Zina mwa zifukwa zikubweretsa mavuto ku chipani cha DPP

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024

Комментарии • 223

  • @chrisboyce229
    @chrisboyce229 Год назад +6

    Dausi asapangetu zachibwana ife tili pa mbuyo pa APM ❤❤

  • @rajabumustafa729
    @rajabumustafa729 Год назад +9

    Enanu ngati mukuona kuti zimene akukamba sizikukusangalatsani bas siyan kuvera zokamba zake mukasiya mmalo mwainu apezeka athu 10+ okonda chanel imeneyi

    • @abe9104
      @abe9104 Год назад

      nice answer man

    • @user-ix4yp5lp8m
      @user-ix4yp5lp8m Год назад

      Yes eti MUNTHU OKUTI sizimakusangalatsa koma osadiya kumangolankhulabe haaaaa umbuli CHANI???

  • @AshrafuBwanali-qi3my
    @AshrafuBwanali-qi3my Год назад +5

    Kod abwana bwanji osapanga press conference anthu tikuziwine you are like professor lumumba 'you talk 👄 reality without fear 😨 and favor your words are full of wisdom

    • @suprianomgalla5512
      @suprianomgalla5512 Год назад

      Ndipo we need to know him mweee😂😂 I can't stop liking this guy

  • @jamesnzokomera2775
    @jamesnzokomera2775 Год назад +3

    This guy always says only the truth keep it brother

  • @user-ix4yp5lp8m
    @user-ix4yp5lp8m Год назад +5

    Apa zanveka bwino tsopano inuyo mumatithandizatu.. ndipo piter ndiwanzeru kwambili

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Год назад +3

    Exactly BG. On point you never disappointed us respect to you bro

  • @Dickiez99
    @Dickiez99 Год назад +4

    Good job and well articulated❤
    Zomveka mvemvemve ndithu.

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam Год назад +2

    Adad woyeeee

  • @JeofreyNamalima-yn4tj
    @JeofreyNamalima-yn4tj Год назад +6

    Ife tikufuna apm bas ❤❤❤

  • @tech-portmalawi5676
    @tech-portmalawi5676 Год назад +2

    Great mind.May God bless you bro

  • @LotiBanda-uo5vy
    @LotiBanda-uo5vy Год назад +1

    Zoti mcp imadalira chuma cha Kamuzu wanama mkulu iwe

    • @WatsonShawa
      @WatsonShawa Год назад

      Akunamadi, nkuluyi ndi wa DPP

  • @rashidstamburi2705
    @rashidstamburi2705 Год назад +6

    Nkhani yabwino koma adad ayimeso basi nde zomwe tikufuna

  • @Patrick-br1fy
    @Patrick-br1fy Год назад +2

    Apapa tadziwa chilungamo chifukwa dausi amaoneka ngat ali pa chilungamo chifukwa chakudziwa kuyakhula

  • @Apschap-re7ch
    @Apschap-re7ch Год назад +2

    Mmatisegula maso bro..keep it up

  • @vusoacquaron9084
    @vusoacquaron9084 Год назад +2

    APM akuyenera kuyima basi enawa apeze zochita Dausi Nd zizingu zake zija akakhale pansi anthu osafunira zabwino dziko anthu oyipa

  • @hopeskafumbiphiri6011
    @hopeskafumbiphiri6011 Год назад +1

    Mr. Ur number one, vuto anthu ena amangofuna kusokoneza zinthu so ngati akufuna kuti peter azigwilisa ndalama zake nanga mau oti sichipani chake akubwelera pati. chifukwa akudalira ndalama yake Dausi ndinamumva pa Times koma zomwe ankalankhulazo mmmmm zaudani basi

  • @alfredbanda886
    @alfredbanda886 Год назад +5

    Mwini Channel iyi amatha kutambasula nkhani please ndilankhuleni pa Email yangayo ndizikupanga Support uli Ndi Luso kwambiri kumayamika ndibwino

  • @DavieMafunga-f3f
    @DavieMafunga-f3f Год назад +2

    Big man inuyo🎉🎉

  • @franciscoduartie5762
    @franciscoduartie5762 Год назад +3

    Its the narrators voice for me mawu a ndiiiiii😅😅

  • @superiormoses4802
    @superiormoses4802 Год назад +2

    Kuswa kuswa bro

  • @quraishmusakatunga1754
    @quraishmusakatunga1754 Год назад +2

    HRDC ikuopa ndipo anyani ameneo azaziona

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Год назад +1

    Thanks for the video a good one boss

  • @AbdulIbrahim-b6v
    @AbdulIbrahim-b6v Год назад

    Your are saying the truth brother we need to change the party should be for all 😢 member who are at nec to contribute and surpot The party because they are one of the benefits res okay

