BOMA LAMANGA MAYI PATRICIA KALIATI NDIPO ZASIMIKIZIKA KUTI CHIFUKWA CHOMWE AWAMANGIRA NDI ICHI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 553

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 День назад +32

    Iyiyi ndi move akufuna asakayime nawo pa President adziyenda ndi Bello mu thumba... 🙆‍♀️🙆‍♀️🙆‍♀️

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya День назад +11

    Eeeh Koma! There is just too much evil happening in this country. May the Almighty God come to our rescue.

  • @JosephMkuzi
    @JosephMkuzi 21 час назад +2

    Ine Joseph Mkuziwaduka Osadanda masten Sweet for sweat keep it up

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu День назад +12

    BomA la MCP ,,, mwatasa kwambili... Kufuna kubisa imafa ya SKC

  • @ChimwemweZuze
    @ChimwemweZuze 4 часа назад

    Koma ife nde zatizunga mutu msaname ,zungokhala ngati za ma aged person ndithu kuti mwina akula anthuwa abwelera ku wumwana aaaaah 😊

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День назад +5

    From Cape Town mitchells plain town centre. Chakwela ukufuna chiyani. Iweyo manganya ndimbuzi yamuthu kwambili ukuziwa kt upule sungatenge ndichingangawa wakoyo

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 День назад +8

    Iyi ndi pulani kuti asaime pa koveshoni ndi Michael usi wagwirizana ndi chikangawa

  • @Isakaymw
    @Isakaymw 6 часов назад

    Ndi plan yachikangawa imeneyo ndiyemwe wamuona Kut atha kumupasa bizy thaw ya kampeni ino.amanga bwanji Muthu opanda milandu, zake izo Ife nde boma tikusitha Patt!!?

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f День назад +7

    Manganya ameneyo,,mafuta kulibe kummanga munthu wa utm akulira maliro achirima

  • @KhadijahMuhammadah-my7lc
    @KhadijahMuhammadah-my7lc 21 час назад +1

    Never give up pk

  • @AKMASEKO
    @AKMASEKO 22 часа назад +1

    Komatu utsi sufuka opanda moto dziko lonseli sangangoma Mayi Kaliyati! Akulu anati kang'oma kolilitsa sikachedwa kung'ambika osangoti poti ndimzimayi koma ngati alakwa afunika akumane m'chigamulo osamangonyoza boma.

  • @DesireMjojo
    @DesireMjojo День назад +11

    Kalindo adanena kale izi ,sizodabwitsa

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 День назад

      Kalindo ndi Katundu he never disappoints

  • @JoelMwenegamba
    @JoelMwenegamba День назад +9

    Angofuna kuti kweni asapedze ku convention it's like government want to finish U T M. But God is watching.

  • @cuthbertjafali6059
    @cuthbertjafali6059 День назад +3

    Koma ndi chani makamaka, God have mercy on us

  • @blessingbanda6206
    @blessingbanda6206 День назад +1

    But why mukumayika zithuzi nkhope yamagazi ngati munthuyo wakhapi propaganda

  • @ShanifaMustafer
    @ShanifaMustafer День назад +4

    Our country now is more 𝕎𝕠𝕣𝕤𝕖 𝕥𝕙𝕒𝕟 𝕓𝕖𝕗𝕠𝕣𝕖

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x День назад +3

    Mulungu si James pemphero mulungu amutetezere mai a kweni ndipo mzimu wa chilima uwakanthe anthuwo

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k День назад +2

    Tru,,God z watching,,Mulungu awamenyera Mai kaliati nkhondo Ali cete

  • @AubreyShaba-b5d
    @AubreyShaba-b5d День назад +3

    Perekani chifukwa chomangira ...kungoti felony...timve zifukwa... felony sichifukwa..mukutisokoneza...

