ZODABWISA ZIMENE ZACHITIKA PETER MUTHALIKA ATANGOFIKA LERO KU MWANZA EEH KUNACHEMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 ноя 2024

Комментарии • 143

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 2 часа назад +25

    Koma kuzangolengeza kut chakwera wawina mmmm mademo azavuta chifukwa pa ma president onse amene akukondedwa nd amalawi nd muthalika bas ndpo wawiniratu uyu

  • @MarriamVincent
    @MarriamVincent Час назад +2

    APM MWAYENELA . We can't do mistake twice I'm so proud of u APM ❤❤

    • @Janaphiri
      @Janaphiri Час назад

      Udavotera pita iwe 2025 ulilamso

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 часа назад +6

    Father of the nation
    Katundu machine ❤

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 2 часа назад +2

    Ili ndiye booooomaaaa la 2025 Peter Muthalika is my vote DPP woyeeeeeeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🥳🥳🥳🥳🥳🎉🎉🎉🎉🎉

  • @SamChimwala-nb1en
    @SamChimwala-nb1en Час назад +1

    Koma nawenso wamakosana network ikukuvuta... ukuyuza itel ert😂

  • @OSCARBANDAH-x2g
    @OSCARBANDAH-x2g Час назад

    APM fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
    Sizimene tikumazimva akuti ma Speech a president koma manyaka enieni

  • @KossimasiMaluwa
    @KossimasiMaluwa 2 часа назад +9

    apapa Bola kumasakha anthu okalamba omwewa chifukwa sapanga zibwezi achinyamata akumachusa zibwezi kwambili osavotelaso mcp muzatiphesa tose Dzikomo

  • @DuncanThambala
    @DuncanThambala Час назад +2

    Muthalika grow old but still remain wise and leadership blessings in him not coward chakwera the don't know kkkkkkkkkkkkkkk.

  • @HannahKamphulu
    @HannahKamphulu Час назад +3

    Amene zumunyasa akakolope nyanja,atifukitsa ku dziko la chilendo bas tizisekera zimenezo mkumati zinthu zilibwino tiyeni tiziuzana chilungamo

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Час назад

    ❤❤❤ Peter muthalika ndi yekha azalamulira dzikoli

  • @AnsaAsante
    @AnsaAsante 2 часа назад +5

    Soka kwainu amene mukuti apm ndinkhalamba ifetu nkhalambayo chomwe timaisungila ndichemenecho imatiuza kuti mcp ndiyakupha tikakanila koma lelo mmmm amiya bwanji chilima bwanji nkhalamba yaife ilibe ufiti simakwanisa kudya zizukulu 😂😂😂 ukumva bwanji neba

    • @Janekapats
      @Janekapats Час назад +1

      😂😂😂😂😂 ndipo live nkhalamba yathu ilibe ufiti sure🔥🔥🔥

    • @gkay-striker
      @gkay-striker Час назад +1

      True 💯

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 47 минут назад

      Adad sanaphe munthu

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 2 часа назад +2

    Inva voice iwe a true leader he is mutu amkaba koma dziko limakomera onse osati zinati kutiliza kuti mpeeee no fuel no fertilizer no medication no passport chimanga kukwera kuti zinveke bwanji boma labvizungu koma everything anafeliya anafeliya azipita iiiii we need a relief

  • @SueWahna-y8m
    @SueWahna-y8m 52 минуты назад

    Ukalamba opasa chidwi ukalamba odalilika ukalamba opasa chilimbikiso fada vote yanga ikudikila inu 💙💙💙💙💙💙💙

  • @Samkay66
    @Samkay66 2 часа назад +3

    Kuli Manoma , Nde kuli Dpp, Nde kuli Asilikali kaya Nyimbo zawo amapeka Ndani??? kkkkkkk Anthu amenewa Amakhala ndi Nyimbo zawo zawo man

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga Час назад

    Katundu omangilila ndimawaya APM my vote ❤❤❤

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 Час назад +1

    I love this guys .God bless Malawi keep it a land of peace by providing DPP back.

  • @AlexKanyumba
    @AlexKanyumba 2 часа назад +5

    Chakwela. Anali mphawi mpake dziko kusayenda bwino akungoba ndalama

    • @MathewsDyson-z6z
      @MathewsDyson-z6z 2 часа назад

      Ndiye bingu anali wolemela? Ndinu makape a DPP ulibe mfundo iwe chisilu chamunthu

    • @ReginaMzunga
      @ReginaMzunga Час назад

      Iwe nde ukhale ndan

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Час назад +2

      Sinkhani Yokut Chakwera anali mphawi koma kut, Boma ili langozaza ndi anthu wamtima wa kuba kuyambira president.

