Andale awa ndi Anthu onama kwambiri Komanso ndiamodzi anthuwa Alingati anyani afisi omasintha mapiri Ma bank awo ndi odzadza ndi Ndalama Kaliyati wakhala ma unduna ndi a Chakwera omwewo Lero akukamba izi Inu mukungona ndi njala Zauchitsilu basi
She is talking as UTM, Kaya anali ndi udindo mu Alliance or not if akuona kuti mgwilizano sukuyenda bwino they are free to move out, ngati ine Kaliati wayigwila ntchito yolimbisa chipani, posathamangila dyera
Mai kaliati alephela kuyankha mafuso , vuto amazitenga ngati ozindikila all the time choncho si bwino Mai wangwilo azizichepesa koma si mai kaliati chiwanda chenicheni nzake ndi jessy kabwila vela kantukule azimai awa ndale anafika nazo poipisisa alipo ka gulu ndithu azimai oti amaimilira satana oipisisa kwambili
@@GiftNkhoma-n2w aaah ine ndinamuona kalekale ndi chisilu koma saziwa kaya ati kwao amathandiza ndi zake zimenezo and anakakhala kuti amathandiza ziko lonse bwezi titamuika pa map koma aaaah satana weniweni wa mai alibe ulemu ngati mai wankulu athela komweko akunama
Mukunama fuso lomwe sanayakhe ndilitilo ena afusa zopepera zoti ena afusa kale Iwo akubwera kuzafusa zomwezo or Ku school ukamafusa zoti wina wafusakale ati ndiwe opanda nzeru so take note that I think mwanvetsetsa pamenepo
Being talkative does not make you a best leader, Leader azikhala wa timming Ngati chilima osati emotional. a Kaliati ali ndi mkwiyo ndipoakufuna kugwiritsa ntchito infa ya Chilima for plolitical oportunity akanakhala wina akanangochita focus kupanga reorganize chipani osatikumalimbana ndi ena. MCP zake zada but kulimbana ndichitsiru umasandukaso chitsiru.
Manganya si wa UTM tikudziwa inde kut adali running mate wa Chilima komano panopa ndi MCP n,ndiyemwe akufuna MCP kumugwiritsa ncthito kut aphe chipani cha UTM
Nose ndinumakape amene munakhala, ine ndinali was UTM before the death of SCK but now aaaaaaaa no one can reading the party. Pano takwera ya Dr chakwera the wise man.
Zaboza nawe know that kweni she's always serious on interested things ok koma ndinzimai ocheza bwino mwina simunakumane nae live mwina munena wina phunzirani kunena zoona
Mother of Malawi madam Patricia Kaliati you are the best one of UTM never give up go ahead ❤❤🎉🎉🎉🎉
A very wise woman Patricia ❤❤
I like the questions were answered and the settling down of dust in the party.
Akhaulitsa ndan inu mukamalemba zinaz mu dzikhala manyaz UTM forever
Ndipo sukunama azilingalira ma title akafuna kutsindika nkhan
Hi
Akweni pitiilizani kuyima pa chilungamo chocho Ambuye ndi amene azikutetezani ❤❤❤❤
I can see merry chilima becoming a president of utm this will happen
Kaliati ndimafuna daily ndizimva voice yanu inu ndi one❤❤
Yes, God bless UTM and the readers, never give up go ahead UTM 🔥 like it
Awasiye a UTM manganya si wa UTM nfiti ya munthu
Mfiti bwino
MY BELOVED PARTY UTM EVER
Kodi mayankhidwe anzeru ngati awa mumawatengakuti inu shaa❤❤
Ndikuchikwezatu
Ndipo mwamakosanawadi mwagona mfundo komaso nzeru zopambana
zoonadi kudabwa amakozekelatu mai uyu ndimoto
The publicity secretary is very composed .I like it
Strong woman. Patricia kaliyati
Unstoppable party we are there for it , leaders be strong enough God be with you we are at your back
Akweni number one ❤
Andale awa ndi Anthu onama kwambiri Komanso ndiamodzi anthuwa
Alingati anyani afisi omasintha mapiri
Ma bank awo ndi odzadza ndi Ndalama
Kaliyati wakhala ma unduna ndi a Chakwera omwewo
Lero akukamba izi
Inu mukungona ndi njala
Zauchitsilu basi
Mbabva zokhazokha izi kkkkkkk Kaliati wakhala Mu zipan zingat?😅😂
Ndipo inuuuuu
Ndipo mbuzi Za wanthu izi UTM candle 🕯️🕯️ party
She is talking as UTM, Kaya anali ndi udindo mu Alliance or not if akuona kuti mgwilizano sukuyenda bwino they are free to move out, ngati ine Kaliati wayigwila ntchito yolimbisa chipani, posathamangila dyera
Exactly. And I don’t see the hype for this woman at all
Well done my akweni
Koma kaliat Mulungu anampatsa lilime mmmmh
My vote is still for ❤u
Bravo💪🔥 mum.. your number one mum
Anthuwatu akuyankhulamwachikulu,
Oipa athawa yekha muchipani cha UTM,
Absolutely
Mai Kaliyati anakonza 😂😂😂😂 usazafe uzangosowa ❤
You guys you are doing well keep it up please don't allow to fall back keep focus on you'll take it with God's help
Manganya ali ndi chipani chake odya zake alibe mulandu
Manganya tisamutaye akuziwa zomwe akuchita coz ukafuna kuziwa zambiri umalolela kukhala chisiru
Kuyankha mwa ukadaulo ..... Koma kwee anakwiya.... Mpaka ntolankhani wathawa 🤣🤣🤣🤣🤣
Michael usi akuchedwetsani, ameneyo simunthu ndiwa kupha.
