Economist Intelligence Unit; MCP sidzawina chisankho mu 2025."

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 сен 2024

Комментарии • 338

  • @charliepoulaliecky1893
    @charliepoulaliecky1893 Год назад +29

    Akulu mwakwiya ndi chakwera tu mpakana akangomanga nyumba ku bwalo la ndege komweko😂😂😂😂😂 you never disappointed us bro

  • @vincentngalande3672
    @vincentngalande3672 Год назад +2

    None knows this. The future is determined by the Creator. Leave everything in his hands

    • @tingo3155
      @tingo3155 Год назад +1

      The creator has people to inform his people about the future

  • @isaacganizanikaziputa4901
    @isaacganizanikaziputa4901 Год назад

    Ku Malawi olo ku talowa President wanzeru ......sizizasintha pokha pokha system ya Democracy itasintha. ....Mumumve Yeremia Chihana ...Exclusive anapanga ndi Brain Banda. .......Please next time a Bakili Channel pangani mobilise anthu za Federal Government System ....otherwise mzakhalabe munena zomwezi mwinaso mati bola manyazi awawo

  • @slajieramzy
    @slajieramzy Год назад

    🤣🤣🤣🤣🤣 Angomanga ka gowelo kodi, kkkkkkkkkkk

  • @AbdulmalikAmanu
    @AbdulmalikAmanu 4 месяца назад

    Athu onama kwambiri achakwera Ndi achinana chiima

  • @GeorgeChitapapata
    @GeorgeChitapapata 3 месяца назад

    IA just dreaming

  • @francokaunga2707
    @francokaunga2707 Год назад +8

    Problem of chakwera is , he does not have advisor! What you must know Malawians is every rich family there is a strong wife behind so the wife of chakwera she doesn't think. Bingu wamutharika did a lot of development because the wife was strong and loving woman. Good advice always Start from the bedroom.

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Год назад +5

    Tonse alliance ikazangoyelekeza kuwina mobela , ndithudi mundimvesebwino Malawi adzayaka moto , pokhapo mundimvese bwinobwino , Lelo date ndi 30 June 2023 , aliyense akhale ready chakacha 2025

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Год назад +6

    Akuwona ngati Malawi wake wakale, ayembekezele kuzumidwa akayamba kuyenda misonkhano. Ineso ndnakwiya naye kale😒😒😒

  • @MjombaMjuba
    @MjombaMjuba 3 месяца назад +1

    Za bodzazo, za zii ndiye uganiza idzawine ndi UDF? Mangochi ndi Machinga singawinitse munthu, forget your hypocrisy, your wishes will never come true. Wishful thinking.

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Год назад +8

    Well done

  • @thandiechipepu717
    @thandiechipepu717 3 месяца назад +1

    Ubwino wake azungu savota nawo, ife timuvormtela

  • @merviselias6230
    @merviselias6230 Год назад +3

    Ndipo ndiye chakwera watikwana abale, ngati 2025 likhale mawa, mavuto anyanya abale,nanga kumangodya mbatata,nanga mbatata zikatha abale

  • @ChembeSolomon
    @ChembeSolomon Год назад +7

    Never give up ❤

  • @FanizoKawindula
    @FanizoKawindula 3 месяца назад +1

    Akadzavota okhatu a intelligence ndi iweyo chitsiru we

  • @davidwakhokamoto1124
    @davidwakhokamoto1124 Год назад +3

    Chakwera ndigalu heavy palibe kuzakhalanso president ndizake chilima agalu opusa

  • @kennedybanda
    @kennedybanda Год назад +1

    Edgar Nkanda the one who has big lips?

