless you

    • @SteveniBanda
      @SteveniBanda 2 месяца назад

      Miyimaso achemwali mumatiyi milira ndizowona tikudziwa andifuse ife ndizowona timapita ku school limozi ndimawona taphuzilalimozi mukunena zowona chitukuko tikuchiwona pantambanyama kuchoka phungu thoyolo thava zowonadi

  • @JonesBenNgaiyaye
    @JonesBenNgaiyaye 2 месяца назад

    Wishing you all the best for the position you are hoping for and am seriously praying for you mama

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u 2 месяца назад +7

    Love you dpp love you mom

  • @PatrickMalaw
    @PatrickMalaw 2 месяца назад

    Blessed woman of grace

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa 2 месяца назад +5

    Apm my vote 🗳

  • @fahadmilanzi
    @fahadmilanzi 2 месяца назад

    More fire

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 2 месяца назад +5

    Hon Mary Navitcha kms Hon Sameer Suleiman ndi akatundu ku DPP ndipo ndi omwe akulimbitsa Chipani chathu chokondwa 🔥💙💙

  • @TisungeBota
    @TisungeBota 2 месяца назад +2

    God bless marry and dpp

  • @QueenMoses-c1n
    @QueenMoses-c1n 2 месяца назад

    Stay blessed mother

  • @LloydSouza-q6w
    @LloydSouza-q6w 2 месяца назад

    PAM my vote❤❤❤❤

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 месяца назад +2

    Mai inuyo musazafe....ndipo..musazasowe...Ambuye Apitilize kukupasani...mtima wa Chifundo......okonda Amalawi...Azanu ndipo ife... business tinaduka....kare kare kma..pano.tili ndi Chikhulupiliro kuti sikulina..dzuwa liwaraso... Ambuye Akudalitseni....mai..🙏💪

  • @JonesBenNgaiyaye
    @JonesBenNgaiyaye 2 месяца назад

    Long live madam Mary Navitcha

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj 2 месяца назад

    Maonekedwe anu akusikimizila chomwe inu muli..Pokhala Hon koma nkumaonela mwa naturally as if mulibe khobili sichinthu chophweka iyo ndi mbali imodz yomwe ikukamba za kuzichepesa kwanu.....Muzilimbikila kupemphela musalowese ajuju mu machitachita anu..may the good Lord bless youmy dear sister

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 2 месяца назад

    My model

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l 2 месяца назад +1

    may Mary navitcha mumakwana mam Mulungu akudaliseni APM my vote

  • @JamesMalango-e1g
    @JamesMalango-e1g 2 месяца назад

    So powerful

  • @BrianMaganga
    @BrianMaganga 2 месяца назад +1

    Mary Navicha woyeee

    • @WistarChauya-b7c
      @WistarChauya-b7c 2 месяца назад

      Mary Navitcha Woyeeeee❤❤❤

    • @spargomw
      @spargomw 2 месяца назад

      Chiphadzuwa❤❤❤❤

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад

    Dpp 💙💙✊ my vote 💙

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад

    Mama limbikani campaign mwamphanva.. ndimachikonda chipani chabwino.
    ❤❤❤❤

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 2 месяца назад +4

    Nanunso2 inu amakosana ujeni yanu ndiyopoira kwambiri chifukwa ikumaduka duka conzani Studio yanu kuti idzimveka bwino

  • @JonathanMsiska
    @JonathanMsiska 2 месяца назад +4

    Amayi navicha mukunena zoona olo nkhope yanu ikuwoneka simunapange chibwana pitilizani ndipo dpp musayisiye.

  • @BrieMajoni
    @BrieMajoni 2 месяца назад

    🎉❤

  • @ChikuMega
    @ChikuMega 2 месяца назад

    May navitcha muli ndi fundo zabwino kwambiri ndpo mulungu apitilixe kukupasan moyo wawutali ndpo muzatilamulila muzakhla presidential presidential president waziko la malawi love you mom❤❤

  • @TiyaMtete-o3h
    @TiyaMtete-o3h 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤❤

  • @HamiltonwaNamuwah
    @HamiltonwaNamuwah 2 месяца назад

    Eeeeeee uyuyo ndi akatundu si anyapapi ngati kamajekete ndi chikangawa

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s 2 месяца назад +3

    Tatiphulani inu a dpp, tikuphula njerwa za moto a malawife, tili ku aigupto ifeee

    • @SymonNjati
      @SymonNjati 2 месяца назад

      Mayi Navitcha,am very impressed with ur back ground and what it has taken you to be where u are,thanks for the Education foundation u instituted and it has worked and its working for that Child coming from that poor family,May God bless you and continue helping the Less privileged

  • @Vascomw
    @Vascomw 2 месяца назад +2

    Powerful 💪

  • @jeneziochisonga2819
    @jeneziochisonga2819 2 месяца назад

    Fitness eeee, ndalama zamuyanjatu. She was cute then now it is a different story.

