ZIKUCHITIKA POMPANO CHIPANI CHA UTM CHAYAMBA ZIONETSERO KU LINGAZI POLICE POMANGA PATRICIA KALIATI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 373

  • @DoniasKamwana-l7r
    @DoniasKamwana-l7r 22 часа назад +12

    Utm Lower Shire Youth wing, Ikupempha achinyamata onse kuti mmawa tili ndi mapemphero wopemphelera Hon: Secretary General wathu SKWENI , Kuti ambuye atithandize kt chilungamo chiyende ngati madzi. Wotsogolera ndi Evangelist Donias Kamwana, Wa mpingo wa UNITY IN CHRIST.

  • @LovemoreAlbert
    @LovemoreAlbert День назад +22

    MCP is an example of Malawian evil political parties

    • @EmmanuelNgambi-y6h
      @EmmanuelNgambi-y6h 23 часа назад

      Exactly mcp is more than evil

    • @DeveliousMasinja
      @DeveliousMasinja 21 час назад

      Aaa simulidziwa kanthu inu zomanganazi zidayambika kalekale

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 17 часов назад

      Mukamapalamula mudzimangidwa kumene , good job Malawi police.

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q 23 часа назад +14

    Dr usi akudziwapo kanthu ndipo ndimunthu oopsa muopeni ndi udasi ameniyo afe sitingamusapite ndamene akumenya nkhondo yapamsi ndi MCP

  • @TimothyKabumbuKendrix
    @TimothyKabumbuKendrix День назад +24

    Kukhale kuyamba kwa zionetsero basi osadkira pa 29 kapena pa 30 ayi, more fire 💪💪

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 22 часа назад +6

    Osawopa osafooka we are together with you almighty God will protect you this plan is for manganya

  • @PiksyLami
    @PiksyLami 22 часа назад +6

    History ya mcp ndi ya chabe chabe from long time........mziko lawakanika awa ndiye angoganiza zomangomanga anthu ....

  • @SalamSala-c8q
    @SalamSala-c8q 11 часов назад +3

    Akufuna kusokoneza UTM Koma MCP Idziwe Kuti thawi ndikachitsilu

  • @ReginaZande
    @ReginaZande День назад +6

    Akadakumbukira padzana ndi imwewa anawaliwetsa mmboma anagwira ntchito Mai awa ndipo kaya lakwachani akadaganiza mwaumunthu anawina ngati alliance because of these strong people,all the best akweni

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День назад +8

    Amanga bwanj muthu wopanda sifukwa koma sizoona ai izi komano mapulani achakwela ndi manganya akupanga bwino ai.

  • @raphaelchammagomo8511
    @raphaelchammagomo8511 23 часа назад +6

    God is with you Madam Kweni

  • @JamesGeorge-l9o
    @JamesGeorge-l9o День назад +13

    Dr usi akudziwapo kathu , why am saying like that, just because adakakhala kuti sakudziwapo kathu ndipo ndidabwa bwezi iwowo ali munthu oyambirila kukaonekela Ku police koma angokhala chete why?

    • @SaidSamuden
      @SaidSamuden 23 часа назад +2

      Mcp ndiye imeneyi mwina timangonva makolo anthu akamadandaula lelo tizionela tokha

    • @LouisKhomani
      @LouisKhomani 22 часа назад

      Akamuone chifukwa chani mesa patricia amamunyozaso usi yo

    • @JamesGeorge-l9o
      @JamesGeorge-l9o 22 часа назад

      @@LouisKhomani ziikugwilizana chani? Anyozana pantendele so this is a big problem sakuyenela kusungilana nkwiyo koma zingoonetselatu kuti iyeyu usiyu nde driver wa zithuzi

    • @JamesGeorge-l9o
      @JamesGeorge-l9o 22 часа назад

      @@SaidSamuden vuto timakomedwa ndimawu osaona m'maso mwawo kuti ndizilombo

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike День назад +6

    More fire UTM. Weniweni wa UTM waoneka lero. Osati ena onama aja... ovala zanyuwani aja

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 23 часа назад +7

    Zimene akupanga M.usi sure aononga chipani please muchotse uyu

  • @ChikondiLuntha
    @ChikondiLuntha День назад +7

    Chiyambi chachimwemwe pamoyo wamunthu chimayamba ndimavuto ndipo osafooka zabwino zili mtsogolo

  • @KennedyKutembo
    @KennedyKutembo 23 часа назад +4

    Mwana akalilila nsasi musemele UTM inakana DPP ndigwilizana ndi MCP lelo ndizimenezi chisankho choipa is like a game of Chase u make a long move u face a panishiment akulilila kuusi zitengelepo phunzilo zipani zina tiyeni tizikonda zikolanthu