  • @DanielKaombe-im3pr
    @DanielKaombe-im3pr Год назад +2

    2025 kwatalika. Chakwera and chilima must go... they're wasting our time

  • @InockKimu
    @InockKimu Год назад +2

    Kkkkkkkkkkkkkk

  • @Major-v3u
    @Major-v3u 9 месяцев назад +1

    Azipita uyo

  • @rashidstamburi2705
    @rashidstamburi2705 Год назад +2

    Chakwara ndi galu uyu ndipo akundinyasa kwambiri 🤦🏻‍♂️🤦🏻‍♂️

  • @ibrahimatibu8784
    @ibrahimatibu8784 Год назад +4

    😅😅😅😅 Komad azigona ku airport komweko

  • @CHINDEBVU
    @CHINDEBVU Год назад +2

    😅😅😅😅
    Koma ya Chanel yanga lero 😂😂

  • @Pungwe123
    @Pungwe123 Год назад +2

    😂😂😂😂koma ndaseka azigona kuti?😂

    • @mbwindinga
      @mbwindinga 9 месяцев назад

      Komweko mama zachabetu

  • @ShadreckMatenje
    @ShadreckMatenje Год назад +3

    My brother from another mother umakwana respect

  • @jacksonmaster2288
    @jacksonmaster2288 Год назад +6

    I like the way you analyze your story, iweyo ndi m’banga

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Год назад +1

    Koma ndiye angomanga gowelodi kkkkk

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Год назад +2

    😂😂😂😂 komatu lwe kagowero kodi 😅😅😅

  • @HassanChimanda-u9q
    @HassanChimanda-u9q Год назад +2

    Zoona ndpo sixaboza

  • @milajimussa4120
    @milajimussa4120 Год назад +4

    Well done ❤❤❤

  • @Eliasiwhite-foreveryoung
    @Eliasiwhite-foreveryoung Год назад +1

    Ndpo inu

  • @BiancoLongwe
    @BiancoLongwe Год назад +2

    We like you brohh help us to more

  • @GABRIELLUNGU-rc6nq
    @GABRIELLUNGU-rc6nq Год назад +2

    Guys kamwendo mnjira kunena president😂😂😂😂😂😂

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 месяца назад

    Kkkkkkk koma iyiyi ndiye munamenya amangeni ka gowelo ku airport kokodi

  • @LEONARD-l5v
    @LEONARD-l5v 3 месяца назад

    Thanks a lot for your polite, true and honest words concerning the M. C. P. WITH THE PASTOR LAZARUS MACARTHY CHAKWERA... SHAME ON YOU 😂😂😂😂

  • @thomasmaluwa3408
    @thomasmaluwa3408 Год назад +2

    Umakwana bwanawe

  • @folamitowing238
    @folamitowing238 Год назад +1

    Ndipo galu ameneyu akadzachoka m'boma tidzakwizinge zingwe mwamphamvu

  • @Raheem-tm4jw
    @Raheem-tm4jw Год назад +2

    Izipita ndipo yatikwanadi

  • @FrancismkopokahIshmael-xi3wl
    @FrancismkopokahIshmael-xi3wl Год назад +3

    Big up bakili muluzi tv

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 Год назад +2

    Lifulendamu achakwera must go

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 Год назад +1

    Chakwelayi ndi bwantasa

  • @ClarenceNdunya
    @ClarenceNdunya 4 месяца назад

    Mcp uyelekeze kuwina 2025, secret revolution Army yathu tidzayambisa nkhondo dikira tidzakuonesa

  • @andreabrighten301
    @andreabrighten301 Год назад +2

    Kkkkkk kokapempha bas achakwela

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 4 месяца назад

    Vuto ndilakuti amalawife ndinafasa mopusa kwambili .....pamene zafikapa kunali kugwilizana ma demostrations dziko lonse ......chakwera ndi mbuzi ya munthu

  • @yasinkamwendo-jf7sc
    @yasinkamwendo-jf7sc Год назад +2

    My brother loves you so much ❤

  • @mustaffahhemmad
    @mustaffahhemmad Год назад +1

    Eeeish Galu palibe chichita iye

  • @AndrewUnderson-e1m
    @AndrewUnderson-e1m 20 дней назад

    Koma Anthunu mukuganiza bwanji zitukuko zosezo 4 years malawians

  • @kingsleychatha7492
    @kingsleychatha7492 Год назад

    pama president onse uyu nde zero pa handede kkkkk

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 3 месяца назад

    My fellow Malawians quote me right-Malawi will not and never transform if our political leaders are power hungry.Besides, if our religious leaders are cupidity minded and politically oriented.

  • @vitumbikochinguwo6227
    @vitumbikochinguwo6227 3 месяца назад +1

    We shall vote him in power again

  • @LingsonManda
    @LingsonManda 4 месяца назад

    28june yake yiti poti panopa ndi pa1june2024 osamanama pasocial media.muzichita manyazi ponena bodza

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 3 месяца назад

    Yanama imeneyo ndipo amen sadzirima akhaula ndipo mcp mpaka 2035 wooooh. Mulira ndipo mulengeza zonama za Achakwera koma ife fziko lino ndipatsogolo ndi mcp ndipo patsogolo ndi Achakwera. Ife tikufina mmene fziko lasinthira sitisowekaso kuti wina afxitinamiza

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Год назад +1

    😂kamwendo njira anadya mathako agalu mbuzi iyi yamunthu. Thanks very much bg mn respect ndawi zangawine uyu srs

  • @elwinsomanje9057
    @elwinsomanje9057 11 месяцев назад

    If Malawians cannot remove this president come 2025, know that we are doomed as a nation..

