CHAKWERA WAKHAZIKITSA COMMISSION OF INQUIRY IFUFUNZE ZA IMFA YA CHILIMA NDIPO WAIKAMO ANTHU AWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 150

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 часа назад +15

    Akungofuna alepherese mademo akupusitsa anthu chabe MCP simukuidziwa mwina

    • @honmitrus
      @honmitrus 2 часа назад

      Zoonadi

    • @BlessingsMosesChirwa-eu2ye
      @BlessingsMosesChirwa-eu2ye 11 минут назад

      Kma sivikuveka kd anali kut nthawi yoyesi pangengo yose

    • @BlessingsMosesChirwa-eu2ye
      @BlessingsMosesChirwa-eu2ye 4 минуты назад +1

      Kma nizoona anthu awa aya nkhula nthawi yaitali ndye kuyankhapo kwawo kwalelo sikoveka pati tasowekemala mayankho awo nthawi yaitali ndye tatumizaniso zithu zoveka kwamalawi

  • @JamiesonKaunda
    @JamiesonKaunda 2 часа назад +6

    Ku Malawi 🇲🇼 kulibe president ayi!!! Koma mbava ndi okupha anthu chikangawa

  • @DicksonGomani
    @DicksonGomani 2 часа назад +7

    Km atulutse. Black box ndiyomwe ikufunika umboni uli mmenemo. Zopusa ayi osamatiputsa ife😢😢😢

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 3 часа назад +7

    Palibe chomwe Chitaphulepo inu izi ndikukuuzanitu

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 2 часа назад +6

    Kuopa mademo kumeneko, president opanda mnzeru.

    • @FrankMankhokwe
      @FrankMankhokwe 39 минут назад

      Iwe umaganiza mopepera inquiry yakhazikitsidwa monga momwe anthu timafunira pano wayambapo kulubwalubwa nzeru ulibedi

  • @LukaAfromad
    @LukaAfromad 2 часа назад +3

    Yabodza imeneyo nthawi yonsei amadikira chiyani?😭😭😭😭💔💔💔

  • @opportunityinternationalma3892
    @opportunityinternationalma3892 55 минут назад

    I'm happy kuti Anamiwa alimo mwina winiko akhoza kuchita manyazi pamenepo

  • @OwamThoko
    @OwamThoko 2 часа назад +3

    Asa khe anthu ochekela zipani zonse.ma church.kubanja la ofeledwa.ndi mabungwe osiyana siyananso komanso mukhale atola nkhani amaradio osiyana siyana ndi mamfumu osiyana siyana

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi 41 минуту назад

    Aku banja mulibemo Aku mpingo mulibe Aku chipani mulibemo and Mr kalindo mulibe asakheso bwino

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma 2 часа назад +3

    Chakwera wakhazikitsa bwanji commission of enquiry koma wopha chilima niweyo usamale kwambiri

  • @joebonface4443
    @joebonface4443 2 часа назад +3

    Komaso why have they prioritise kumanga Patricia Kaliati then nkumatulutsa Commission of inquiry. Why??

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa Час назад

    Osalola ayi adikile mademo kenako ikwaya yanuyo zopusa kuona kuti sizikugwilizanaso continue mademo asathe

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 часа назад +4

    Ngati ili ya Fake Commission Of Inquires imeneyo Malawi ayidziwa kudzera Ku BAKILI MULUZI TV NDI Limpopo FM WITH Mtanyiwa.

    • @joebonface4443
      @joebonface4443 2 часа назад +2

      Ntanyiwa wanena kale dzulo kuti akhazikitsa enquiry imeneyo chifukwa chothawa ma Demo.

  • @EthelChinyama-u8u
    @EthelChinyama-u8u Час назад

    Ine Kawanga Makwacha from KU pamenepa apre apanga chiganizo chabwino kwambiri kuti nkhani ifufuzidwe mwamachawi chilungamo chiyende ngati madzi.

  • @LevieMwanayaya
    @LevieMwanayaya 44 минуты назад

    Azipani akhalemo,akubanjanso akhalemo ,winiko akhalemo amabungwewo akhalemo okwanila nt Anamiwa ndi akariwa okhao ai,even antolankhani akhalemo

  • @StevenKupheka-k6b
    @StevenKupheka-k6b 2 часа назад +4

    I think the air which chakwera breath is mixed with weed

    • @Chancenyangulu
      @Chancenyangulu 50 минут назад

      😂😂😂😂

    • @StevenKupheka-k6b
      @StevenKupheka-k6b 43 минуты назад

      @@Chancenyangulu 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 bro serious am not lying why asakha commission of inquiry amayembekeza chan weed is breathing by chakwera