    • @engieberlmaguaire5473
      @engieberlmaguaire5473 23 часа назад +3

      Karma is real, zofuna izi. Amalawi ntendere sanawufune

    • @LOKAMJ
      @LOKAMJ 10 часов назад

      Kusamva lero ndi izi

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 23 часа назад +5

    Micle usi ukupanga ndale zopusa tikuziwa kt iwe ndi wa mcp ndipo ukufuna ugulise chipan

  • @CourageBanda-d1g
    @CourageBanda-d1g День назад +4

    Ndikamva nkhani zaku Malawi ndimafila pain kwambiri 😢😢

  • @HamaHanna-u1e
    @HamaHanna-u1e 23 часа назад +3

    We malawians we are very quiet lets take action now

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb 23 часа назад +4

    Akungofuna kungosokoneza conversation

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 19 часов назад +1

    Zonsezi akupanga ndi Michael Usi akuziwa kuti palibe angazamuvotere Usi

  • @MwayiMagetsi
    @MwayiMagetsi 12 часов назад

    Don't worry Mamie God is with you all time

  • @IshumaelAlabiy
    @IshumaelAlabiy 12 часов назад +1

    MCP sangasithe oro patachedwa bwanji athuwa alindiziwatha zoipa opanda chisoni ndi azawo akweni alakwa chani anyamata anachita kuswa magalimoto Dpp sakuwamanga phakalelo amalawi tilindimafuso ambili

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 23 часа назад +2

    Zonsezi ndi nthira kuwiri maguya ndiyemwe akupangitsa .usamaletu koma.uona Zokhoma walakwanji kaliyatu.

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 18 часов назад

    A stitch intime indeed serves nine ,this is time for all Malawians to take part ,,lets have a concrete decision by showing our deeply concern "demonstration" this is too much

  • @AlexThembakako
    @AlexThembakako Час назад

    Mmmm campaign yose ija UTM , lero zafika pomaphana, kumangana Kodi mwaiwala Ntchito inagwirika ija kuti MCP mupezeke mboma

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 15 часов назад

    MA plan a wanthu olephera amakhala ngati amenewa😂😂😂 apa mayiyu nde ampatsa MA vote ambiri ku convention, Amanganya ndi Mr chikangawa ndinu Ana pandale ngakhale sindine wa ndale😂😂😂😂ndale izi or mwana wakuwonelelani😂😂😂😂

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics День назад +8

    More fire 🔥 🔥 Utm

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 20 часов назад +1

    Everything you do, remember, there is tomorrow....
    Be very careful...

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 23 часа назад +1

    Kodi a MCP m'malo mothesa njala ndi vuto lakusowa kwa mafuta, muli busy nso kumanga anthu?? Are serious? Kod kutuluka mu alliance ndichifukwa?

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 22 часа назад +1

    Whats wrong she did to arrest her innocent woman this plan it wont work guys

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 23 часа назад +1

    Mayi Kaliati is a threat to the government , mayi Kaliati ndi katundu , chakwera will fail

  • @PatrickZimbiri
    @PatrickZimbiri 11 часов назад

    Chipani choipa ichi , chokhetsa mwazi wa a2 osalakwa... Eeeesh ooh God have mercy with us!

  • @KondwaniMunthali-vf1ws
    @KondwaniMunthali-vf1ws 21 час назад +1

    A dikira bwanji 48hrspowamanga ndimayesa Anali at amaliza ma investigation? Tikuyatsirani ma candles

  • @JacksonNamathawa
    @JacksonNamathawa 23 часа назад +1

    It's too bad kumanga akweni to silence opposition?it's not good

  • @CHITSANZONOTA-oz4mv
    @CHITSANZONOTA-oz4mv 22 часа назад

    Inu a utsi , know God first,Mulungu sanakusankhen ,simukwanilitsa mission iliyonse inu ,God has more powerful ,iwe utsi ndiwe amene udapereka chilima kut aphedwe ,ndiwe mfiti oyipa kwambiri,tsoka kwa ana Ako utsi

  • @ALINAFEMTALIKA
    @ALINAFEMTALIKA 10 часов назад

    Nde kuti chipani chathu cha utm athuwa chikuwaopya kuesela Mbali zonse kuchifinya ummmmmm 😢😢 amanganya muliko mulungu akuoneni

  • @TonyMhone
    @TonyMhone День назад +8

    Ntchito za Usi zayamba kuonekera poyera.