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 месяца назад +4

    Zoona mama tumikirani dziko ndi chikondi kwa Ali yense Malawi chonde pangani zinthu zokonda Malawi yathu

    • @EmmanuelNkosi-ts8bn
      @EmmanuelNkosi-ts8bn 2 месяца назад

      DPP imangopanga zakumwera bas nde mpovuta kwambiri kuti akumpoto akusapoteni

  • @MosesNkumaniza
    @MosesNkumaniza 2 месяца назад +1

    Koma kuyakhula mosaonjezera mau zimai Ali pa mabvuto kuposa ife abambo mai tiyeni nadzo 2025 tikupasani vote yokwanila mulowe boma

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 месяца назад +1

    Zoona eneso ndine mboni mumene zinthu zililipano ayi ndithu mavuto afika pa mwana Akana phara panopa chilichose mavuto okhaokha palibe chomwe chikuyenda kukakhara kudya ndi kawiri pa week

  • @ComfortChiombangoma
    @ComfortChiombangoma 2 месяца назад

    I'm in love with her and I wish akanakhala MG2 wanga.

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt 2 месяца назад

    Dpp my vote💌

  • @WistarChauya-b7c
    @WistarChauya-b7c 2 месяца назад +2

    Mary Navitcha ❤❤❤❤

  • @samuelmchekachilenje1259
    @samuelmchekachilenje1259 2 месяца назад +1

    Nkhaniyi ndiyoona. Adaliyekha kwathu ku Nsanje North. Udzudzu wakwathu sadauope mayi ameneyu. Moti ine ndimadabwa mpaka pano kuti kodi u leader of opposition uja adamulandiranji? Mulungu adampasa mphatso ya utsogoleri mkazi ameneyu. Umboni wina ndi umenewu woti pakanthawi kochepa adabebetsa u Leader of opposition.

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад

    My vote Dpp

  • @SamsonMafaiti
    @SamsonMafaiti 2 месяца назад

    Welcome mayi

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 2 месяца назад

    My vote 💙💙💙💙

  • @DavisMisiti
    @DavisMisiti 2 месяца назад

    Mai olimba mtima washing from Lusaka Zambia

  • @KennedyPaipi
    @KennedyPaipi 2 месяца назад +2

    Kodi mai Navitcha simungabweleko ku monkey bay kuno choonde?

  • @CharlesMuongola-mt4sv
    @CharlesMuongola-mt4sv 2 месяца назад

    Mama go to contest pa Vice President

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 месяца назад

    Navitcha Suleiman 2025

  • @AffectionateGeyser-fm7dl
    @AffectionateGeyser-fm7dl 2 месяца назад

    Mbambande Asisj,inuyo ndi one

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 2 месяца назад

    Panu muyambe kumapanga Ma Demo.
    Anzanu anatenga ndi Ma Demo ndiye inu mukuti anthu awa angokupatsani Boma?

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda 2 месяца назад

    Kkkkkkkk
    You want to come back and put nany people of DPP on Government pay Row . Wayilasha

  • @HappykamwanamwanaBwaila
    @HappykamwanamwanaBwaila 2 месяца назад

    Mzabwere kwa2 kuno ku Mzimba south east Khosolo mama Navitcha chonde chonde mama. Dpp woyeeee!!!!!!,,,,,voti yanu mdzatenge kuno.