  • @EnockLichenya
    @EnockLichenya День назад +4

    Masiku atha kale awa tionana this coming year, kutha nzeru kwa Boma uku😢😢😢😢

  • @JafaliAdams-l5k
    @JafaliAdams-l5k 22 часа назад +1

    Amawonjeza kma kupanga ndale sanyozana mayi uyu akhale nd displin

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 День назад +1

    Politics yo dyetsana Manyi..
    .We ready to die for this flag
    Zachimizi
    .Lilongwe sewage kwacha down youth struggling...and you want to bring fear to my head...No ! This is not 1993

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya День назад +3

    Muja Paulos amanzunzira osatira Yesu ndi pamene Chikhristu chinafalikira kwambiri.Mungoonjejera mkwiyo wa pa 29 ndi 30 OCTOBER.

  • @EddahKaunda
    @EddahKaunda 23 часа назад +1

    History is best teacher koma kusanva anthu

  • @OmarMakawa
    @OmarMakawa День назад +1

    Mayi ameneyu nayeso ndiosokoneza achita bwno kumutapa mesa ndi amene anathandiza bomali kt likhale pa pando eya uliziwe ziko zomwevlimapanga mwina uleka

  • @GraceKamanga-k8v
    @GraceKamanga-k8v День назад +2

    Ku Malawi timayankhula Chichewa,chitumbuka atinthandauzire mlandu wake timve bwino bwino

  • @SameBanda-q5q
    @SameBanda-q5q 23 часа назад +1

    Ngat walakwa amangidwe basi bcoz nobody is above the law

  • @victoriasamarthankhata
    @victoriasamarthankhata 13 часов назад

    Ndingoziwa nawwo kuti azukako bwanji amai lero kuchitokolosi,ndadzuka ndi matha zedi😢😢😢,so God help us

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama День назад +2

    Basi manyodza dpp ameneyo lelo adziwona okha kuti boma ndi dpp chipani cha ulemu

  • @MerryBiyela
    @MerryBiyela 7 часов назад

    Good make it truth on one life

  • @SitithanaSonani
    @SitithanaSonani День назад +1

    God deliver our beloved country whr r we going

  • @EliaSiska-n6r
    @EliaSiska-n6r День назад +1

    Inka Malawian politics very few women speak out. Kaliati is a voice for women.

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 12 часов назад

    Politics in Malawi is cleartivity that dazzles

  • @SostenPiyo
    @SostenPiyo День назад +2

    Manganya akudziwa za kumangidwaku, Mulungu akuona, opposition be careful about

  • @EdsonchilongoSitoe
    @EdsonchilongoSitoe День назад +1

    Iri si boma ayi akufuna kuti kumbutsa nthawi ya kamuzu banda from mocambique

  • @AllanGonthi
    @AllanGonthi День назад +1

    Anthu a MCP ma plan awo amakhala olephera nthawi zonse adapanga plan ya Chilima anthu adawatulukiranso mwachangu lero apangaso izi anthu awatulukiranso nonse a MCP mulibe m'zeru ndale zanu ndi za anadi nokhanokha

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 День назад

    Michael Usi amadziwa kuti sangakhale president, Akweni for President,we are praying for you Akweni and our country Malawi

  • @PreciousElijahKayinga-li3cn
    @PreciousElijahKayinga-li3cn День назад +1

    Mukamabweretsa nkhani zanuzo timaona ngati mwafufuza nkupeza chimene wamangidwira koma inunso muli mbuli pankhaniyiii moti mkumakasaka mma comments aanthu

  • @TinaKazembe-l7d
    @TinaKazembe-l7d 23 часа назад +1

    Akaliyat amaonjeza kunyonza

  • @MiracleRose-f9x
    @MiracleRose-f9x День назад +1

    Kodi akufuna kumpha athu angati chifukwa chani m dima umadana ndikuujika bas tikufunabe commission of equrery