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 22 часа назад +1

    Pochosa Chilima amaganiza ngati athana nayo utm koma azindikila kuti mitu idakalipobe choncho akufunafunabe njila yowamaliza

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 20 часов назад

    Ngakhale ine ndale sindimazitsata koma kumangidwa kwa kaliat pa mulandu wa treeson zandikhudza ndimulandu wakulu .koma zonsenzi zikuchitika pazifukwa zandale 😢😢😢koma bola musamuthile poison kumeneko kapena kumupha ku malawi kuyamba genoside srs😢😢

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 День назад +2

    Time is coming when Babylon will fall drastically

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane 22 часа назад +1

    Komatu mulingo omwe umamuyezela nzako siku lina anzakuyedza iweyo manganya akuziwapo kanthu

  • @LenardMakunda-i9i
    @LenardMakunda-i9i День назад +4

    Ausi akudziwapo kathu

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r День назад +1

    Manganya ndi chani? Same boma same Malawi nkhondo ndi mnasi, saulos anaphedwa ndi ma friends

  • @RaysBvumbwe
    @RaysBvumbwe 16 часов назад

    Anthu Ali ndi Mantha ndi UTM. Cholinga chowamangila mayi Kaliati sangafotokoze chifukwa palibe mlandu. Akungofuna kupeleka mantha kuti anthu azikhala ngati nkhosa komanso tikamayenda tidziyenda ngati nkhanu dziko lathu lomwe. Zochititsa manyazi. Ndipo amene wapanga izi mulungu achita naye.

  • @RachealNyondo-y8g
    @RachealNyondo-y8g 4 часа назад

    Mwazi wa skc ndi anthu 8 kuchikangawa uyende Malawi yese ndiku zunza onse wochitira choyipa chipani Cha UTM. A usi inu munthu woyipa nkhope ndi mtima womwe munapera chilima adafa pano mwapeleka kaliat inutu ndi dyabulosi

  • @jacquelineboya9529
    @jacquelineboya9529 23 часа назад +1

    A usi ngatidi Ali dolo osangoyambisa chawo chipani bwanji or kungo joiner MCP yo

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 20 часов назад

    M.usi,chakwera,chimwendo,,kunkuyu,ndi Team Yake ndamene adapanga chiwembu kuchikangawa,amaonamgati akaphapha chilima basi sapezekaso wina owasokoneza,komwe kulikulakwisa.achitazi sindaleayi .Akanangovomereza kuti zawavutabasi.

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 23 часа назад +1

    Akulu akulu apa MCP yawonjeza .

  • @LovemoreDmphambanula
    @LovemoreDmphambanula Час назад

    Tilinanubmai kaliat sitikusiyani tikaona Inu timakumbukila tsogoleri wathu Dr skc chilima

  • @mosesmanjolo8596
    @mosesmanjolo8596 23 часа назад +1

    i'm with you 💗 a.k.a kweni

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 19 часов назад

    Michael Usi ndiyemwe adapha nawo Chilima ndiyemwe akupanga izi kuti Mayi Kaliyati amangidwe

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole День назад +1

    🔥 utm osaopa osatopa osafooka muotche police imeneyo.

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 20 часов назад

    😢😢 zikufunika ma demonstration izi anyamata ndi anthu wokonda dziko tiyeni tigwilane manja amalawi

  • @RodneySupply-tx3ul
    @RodneySupply-tx3ul 18 часов назад

    MCP ndi chipani cha nkhaza chokupha ndipo sichingasinthe sichizasintha and this is a fact its just unfortunate that Malawians sachedwa kuiwalira,why putting this party in government after all the athroceties they committed in our own eyes Dr Bakili once said kuvotera mcp ndiye kulozedwa I suppose a malawi analozedwadi ndiye muona mmene chizunzire anthu ndikupha komwe

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 часов назад

    Amene timamangidwafe ndizinyama aliyese azimangidwa basi akalakwa

  • @kaphika
    @kaphika 3 часа назад

    a Matthews Kabambe ndiye atinso? utolankhani winawu eeesh

  • @PatriciaNkhambule
    @PatriciaNkhambule 8 часов назад

    MCP you will be rewarded it's very soon

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 21 час назад

    Usi wationjeza kwambiri usaone ngati sitikudziwa walakhula dzana kwa Azima munawaveka ngati a UTM aja zonena a SG lero kuwapangiraso mulandu and usaone ngati kuti sitidziwa kuti unapanga nawo upo opha Dr Chilima pomatenga nkhani kwa Bwana kumakasiya kwa Dr Chikangawa one day uzatimve kuwawa mphamvu zimenezo zikazatha