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi 38 минут назад

    Namiwa usakhale Kuti akugula osalola Kuti upite wekha Aku banja ,Aku mpingo ,Aku chipani ndi zipani Zina atengekoso anthu

  • @AfricanChina-im1op
    @AfricanChina-im1op 2 часа назад +6

    Wakopakopa athu omwe wasankhawo ameneyo

  • @GaliGali-uu3yb
    @GaliGali-uu3yb 2 часа назад +1

    Voice ngati cardinal 🎉

  • @StevenTembo-mb7rm
    @StevenTembo-mb7rm 58 минут назад

    Ayikemo inkosi ya makosi Gomani komanso akubanja a wina aliyense amene anafa pa ngozi ija otherwise ndi zopepera zeni zeni

  • @isaacmhango-h8z
    @isaacmhango-h8z Час назад

    Chilima anagwa ndi ndege basi may his soul rest in peace Ngati anaphedwa anaphedwa ndi ndege, Kafukufuku wa nzelu ngoyamba uja azibusa amayidziwa ndege?

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 2 часа назад +2

    Koma mademo alipobe palibe kusintha coz zifukwa zopangira mademo ndizambiri

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 18 минут назад

    Ndichifukwa chiyani sanayikemo aku Banja komanso a zipani zosusa

  • @SALIMASSAN-vr8ld
    @SALIMASSAN-vr8ld Час назад

    Kkkkkkkkkkkk km chakwel ndigalud srs thaw yosey munalikt kuwop maden kumenek

  • @MakeSunshine100
    @MakeSunshine100 Час назад

    Ngati pali judge wa corrupt. Wokhalila milandu ndi amene akamupezayu kuti atsogolele commission of enquiry. Abale anga, musayembekezele zambiri. Mau anga mudzawakumbuka.

  • @chrisneySwanepoel-yu5vd
    @chrisneySwanepoel-yu5vd Час назад

    Afufuza bwanji opanda black box, akuthawa mademo omalawi osalora zopusa

  • @janschutte7515
    @janschutte7515 2 часа назад

    Enawo akufuna ndalama pomwe akubanja, akufuna chilungamo. iyi osayikhulupilira ayi. koma boma lidziwe kuti God he's watching you.

  • @ThocoThawan
    @ThocoThawan Час назад

    Zaziii musiyeni mulungu ndamene akudziwa

  • @YusufJumbe
    @YusufJumbe Час назад

    😂😂😂😂
    Odi ndipite mkauluke ine

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate Час назад

    Aaa zamanyi basi awopa mademo akubwerawo pantumbo panu nose a MCP

  • @JafaliAdams-l5k
    @JafaliAdams-l5k Час назад

    Congrats Mr President mmm anthuwa awonjeza

    • @ClementinaViola
      @ClementinaViola Час назад

      @@JafaliAdams-l5k nde akugulirani mashon? Za ziii

  • @GraciousKadzuwa
    @GraciousKadzuwa Час назад

    Too late it will not change anything

  • @Alexkalonga-t9s
    @Alexkalonga-t9s 2 часа назад +1

    Km bwanji wachedwetsa chonchi ife chilungamo tinachiziwa kale zoti anapha

  • @brianjames211
    @brianjames211 2 часа назад

    Why the president is choosing what or who must be involved in the committee, it should have been the Malawi eni ake and all non governmental institutions, why Jabba alide out of all the pple as a chair? Awagula kale kale

  • @BAULENIBAMUSI
    @BAULENIBAMUSI 43 минуты назад

    Zabodza izi cz it's part of campaign so tisamale kwambiri chifukwa asankha anthu ni iyeyo

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo Час назад

    Anamiwa musavomereze munthuyu Chakwerayu ndi mfiti

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani Час назад

    Zoti ku Malawi tili ndi mtsogoleri ine ndimatsutsa koma tilindi Mbava,chigawenga,Satanism Chakwera

  • @TristerLitanda
    @TristerLitanda 2 часа назад +1

    Shabwino. Ine pheee kumastand kudikila report

  • @Belinda-c6e
    @Belinda-c6e Час назад

    Ndiye nanga buanj sanaikemo osusa boma kma chakwera akutitora kwambiri kma mulungu akuona chilichonse

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 2 часа назад

    Zaziii!!!!!!! Mbuzi zawathu,,,kutiveka chijuzi kumaso chofiira cholemba nambala 2.mwatitola.

