We know that you, Bakili Muluzi TV, are king of kings of history and whatever you report on Dr Chilima's death is true. May God bless and give you long live. May Chilima's soul rest in peace.
Thanks to to bakili muluzi tv.they are serious indeed to continue with sacrifice like they saidBut Malawi need to wake up.MCP must be canceled from Malawi as a politically
Bakili muluzi tv ubwino wake nkhan zanu sumangopeza ndipo zinthuzo zimaziyabkhulanso zokha zomwe Ainu akewo zimachokera mkamwa mawwo keep it up bakili muluzi tv
That time Symon and Kandal were composed & released a morale song @Chilima nda Chakwera agwirizanaa!!! Ayambapo manong'onong'ooo!!!! 😭😭😭😭 rest well skc!!!
Ubwino waBakili muluzi tv ndiumenewu iye Lero sanayankhulepo koma tazionera tokha ndimaso zomwe zimakambidwa ndi a MCP akanganyawa zoona mission yawo adayamba 2022 Lero amugoneka mzawo mmmm only God knows 😭😭😭😭
Malawi is no longer Godfearing nation because our leaders in all sectors Lack philanthropy and patriotism. May God rebuild and guard Malawi against lucre minded spoilsports!
Umboni ukufumbuluka oka chakwera ziko muliva kuwawa thanks bakili muluzi TV your very perfect person ❤❤❤❤
Ambuye akuona ndipo akudziwa chilichonse,RIP Dr Chilima ,moyo ukupweteka nsaname😭😭😭
ndipo mmene moyo ukupwetekeramo,mhhh only God knows and God will take action on this chilima assassination
The home of history bakili muluzi tv we love you brother and never give up and don't change the name of the channel
Zoonadi
Abale anzanga chakwera iois completelly bad
Good
Mmmmm, you keep history, you deserve an award, home of truth. Keep it up, may God protect you brother.
Ndipo amasungila mkuluyi
History is the best teacher. Rest well Chilima 😢
bakili muluzi TV ndimakupatsani ulemu watsikunditsiku wamwambayo apitilize kukuttezani kuti akanganya amenewa zomwe amafuna kwainuzisazateke Coz matidziwitsa zobwisika zomwe sitimadziwa love youuu
Zastrop channel imakupasa ulemu iwe ndi wani
awa anachita kukhoza koma guys moyo wanzako kumupha chonchi 😢😢mulungu ayankhe for sure
What goes around comes back around let's wait and see the truth will come out very soon please God help us
Iwe ndakatundu. You deserve 100k + subscribser within before tomorrow Sunday 16 June 2024
My eyes are now open,,😭😭mwana osalakwa wafera kufuna kutumikira a Malawi
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
History is repeating itself Chilima your gone but God will expose them.
I believe so too
Keep it up anthu asatinamize kuti akugwirani, mudzitulutsabe mavidiyowa amve nyunyunyu agalu amenewa
😂😂😂😂
This is true story may God bless you and protect you Brother go forward Bakili Muluzi TV 🔥❤❤❤❤ umboni uyuyu ndi gwero la umboni onse
He was hero ambassador to the youth of Malawi rest in peace Saulos Klaus Chilima 🙏💔
We know that you, Bakili Muluzi TV, are king of kings of history and whatever you report on Dr Chilima's death is true. May God bless and give you long live. May Chilima's soul rest in peace.
Ana ama 2000 Voti yanu zayiyendetseni bwino (RIP Chilima)
Ndipo kwambiri tu mmm
The pain am filling eish 😭💔💔🙌🙌🙌
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Thanks to to bakili muluzi tv.they are serious indeed to continue with sacrifice like they saidBut Malawi need to wake up.MCP must be canceled from Malawi as a politically
Our best tv in malawi ❤
Bakili muluzi tv ubwino wake nkhan zanu sumangopeza ndipo zinthuzo zimaziyabkhulanso zokha zomwe Ainu akewo zimachokera mkamwa mawwo keep it up bakili muluzi tv
Gottan Hara amuna ake amapha anthu nowonder she has a stone heart.