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 Час назад

      ​@@MathewsDyson-z6zchikangawa party yapsa mtima after kumwa magazi aku chikangawa
      Iwe nde galu kanyimbi onunkha mmakwapa satana osaseta

  • @SamsonSelevasio
    @SamsonSelevasio Час назад +2

    Mkango bambo 🔥🔥🔥🔥✅✅

  • @mikekaliza-bw4yg
    @mikekaliza-bw4yg Час назад +1

    Dpp my vote ndikamavera nkhani za dpp ndimava kukoma ngati nadiya peyala

  • @LauraNtala
    @LauraNtala Минуту назад

    Vote yanga ndaisunga pabwino..... Adad woyeeeeeeèeee

  • @immikhonat
    @immikhonat 32 минуты назад

    mutharika ndi wobwino koma wokaramba kobasi tsapano .....party needs a new leader...if it needs to see any future

  • @ShillaShamil-v2y
    @ShillaShamil-v2y 52 минуты назад

    ADAD 💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @JoãoChirwa-n3l
    @JoãoChirwa-n3l 3 минуты назад

    🤣🤣🤣🤣akulongeza katundu wayo azipita awa atikwana kwambi asa boma lakhaza njala zibwezi phiii

  • @Felista-m4q
    @Felista-m4q 41 минуту назад

    Ndiyekhayo amene atichotse mmavutowa mulungu akusunge ndimoyo apm

  • @GilbertMughogho
    @GilbertMughogho Час назад

    Old bloom sweeps clean adadi my Vote basi sealed

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 18 минут назад

    President koma Peter wina lero. Kupita. Ku Nathenje kupezako anthu six okha

  • @MagdaraneChidamula
    @MagdaraneChidamula Час назад

    Adad Mulungu akudaliseni munatikonzera nseu wa Thekerani timanzunzika i believe kuti mukobzanso wa anzathu kumwanzako DPP woyeeeer😂😂😂😂😂

  • @andreambewe1851
    @andreambewe1851 2 часа назад +1

    APM ND NUMBER 1

  • @BOSTONMALISAWO55
    @BOSTONMALISAWO55 Час назад +1

    PRESIDENT WA CHIPANI CHA FUKO DPP YOMWEYO

  • @JaphetDevi
    @JaphetDevi 55 минут назад

    Dpp woooooooooyeee❤❤❤❤❤❤❤

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 21 минуту назад

    Is good nice now president pither

  • @jedoforsure2842
    @jedoforsure2842 Час назад

    MCP My vote

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 2 часа назад +2

    Achinyamata achina chakwela ntchito kubwelesa mavuto kumalawi

  • @abdulllahanubieimran06comanubi

    My vote APM

  • @EnwellSibale
    @EnwellSibale Час назад

    Niye munthu wapanga retire ndikuvomera kupangaso ndare dyer a munayiwara chaini asiyireni anyamata muzagwera mgalimoto

  • @EnwellSibale
    @EnwellSibale Час назад +1

    Inu mupha nkhalamba ikukanika nkulakhula

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 часа назад

    Apm my vote❤

  • @mariawachesterweluzan
    @mariawachesterweluzan 37 минут назад

    Katundu opanda minyama pangolin DDP 2025 Boma 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MafavukeJere
    @MafavukeJere 3 часа назад

    APM my vote🔥

  • @AlabAjuli
    @AlabAjuli Час назад

    kuyakhula nzonveka pamaso paathu zona.zokhazokha osat kunena zabodza aaai

  • @TestReznov
    @TestReznov Час назад

    Chonde timfunile zabwino ntsogoleri wa DPP. Koma zina la mpulumutsi asavekedwe kuopera kumpereka ntsogoleriyu ku mkwiyo wa Mulungu. Mpulumuti ndi Yesu Christu basi. Chonde

  • @EmmanuelKaliati-u5d
    @EmmanuelKaliati-u5d 2 часа назад

    APM woyeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @limbaniDines
    @limbaniDines Час назад

    Ili ndie bomad wina afune asafune dpp palibexo

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 29 минут назад +1

    Chipani cha m'banjaa. Family party

  • @AnnepherKautare
    @AnnepherKautare Час назад

    Boma ndilomweli😂

  • @AnnieChipofya
    @AnnieChipofya Час назад

    Musewu wabwela lero kkkkk

  • @stagoanointed
    @stagoanointed 2 часа назад +1

    Kkkkkkk kodi njala,,mmanyumbamu amabweletsa ndi president? Kodi vula ,, amagwetsa ndi president ku Malawi kuno? Tiyeni tiziima pachilungamo. Osaiwala Kuti tili mmasiku otsiliza. Kwa ine ndikukaika ngati kumene tikupitaku tingadzakhaleso ndi dziko lankaka ndi uchi,, tiye nazoni.