  • @DickMdala-pn4pd
    @DickMdala-pn4pd Год назад +2

    Akumuwopa APM komaso achina nankhumwa alembedwa ganyu

  • @esaumwanza3524
    @esaumwanza3524 6 месяцев назад

    No fear no fever straight to point ❤

  • @josephinemisomali6840
    @josephinemisomali6840 Год назад +2

    Koma kunena zoona interview ya Dausi ndi Brian Dausi ananena kuti APM asayime komano ananena kuti dongosolo lake silinayende ngati mmene chipani chimayenela kuchita ndipo kumapeto ananena kuti alibe vuto ndi APM koma ngati ndi Democracy aperekenso mwayi kwathu ena kaya adzaina APM iye adza support kodi ku DPP kulibeko anthu ena ofuna kupikisana nawo sindikusapota ndausi koma ndimmene ndinamvela pa interview yake

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Год назад

      2010 bwanji sanapereke mwayi kwa Joyce Banda? 2018 sanapereke mwayi kwa Chilima. Lero chifukwa apanga endorse ndi anzake basi kuyamba kulira?
      Ngati unamvera interview ananena kuti membership card isakhalepo kusonyeza kuti anthu asamasonkhe chipani chizithandizidwabe ndi Mutharika

  • @PatriciaFatch
    @PatriciaFatch Год назад +3

    Daus ndiamzake akufuna kusokoneza chipani, adad omweo

  • @lyiemax
    @lyiemax 8 месяцев назад

    Dausi ndi Nankhumwa ndi anthu osokoneza kwambiri, we are tired with them

  • @mkupabanda-nd2vb
    @mkupabanda-nd2vb 3 месяца назад

    Best chanel pa dziko lapansi pano

  • @beatricegulani5602
    @beatricegulani5602 Год назад +1

    Dausi sakulakwisa

  • @user-pt1fy3qg4u
    @user-pt1fy3qg4u Год назад +3

    Never give up ❤

  • @khalidwetchaua24
    @khalidwetchaua24 Год назад +1

    Apa mwayankhula zoona Bro ,,, Nankhumwa ndi Dausi kunena chilungamo akusokoneza chipani

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 4 месяца назад

    Good message Bakili Tv ❤

  • @symonyohane6989
    @symonyohane6989 Год назад

    APM emweyo

  • @Francischibwana-o7n
    @Francischibwana-o7n Год назад

    Let Peter Munthalika to stand l support him forever

  • @alicemalika677
    @alicemalika677 Год назад +1

    Very interesting Namkhumwa is failing to stand firm in the Parliament as leader of Opposition but he wants to be reader of Opposition in his own party. Koma ndizidabwitsa bwanji he can win

  • @Danp-q4n
    @Danp-q4n 19 дней назад

    Mumakwana Mr BM tv

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Год назад +1

    I will never disappoint you sir

  • @alickziba6756
    @alickziba6756 26 дней назад

    Powerful as well

  • @BROWNKCMARCDORMAND
    @BROWNKCMARCDORMAND Год назад +1

    Paja awa nga dpp

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Год назад +1

    Anankumwa nd Dausi ngati akuzimva ndalama angotuluka bas ayambise chipani chawo vuto palibe ife zatikwana☹️☹️☹️

  • @johnman4619
    @johnman4619 Год назад

    Komanso adausi akuziwa zambiri zakuphedwa kwamalubinho ndioo adausi ndi nankhumwa komanso Ben botolo anapha alubino uja waku nkhatabay Mr makwenda phiri ndioo adausi ndi tim ya apm yomweyo mulamulilo wao akuziwa adausi kuti zao zidada ku dpp alibe chance

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib Год назад +1

    Vuto lake Chilungamo Chinayandikana Ndi Mabi😮 Dausi Ayambitse Chake Basi

  • @jamesjealous-p4v
    @jamesjealous-p4v Год назад +3

    Jealous nde vuto lalikulu mmalawi 😂😂😂

  • @moffatnsolomba6082
    @moffatnsolomba6082 Год назад +1

    Analysis yanu ya nkhani za Ku Malawi kuno mumakhala ndi mbali....

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Год назад

    100% agree with you man

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Год назад

    You are always right bro, dpp for life ndipo nankhumwa, botman ndi dausi ndi osokonedxa we know

  • @johnman4619
    @johnman4619 Год назад +1

    Dausi ndi mbuli yazinthu sadziwa ntchito ndipongasanje safuna anzao kuti azimveka Ali .ngati Symon vuwa Kaunda komanso khumbo kachali Sanji twoo much

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Год назад

    HRDC instead of fighting problems that are making Malawians poor you're busy with APM. This is stupid.