  • @getrudeminikwa9636
    @getrudeminikwa9636 23 часа назад +1

    Tikamatche basi anthu amenewa atitopetsa serious,,usi akusewera yapansi

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 23 часа назад

    Simukudziwa kuti kutero mukupeleka Moral Ku UTM;chifukwatu apolice alibe vuto coz , amangogwira ntchito yomwe atumidwa basi. Ndichifukwa chake a Police omweo mawa adzakumangeni ndiinuyo

  • @FaliahaHassan-n4y
    @FaliahaHassan-n4y 2 часа назад

    Osatopa asagonja mai ndimuthu modzi olimba mtima ngati umapita kuleba ndiye muthu ukaope kumenyela ufulu wathu

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga 23 часа назад +1

    Yooo my country is finish😢😢😢

  • @Malani41
    @Malani41 21 час назад

    If she committed a crime it doesn’t matter what her political stature and power are. Her supporters and Kaliati better hope that the police is lying that it has evidence.

  • @BatisonKalonga
    @BatisonKalonga 20 часов назад

    Amalawi tili ndi mvuto chilichose timachilowetsa ndalale muthu akamangidwa samangidwa asanapalamule anatani kumanga akabambe or kambala tisatsogoze ndale iyiyi ndi nkhani ya police asiyeni agwire tchito yawo

  • @Mbeta-q8v
    @Mbeta-q8v 9 часов назад

    Atuluke pompapomano
    Usi ndi chakwera wakoyo somewhere you
    AMichiel usi ndi chakwera
    Mukuputayo ndiye timati
    NKHONDO
    MWAMVA?

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 20 часов назад

    Athu a UTM tinkakuuzani kuti Congress ndi yoipa. Lero ndi izo.

  • @HeyGehhe
    @HeyGehhe 20 часов назад

    Ndipo ngati simuwamasula amai tiotcha paliament muonatso tatopa nawe chikangawa wakupha iwe😊

  • @DeodataKachapira
    @DeodataKachapira День назад

    Mulungu akhululukire utsogoleri wa dziko la Malawi. Mulingo womwe umamuyezera mzako Mulungu amagwiritsa ntchito womwewo pa moyo wina uli wonse. So let God intervin.

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 23 часа назад

    MCP! MCP! MCP! chonde khalani busy ndi kulongosola Economy yathu Not kukhala busy ndi Kumanga athu ( Iwe Richard Chimwemwe banda uli ndi masiku Owelengeka ndipo Mulungu achite nawe.)

  • @ZaithwaMatchado
    @ZaithwaMatchado 20 часов назад

    Komatu asamuphe please please Ambuye mukhale nafe akweni alakwa chiani abale

  • @ChindikanChipeta-f3u
    @ChindikanChipeta-f3u Час назад

    Koma tilinanu secretary general

  • @ImmanuelndagomaKondowe-n1v
    @ImmanuelndagomaKondowe-n1v 20 часов назад +1

    Manganya injunction ya convention yamuvuta

  • @IreenChilingulo
    @IreenChilingulo 22 часа назад +1

    Masiku amathela ku chiseko asiyeni azayaka

  • @ambrozonamazemba8986
    @ambrozonamazemba8986 22 часа назад

    Mpana mathews Kabambe.. Kof aliyese ku utm ndi Kabambe eti😂😂😂

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 День назад

    Otchani police yo,mupitenso mmanyumba mwawo muotche nyumba zawo ndikuphanso wana wao Ngati m'mene achitira Wanthu aku Maputo Moçambique, apólice amocambique Ali Ndi Mantha Ndi Wanthu, Ngati MCP ikudalira apólice iphani apolisiwo Ndiye popeza Amalawi Ndi opusa khalani

  • @spargomw
    @spargomw 21 час назад +1

    Ku boma kwangodzadza Zitsiru, kuyambira mtsogoleri kufika omutsatira onse zitsiru zokhazokha. Dziko lanji loyenda ngat lilibe Mtsogoleri? Chitukuko mwaona inu mkumanga anthu? Osamamanga misewu bwanji? CONGRESS Chipani cha mbunde zokhazokha

  • @patrickkamsale6399
    @patrickkamsale6399 21 час назад

    Matthew's kabambe nde uti kape iwe😂

  • @MonicatimanyeShaba
    @MonicatimanyeShaba 21 час назад

    Asazitengele one party azazuzika nazoizi panali azawo pamenepo asayiwale or amanganyawo ngati ili pran yofinaku nthana ndi utm kambaka u vp wawowo azawona polekela ndale zotele zakele kwambili osati pano ndetizizi chilima sana chite kuphedwa milanduyo ayipeza lilti kuti amange nthu lelo mawa kuli meeting yayikulu yachipani akuwopa chani phamvu kuchuluka eti azawona polekela asiyeni