Afana oganiza bho aja basi achakwera apereka nsembetu 😭😭😭😭
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 chilima uja anangomulodza guys coz zonsezi amazinva and ankaziwa kut anthuwa sakumufuna koma nchifukwa chan samapanga chitsankho chotuluka nthaw yabwino? Even kusalankhula lankhula kuja kunali kulozedwa guys😢😢😢😢😢😢😢
For sure
Ineso ndikuganiza chocho man
Zovesa chisoni abale😢😢
Makhwala anagwila tchito😭
Nanga apa utumizaso aporisi kuti akamanga ndani chirungamotu tawonanitu zobisika zaururika adamangadi
Mr chakwela , where is sidick mia ? And where's mr saulos Cláuds Chilima ?
Choyamba kumangidwa pansi pano chimene kumwambaso chinamangidwa chinali mgwirizano umene anasayinilana... Ambuye tiwoneni Ife ana Anu...mtima ukuwawa, pena ngati maloto 😭😭😭😭😭😭💔
Goodness gracious. Politics man, rest well Chilima.
Ine mawu ndilibe ndipo sinszaiwala
Mxiiiieee my Hero is gone , politics will never be the same , my heart will never stop crying for this VP, this History will never be forgotten
God bless you BM,,thx for keeping the records,,keep it up!God to protect n enlarge yr territories in Jesus christ name
Wow I was waiting for this
What a sad ending for Chilima
...and for malawians
Is so sad
home of the truth and best tv i love you and i will love you ever.
The home of history
R I P
That time Symon and Kandal were composed & released a morale song @Chilima nda Chakwera agwirizanaa!!! Ayambapo manong'onong'ooo!!!! 😭😭😭😭 rest well skc!!!
History repeats itself
Thanks very much for the video
May our almighty Jehovah God bless you and your family and give the spirit to the family of chilima
Best tv bakili muluzi❤
At we have to continue sacrifice 😢😢
Asatana awa a satanic chilima got majority apanga I sacrifice devils💔💔
😢😢😢
We love you Mr bakili muluzi tv continue
History is the best teacher 💪💪💪💪
MHSRIP 🌹 and may the souls of those tht passed with him rest in peace 🌹
Koma iweyo ndikatundu ase ndipo u deserve respect,,,, anthu akulephera kuvindikira bonza koma sizikutheka
But I think this guys really respected anthu amulungu ndithu. Angokhala kuti abusawo eeh. Afuna kutukwanitsa chiutaa
Ifeyo m'dima ukutichoka kamba luso komanso chilungamo chanu
Peter Muntharika ananena kale Koma kusanva
Eishhh koma zovuta bwanji
TV imene ikutsegura maso amalawi ndi ino❤❤❤
apa ndiyedi tamva chilungamo mulungu akhale, ndipo akutetezeni Amen in jesus almighty name 🙏
MCP ndi ng'oma za mmabango 😢😢😢😢
Tikuweta mikango
You are the best journalist who I ever seen.
Bravo Bakili Muluzi TV..Never stop informing Malawians
I love this tv
History it's best teacher l love you bakili muluzi tv
Aiiii zikomo bambo Chakwera pamodzi ndi MCP yonse ife kuno ku Ntcheu Central BAWI pankhumba tikuti Zikomo!!! 🙏 Rest well Bambo Biyeni SKC💔😭😭😭😭
Pa nkhumba....missing that area
The home of history best TV ever
Pambuyo a Biwa akuti anthuwa ankagwirizan shame on Mibawa (Gwedegwede program).
Just imagine after all then amuchosa last minute before next year elections ...anthu oipa kwambiri
Chilima was indeed going through alot. Ma guys a mcp awawa really maltreated this guy. So sad.
Ndi chi hule chimene mmati chogatanicho eeti okay Okey hule amaneyo mulungu Akuona zonsezo 😭😭😭😭😭
Mi staying on this channel 💪💪💪
Kufera chilungamo ndipo chilungamo sichifa ife tizausa mkwiyo umeneu🇲🇼😠😠✊️💪🏋
Eeeh these guys are unpredictable indeed 🙌🥺💔 akukanadi zinthu zoti anagwirizana💔🙌
Chimwendo Banda Mulungu Akuone kwanbiri
akut we have to continue sacrifice 😭😭😭😭.
