BASITU NKHANI IJA YANG’ALULIDWA PA TIMES PAMENE AMAWERENGA NKHANI ZOMWE ZACHITIKA LERO KWACHEMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 90

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Час назад +1

    Kungopanga zoti ena azidziwe basi ❤❤❤

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 2 часа назад +5

    Is good nice now Zikom mulungu asikudalisapo chakwera achoke 2025

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 2 часа назад +5

    Very good every body must register inorder to exercise his or her to vote.

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 45 минут назад

    Ili ndi dziko la Mulungu zikomo Ambuye ndinu Mokha mumakhala ndi mayankho anthu anu a Malawi ❤❤❤

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 6 минут назад

    Kma yesu ameneyu aaaaa watimenyera nkhondo ife tili chete

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa Час назад

    Amen nthawi ija yakwana yochoka pa pando Mr chikangawa wagwa nayo keasala nkumapita ku Court every week ya 2025 nyiiii

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza Час назад +2

    Amen mwatimenyele nkhondo ife tli chete chi satanacho chichite manyazi

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z Час назад

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MariamAlabi-t3n
    @MariamAlabi-t3n Час назад +1

    Democracy woyeee Mizimu ya anthu 9 aja uwuse mumtendere not forgetting Ralph Kasambala ,chonde timenyereni nkondo ,

  • @ShazidaAlfred
    @ShazidaAlfred Час назад +3

    Amen ambuye zikomo mwatiyakha pepho lanthu

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 2 часа назад +3

    Amen kumwamba kuli mulungu

  • @PatriciaChiwerenga
    @PatriciaChiwerenga 2 часа назад +1

    Hallelujah 🖐️🖐️🖐️🖐️🖐️🖐️🙏🙏🙏

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 2 часа назад +2

    Mayi Joyce banda amamupotsa chalakwe poganiza.

  • @jollyfriday1892
    @jollyfriday1892 57 минут назад

    UTM vote yangaaaaaa

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 32 минуты назад

    Osaopa amalawi dzikoli ndilathu

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r Час назад +2

    Khoti layamba kuopa lawyer uja kuti awaulula

  • @martinsailesi1731
    @martinsailesi1731 16 минут назад

    Passports and driving licences belong to the government please.

  • @PeterMorgen-k4b
    @PeterMorgen-k4b Час назад

    The smoldering charcal👐👐👐

    • @JustinLipipa
      @JustinLipipa Час назад +1

      Kodi ndingalipeze kuti Buku la smoldering Charcoal 😂😂😂, nchere, Bota aaaaa you just reminding me in those good old days

    • @PeterMorgen-k4b
      @PeterMorgen-k4b Час назад

      @@JustinLipipa Tafufuzani mma book-shop Blantyre ko

  • @RuthBeyala
    @RuthBeyala 2 часа назад +2

    Ambuye musasiile pomwepa chonde tioneni ife ana anu

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z Час назад +1

    Wagwa nayo Anabel izoooo usova 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @WysonAdamu
    @WysonAdamu 19 минут назад

    Mulungu sichakwela kapene chimwendo ayi dzikoli ndilamuthu Wina aliye sidzimene amafuna makape enawa

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 30 минут назад

    Mulungu mutiyankhe tilimuwulamulilo asatana mcp yikutizuza amalawi

  • @PeacefulBackpacker-mn2gi
    @PeacefulBackpacker-mn2gi 24 минуты назад

    Chakwela ndi mbuzi yopanda zelu

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix 2 часа назад +2

    Murungu aremekezeke ndizo timafuna zimenez

  • @MaryNgola
    @MaryNgola Час назад +1

    Aleluya

  • @HenryChiwaya-g4d
    @HenryChiwaya-g4d 2 часа назад +1

    Zochitika kuno ku malawi ndingoti Dzuka MALAWI

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w Час назад

    Amen

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 2 часа назад +1

    MULUNGU SI JEMUSI!!!!!! KUMENYA KUGWETSA BASI

  • @violetkamfose6693
    @violetkamfose6693 27 минут назад

    An assessment need to be done on condition known as dyslexia

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 2 часа назад

    Nkhani, yabwino kwa amalawi okonda ziko lawo salute

  • @HarryMwakimeme
    @HarryMwakimeme 2 часа назад +2

    Zoona masten

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Час назад

    ❤❤❤❤yaah

  • @GradinaNgalande
    @GradinaNgalande Час назад

    Chilima musagone mwachangu paka tizavote chifukwa tizasowa zimu wanu pathawi yovota chakwela mazi basi

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r Час назад

    Mcp ija pa ulendo basi ma plan anu aduka,

  • @ADAMSONGONDWE
    @ADAMSONGONDWE Час назад

    Smartmatic isagwiritsidwe ntchito

  • @InnocentChauwa
    @InnocentChauwa Час назад

    Ameen

  • @elizasingano
    @elizasingano 2 часа назад +2

    Nkhani kma imeneyo

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Час назад

    Wagwa nayo.ndani
    Chiletso sichintheke

  • @RaffickAllie
    @RaffickAllie Час назад

    Apa mudzi onse wakwathu tikavota basni kkkkk Moto kuti buuuui

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona Минуту назад

    MCP yomwe ikulamula panoyi ndi yomwe ijayi ya ku Ghana ya kamuzu banda.Chakwerayu wangokhalapo ngati chukwangwani chabe.🐊🐊🐊🐊🤦🤦

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Час назад

    Atsogoleli athu simuchita manyadzi ponamiza anthu awo.