    • @TrizaMbesa
      @TrizaMbesa Час назад +1

      Ngakhale sagwetsa mvula lo kutupatsa chakudya tikavuti. President ndinyali younikila dziko lake ndichifukwa chake tinavutika amapita kumaiko akunja kukapepha thandizo kuti ife tipulimukd kunja chufukwa choti mvula sunabwele bwino lero chakwera akumapita kunja kukapepha mumdzina la ife ovutika koma thandizo akalandila zikumathela mmatumba mwawo adad amadziwa kuvutika kwanth adzatisamala akalowa m,boma adad woyeeee

  • @KayifaChikaphonya
    @KayifaChikaphonya 2 часа назад

    Congratulations ❤

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 2 часа назад

    More fire apm my vote 2035

  • @AnnieChipofya
    @AnnieChipofya Час назад

    Akulephera ndikuyankhula basiangalamule ziko nkharamba kkkkkk

    • @bisweckchimphamba8497
      @bisweckchimphamba8497 Час назад

      Iwe usandichimwitse mkuyankhula,amene odziwa kuyankhulawo akuchita chiyani mdziko muno

  • @JeseGwile
    @JeseGwile 2 часа назад

    Ukakhara kuti Bible sulidziwa zolumanazi sizitha sure mpakana mpulumutsi wabwera ambuye tioneni dzikolamera mano

  • @jafalibinali7393
    @jafalibinali7393 Час назад

    Boma komaili, losachititsa manyazi

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 2 часа назад

    Koma. Guys adad APM akomola anthu a MCP ndi chikoka chomwe alinacho, wa MCP akumva pain

  • @timothymhone2340
    @timothymhone2340 19 минут назад

    Mkanena kuti zodambwisa mkuthanthaudza chani amapanga matsenga

  • @Elias-q7n6b
    @Elias-q7n6b Час назад

    Adadi awo

  • @DuncanThambala
    @DuncanThambala Час назад

    Apm is athunder to Mr 😊chakwera the old evil pastor

  • @JosephGabriel-y7w
    @JosephGabriel-y7w 3 часа назад

    Ioooooo boma moto kuti bhuuuuuuuuuuuu❤

  • @mercymagaleta9672
    @mercymagaleta9672 36 минут назад

    💙💙💙

  • @PeterMPWWailes
    @PeterMPWWailes Час назад

    Koma thambani ground yamukana

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Час назад

    Zazibamboooooooo ine pheeeee

  • @EnwellSibale
    @EnwellSibale Час назад

    Akalamba azipuma

  • @UfuluManondo
    @UfuluManondo 2 часа назад

    Daddy my vote

  • @oswardzenizeni1458
    @oswardzenizeni1458 2 часа назад

    Mmatiyimilira adadi

  • @josephysweet134
    @josephysweet134 Час назад

    APM 2025 BOMA !!!!!!

  • @DamsonSabitt
    @DamsonSabitt Час назад

    Tiwonana chaka chamawa

  • @HajjAmadu-e1u
    @HajjAmadu-e1u 2 часа назад

    Ineyo ndie vote yanga ndi adadwooo

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 2 часа назад +1

    Palibe chomwe walankhula buluzi ameneyoo khalamba kwawo iyiiii inafoka

  • @CharlesMatope-xg6ln
    @CharlesMatope-xg6ln 3 часа назад

    Apm vote

  • @stagoanointed
    @stagoanointed 2 часа назад

    Kodi namondwe wa Fredy anabweletsa,, president wake nindani? Ndale zakuno ku Malawi zimakhala bwino kwa amene alikubwalo. Omwewa awa!mawa akadzalowaso mmbwalo. Ndinu nomweso mudzayamba kumawatakwanaso ngati mmene akutukwanidwila Chakwela.

    • @ReginaMzunga
      @ReginaMzunga Час назад

      eeeeee koma chakwela waojexa palibe chomwe tigaloxe chokoma

    • @AlexSilomba
      @AlexSilomba Час назад

      Poti mwati ndi ndale Koma zoona mpakana namondwe

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Час назад

      Komano Chakwera is more than empty tin.

