DALITSO KABAMBE CHIFUKWA CHANI ADATULUKA DPP.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 авг 2024

Комментарии • 38

  • @LovelyGalaxy-rb7yl
    @LovelyGalaxy-rb7yl Месяц назад +7

    Ayende bwno mwana waukape Awona ngati akapeza upele ku UTM, KOMA AXIWE KUTI NDIMWANA PANDALE 😅😅😅

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Месяц назад +3

    ngani yankulla and yakt ankufunna nkumugulla ndi m c p nkoma saneena nkandu ankabambe

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 Месяц назад

    At this stage, we need to concentrate on National Interest and not political. Mavuto akula ku Malawi. Malawi must unite first to defeat MCP. That's top on the agenda. Politics ndi maudindo later.

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w Месяц назад +3

    APM akuzasosora aswiswiri onse awo achoke alibe meaning ku dpp

  • @ThomasChiwaya-qx9mf
    @ThomasChiwaya-qx9mf Месяц назад +2

    Ine mau ambiri ndilibe kom Peter mulungu adalise amalaw tinaphuzir bas kut chikuni chachikulu chimasunga moto bas

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Месяц назад +1

    Kabambe wachita bwino akhale President wa UTM basi best wishes DK

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 Месяц назад

    DPP my vote

  • @OmegahThipa
    @OmegahThipa Месяц назад

    Ngakhale anthu ambiri angayike maganizo awo motani, Ndichisankho chawo koma sikuti DPP ingagwedezeke palibe (APM 2025 boma akutenga

  • @JayoneAmbitious
    @JayoneAmbitious Месяц назад +1

    Kabambe apanga phuma peter anafunika awatenge akabambe kukhala vp wao after 2or 3 years akanapanga resin kuwasiila akabambeo km paokha sangawine

  • @user-nj4ob8jw6y
    @user-nj4ob8jw6y Месяц назад +1

    Mbabva iyiyi sidatuluke ku DPP, koma a Peter Mutharika amutuma kuti akayimile ku UTM cholinga ndichofuna kukatenga mabvoti a UTM kukapeleka ku DPP. Chonde a Malawi chenjerani

  • @gifttembo2306
    @gifttembo2306 Месяц назад +1

    DPP ndiyochenjera akudziwa kuti utm ikhala pa mgwirizano ndi dpp and akufuna adzachithetse mphamvu chipani cha utm in the coming yrs. pomuika madalitso kabambe as vice president

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 7 дней назад

    Pali ndale zoopsya dpp ndi a katundu,akudzaphatikizana dpp ndi utm

  • @user-lu8px7td6p
    @user-lu8px7td6p Месяц назад +1

    Akufuna udindo wa uprezident

  • @user-hb2hr5oc9l
    @user-hb2hr5oc9l Месяц назад

    vuto anthu ambili sakufuna kunthandiza Malawi Koma Kuba ndalama Za boma akakhala pa udindo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Месяц назад

    Ameneyu ndi wandale. I don't believe he has left DPP. Why? Here is the reason: HE ENDORSED APM.

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki Месяц назад

    Sanalakwise Ali Malawi momuno kulikose kumene angalowele akatumikila amalawi

  • @adamu1287
    @adamu1287 Месяц назад

    Komano kunena zoona kabambe simunthu wandale

  • @AndrewSimakweli
    @AndrewSimakweli Месяц назад +1

    Akabambe si andale

  • @user-zo3bf3ec3g
    @user-zo3bf3ec3g Месяц назад

    Muyendako bwino koko

  • @bornface4786
    @bornface4786 Месяц назад

    This is not a right time for the Kabambe to move we can he doesn't lo Malawi

  • @AntonyEdwinMuyila-ij4sx
    @AntonyEdwinMuyila-ij4sx Месяц назад

    There is no future for the youth in Dpp.

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv Месяц назад +1

    Uyu sanatuluke ku Dpp achita kumutuma

  • @user-dc7qq9yz3v
    @user-dc7qq9yz3v Месяц назад

    Akamati mfulumila ndiumeneu

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c Месяц назад +2

    Achinyamata akutulula kamba koti APM sapeleka mpata kwachinyamata ndiye ataya chikhulupililo

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Месяц назад

    Kabambe anatuluka kalekale ku Dpp, the thing is iyeyu Ali ngati nankhumwa amafuna president komaso ndiwa phuma nde no wonder palibe move apa ndi APM koma iyeyu wafuna you can see ma meeting ambiri adpp samapitako.. Ayende bwino

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he Месяц назад

    This is a plot for DPP 😢, APM will make him his running mate
    Kutuluka DPP ,kudzagwiranso ntchito ndi DPP yomweyo😮?? Pali nzeru apa??

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly Месяц назад

    Muononga dziko ndiinu amene achinyamata simuziwa chomwe mukuchita munasonkhana mu 2020 lero ndi izi mumazitenga ngat otsogola lero mukuzinzika

  • @user-nj4ob8jw6y
    @user-nj4ob8jw6y Месяц назад

    Kabambe ndiwe mbabva wakuba. Udaba ndarama zambiri, zankhani nkhani. If u think that u r clever, Ukunama. U will never become president of UTM, never. Ndiwe mwana wa ng'ono pa ndale ku Malawi kuno.

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u Месяц назад

    Kuthamangila udindo.saphulapo kanthu awa

  • @user-bp1cu2rb4f
    @user-bp1cu2rb4f Месяц назад

    Kape iwe:Palibe chomwe uli.Galubwakoooo.Kachipanda ka peter bwenzi ulingati ndani?

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj Месяц назад

    Kuba bas ndizimene akufuna anthu kufinya mukaka ng'ombe yakuwanda kare

  • @JustineAdani
    @JustineAdani Месяц назад +1

    y⁷

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di Месяц назад

    MOTi ku UTM kulibe oti angaimile u president? Zikukhala bwanji?
    UTM say NO to Kabambe ( UTM presidency).

  • @user-bz4fs6gv8v
    @user-bz4fs6gv8v Месяц назад

    Uyu amutuma serious

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b Месяц назад

    Let just Mary chilima stand guys to heal the heart s of Malawi