Musadane ndi Mai JB musiyeni mai wachikondi ndi anthu ...zipangani zanu ndi achitsilu anu achakwelawo.... chitsilu chizako chakwelacho mbuzi ya tsogoreli 😊😊😊
Ya Allah amene mumamva mapemphero athu ndpo ndinu nokha oyankha ndnu nokha odziwa ya Allah tipaseni sogoleri oopa inuyo wachikondi ndi anthu ake ya Allah tiyankheni tikukupemphani ameen🤲🤲
Mayi woyipa kwambiri ndiposo wakuba uyu kwabasi, anatibela ndege, ataluza chisankho ndikuthawira ku America for 4 for four years. Amasuka akuwona ngati mulandu unatha.
Chilikwamzako chigwile Nyanga chilikwako chakoma munali mboma munachita chani kunyoza basi munaba ndalama zaboma kunthawira kwa America ndege yaboma yilikuti?
CHAKWERA, JOYCE BANDA AND PETER MUTHARIKA ALI BUSY KUUZA ANTHU KUTI KALEMBETSENI MUDZANDIVOTERE PAMENE PRESIDENT WATHU KABAMBE ALI BUSY KUPANGA MA DEMO. WAKE UP KABAMBE MUCHEDWA NAZO ZA MADEMOZI. PITANI PA GROUND NTHAWI YAKWANA
MCP idzaduse mosavuta sichoncho ya Rabbi ya Allah Mulungu modzi ndnu oyenera kukupembedzani tichosereni MCP ya Allah imvn kulira kwa ana anufe ya Allah ameen 🤲🤲
Woman of wisdom osati chakwera mbuzi ya munthu.
Jb you did your part and we still miss you.
Woman full of wisdom
Kukhala mzimayi sichifukwa 🎉 JB bomaaaaaa
Musadane ndi Mai JB musiyeni mai wachikondi ndi anthu ...zipangani zanu ndi achitsilu anu achakwelawo.... chitsilu chizako chakwelacho mbuzi ya tsogoreli 😊😊😊
Mai Joyce banda mumatukula anthu akumudzi wombvutikitsitsa ulemu wanu koma cash gate nde inawonjeza
😂😂😂😂😂chotaniso😂😂😂
Amalawi mwatopadi kkkk zinafikapodi😅😅😅😅
@@salmankhanofficiel.5018kumangopeza paliponse zindalama
Bola pamenepo Jb my vote.
Koma Mayi JB amayesesa kusiyana ndi mbwelera zachimuna za Mcp zikulamula pano mwankhanzazi
Ndipo zowona
Ndipo Amayiwa anayesetsadi pokhalanso Mzimayi kusiyana ndi zimene zilipozi ndi mbwerera zenizeni
Mmmm mufuna kugulitsa anthu amai ku MCP
Ya Allah amene mumamva mapemphero athu ndpo ndinu nokha oyankha ndnu nokha odziwa ya Allah tipaseni sogoleri oopa inuyo wachikondi ndi anthu ake ya Allah tiyankheni tikukupemphani ameen🤲🤲
Amen and Amen
All who like makosana let's gather here
Mayi woyipa kwambiri ndiposo wakuba uyu kwabasi, anatibela ndege, ataluza chisankho ndikuthawira ku America for 4 for four years. Amasuka akuwona ngati mulandu unatha.
JB the wise Woman ever
She's wise
Zowonadi ulemu wanu mai❤❤❤
Bwerani ku utm maaa tipange alliance simuzakhumudwa
Amay osafooka 2024 BOMA 🔥🔥🔥🔥
Inuyo masten mumatha ma umboni tili nawo
Tiona zinthu malawi ❤
Ambuye akupatseni moyo wautali Amayi Banda
Apa aliyese angolamuriala kwawo kwawo
MY vote
Tangogwiranani manja ndi DK mutenge boma inu kkkkkkk
Ndipo live
Amai mumayiwalatu kuti munakweza malipiro aphunzitsi ndianthu ogwila ntchito mu Boma.
Nkhani ya machine mpaka ine ndipita kukalembetsa ku ck from bt
Chilikwamzako chigwile Nyanga chilikwako chakoma munali mboma munachita chani kunyoza basi munaba ndalama zaboma kunthawira kwa America ndege yaboma yilikuti?
Mtsogoleri yekhayo wachikondi
Yaah zafika ponyanya
Kkkkkk azungu andituma ndipo akuti......😂😂😂😂😂
Akut tigulise ndege,,,mayi awa amwene 😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂@@chifundocharles2348
Msamaliya wachifundo
Woganiza bhooo
Mama yeleyo yakuwechetayo ishene indu ishawishe kuchilambo wandj akuladga ni sala
Chokani apa ndimadiresi anuwo boma ndilomweri lachakwera
Boma lokanikali
ABITI NTILA😂
Mai kuluma chiyao
Mtsogoleri yekhayo wa masomphenya
Enafe sitikuva yankhulani chichewa mayi
CHAKWERA, JOYCE BANDA AND PETER MUTHARIKA ALI BUSY KUUZA ANTHU KUTI KALEMBETSENI MUDZANDIVOTERE PAMENE PRESIDENT WATHU KABAMBE ALI BUSY KUPANGA MA DEMO. WAKE UP KABAMBE MUCHEDWA NAZO ZA MADEMOZI. PITANI PA GROUND NTHAWI YAKWANA
Nde kuipasa motootu
Abiti cashgate
😂😂😂😂😂😂 nde mukut abit ndani ??????
@@AngolaChingadyaman akut cashigeti😅😅😅
JB is clueless, they know each other ndi Chikangawa, dont trust her
Keep dreaming
Who told you to trust her ?
Very true kungofuma kugawisa mavoti a DPP kumwela, chitsilu chamunthu.
I like she got good manifesto ena awa kulankula pakamwa pokha amayi amphavu
Boma lilipoli bolani mayiyutu
Nde sitose timanva chiyao,,yankhurani chichewa kuti tonse tinve
Aaaaa a inu Chichewa chake chit nanu fuck
Chakwera boma
Mwachita bwino amayi muzayime nokha muzangogawanisa mavoti akumweraku basi
MCP idzaduse mosavuta sichoncho ya Rabbi ya Allah Mulungu modzi ndnu oyenera kukupembedzani tichosereni MCP ya Allah imvn kulira kwa ana anufe ya Allah ameen 🤲🤲
@ShamimuBiameen ndipotu mzomwe akufuna maiwasani
Alot of Muslim 😂😂😂 kwathu uku
Apm motomoto
Amai ntchito zanu zimaoneka ndimaso mpakana lero... Ambuye apitilize kukudalisani