Manganya cholinga chake nkugwesa utm becareful original utm
Zero pa ten, he can't achieve taking down UTM
Zero pa ten, he can't achieve taking down UTM
UTM is the strongest party which has a strong mandate to mobolise the povo to vote for it .
Wowwh utm motooooo it is good team I love UTM
This is the way to go
Following 100%
Mmene mukwawonera amenewa ndifuso liti limene lingawakanike kuyankha? Viva UTM crew.
afredo umatiyimilira 🎉🎉
Dr chakwera 🔥🔥🔥🔥
mwayi a fredoks pomwe anali kutali ndi udindo eeeehe koma lfa ena akupindera nayod
This is not democracy,everybody has right to wear what we want
Yes democracy, but I'll ndi malire chilichonee goes with orders, not chisawawa
Ku Utm kuli anthu anzeru.....Press conference well organized prepared to respond media questions
A mother of all, akweni inuyu anakoza ❤❤❤
Makape okha okha nindani wazelu angakutsatileni
Ife pano tilipo man
Atola khani musamatinyase
Mai kaliati alephela kuyankha mafuso , vuto amazitenga ngati ozindikila all the time choncho si bwino Mai wangwilo azizichepesa koma si mai kaliati chiwanda chenicheni nzake ndi jessy kabwila vela kantukule azimai awa ndale anafika nazo poipisisa alipo ka gulu ndithu azimai oti amaimilira satana oipisisa kwambili
Zoonadi mai kaliyati mmmm amazitenga ngat munthu kuposa anthu ena chifukwa chan 😊
@@GiftNkhoma-n2w aaah ine ndinamuona kalekale ndi chisilu koma saziwa kaya ati kwao amathandiza ndi zake zimenezo and anakakhala kuti amathandiza ziko lonse bwezi titamuika pa map koma aaaah satana weniweni wa mai alibe ulemu ngati mai wankulu athela komweko akunama
Mbuzi yamuzimai kaliat
Kutuluka Kulibe kanthu Iya
Mukunama fuso lomwe sanayakhe ndilitilo ena afusa zopepera zoti ena afusa kale Iwo akubwera kuzafusa zomwezo or Ku school ukamafusa zoti wina wafusakale ati ndiwe opanda nzeru so take note that I think mwanvetsetsa pamenepo
The very best secretary general, very capable to manage her office
The ideas are nicely flowing in taking questions from journalists
Utm pala mukukhala makola yayi pasi, imwe wa wakumipando ndiwe mukomenge chipani, chifukwa kuzizipizga mwaimwe mulije, chifukwa kuyowoya kwinu nkhwaudani , vakuyowoya vinyake vilekeninge, imwe kolani chipani
Palibe chazelu apa wosewa ndi aboza ziko ndilovuta kulamula wosati kuyambanako
🎉🎉🎉
Nice press briefing, mwawayankha bwino akanganyawa
Kaliati yankhafuso osati ufuseso
A UTM chonde Usi osakamuika pa udindo ,ndi mfiti ya MCP
utm Inali ndieniake pano vomerezani kuti inathaa
Utm yatha yagawana zida musatipusise
Muchila
Osawopa utm moto kt🎉🎉🎉
Tamuyamikani inu ma members pa khumano yanu ndiponso atolakhani mwa ayakha bwino kwambili amen
This Lady was naturally born a Leader
Being talkative does not make you a best leader, Leader azikhala wa timming Ngati chilima osati emotional. a Kaliati ali ndi mkwiyo ndipoakufuna kugwiritsa ntchito infa ya Chilima for plolitical oportunity akanakhala wina akanangochita focus kupanga reorganize chipani osatikumalimbana ndi ena. MCP zake zada but kulimbana ndichitsiru umasandukaso chitsiru.