  • @victoriasamarthankhata
    @victoriasamarthankhata 13 часов назад

    JESUS JESUS INTERVINE IN THIS SITUATION 😢😢

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka День назад +2

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 День назад +2

    No good,no rest for the wicked

  • @AlfredJuliusTemboh
    @AlfredJuliusTemboh 11 часов назад

    Bwana Chakwera zomwe akupangazi adzafa ngati mwana ndipo sikale chifukwa pano anthu atopa nazo. Inu muzigona ndithu

  • @lawrencedanielmandauka
    @lawrencedanielmandauka День назад +1

    Nde mukanangokhala chete osabwera ndi nkhani zossmveka spa mudziyamba mwafufuza kuti anthu adziwe chenicheni

  • @SamuelMponda-y3d
    @SamuelMponda-y3d День назад +1

    Angofuna kupeza mpata osokoneza nsonkhano waukulu wa UTM pa 17 Nov. 2024

  • @MissiPhiri-h3w
    @MissiPhiri-h3w День назад

    mulungu chonde chonde munarenga malawi ndiinu kodi dziko ra malawi muritetedze kuti anthu anu amene munawarenga akudzuzana okhaokha inu ndi chikondi kodi munarenga ndarama ndiinu chonde chotsani choipa ku malawi ko ngati mvuto ndiifeyo chonde tikhululukireni pomupanga chakwera kuti ariramurire mumava kurira kwa aphawi yakhani mulungu mwadongosoro ranu amen

    • @JohnJohn-og8rt
      @JohnJohn-og8rt День назад

      Tupere ananena komaso phiter adadi wofa athu inu chaka chamawa uphusezo akumfunika tupere uzogoleri wabwino ❤

  • @ChimwemweSamson-l5s
    @ChimwemweSamson-l5s 23 часа назад +1

    Ndale zaku Malawi

  • @WelosChifunga
    @WelosChifunga День назад +2

    Boma limeneli ndi loipa kwambili tionetsana 2025

  • @James-w6j8z
    @James-w6j8z 9 часов назад

    Boma ili ndiloyipa kwambili don't warry amalawi tiligwesa popanopopano Muthu sumaluma Chala chimene chimakudyesa phala

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 День назад +1

    Manganya panga manyazi ulibe umunthu Chocho kumati muzakhale president

  • @GreysonChilongo
    @GreysonChilongo 23 часа назад

    MCP yikuopa chisankho ndichifukwa ayamba musokoneza mwapha chilima mwayamba kaliati nikufuna kusokoneza UTM afiti imwe a satanic imwe ba MCP agalu inu from Zambia 🇿🇲

  • @ShemjuniorMweramkulu
    @ShemjuniorMweramkulu 22 часа назад

    This is what we expected from Mcp with it's president too bad

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma День назад +1

    Ukayenda usasiye mlomo amayiwa amazitenga ngati adzao alibe pakamwa

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd День назад +2

    AMUCHITA BWINO HIM AND CHILIMA AMAYELEKEDWA KUMANYODZA MUNTHALI KA...IN SUPPORT OF CHIKWERA...LERO WADZIWONAH!!!!!!

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx День назад +1

    Akufuna manganya kuti atenge chipani kuti chibwerere ku mcp a kunama tu manganya anthu savoteratu

  • @PercivalKalua
    @PercivalKalua 14 часов назад

    Uku ndi kuwonjezela nkwiyo wa chikangawa airport.

  • @horacechera6978
    @horacechera6978 День назад +1

    Timaona ngati muzitifotokozera nokhatu nanga mukuwerenganso zomwe alanda anzanu ku page kwawo Ife tingopita ku page konko kaa

  • @PatrickKondowe-f7o
    @PatrickKondowe-f7o День назад

    It's normal ngati walakwa amangidwa ndithu. It's not politics but normal.

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 14 часов назад

      Chilikwamzako mudzaziona man

  • @EneyaManda-r1p
    @EneyaManda-r1p День назад

    Malawi
    Wachpka pamaso pa Mulungu Tikuyeñda ndi zeru zathu sitinati.