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Год назад +1

    Thanks: kusonka kwabwino chipani sichingagwe .

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Год назад

    Zoona bg mn respect ndawi zonse

  • @festongrido3192
    @festongrido3192 Год назад +1

    Zikomo Braz izizi ndinkhondo yomwe akuisaka satidzalora zimenezo

    • @phillipstamaley7901
      @phillipstamaley7901 Год назад

      Lumumba ndi patali abwana just appreciate him not compare with lumumba

  • @chitimbethegreat-pc1bp
    @chitimbethegreat-pc1bp Год назад

    Dausi wagulidwa ndi MCP uyu asatinyase azipita ku MCP ndipo DPP ikuyenera kuchosa mbava ngati zimenezo

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Год назад +1

    U r my hero

  • @suleimanrabson4367
    @suleimanrabson4367 Год назад +1

    Talking true bro

  • @ndugwamoses2467
    @ndugwamoses2467 Год назад

    HRDC very useless asowa zochita mmalo mopanga zachitukuko akulowelela za ndale. failed organisation!!!

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 2 дня назад

    Anthu onsewa akunenedwawa ndi oumira nakhumwa Dausi botoman palibe anapasapo ndarama munthu ndikwaziwa amenewa

  • @michealchilemba3149
    @michealchilemba3149 Год назад

    Nankhumwa akulandira ndalama ku chokera ku Mcp kwa Simbi phiri ndi kwa Chilima kuti Asokoneze DPP

  • @CassimMtambo
    @CassimMtambo Год назад +1

    Mumatiimilila Bg

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Год назад +2

    BIG 👍

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl Год назад +1

    Cadet kulira mokweza dpp sidzalowaso mboma brother

  • @maskinmsungeni8763
    @maskinmsungeni8763 Год назад +1

    DPP is for the Mutharikas family, Why can't u, the Dausis form ur own Party? Go a head APM .

  • @johnjameskapito5151
    @johnjameskapito5151 Год назад +2

    Dausi ndi mfiti

  • @vincentharry-ct3sw
    @vincentharry-ct3sw Год назад

    DPP yonseyo ndi yakatangale not only Dausi

  • @idrissaKGO
    @idrissaKGO Год назад +1

    Akulakwitsa kutero amusiye anytime piter yemweyo

  • @ChipililoWame-lc8ul
    @ChipililoWame-lc8ul Год назад +1

    Dausi ndiwozungulila mutu kumalawi kuno kuli zitsilu

  • @user-ix4yp5lp8m
    @user-ix4yp5lp8m Год назад

    Daus ndi Nankhumwa ndimbuzi zawanthu...ngati ayambitse chipani chawo Adad bas

  • @YunusuOfesi
    @YunusuOfesi Год назад +1

    Dausi Ali ndichibwana kwambiri

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Год назад

    Ayambitse chawo amenewa Dausi ndi nakhumwa yambani chanu please

  • @stanleykumwembe4719
    @stanleykumwembe4719 Год назад +2

    Sometimes mtolakhani uyu, amaometsa mbali, khani ija yasokomekeranso…

    • @jacksontembo1530
      @jacksontembo1530 Год назад

      Inenso ndimaona choncho awa azingonena ma history omwewa onsati za ndale

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Год назад +2

      Uyu amanena fact. HRDC inasapota MCP, ndi chifukwa chani akufuna kulowelera zochitika ku DPP amenenso ali adani awo? Ndimawerenga nyuzipepala ina yake HRDC chairperson kumpoto akufuna kupita ku khothi kuti akamuletse APM asayime. Mtolankhani uyu amanena chilungamo chokhachokha man. MCP yapanga endorse Chakwera palibe wanena kuti si democracy. Ena apanga endorse APM akuti si democracy. Mtolankhani uyu ndi 1

    • @user-ix4yp5lp8m
      @user-ix4yp5lp8m Год назад

      Amene mukumasutsana Nayenu NDI mbuziso zawanthu...uyu amalankhula zogwila mtima..zoona zokhazokha

  • @EDOHMUSTAFA
    @EDOHMUSTAFA Год назад

    Iwe ndi bg MN

  • @GeorgeGeorge-bu6cy
    @GeorgeGeorge-bu6cy Год назад +1

    Ulemu wanu brother

  • @issabrightsaidibright1274
    @issabrightsaidibright1274 Год назад +1

    Ngani ijaa ndayivesesa sopano APM YEMWEYO

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt Год назад +1

    Ife timaziwa kale kuti Dausi ndiwosokoneza

  • @AbdullahDewas-k8q
    @AbdullahDewas-k8q Год назад +1

    Kumenek ndiye kulangula tisangomenyana basi anthuwa akutenga machasi

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Год назад +1

    Akuwopa chiyani amusiye peter azayime , dausi ndiwosokoneza malawi atapoa ndi ulamuliro wa chakwera