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 9 месяцев назад

    MUTHU wakupha chakwela MCP yoipa please don't try again

  • @CeciliaMphili
    @CeciliaMphili 3 месяца назад

    Or ndiotchetcha tchire omwe sanayambe😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 3 месяца назад

    Aliyense akudziwanso ndiye mudzayelekeze mudzabere anthu adzaphana

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc Год назад +4

    😂😂😂😂😂 koma abale azigonadi konko ku airport

  • @NophasJbanda-gk5cg
    @NophasJbanda-gk5cg 10 месяцев назад

    Olo achipanda kutero ndizachidziwikile kut sangawine kumene.

  • @SophyGogo-se7px
    @SophyGogo-se7px Год назад

    Ndipo asazinyase akwakhuluoirila umve bwanji

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 3 месяца назад

    I know the president saw what happened to Kenya is also coming to Malawi soon

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 4 месяца назад

    Moses ngati adapha Wittika ndiye angakhale ndichisoni kwa Mmalawi osamudziwa?

  • @innocentpelesi3390
    @innocentpelesi3390 Год назад

    Political leadership is not religious leadership.

  • @WistarChauya-b7c
    @WistarChauya-b7c 4 месяца назад +1

    My brother loves you so much ❤

  • @lamuelkaphamtengo2924
    @lamuelkaphamtengo2924 Год назад

    Udzakhumudwa akadzawina. Ungoyamba ndale udzawwine ngati ungadzawine. Iwe ukuona kuti angadzawineso ndani? Pamudzi sipalephera ozungulira mutu.

  • @atanasiomanuelsinossi6821
    @atanasiomanuelsinossi6821 Год назад +2

    koma inu ndi one

  • @BenissoneErnesto-kn9bd
    @BenissoneErnesto-kn9bd Год назад +1

    Aluze kumene zindisangalasa kopya boma loyipa kwambir ili

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 3 месяца назад

    Moses kunkuyu ndi chakwera chimwendo Banga zakhare ng'ono chakwera azalamulira anthu ake amenewo km ifeyo a Malawi zosatheka sazawona voti ya amalawi

  • @dartweedzmdawali5063
    @dartweedzmdawali5063 Год назад

    This is chakwela and his poor government

  • @vusoacquaron9084
    @vusoacquaron9084 Год назад

    Sazawinaso sitikuwafunaso palibe cha nzeru chomwe apanga

  • @caigondon1126
    @caigondon1126 Год назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂 kulakhula kwa bwanj uku angomanga nyumba ku airport 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @lukakapalamula4653
    @lukakapalamula4653 Год назад

    Iweyo osabazako bwanji zikuvuta bwanji mbuzi imadya pomwe ayimanga

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 месяца назад

    MUWAUZE A BRITAIN KUTI AZATITHANDIZE CHIFUKWA AGALU AWA AKONZEKERA KUBERA MASANKHO NDIYE UBWINO WAKE AKUZIONA ZOMWE ZIKUCHITIKA ASATISIYE CHONCHO

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 Год назад

    Or adzaluze koma ngati inu simulimbikira tchito mudzafera mu uphawi chazelu pezani zochita muziona chogulitsa kuzolowera kupepha

  • @gracelimani1526
    @gracelimani1526 Год назад

    Abambo amenewo kuyenda ñdi kwawo mene anali ku president wa church amayendaso choncho ngati ofuntha ambuye awakhululukire awonongelatu malawi yathu kaya idzabwerelaso monga kale pano ili worse tiyeni tidikilire 2025 sakuti awinaso nawonso akunkuyo atisale mwina adzavotera anthu mudzi mwawo wokha

  • @LingstonWatison
    @LingstonWatison Год назад +5

    ❤❤❤ More love to you big boss for ur information

  • @clementmwale9222
    @clementmwale9222 Год назад +1

    Zoona zake man

  • @WisdomMwitha
    @WisdomMwitha Год назад

    Zoonandi big chitsilu cha president buzi yamuthu watichititsa manyazi koma uyu galu

  • @FelixBMcdonard
    @FelixBMcdonard 7 месяцев назад

    Azatifuna chakwela ife amalawi 2025 komanso azagwada ameneyi matako ake

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Год назад +1

    🛌 ndiuse ine

  • @patiencetebulo
    @patiencetebulo Год назад

    Achakwera angopeselapo mwayi oti aziwe mayiko bas ndikuba komaso kudzudza anthu osalakwa ngat ma bulundi

  • @musicoftheviolinstudios.1109
    @musicoftheviolinstudios.1109 Год назад

    achake basi abusa anazolowera kudya zosakhetsela thukuta.ntchito kudya ndi kuba ndalama za amphawi.