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 Час назад

    Zikomo bwana Mtanyiwa poyineneratu nkhaniyi

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 часа назад +1

    Wina akuopa ma demo uku

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga 2 часа назад +1

    iwowo apresident asankha bwanji komite yoti afufuze zirongosoka apa ndizowona koma akunama murungu simunthu

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 Час назад

    Chomwe munkafuna ndi inquiry ya ndege n akuikirani anthu omwe akhala akuyankhulitsa pankhaniyi like anamiwa ndiye pano mukutiso chani, anthu oipa inu, musa zomwe munkafuna akupangirani so mwayambaso kutukwana, chomwe mukufuna ndichani😂😂😂😂😂😂😂 chitani manyaziiii

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s Час назад

    Osaika azipani zinazo bwanji poti nkhondoyi amathandizana anamiwa ndi amzawo

  • @Enelles-h6v
    @Enelles-h6v 52 минуты назад

    Kkkkk koma chakwera ukutenga amalawi kupusa chani

  • @alickziba6756
    @alickziba6756 2 часа назад

    Wa utm, dpp,udf,afford, akubanja a khalemo. Apo biiii, deeeeee

  • @KaitanoMafuli-g3s
    @KaitanoMafuli-g3s 2 часа назад

    Ndiyamika Mulungu pakukhazikisidwa kwa commission imeneyi, bola anthu amenewa asagulidwe posokoneza choonadi. anthu mwasankhidwanu
    Ngati simugwira ntchito ya ambuye muyembekezere chilago chosatha.

  • @MercyKziphondo
    @MercyKziphondo 2 часа назад +1

    Ndukaika zoti anena chilungamo

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 2 часа назад

    What about achibare

  • @AlexBanda-d5v
    @AlexBanda-d5v Час назад

    Nthawi yonsei amadikira chan
    Nanga brackbo

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s Час назад

    Zauchitsiru zimenezo Asia anthu ofunikila ochuluka

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola 2 часа назад

    inu akufuna atinameze uyu Kalu wakupha uyu anthu amene anapha chilima tikuwaziwa ena ndi akunja ena ndiyamalawi omwe Ali asikali komaso chilungamo chikubwela 2025 ndi chipani China osati MCP ayi

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka Час назад

    Kodi MWATI mumafuna chani?
    Inu a opposition ndale zakukanikani basi

  • @DenesceFredericks
    @DenesceFredericks 43 минуты назад

    Umakana paja lero ukuopa madem galu iwe utuluse black box zonse zili momo mpaka miyezi 4 woipa iwe

  • @ChipiliroSpencer
    @ChipiliroSpencer 2 часа назад +1

    Zompusa bsi commission yanji yopandamo akubanja aathu omwe anafawo kungosakha athu oti sitikuwaziwa akanatenga akubanja ose aathu omwe anamwalilawo komaso akulu akulu achipani cha utm komaso a opposition akhale nawo mu commission imeneyo osati zimenezo zaziiii kufuna kupusisa amalawi bsi tizapanga commission yathu yeniyeni tikasitha boma 2025 pano musatipusise

  • @ChimwemwePhiso
    @ChimwemwePhiso Час назад

    Kkkkkkk koma maganya😅😅😅😅😅

  • @FosterDziwani
    @FosterDziwani Час назад

    Aaa nthawi yonsey analikuti

  • @LawrenceJana
    @LawrenceJana 2 часа назад +1

    Bwanji achita izi kutsatila atamumanga Kaliati?
    Adzifufuza atamumasula chifukwa pamenepa Pali ?

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 2 часа назад

    Mademo what's the way forward

  • @michaelchimwala-x8t
    @michaelchimwala-x8t 2 часа назад

    Anthuwo achepa komaso posankhapo amaganizila kuti anthuwa athandiza nanga amabungwe enawa

  • @AmanaKaisi-p3e
    @AmanaKaisi-p3e Час назад

    Amalawi musakayike ziyenda ndithu, palibe za ma bread kukamwa apa

  • @HendersonLuka-f5j
    @HendersonLuka-f5j Час назад

    Akufuna ampake ndan ife tikuzwa kut ndiyeyo2 anapha

  • @PeterTens-hu9qw
    @PeterTens-hu9qw 2 часа назад

    Anakasiya akumabanja nawoso akhare ndianthu awo momwemo afufuzire rimozi

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo 2 часа назад +1

    Thawi yonseyi amadikila chani 🚮🚮🚮zikutathauza kut madandaulo ayise a Malawi tikamadandaula kut ife a Malawi tikuvutika amamva et

  • @alickziba6756
    @alickziba6756 2 часа назад

    Pamene commission of inquiry ikuyamba ntchito yo fufuza kwinaku mademoso a nyoooooo!!! Azichitikaso. Palibe kugona.