  • @nelsonkajawo5176
    @nelsonkajawo5176 2 месяца назад

    😂😂😂😂 koma anthu simukhala serious, mpaka mayiyu mwati azakhale next president eish

  • @ChrissyBhima
    @ChrissyBhima 2 месяца назад

    Kukhala nkhalamba sivuto koma nzeru ndizomwe timanena,apeter tu kukalamba sikuti kwabwera lero ai, apeter anatengapo boma 2014 koma amalawi zikoli amalimva kukoma osati zaziiiii tikuziwona lerozi,nyamata wanuyo chakwerayo akupanga chani?nkhalambayotu zitukuko zake taziwona,nanga nyamata wanuyo chakwera wapanga chani?musawapotoze amalawi,amalawi akufuna apm osati chikangawa ai

  • @LucyJoacquim
    @LucyJoacquim 2 месяца назад

    Amen

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    Ndipo inuyo mulungu azikudalisani

  • @AlliePaipie
    @AlliePaipie 2 месяца назад

    Sameer Suleman ndi mery navicha ndimakufunani awilinu mulibwino kwambi ndiyimbileni ndikufuna wina akhale president wina VP

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 2 месяца назад

    ❤❤

  • @LeonardPetro-ky6dq
    @LeonardPetro-ky6dq 2 месяца назад

    Yes DPP ikubwelanso basi

  • @AlliePaipie
    @AlliePaipie 2 месяца назад

    Aaaaaaa kod gayz takozani TV yanuyo bwanj kod mubwezatu ndalama ansaaaah

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 месяца назад

    Ndinu mai mbambande mama osililika,komano mukapita ku parliament musakaiwale nkhani yovotela chaunzika yokha pomwe chanzikacho chikuvuta kuti chituluke

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 2 месяца назад

    Ndizoona Peter Wamuthalika his a good President koma kunena zoona munthu uja wakula kwambiri his 85 nde alamulire zaka 5 azakhala ndi 90 pamenepo ndekuti sitili serious a Malawi ngati 2017 to 2019 amangogona mpakana kumalamulidwa ndi bodyguard Bambo a Chisale mpakana kutisakhila Bwana Chimulirenji kutathauza kutha kwa nzeru akanapeleka udindo kwa munthu wachichepere ndikumamupanga guide, zithu momwe zikuyendera panopa padziko lapansi khalamba ngati imeneyo singakwanitse tiyeni tikonde dziko lathu a Malawi

    • @AnnaPhiri-b8t
      @AnnaPhiri-b8t 2 месяца назад

      Nzeru imagonjetsa chilichonse

  • @vincentkamoto
    @vincentkamoto 2 месяца назад

    Navicha mkatundu eshiiii

  • @InnocentKadoma
    @InnocentKadoma 2 месяца назад

    Mai awa alindimbalume ngati abusa eee🧢🧢🧢🧢

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk 2 месяца назад

    Ndimaikonda DPP ndimoyo wanga onse

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 месяца назад

    ndakunyadirani love you Mami yes

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 месяца назад

    Mayi navitcha ndiolimba mtima ndinawaona nthawi yomwe amqngwirilizira reader of opposition.mayiyu adzaimire u presdent malawi yizasinthqtu alindimfundo zothandiza malawi

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe 2 месяца назад +1

    Zoona.madamu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 месяца назад

    koma nafeso tikukufunani amayi ndingakupezeni bwanji mayi inu mzimayi muzathu ndakunyadirani

  • @LeonardPetro-ky6dq
    @LeonardPetro-ky6dq 2 месяца назад

    Mulungu salephera amai APM Bomaaaaaaa

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 месяца назад

    sikonoyo mutu wake unataya kare ameneyo kuguritsa friend wake rero akunjoya chisiru ameneyo kufera vp

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 2 месяца назад

    Nazoni mayi osafooka apm endanayeni

  • @DivalaKaphaka
    @DivalaKaphaka 2 месяца назад

    zofunika mama

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 месяца назад

    ADAD woye, 2025

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 2 месяца назад +2

    Nthwawi imene munali m,boma sumunkadziwa kuti azimai apolisi aphunzitsi salandila ndalamazokwana mwadziwa lelo mukunamatu nthwawi yatsalai ndiya UTM osati dpp

    • @clashftm369
      @clashftm369 2 месяца назад +1

      My vote

    • @mercybiziweck
      @mercybiziweck 2 месяца назад +1

      Mukapeza mpata munvereko nyimbo ya muchedwa ya kell Kay ija mwanva

  • @idenmkumba-q8j
    @idenmkumba-q8j 2 месяца назад +2

    muzikumbukilatu chomwe chinatulutsa Dpp boma 2019.timayikondatu Dpp koma mukasamale kukomveshoni osakasakhaso adad ayi zimenezo ife sitikufuna