  • @AugrinNgunga
    @AugrinNgunga День назад +2

    Boma ili mulibemo democracy

  • @SamuzZimba
    @SamuzZimba День назад +1

    Sanalakwitse adziwe kupeleka ulemu Kwa akulu akhale zaka 3

    • @rodgerskampira9412
      @rodgerskampira9412 День назад

      Adziwe akulu ake ati? There is no way MCP can stop Malawians from seeking justice. Awa akupita kumapeto a nthawi yawo. Apa Amalawi taphunzirapo kuti MCP siinasinthe.

  • @judithphiri348
    @judithphiri348 День назад +3

    Awa atitha onse😢

  • @MussaMbota
    @MussaMbota День назад +1

    Azimai musanamizane zosayenda mbulanda coz mukangoziyalutsako

  • @HappinessSauzande-h3r
    @HappinessSauzande-h3r День назад +2

    Zirikotu 🙌

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 День назад

    Aaaa adzi ndidzimene kaliyati ndi malemu chilima amafuna onena analipo koma kutsamva MCP yoyipa koma kakaka idzi anthu ambili omangidwa pa dzifukwa dziiiii kufuna kuti MCP itsachoke boma koma dzilikotu

  • @AdamusuwediMandela
    @AdamusuwediMandela 23 часа назад

    Kunzuza azimayi ndi mavuto akulu kwambili kaliati amatukwana bakili muluzi koma sanammange boma la chakwela ndi lolephela atetezeni azimayi onse nzdiko muno kusaziwa ndale ndi matenda

  • @KelevraKatesa-g3z
    @KelevraKatesa-g3z День назад

    Strong we stand,free up PK

  • @Harrsoni
    @Harrsoni День назад +2

    Mulandu waukulu oponsa wakugwa kwa ndege ?

  • @LuciousMulipo
    @LuciousMulipo 22 часа назад

    As MCP tries to kill UTM and entire opposition using Kape manganya,, shame

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 День назад

    Malawi is more fire apa ndeeeeeeee zativuta basssss

  • @IsaacBauti
    @IsaacBauti День назад

    Ubwino wake bon kalido the dc mwama owooopsa kwambiri ananena kale Ndie sidzachilendo ai chikangawa paty

  • @YankhoRumwila
    @YankhoRumwila 5 часов назад

    Akudziwana awa ndi momwe amadyera. Anthu a ndale zawo ndi zimodzi.

  • @JacobVictor-z7r
    @JacobVictor-z7r День назад

    Munamutenga nokha Lazalo ku chipiku kuti akhale president wanu lero akumangansoni mukhaula naye Chikangawayo

  • @HashrouYassin
    @HashrouYassin 23 часа назад

    Awamanga chifukwa Choti anawakana chibwenzi apule,zoona mungamalimbane ndi mzimai mukufuna muzikhala busy kumugwilira kumeneko

  • @mathewsthawe5270
    @mathewsthawe5270 5 минут назад

    Kod tamakambani ndi PK apalamula mulandu waukulu mlandu wake uti felony simulandutu tanenani Mulandu wake

  • @esterechamba9343
    @esterechamba9343 День назад +1

    Azimai tiyeni tikayende mbulanda Ku mnsewu zanyanya

  • @ChisomoLester-h7x
    @ChisomoLester-h7x День назад +1

    Ndi za ndale izi muzingovutika ndinu anthu ovutika, olo kaliyatiyo akuziwa chikuchitika

  • @EmmanuelSteve-q7b
    @EmmanuelSteve-q7b 23 часа назад

    Izo ndindare manganya ndichikangawa afuna kuzunza azawo mmalo mosakha njira zotesera mavuto mmalawi muli bize kukorezer mukwiyo amalawi

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya День назад

    Can delay Change but cannot deny it.