Tili pa mbuyo pa UTM
Good answers madam Patricia
Manganya si wa UTM tikudziwa inde kut adali running mate wa Chilima komano panopa ndi MCP n,ndiyemwe akufuna MCP kumugwiritsa ncthito kut aphe chipani cha UTM
Our mother akweni mumakwana moto kuti 🔥🔥🔥🔥
Mwayankha bwino akulu akulu a UTM chimenecho ndicho chipan
Rosendo Roads
Akhaula ndinu atolakhani osati UTM.
Ndithandizeni ndingomdyela manganya😂😂
😂😂kma ase iweso usabdiwaze ase mpaka akumenyele ngondo kt uwadyele bambo asikono ase😂😂😂😂😂😂
Headline zosiyanilanatu mzochitika. Kumakhala kugulisa news kodi?
Ati akulemberani 😂😂😂😂😂😂😂
❤ Mpaka tilamulira, zipewazo tikuzifuna kuno ku Capetown
Nose ndinumakape amene munakhala, ine ndinali was UTM before the death of SCK but now aaaaaaaa no one can reading the party. Pano takwera ya Dr chakwera the wise man.
Machende ako iwe atalokhani ake amenewa sangatikhaulitse mapwala ako ndi chakwera wakoyo
Akaliyati mamalo momanga chipani mkupasula kufuna usogo simngakwanise chilima anali wanzelu ndiposo wokhwima mmaganizo not inu muli ngati adpp mkuutukwana ausi koma anawasankha ndi achilima audasi inu ndipo simkuziwa chimene mkupanga
Zeru zachilima mukukukambazo pano zili kut Mesa anamwalira chibwanatu
Madam kaliat you are so intelligent
Ukananenaso kuti ngati kupangitsa klmsokhano wa boma a utm atha kupita chifukwa wa boma si wa mcp
Mayi kaliyati tikuthokoza kugwirisa chipani cha UTM
Great party 🎉
😮kkkkkkkk but boza muphesa amalawi inu a utm
Mai akulu ku Malawi kaliati mulungu apitilize kupatsani chisomo thawi zonse zikomo
alakhula bwino koma ine si was utm ai ndine wa boma ndilomweli mudziwa kale😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma yaaaa
Osafooka Osatopa
Seventh day songs
Akwen smuzatheka mmatiyimilir ahundup plz
❤❤ manganya ndi wa mcp si wa UTM
Wishing #UTM strength and unity.
Mpaka anawalembera?🤣🤣🤣🤣🤣🤣💋
Ndakondwa koposa apa zikuonekakuti utm ikhala pamodzi. Guys sibwino kumagalukilana nokhanokha
A kaliyati ndi a njawala mukwatilane basi 😅😅😅😅😅
Kaliati 😂😂 kuyankha mafutso olemberedwa😅
Kodi kukhaulitsa kulipati kapena ndi taitol yakhani
ntchana ndi one ndale waziyamba uli mwana one day uzakhala ngat ibrahim president wa bukina faso
Ndiye palibe kukhawulisa ndimafunso
Akunena zowona anthu awa akuyankha mwazeru👏👏❤❤
Mai Kaliati muziyankha bwino mafunso. Musamakhale ndi mkwiyo. Mafunso abwinobwino inu mukuyankha mwano. Fredo akuyankha bwinobwino zanzeru koma inutu mutibalalitsira anthu.
Simunati musova.
😂😂😂😂😂@@SolomonNjolomole
@@SolomonNjolomolemuzasova when she’ll be the one of the people to worsen things for you just like Chakwera is doing
Zaboza nawe know that kweni she's always serious on interested things ok koma ndinzimai ocheza bwino mwina simunakumane nae live mwina munena wina phunzirani kunena zoona
😂😂😂😂😂 mwakwera chakwera mukuwoneka Chifukwa chan mukulondora Usi alinso amene adapereka Chilima koma athu inu lunena zooona muli ndi mr chikangawa 😅😅😅😅😅
Mai kaliat my vote to be utm president
Bwato la Mila mkona akumazembera kuvala nsalu zathu
Dzinamuvuta anadziwa kuti anthu akumudziwa pano kuti tsi wa utm kuyambira anari momwemo komaso anagulitsa chilima pogula mpando wau vice
Waboza iwe a utm nd amenewa mani koma ndye mwana wa achikangawa
Romaguera Rapid
Usi mkt mlinayo limozi lero akamayenda akt chakwela ndiwabwino mawa azanene kt botelani ife usi aktibalalisa asiye zothokoza chakwela
Ndikutsatira bwino
Ndikuchita kumva kukoma
Kuyankhula koma kumeneku 😅
Komano kaliat akuyakhula chilungamo ndipo mwachita bwino kuiminsa mafunsa opusa okhuza ngwilizano