APOLICE AYAMBA KUPONYA TEAR GAS KWA ZIPANI ZONSE ZOMWE ZIKUYAMBITSA ZIWAWA PAMENE KALIATI WAMANGIDWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 77

  • @josephjana695
    @josephjana695 3 часа назад +5

    Akuti mulanduwake amafuna kupha ndani? Khalani serious guys kodi amene anapha nzake ndi ndani?. Ndiolose ndikakutafune #TRAESON mugwadi ndi bp chaka chino

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 3 часа назад +5

    More 🔥 a Malawi tisafooke mpaka chilungamo chioneke

  • @AnganilyEKNyirendah
    @AnganilyEKNyirendah 2 часа назад +1

    The country has really changed mulungu chitaniponi kanthu

  • @FalesMdemba
    @FalesMdemba 2 часа назад +1

    Utm my vote osaopa osafoka osatopa anyani a mcp anthu ankhaza chipani chakupha

  • @ChifundoThomas
    @ChifundoThomas Час назад +2

    Boma Ili tinaliyika tonkha tichotsaso tonkha Chaka cha mawa

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 3 часа назад +3

    Bravo UTM and UDF Aford. God Bless

  • @hesbaluku7281
    @hesbaluku7281 Час назад

    Km raster uyoyo Ali nd confidence 😊atha kuthibura koopsa

  • @natashamathala8715
    @natashamathala8715 2 часа назад +1

    Kodo apolice amathamangila kuponya utsikamba ka chani koma anyani awawaaa?

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v 32 минуты назад

    Apolice anthu ndiatinke nawo ngakhale mumange wanthu chikangawa sakupatsani kalikonse Apolice mukhangati sinu anthu nanu muvutika tidzikumenyani mamidzimu muzolowela zomamanga anthu dziko ndilanthu sikuti mukavala uniform tidzikuwopani sitikuchita mantha

  • @Xolani-jd7fo
    @Xolani-jd7fo 24 минуты назад

    The dc🔥🔥🔥❤️❤️

  • @BerthaMkwinika
    @BerthaMkwinika 3 часа назад +1

    Dzikoli ena azimangidwa ena ayi chonsecho onse alakwa sizoona, aliyense akaphwanya lamulo azimangidwa

  • @VincentMapira-h1f
    @VincentMapira-h1f Час назад

    Ine ndimafuna nditatero km vuto ndikibe lawyer komanso kabunthabuya

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 33 минуты назад

    Chakwera ndi mbuzi yamuthu muthu oyipa kwambili ngati idya amin koma thawi yake yasara pang'ono basi atuluke

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 3 часа назад +2

    Zoonadi the DC ifeyotu timakunyadilani

  • @OwamThoko
    @OwamThoko 3 часа назад +1

    Ngati apolisi akuphulisa usi munseu amalawi pitani mukhaphulise usi ma office am.boma

  • @TimeAbilu
    @TimeAbilu Час назад

    Wanted woman can not be in custody for long time, which means can happen something

  • @masingatichilumba8263
    @masingatichilumba8263 2 часа назад

    Muthamangitsa bwanji anthuwa pomwe akufuna amvere mtsogoleri wao ndipo sakupanga ma demo ayi,

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga 2 часа назад

    Lilongwe wake uti wavutayo.aa.omwewo osowa zochitawo ndamene ali wekaweka.atoziwana.Lilongwe business usual.

  • @AgnessKaliza-f8i
    @AgnessKaliza-f8i Час назад +1

    Osaopa osafowoka osatopa 💪💪

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn Час назад

    Manganya akuona ngati 2025 azakhabe vice president galu kufupika

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 3 часа назад +2

    UDF igawanikaso pompano 😂😂😂

  • @ZioneMkangadzula
    @ZioneMkangadzula 3 часа назад +1

    apolice musatero asiyeni anthu averere milandu mumaziyamba daratu

  • @SuzanVictorMadengu-k6v
    @SuzanVictorMadengu-k6v Час назад

    Osatopa osafowoka osaopa dziko ndi lathu ili a Malawi wo nde ndifeyo nde asatiopseze ngati ndife obwera ayi

  • @AnthonySiyasiya
    @AnthonySiyasiya 41 минуту назад

    Kaliati simunthu wamba aMCP munyera Naye ameneyu kaliati ndi President kale

  • @FestonYona-r9t
    @FestonYona-r9t 2 часа назад

    Mwatizuza kwakwana tsopano muweluzidwa inu a mcp

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Час назад

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 2 часа назад

    Chakwera anapha chilima bwanji mlandu sakuyakha or kumangidwa a police osamakondera pomangaathu

  • @shaddaimaonga5832
    @shaddaimaonga5832 2 часа назад

    Koma ndikutha kunvetsetsa, umangotolera zomwe anzako ayika kale

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 2 часа назад

    Chakwera amangidwa lit zaimfa yachilima

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn Час назад

    Imeneyi ndi plan ya Micheal Usi munthu oyipa uyu Manganya

  • @EthelOsman
    @EthelOsman 3 часа назад

    Koma chilima ayi Zikomo kwambiri mulungu analola kuti mupite dziko lidziwe wabwino ndi oipa