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 месяца назад

    I will deal with Chakwela my self on 2025

  • @CentinoMatewere-en2vu
    @CentinoMatewere-en2vu Год назад

    Chakwela wationjeza mmm zambili wangotiyenda pansi

  • @emmanuellemson2683
    @emmanuellemson2683 Год назад

    Chakwera sadzatheka paka kufikira atasamusidwa pa udindowu. Uyu chomwe adziwa ndi bodza komaso kusaphweketsa nkhani ya mayendedwe.

  • @andrewmwale1912
    @andrewmwale1912 Год назад +1

    Bola idzavote chifukwa ovota ndi ena iwo ndi ma prophet chabe

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu 8 месяцев назад

    Kumkuyu alibe nzeru akuona national amalawi ndi ogona ku.kuyu ndikuudze amalawi tinDzindira ndiwe opusa

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 7 дней назад

    Kkkkkkk km adawa eeeea akut tangomangani kagwel komwek

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 4 месяца назад

    Koma agalu awa atikwana ka nthawi kochepa ndipo kungowinanso abale tikhala pamavuti azaoneni

  • @Michaelchimwala-c6l
    @Michaelchimwala-c6l 8 месяцев назад

    Chitsiru ichi chakwera ndi mbuzi yamunthu uyu ndi satana wenwen

  • @allanimindozo9937
    @allanimindozo9937 Год назад

    Vuto kumalawi kulibe asitikali bwezi ataba galu ameneyo axikhara kunjakoko

  • @CharityGondwe-bw9gs
    @CharityGondwe-bw9gs 4 месяца назад

    Mumatiimirira Ife osatha kuyakhurafe zikomo

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 3 месяца назад

    President dzina lake latsopano ndi kamchacha

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 3 месяца назад

    Chakwera koma ndiwe onyasa ngati maliro 😂😂

  • @CrissyMponda
    @CrissyMponda Год назад

    Mwangowada bwanawa britain si malawi makosana tiyeni tivomereze abale malawi tiyeni tisamupange kukhala godi wa anthu andale ayi koma malawi tiye tidzidalire pa nzose kodi tidzasintha ma president mpaka liti chenjera malawi dziko lanthu la malawi muli anthu ochepa ophunzira bwino koma vuto lawo amanamidza kwambiri anthu omwe sanaphunzire koma nyengo ndizosintha nthawi nzotse zamoyo kodi chani chomwe tikuyembekezera olo achakwera atachoka pampando abale anga chonde malawi azungu asatirekanitse ndipo amankhala kosiyana ndi malawi pa chilichose koma amapindula kudzera ku zinthu zili ndife anthu akuda

  • @EdwardRichman-zs5pl
    @EdwardRichman-zs5pl 3 месяца назад

    Km ngati panopa zinthu zikutenda ndichifka chakuyenda kwacha kwela zitukuko zomwe akumaliza chakwela ndizomwe azipani zomwe zinatuluka boma zamwe ndalama zake anabamo nthawi yomwe ankalonjeza anthu km chakwela wakwanitsa zosezi nde zona ma zakozo peza ana akoo uziwanamiza boma lilose limakhala ndi anthu osangalala ndi onkhumundwa maboma osewa ifeyo tinalipo tikudziwa u bwino komaso kuipa kwake

  • @ShyreenKafumbwa-bg2nu
    @ShyreenKafumbwa-bg2nu Год назад

    Eee munthu uyu chopanda nzelu bwanji osamasilila maiko ena mmene akutukukila kungowina ka mwendo njilayi ndi nkhondo yayambika pamenepopo tasukusula nafe

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Год назад

    Angomanga kagowero adzigonera ku airport komko kt asamawavutitse anthu

  • @isaacwgcgmelicomWGC-po5qv
    @isaacwgcgmelicomWGC-po5qv Год назад

    Chakwera ndi galu sitikumufuna ife chonde

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 4 месяца назад

    Amange nyumba ku airport kamwendo njira