  • @alicklongwe6375
    @alicklongwe6375 Год назад +1

    Adha awawa ulemu wanu

  • @WatsonShawa
    @WatsonShawa Год назад

    Munthu onena chilungamo chothirako bodza ndi wowopsa kuposa yemwe amanena bodza lopanda chilungamo.

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Год назад +1

    Dausi ndi galu wadyera

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Год назад

    Yes ndi zoona kuli gulu Lina likukakamiza APM kt ayime iwe ukumbukile APM 2021 anane yekha kt sazayimeso koma pano anthu awo akumusokoneza APM kt ayimeso ndi zoona izo ???

  • @OcaciahMahomed
    @OcaciahMahomed 10 месяцев назад

    Muli bho

  • @MosesSailes-ib6bv
    @MosesSailes-ib6bv Год назад

    APM yemweyo watikwanila

  • @saidichirwa5456
    @saidichirwa5456 Год назад

    Bola munthalikayo.Awo asatiputsitse ndimbava zosakhutitsika ayi.Kulibe zimenezo.Iwe tokota osawopa ife umatitokotela history mopeleka chidwi and umakhala ndi maumboni okwanila.

  • @nyararaishumba9288
    @nyararaishumba9288 Год назад +1

    Dausi ndiopa kuyambira kale atuluke mchipan akayambise chake akapume waba zambiri galu amenei

  • @user-ps8vq5co8n
    @user-ps8vq5co8n 7 месяцев назад

    Bg mumatha kulongosola zinthu

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Год назад +1

    Angochoka muchipamo basi amusiye Apm

  • @Misasi19
    @Misasi19 Год назад +1

    Akumuopa Apm

  • @AhmaduAdini-r1i
    @AhmaduAdini-r1i Год назад

    Big ulemu wanu Big ndi makunyadilani

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Год назад

    Peter azawina basi ngati palibe kubera

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 Год назад

    Zitsilu zitatu zimenezi zisokoneza DPP maka uyo wonenepa ngati nkhuku ya vertinary.
    Ngati akuti Muthalika family azipanga yekha ndiye ali ndi ufulu wambiri even wochotsa anthutu.DPP inaluza coz of Nankhumwa ndi Dausi dyera.HRDC pamsana pano nonse ndinu mwawononga zikoli ndipo ndinu zitsilu musamalowelele za zipani agalu inu

  • @usg435
    @usg435 Год назад +1

    Dausi bottman ndi nankhumwa ayabise chipani chawaoo

  • @maxwellchilima5440
    @maxwellchilima5440 Год назад

    Peter sangathe

  • @KINGMANMAKALA-hb9gs
    @KINGMANMAKALA-hb9gs Год назад +1

    Pita ayime basi

  • @KelvinmolganMasamba-th9by
    @KelvinmolganMasamba-th9by Год назад +1

    Kungoti dausi ndiwamanyi ndipo akuyenera achoke akayambise chipani chake shatapuiiiii

  • @antonychika15
    @antonychika15 Год назад

    Anafufuma Masaya kkkk iwetu iwe

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib Год назад +1

    Ubwino wake ife Sitikufuna APM Atibekekere Mwana 😅 Tikufuna Ntchito Zake zibwelere, Osat Wakura Wakura Wakalamba Ngat Akapanga chinkhoswe Ndi Mwana wa 2000

  • @EmmanuelZiba-qz6ug
    @EmmanuelZiba-qz6ug 20 дней назад

    😢😢😢😢 god bless you brother

  • @HamzahrichardSuman-pg5mf
    @HamzahrichardSuman-pg5mf Год назад

    osanyengerera chilungamo chiyende ngati madzi popanda inu sitingadziwe kanthu

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 Год назад

    Izidi zikudabwisa kuti HRDC ikulowa Pati agulu awa ndiyamene ationongela zikoli ,,,inu a HRDC mukapitiliza zomalimbana ndi DPP tikuochelani mmanyumba mwanu Momo

  • @AnordThomson-iw5ny
    @AnordThomson-iw5ny Год назад

    HRDC all of them they are stupid, ndiwanthu omwe anatipatsitsa mavuto ife a malawi, ife a malawi tiyeni tikavotele APM tatopa ndimavuto