  • @shaddaimaonga5832
    @shaddaimaonga5832 2 часа назад

    Iwe kapolo tazingoyika osati kulankhuliralankhulura. Ukalemba zakwana basi

  • @SolomonAmiduh-y6x
    @SolomonAmiduh-y6x 2 часа назад

    Dpp bwanji sinabwele kumeneku?😊

  • @allanmvuma1891
    @allanmvuma1891 45 минут назад

    Chifukwa cha ndale akaliat sanalakwe

  • @StaffordNgalande
    @StaffordNgalande Час назад

    Koma Mulungu sangalole kut athu ake azivutika chifukwa cha M C P Mulungu akatha Chakwela posachedwa a Malawi khulupililani pepani a Mai Kaliati

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 часа назад

    Nthawi imene chilima ali moyo adamangidwa izi kudalibe tinene kuti zikuchitika chifukwa chani

  • @MercyDzonzi
    @MercyDzonzi 2 часа назад

    Kodi ndekuti ndi one party system

  • @Xolani-jd7fo
    @Xolani-jd7fo 25 минут назад

    osaopa osafowoka osatopa💪💪💪💪

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v 2 часа назад

    Let's go DC more fire

  • @VictorPhodogoma
    @VictorPhodogoma 2 часа назад

    Ukanenetsa kwambiri akutengeta ku chikangawa ohooooh

  • @LovelyAntenna-rs4pz
    @LovelyAntenna-rs4pz Час назад

    Khaza

  • @MercyMjima-tv5py
    @MercyMjima-tv5py 2 часа назад

    Nanu muziponya khuni za Moto ayake amenewo omawaopa athu amenewo

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h Час назад

    Osatopa osaopa osafooka

  • @LOKAMJ
    @LOKAMJ 2 часа назад

    Nkukuyu sakumumanga bwanji,,,,

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 3 часа назад +1

    Dziko ndi anthu ake

  • @JeremiahKapundu-j1p
    @JeremiahKapundu-j1p 2 часа назад

    Osaopa osafoka mpak chimbaz adyacho asaze

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 3 часа назад +2

    More 🔥🔥🔥 DC

  • @BillyBentryMunthali
    @BillyBentryMunthali 2 часа назад

    Mkutaya nthawi

  • @MbiNauli
    @MbiNauli 3 часа назад

    Kuipa mtima kotani uku

  • @MagretSaizi
    @MagretSaizi 3 часа назад +1

    Aponyeranji tiregus aaaaa

  • @MaloneFundo
    @MaloneFundo 3 часа назад +1

    DC wenwen

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 часа назад

    The dc 🔥❤️

  • @JoyceGondwe-ve1zu
    @JoyceGondwe-ve1zu 2 часа назад

    Athireni usiwooo. No future

  • @JohnBanda-e5x
    @JohnBanda-e5x 2 часа назад

    Aone nyekweeeee!!!!!!!

  • @JabulanKelvin
    @JabulanKelvin 2 часа назад

    UTM for life

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 2 часа назад +2

    Osaopa, osafooka n osatopa, it's fight for real democracy as real nation don't fear anyone just fear i will fight for and de reality will set Patricia kalita will set her free in Jesus name

  • @JosephGabriel-y7w
    @JosephGabriel-y7w Час назад

    Moto kuti booooooo😂😂😂😂😂😂🎉

  • @ChristopherTheu-y3r
    @ChristopherTheu-y3r 2 часа назад

    Kwaola hvy

  • @StevenPhiriJoshua
    @StevenPhiriJoshua 2 часа назад

    Osaopa, osafoka,osatopa

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 часа назад

    Koma pamene mwayima apo ndipa chitukuko Cha chakwera misewu yikubeba

    • @MalickMkweche
      @MalickMkweche Час назад

      Iwe chakwera wakokoyo ali ndi ndalama zomangire nsewu wasowa zokamba eti

    • @Edson-sj8vn
      @Edson-sj8vn Час назад

      Misonkho sindalama zachakwera wakoyo galu ngat amenei

  • @trynessmsowoya4187
    @trynessmsowoya4187 3 часа назад +1

    Koma dziko lanthu likupita kuti esh

    • @Twayaibrahim
      @Twayaibrahim 2 часа назад +1

      Kkk latchena kwambiri het? 😂

  • @EusterGoliath
    @EusterGoliath 2 часа назад

    Sizona

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 3 часа назад +1

    Moto buuuu

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q 3 часа назад +1

    DPP Kodi sonabweleko lelo

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 2 часа назад +1

      Mwina apita kukavelera mulandu wa ku mec paja amati chigamulo chiliko lero

    • @LOKAMJ
      @LOKAMJ 2 часа назад

      Aliko,,achina sulemani

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 3 часа назад +1

    apapa ma demo ndiye ayamba mpaka pa 30 OSAOPA💪
    Alunta Continua 💪
    (SKC💔)

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu Минуту назад

    Foseki

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 3 часа назад +1

    Anthu mukusowa zochita et 😂😂😂

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 3 часа назад +1

    Osaopa osafooka osatopa