  • @blessingschimwala229
    @blessingschimwala229 20 часов назад

    Muthana nokha paja campaign wa tonse alliance munkapangira limodzi

  • @EddahKaunda
    @EddahKaunda 21 час назад

    Remember kusunga munthu mokakamiza ndimulandu so why police department akupanga zinthu zachibadzi iiiiii koma moyo ukuwawa

  • @husseinMaundala-p1z
    @husseinMaundala-p1z 22 часа назад

    Tinadziyikira dziko lathu pa Moto,,,, MCP ndi yakupha amalawi kuyiwala mwachangu,💔💔

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya 23 часа назад

    Mulipambuyo paw pa social media po ? Mapazi Anu munya simunati shupt mayi uyu amayankhula ngati chumba kd bwanji mwana wake ndi nduna aliku china bwanji osamuchotsa kt tidziwe kt awawa akuyankhuladi chilungamo awamange awa fwetseke

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 21 час назад

    Chosecho apolisi akuyenda ndisapato yophulika. Dzukani apolisi muyambe kuvhala sapato zabwino!!!

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo День назад

    Kodi a Usi apitako ku Police?
    Chonde a Usi. Pokhala Presdent wa UTM pitani m'kamuone Secretary wanu.

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf День назад

    Mdima umakulirakulira pomwe kunja kukucha. Yehova pitirizani kutsogolera ana wanu mu nyengo zowawitsazi.

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq День назад

    Km MCP ikuziwa kuti Malawi ndi ziko la democracy komatu mwala obwezela kuwawa muzalira Anu a mcp

  • @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
    @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb 23 часа назад

    Munthu akalakwila malamulo walakwa basi amayenera kumangidwa Kodi atsogoleli samamangidwa?

    • @NgeyasjuWadeya
      @NgeyasjuWadeya 23 часа назад

      Nde bwanji simudamange nduna ija idapezeka ndi ma million ku airport ija bwaa??

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 11 часов назад

    Panyopako chakwera pamodzi ndi nonse ku state house

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 23 часа назад

    Lero ndakwera transport mtengo double koma agaru awa andikwana za mamina basi, kaya alamulira zaka 1million koma azayakha

  • @DanielTwiscombewe
    @DanielTwiscombewe 22 часа назад

    Kod inu mukumawona ngat kt tikhala mbuli mpaka lit nikuwuzen ichi anthu andale dxikoli ife nianthu atendele ngat simokufuna kt ku Malawi kuyake moto muwamasule cifukwa zosezi tadxidziwa ifeso nianthu

  • @MiliamBiya
    @MiliamBiya 23 часа назад

    Kugoluza mcp muli madzi nonse tidzabweza khaza zimenezo😊

  • @GeraldMukhuna
    @GeraldMukhuna День назад

    Tiyeni kuzioneselo apa zayambika kulingazi ini go konko kuyambalelo mpaka pa 31 owo dairy abon kalindo mumachedwesa masiku zioneselo zayambalelo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 23 часа назад

    Komatu kumangidwa kwa Akweni palib angapindule koma kungotenga minyama achipha bwanji Chi Chakwera chimayenda ndi asilikali 100milliona zaziiiiiiiiii UTM

  • @BlackLingisoni
    @BlackLingisoni 20 часов назад

    Amay kaliyati amasuleni sitikuwona chowamangila apa

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 22 часа назад

    Koma amalawi tikanaziwa sitikanayika MCP pa mupando this is not freedom guys zimenezi ndi khaza ndithu

  • @VaisonKumanda-l5o
    @VaisonKumanda-l5o 23 часа назад

    A MCP momoti awone mmene zinthu zkuyendera dziko muno ali busy kumanga anthu kumeneko ndkukonza kwa zinthu dziko chibwana achyambachi

  • @IreenChilingulo
    @IreenChilingulo 21 час назад

    Ausi azapitako ku mcp okha ngati akuona ngati athu angamusate walemba madzi

  • @ElufeThom
    @ElufeThom 9 часов назад

    Boma kumalimbana ndi zimai kuyiwala komwe munatulukila 😢😮

  • @ChisomoChunga-z4c
    @ChisomoChunga-z4c 22 часа назад +2

    Mathews kabambe ndye utiyo

  • @RitaBan-t7c
    @RitaBan-t7c 20 часов назад

    MCP ili ndi mabvuto ocholuka m'malo moti mukonze zithu mukungopitiliza kuipira ipirabe Usi ndichilombo chopha athu yooo