  • @OmarMakawa
    @OmarMakawa День назад

    Azimai boza osayenda maliseche muzangoyaluka musiyen ngat mukuona mavuto gulu lake ndilomweli lomwe linalimhlbikisa zisokonezo nthaw ya pita

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet День назад +1

    Mmmm Kodi a MCP icho wakupenga nivichi

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza День назад

    Zonse zikuchitikazi akufuna anthu azikhala busy ndi kuyankhula za Mai kaliyat kufuna kuwayiwalitsa anthu za commission of enquiry

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym День назад

    Iwe kayaka tanena chifukwa chomwe mwawamangila sukunena bwanji...iwe ndi mnzako chikangawa matsiku anu awelengedwa mwazitenga ngati ndnu mashasha, daily kukacha tizimva nyasi za MCP ndi chikangawa mmmm mwanyanya😮😮😮😮

  • @CrispineBetha
    @CrispineBetha День назад

    Manganya plan akufuna akweni asakayime ku convention 😢

  • @isaaczuze
    @isaaczuze День назад

    Boma loyendesedwa ndi zigawenga komanso mbava chonchi tikavotere anthu okuti akumanga anthu popanda zifukwa zenizeni

  • @mikekaliza-bw4yg
    @mikekaliza-bw4yg День назад

    amalawi sisamapange chochi zosezi wapanga ndi usi pofuna kumulepere kuti asamenyere ufulu wa malawi basi tiwuzeni chomwe a mcp mukufuna chencheni

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c День назад

    Koma apolice amene mikugwirisidwa ntchito achipan tizaona boma likadzasintha ntchito za mcp ndizimenezo chipani chakupha iweso jezebelo ziwa kt paudindo umenewo uzachokapo

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis День назад

    Izi wapanga. Ndi manganya kuti asazaime. Pampando wa upresident pajanso ndi yemwe adampeleka malemu. Chilima.

  • @AnnahMpamati
    @AnnahMpamati 2 часа назад

    Nde bwanji mlandu woo sakuwutchula, iziituu khaza akupanga ,kod zonsezi akuchitachi akufuna chani kwenikweni

  • @supa4dupa
    @supa4dupa День назад

    Dictatorship ya Chakwera ndi Usi,zabodza zones akufuna ku opyeza opposition,MCP ya bodza,kuba,kupha,kuyambira Kuma 1960s.Ma International Human Rights ,IMF,UN,World Bank ,EU,stop donating to Dictatorship Chakwera who has crippled Malawi and it's citizens,fuel crisis,poverty,no maize ,no fertilizer, and they killed VP Chilima and others,they are abusing Malawians.Free HON Kaliati,HON Navitcha and opposition.

  • @PingeniChigwenembe
    @PingeniChigwenembe День назад

    Muthu aliyense niwofunika osamawonjeza malakhulidwe

  • @ChoopsyaLloyd
    @ChoopsyaLloyd День назад

    Ngati alakwisa amangidwe basi palibe zoti ndi mzimayi LAMULO LIGWIRE NTCHITO

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer День назад

    Bwanji osamanga anthu omwe anapha chilima nd anthu Ena aja Zinaz ndy ai srs please forgive God tichitiren chifundo mcp tatopa nay srs

  • @embersonmaonga1569
    @embersonmaonga1569 День назад

    🤣🤣🤣 10 ago ndamuona akuchoka kunyumba kwake amumanga nThawi yanji 🥺😂

  • @HaziwellLameck
    @HaziwellLameck День назад

    Cholinga chawo akufuna asakayime nawo PA u president

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 День назад

    The Elect the worst to lead us,kodi akuwona ngati dzikoli la ambuye awo

  • @ShareefAlli-m4l
    @ShareefAlli-m4l День назад

    Kufuna kuwononga UTM uku, Eshhhh koma kumalawi amwene

  • @Chikwawa
    @Chikwawa День назад

    Mayi a Kaliati munakatenga mfiti ku church kuti adzazunze anthu osaoka, onani akumakumangani komanso kumadyanso ena mwa inu. Munatenga zosayenela kuzibweretsa ku dziko.

  • @AllanBanda-x5p
    @AllanBanda-x5p День назад

    But what's happening in Malawi
    😊😊😊