  • @TiwongeChikhoza
    @TiwongeChikhoza Час назад

    Ndipo watsalanso nzimai uja mtali manja atule pasi usindo hule ameneyo

  • @MikeChitambe
    @MikeChitambe 2 часа назад

    Tili komweko bas 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RebeccaChikalenda
    @RebeccaChikalenda Час назад

    Ndubwera lne ndzarembetse lme

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n Час назад

    Wina alira chaka chake nchino

  • @chimwemwechikwawa
    @chimwemwechikwawa 2 часа назад

    Hahahah izi ndazikonda, odi nkalembese ine

  • @thomasmakata8861
    @thomasmakata8861 2 часа назад +1

    Kumwamba kulandire ulemu

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Час назад

    Vuto ndi kaphunzisidwe sikali bwino.

  • @JimmyAlfred-p1y
    @JimmyAlfred-p1y Час назад

    Ambuye tipatseni munthu ozatiimila 2025 popeza munthu tilibe

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Час назад

    Kuyambila inuyo.

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri Час назад

    I can forsee the Rise and Fall of Eid Amin part 2, ahead 😅

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc Час назад

    Sono Za smartmatic zija zilipat guys 🤔

  • @RajabAssan
    @RajabAssan Час назад

    Ndipo live

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga 2 часа назад +2

    Tikavota bas🤣

  • @HasheemSalade
    @HasheemSalade Час назад

    Ndazkonda zimenez

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v Час назад

    Pamenepa zili bwino kwambiri

  • @RichardChathyoka
    @RichardChathyoka Час назад

    Wina alila kkkk😂😂😂😂😂

  • @innobashirbernard7853
    @innobashirbernard7853 Час назад

    Tipatseni ife chakudya chathu chalelo

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 2 часа назад

    on my way going to the shop kukagula mowa kut ndiufile y annabera amandipwetekesa mutu heve any question from joab chakhaza kumangot malamulo athu sakulora relo alikut 🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 38 минут назад

    😂😂😂😂mbuzi za amalawi.....
    How do you recognise the citizen without ID.....
    MCP inawina musavutike....
    The entire mec is MCP family

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh 2 часа назад

    Apa ndye zilibwino tsopano

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 35 минут назад

    This woman has lost her senses Joyce

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga 2 часа назад

    Agwa nao akanganya amenewa

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi Час назад

    Nkhani yabwino kwambili

  • @DakaValilani
    @DakaValilani Час назад

    Indendizona

  • @KassimJumah-s8b
    @KassimJumah-s8b Час назад

    Zopusa basi makape inu

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 2 часа назад

    MEC chair finally defeated

    • @Kabwilachikangawa
      @Kabwilachikangawa 2 часа назад +1

      CHITSIRU CHIJA CHI TONKHWE-TONKHWE

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z Час назад

      ​@@Kabwilachikangawakkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂🎉

  • @GeoffreyWatchipa
    @GeoffreyWatchipa 2 часа назад

    Koma kumeneko 😅😅😅😅

  • @MercyKutentha
    @MercyKutentha Час назад

    God and God alone😅😅😅

  • @YUNGBRÔÔKLYÑ-w1t
    @YUNGBRÔÔKLYÑ-w1t 2 часа назад

    Kumwamba kudyele nyama

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 2 часа назад +1

    Moto kuti buuuu

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 2 часа назад +1

    Nthawani tidusa inu

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 56 минут назад

    Zilibwino

    • @johnjoachim3820
      @johnjoachim3820 48 минут назад

      Milandu yaku Malawi ikukhala bwanji this my first kumva kuti muthu wamangidwa kamba koti amafuna kuphwanya lamulo 😊 ma judge mulipo koma where did you get this power mudziwaletsako a mcp kuti malamulo anu samatelo👣🔊

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 2 часа назад +1

    Deal

  • @Edithmchinza
    @Edithmchinza 2 часа назад

    Tikavota 😂😂

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma Час назад

    Anabel 😂😂😂😂😂😂😂 dweku

  • @DorothySangala
    @DorothySangala 2 часа назад

    Ndetika votela ndani umuvotela akusowa osewa zaozimozi