  • @WelingsLongwe
    @WelingsLongwe 2 часа назад

    Koma iyi Ndi madala team kaya kulibe achinyamata

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 2 часа назад

    Boma ilooooo chala mwamba ichiiii Chala mwamba ichiiii imeneyo ili bhooo mchomwe tikabviike mu ink pheeee

  • @VayletNyirenda
    @VayletNyirenda 2 часа назад

    BOMA NDIROMWERI LA DDP BASI

  • @RosheensSPA
    @RosheensSPA 30 минут назад

    DDp oyeee

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola 3 часа назад

    Awa ndikatundu omanga ndi mawaya

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 часа назад

    Kunalibe anthu😊

  • @KhumzyBeston
    @KhumzyBeston Час назад

    Boma koma ili

  • @EllenMwale-h9q
    @EllenMwale-h9q Час назад

    2025 bomaaaaaaa🎉🎉🎉

  • @MathewsDyson-z6z
    @MathewsDyson-z6z 2 часа назад

    Wakalamba munthu uyu, achina chisale azangopitiliza kuba kwambili

  • @DismasMbewe-u9o
    @DismasMbewe-u9o 2 часа назад

    Koma kayazithebwanji

  • @MwaiDodo-p5r
    @MwaiDodo-p5r 2 часа назад

    Apm boma zili boh

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 часа назад

    ❤❤❤

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 3 часа назад

    💙💙💙💙💙💙🎐🎐my vote APM 😂😂😂😂

  • @MaxonVictoria
    @MaxonVictoria 3 часа назад

    Bona ilo❤

  • @masakaunga4099
    @masakaunga4099 2 часа назад

    Manjawo anatani amayu

  • @EnerstManess
    @EnerstManess Час назад

    Video sikukoma kujama 2much

  • @MavisChit
    @MavisChit Час назад

    ❤❤❤❤😂

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q 3 часа назад

    💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @HellenChejohn-n6o
    @HellenChejohn-n6o 3 часа назад

    Boma ilooooo

  • @ClementHaneef
    @ClementHaneef 2 часа назад

    Apm bomA

  • @ChiyembekezoJohn-v8o
    @ChiyembekezoJohn-v8o 3 часа назад

    Odiiiiii ukooooooo

  • @TonyMkwezalamba
    @TonyMkwezalamba 2 часа назад

    Biggy

  • @LydiaThobowa
    @LydiaThobowa 3 часа назад

    BOMA ilo

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Час назад

    Koma kukupita uyu anthu akutsatira😂😂😂😂❤❤❤

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Час назад

    .

  • @MaupoMhango
    @MaupoMhango 3 часа назад +1

    Talapumani madala sankhani achinyamata apitilize mpqndo wanuwo iyaaaaa! Komaso kaya mkuti bwanji sizikuvekaso ayi 😅😅😅😅😅😅

    • @KondananPetro
      @KondananPetro 3 часа назад +2

      Madala mesa ndabambo akowo

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 2 часа назад

      😂😂😂😂😂​@@KondananPetro

    • @LydiaManzy
      @LydiaManzy 2 часа назад +1

      DPP my vote bee

    • @getbusy7173
      @getbusy7173 2 часа назад +2

      kkkkkkkk mukumuopatu

    • @LoyceChipwaila
      @LoyceChipwaila 2 часа назад +1

      Ife bola okalamba koma wachilungamo komaso wamasomphenya kusiyana ndi wamphamvu koma osaganiza mozama

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 3 часа назад +2

    Nkhalamba zokhazokha......

    • @KondananPetro
      @KondananPetro 3 часа назад

      Nkhalamba mesa ndamako ndabambo akowo

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 2 часа назад

      Zosaba

    • @ROSEKATHYOLA
      @ROSEKATHYOLA 2 часа назад

      Anyamatanu nde mwapanga chani cha nzeru

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 часа назад

      Nanga 145,000000 ija idalowa mu account ya APM? Mwaiwala kuti unali umbava? Anthu inu mbuzi kwambiri, mumalulutira za zii.

    • @KondananPetro
      @KondananPetro 10 минут назад

      @tasmania527 inalowa kwa amako

  • @TimothyMacheso
    @TimothyMacheso 17 минут назад

    ❤❤❤❤❤

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q 3 часа назад

    💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @GrasonMaganga
    @GrasonMaganga 2 часа назад

    Boma ilooo

  • @sailesilikitoni
    @sailesilikitoni 2 часа назад

    Boma iloooooo