    • @Frederick-s4h
      @Frederick-s4h 2 месяца назад

      Ukunama akamusakhe apm

    • @spargomw
      @spargomw 2 месяца назад

      Peter, Boma Boma Boma❤❤❤❤

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 2 месяца назад

    Dpp ndi chipani chamadolo

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda 2 месяца назад

    Kkkkkkkkkk
    DPP ayi ayi ayi ayi
    Kkkkkkkkkkk

  • @GiftChimpani
    @GiftChimpani 2 месяца назад

    Mama inuyo mukukwana

  • @SharifChibwana
    @SharifChibwana 2 месяца назад

    Mbambande inuyo

  • @GiftmillieYunusu
    @GiftmillieYunusu 2 месяца назад

    Koditu ammalawi wake ndi nchewa,achewa ndi mbuzi

  • @WinstonNyadaufe-d1o
    @WinstonNyadaufe-d1o 2 месяца назад

    Inde nchipululu simofela awuzeni

  • @JanuaryGwere
    @JanuaryGwere 2 месяца назад +2

    Mulungu adzikudalitsani

  • @ElitaKaude
    @ElitaKaude 2 месяца назад

    Kutopa ndi zaka four nanga zaka 25 zapitazi simmatipa bwanji pot munali pa chinyezi eti

  • @KinziWindassoni
    @KinziWindassoni 2 месяца назад

    Za bwino zonse Mai navisha iwe mbambande

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 2 месяца назад

    Zidakukanikani kale inu pano musatipusitse ingopangani masters yo basi osati muzitilongolora ife

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 месяца назад

    Boma libwelera 2025 asiyeni achina sikonowo tizaonana

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 2 месяца назад

    Km zonsezo zochokela kubanja losaukazo zisiyeni ilolo ndedziko km masopatsogolo aliyense alimbili yakeyake

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 месяца назад

    My vote

  • @Eddakachere
    @Eddakachere 2 месяца назад

    Ukati uchisilu ukutanthauza chani

  • @FranksonKennethChipande
    @FranksonKennethChipande 2 месяца назад

    Mapoliticians ofoira mumati Boma lisiye kupeleka ngongole Kwa anthu kudikira Inu??? Mulibe mnzeru vuto Malawi muno si usogoleri Ayi.Koma stragety mmene mumapangira M'Boma zinthu.Mungonena kuti muzapitiliza kuononga pamene munalekezera

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 месяца назад

    Very weak lady,

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад

    Uchisilu ndiye mumafuna kuti asiye kupereka ngongoleyo chifukwa cha inu bwanji osamapanga zanu bwanji

    • @AlfredMatthew-v4h
      @AlfredMatthew-v4h 2 месяца назад +2

      No matter what respect your mother kutukwanaku sizingathandize

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад

      @@AlfredMatthew-v4h Pali zoyakhula zina aziyamba aganiza polakhula chifukwa palibe amene sakuziwa chilungamo ndiposo Palibe sogoleri angakomele aliyese iwo ali ndi anthu owasata basi athandize iwo azawoso ali ndi anthu owathandiza ndiposo ubwino wake zipani zonse zidakhalapo ku opposition

    • @clashftm369
      @clashftm369 2 месяца назад

      Ngongole apatsa anthu angat???or 2000 aangakwane Malawi yonse...mmalo mopanga ncthito mkuwalemba

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 2 месяца назад +1

      ​@@clashftm369ndpo ayamba liti kupeleka ngongolezo kkkk anthu saziwa zomwe akuyankhura zomwe ankapanga adpp amatha n chakwera anakati azisatira za chilima bwenzi akupanga zokomera amalawi koma kusamvetsesana ndzo palibe akupangapo

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 2 месяца назад

      wa chikangawa ndakuona😂😂😂😂😂😂

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 месяца назад

    Malawi yadzuka.dzikomo a mayi.

  • @BongoBahati
    @BongoBahati 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @lovenessmuthiya3513
    @lovenessmuthiya3513 2 месяца назад +1

    ❤❤❤❤❤❤❤

  • @Olivia-n2e
    @Olivia-n2e 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤❤❤