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 2 часа назад

    Tiwone zimene mutazakambe , anamiwa anuwo ali momo

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix 2 часа назад +1

    bwanji akubanja ra anthu ofedwa muikepo akuba rachirima osati mafumu ai mungawagure mafumu kuti akukonde mbava iwe

  • @InnocentPotani-lv1on
    @InnocentPotani-lv1on 44 минуты назад

    Akatero awapatsa zindalama zambiri kuti atinamizeso,mmxiee

  • @LingstoneManda
    @LingstoneManda 2 часа назад

    Sorry is tooooo late looks like he is ignoring to do that,,,,😂

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 2 часа назад +2

    Akubanja bwanji 😢

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 2 часа назад

      ku Malawi nkosekesa kwambiri, nonsense 😢

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 часа назад

    Nde azipan otsutsa sanawayikeko bwanji

  • @PraiseKaliwo-x4l
    @PraiseKaliwo-x4l 2 часа назад +1

    Nthawi yonseyi amatani? Ndipo wasankha anthuwa ndindani?

  • @James-v8v8d
    @James-v8v8d 13 минут назад

    Inu mumafuna commission of enquiry Kuti I chitike ndipo inali topic mumisonkhano yanu ndipo mimati tiwapemphe a pile akhadzikitse commission of enquiry Ngati , pano akhadzikitse alakwanso mmm

  • @FiskaniChirwa
    @FiskaniChirwa 2 часа назад

    Uku ndikuzemba chilungamo chowoneka,

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 2 часа назад

    Iyeyo amadikira chiyani nthawi yonseyi

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere 2 часа назад

    😂😂😂 Chakwera ndi Machine

  • @HeyGehhe
    @HeyGehhe 3 часа назад

    Ndipo afa imfa yomvesa chisoni😊

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 2 часа назад

    Chakwera pamtumbo pake ndithu ndichitsiru kwambri

  • @aliwilson7705
    @aliwilson7705 2 часа назад

    Mademo koma akupitili mawarino ku ntchewu

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 часа назад

    Galu kobasi bwanji sadasange akubanja

  • @FletcherGuzani
    @FletcherGuzani 2 часа назад

    Aiwalamo kuika modzi ka Bon kalindo

  • @giftkayome3568
    @giftkayome3568 2 часа назад

    Kuchita kukakamidzidwa mwina wache sankafuna kaya amabisanji

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g Час назад

    Mademo alipo pa 30

  • @malawijohn5297
    @malawijohn5297 2 часа назад

    Achita bwino kwambili apule pomvela pempho la amalawi pa nkhani ya ngozi ya ndegeyi mwina anthu angayankhule dzinza tsopano

  • @malonekalindaj324
    @malonekalindaj324 2 часа назад

    anaikaposo any member from either dpp, udf utm or aford

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 2 часа назад

    Nkhaniyi ikufunika kuwafusa apule Kuti ndimwana wandani amawanamiza maboza Kuti ndege inafika ku mzuzu

  • @MabvutoMwakalinga-yl3ft
    @MabvutoMwakalinga-yl3ft 2 часа назад

    Chiphimba mmaso ...
    Kuopa mademo
    Osafooka
    Osaopa
    Osatopa

  • @ChifundoChiwambo
    @ChifundoChiwambo 2 часа назад

    Mademo alipo yes or not

  • @BrownMaseko-f2h
    @BrownMaseko-f2h Час назад

    Nthawi yoseyi umatani chakwela umatani kt ukhazikitse commission of Inquiry? Koma chakwela iweyo umulungu ulibe kat ulawe upuresdent chf chilima kupanda chilima mkanakhara ndani inu

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 Час назад

    Mpakananso a Namiwa??

  • @aishakachiwale
    @aishakachiwale 2 часа назад

    Mukhale akubanja ndiomwe angatipatse chilungamo amalawi

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 16 минут назад

    Yemwe akuyimila akubanja ndindani?

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke 2 часа назад

    Amafuna asaikemo patricia kaliati kkkkkkkk eeeeeeh

  • @AmosNjoka
    @AmosNjoka 2 часа назад

    Km apange moopa mulungu

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 2 часа назад

    AAA akubanja alikuti????

  • @UmaliMakadali
    @UmaliMakadali 2 часа назад

    Commission equire ya bodza

  • @FabianoJohn-t9o
    @FabianoJohn-t9o 2 часа назад

    Apapa ife ngati amalawi,tikupepha anthu omwe asakhidwawo kuti akaunike mosamala kuti akamabweretsa feedback ikhale yoonad, kapena kut yazoonad zikomo

  • @LawrenceJana
    @LawrenceJana 2 часа назад

    Kunena zoona nkhaniyi sitinayilandileyi.
    Nanga mosemuja zoona?

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 2 часа назад

    Zamanyazi