Ayi nsembe zupelekedwadi. ubwino wake muzazivotera nokha. R.l.P chilima😭😭😭😭😭
Akudalila kubela awa ,pofunika tikavote athu awa Sali bwino olo pan'gono
Ka video aka kandililitsa.?????????????????????????????????????.
This video titha kuona why anatumiza asilikali 8 munthuyu anazungulilidwa ndi mikango
Abale anthu mwapheranji mukadangowauzakutizathapo km paka kuchita chozinga 😢😢😢😢😢😢 chakwela Why
Koma chilima kumene uliko limodxi ndi amzako onse amene mwatisiya chonde bweran muzakanthe anthu amene atenga gawo paimfa yanu plz mitima ikuwawa iyi💔💔💔
Boss ma video anu azitalika ndithu akumatiyiwalitsa zambiri tikamaonera,,,keep on posting long live this channel 💪💪💪💪
Keep the fire burning Bakili tv
Keep it burning bro bmtv may the good Lord bless you where ever you are
History is the best teacher ever indeed ♥️♥️♥️♥️♥️♥️🏋️🏋️🏋️🏋️
Anthu ankhanza mpaka kunenaso verse 😢
Sakuliziwqnso vesilo
Our best channel
Ubwino waBakili muluzi tv ndiumenewu iye Lero sanayankhulepo koma tazionera tokha ndimaso zomwe zimakambidwa ndi a MCP akanganyawa zoona mission yawo adayamba 2022 Lero amugoneka mzawo mmmm only God knows 😭😭😭😭
😭😭😭😭😭😭😭😭 atimpera Muthu osalakwa
Moyo Ukundipweteka naineso over Chilima's death though im a Zambian 😭😭😭
Keep it up brother man ,more fire brother man!!
The Greatest chanel we love you big brother
Malawi is no longer Godfearing nation because our leaders in all sectors Lack philanthropy and patriotism.
May God rebuild and guard Malawi against lucre minded spoilsports!
@augustinechibbalazi8897 Malawi was never a god fearing nation boss.
keep updating us bro & may God bless you
ndie wina uzit nyonyonyo!!!! ngati sukumva
God is faithful,tsiku lina amalawi azadziwa chilungamo 😢
Best bakili muluzi TV
Still keep fire burning. big up bk tv
Maumboni akubwera ndithu
Thank you biggy
Viva bakili muluzi tv ✊
Eish ambuye akuona chilima R.I.P😭😭😭😭
Anthu awa sakuyenera afike 2025, dziko liyake moto mpaka Chakwera atule pansi.
Please please tisalole kuti afike 2025.
Mzimu wa Saulos Chilima uziwusa muntendere, ndidzamukumbukira moyo wanga onse 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Best TV ever in Malawi
Eeeish zosakhala bwino, this is too bad 😞😔
Keep doing good job my brother 😢❤
RIP chilima..your honest will save you in heaven, let them be
Keep it up kutisegula mmaso apapa chikufunika ndi international independent body ifufuze za imfa yawanthu wa basi or else achoke yekha chakwerayo
Chilima my vote 💔
UTM WILL RULE MALAWI
I doubt😅
Abwino sakhalisa Chilima ❤ aaaaaah
Best TV , chilima amuphela chifukwa cha utsogoleli 😭😭
Mawumboni apose apa ng'alurani big musasiye chilichose
History Repeating he self from evil party MCP
Amalawi tinadzirakwira tokha
Tikufuna anthu ngati inu in Malawi we love you brother god bless you
Best teacher
Amene akuziwa gulu loti lingandiphunzise kumenya nkhondo chonde andiziwise
Eisenhower Mkaka, Chimwendo Banda, Moses Kunkuyu, Zikhale Ng'oma, Catherine Hara, Chakwera what is your mission in Malawi?