Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Azimayi a Dpp ndi ngenge osati jesse kabwila maso ali tudzu mmmmmmmmm
😂😂😂😂malawi wanga😂😂😂
Kkkkk koma
Kabwira ndi wa kachaso.
By the grace of God mcp must go
DPP ndimadolo asukulu zedi Mbambande DPP❤
I love dpp this one my vote
Ndzimene zikufunika kwambili boma la Peter muthalika
Am proud to vote for DPP❤❤ ndikuona kuchedwa
INSHALLAH zizayenda bwino ❤❤❤
Ana achepa awa, chikangawa party yi ikupita ndithu
Ndipo kwambiri
😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤ umatha ase kulibe kunjonja mcp mafada bas
Bola pamenepo DPP woyee atambwali awa atipweteka kwambiri
Big up brother man!!
Ndale ndinyama yovuta Dpp sibeledwa
Nkhani yoti awiriwa anakhalapo ku MEC sizikugwirizana apa cos pano sali ku MEC.
Koma Jane akuziwa Chisinsi chobera
😂😂😂😂 mvuto munthu ukakhala wakuba umawonaso ngati azakosp azapanga umbava wakowo
Exactly
Poti inu ndi agwiro
Kkkkkkkkkkkkk zisankho izi za 2025 zizayenda mwa myaaaa koma dpp sizawina chisankho amene ali ku opposition basi
DPP ndi chipani changa. Mu February ndinali wa MCP. Lero September ndine wa DPP. Chifukwa chakuti Chilima anaphedwa ndi Chakwera.
Akamufuse Joyce Banda 2014 zmene tinapanga tanyenya 2025 a MCP ana achepa💪💪💪
Ndipo kwambiri kkk
zilibe ntchito zimenezo coz kwawo adachita ajeni ansa amachita kuonekeratu kut ndi wa dpp galu uyo
Kalikonse tizakaona.
💙💙💙💙
apa tikapanda ku winner ndiye kuti abera koma tizapanganso ndewu mcp ndi fellow citizens of malawi watikwana anthu mpaka mwafika pomadya chitedze ayi ndithu chakweradi
Kkkkkkk ndiye athu aope azimay amenewo akubawo kkkkkkk
Ngati dipipiyo idzawine chopangila mantha. Kuti azanu dzabela ndichani
Koma zithunzi kumaika za recent osati zakalekale anthu adakali ndi mphamvu. Imeneyo ndi njila imodzi yo bela zitsankho
MCP ili mmadzi
Okumba dzenje amageeramo okhaa lero a MCP asala okhaa tiwona ngati 50+1 chilima ndii ijaa amupha
😂😂😂😂mumakwana brother 😂😂
Kkkkkk mesa ukunena mathanga ndameuja Anatha ndi Anthony Bendulo
Chikangawa sangawine
Ine ndikungofuna DPP NDI MCP Kaya apanga alliance ndindani koma asalowe boma
Azadya makobili ochuluka kumeneku kutero akufuna kupusisa Peter.
Alikunja ameneo
Koma Peter mantha. Mpandowu simukhalaposo.
Wina Aliyense ndale ndaleNgat ali ndalama osasekula ma kampani bwanji athu apeze ntchito
Kodi amaberaso zisakho? Mutiuza ndinu 😅😅😅
Umbukira ndiye kt namathanga ndi asa amabera zisakho eeee mwatisimikizira lero ok
Tavanawo Kuti amabera
Aàaa 😂 brz ukhoza kukhala dolo koma ngati suli mi system ndizovuta kwambiri kupanga kanthu
Aaah system yanji akulu? Mudanvapo mau woti all eyes on me?
Ukatchali upezeka Big mani
Dpp my ❤
❤❤❤dpp
Following
Xoona gyz chikangawa ndi MCP must go 2025 DPP boma ndizomwe amalawi tikufuna palibe kubela zisankho DPP yawina kale
Abwana nkhani za Nkhondo ku fb mukuti bwanji
Aaaa or alikonko anachoka bwanji alikunja kwa mec akutumikiranso Dpp chapansi akunama amenewo tizangodikira kuthamangitsana
Mapazi ak iwey mmaso ngt chikangawa
❤❤❤❤❤
Zizavuta kwbili akunama mcp
Anthony Bendulo anathana nayo kale Mathanga panopa tilindi new system ku M.E.C
Dpppp woyeeeee
😂😂😂😂😂 we are in democracy
Mukunana tigwiresa new system
DPP inabela chisakho basi Osatibwatika tipex tipex tipex tipex
Tachokani mbuzi za anthu, ma massage phwi munthu mmodzi zikutanthaudza chani? DPP ndi MCP mbava ndani?
Amwene mwayakhura bwino koma a DPP alimbane Kaye ndi figure omwe a NRB alemba ku central region game ya gona pamene paja
Zonsezo akuzidziwa kale bro ngati tafika pozidziwa anthu wamba ngati ifeyo ase eeeh.
Anthu awawa akuziwa njila zonse za mcp because once anali ndi mcp 2019 ndy akuziwa zomwe akupanga
Ndi m mene mulungu amachitira anasisa ozikweza nakweza ozichepesa choona ndi choona tidalire ambuye mu zonse
Kuchema 2025
Mafiru Dpp
Achakwela ndare ayambalit kut akaziwe kubela ma vote osagwida.
Aaaaaaa big mwatitayatu Ku Facebook what's wrong
Njovu zikumane
Ukakhala wakuba umacheuka cheuka ,that's what DPP is doing
Tiona drama mu 2025😂😂😂
Bolani asamuphenso
Mukuwulurila Mayeso ku Mcp team ya madala
Chisankho ndi funso loti Kodi 5 years anthu mwayuwona bwanji.Ndiye anthuwo amasankha kuwona amene angathandize kupititsa moyo wabwino KU anthu.Ndiye ngati chipani chikukonzekera kubela that's bullshit.That's why Malawi will remain poor chifukwa anthu olephela akukakamira kulamulira
Mcp Nthawi imene iliku opposition imasiyana 5% ndi dpp,ndiye you think kuti panopa dpp ingawine mcp?remember dpp siinalowepo muboma ndi Vote
Aaah 😂 inuso man umbuli wanu wochita kuuluka masanasana mazoba mwatani kodi iwe what's good with this government?
Machende ako ndiye ukuona ngati chikangawa party iwina ?? Muyelekeze kubera mzaona
😂😂😂😂😂😂😂😂
Nde angapange chani kaya azathamangila ku khoti sazapezaso chilichonse ,dpp muyiwale kubwerera boma kwanu kunatha
Send me your details I'll remind you ng'ona chikangawa party yatha sizaonanso mpando mark my words
DPP yomweyo
😂😂😂
a dad. Muve muliko kut anthu Anu takusowani.
DPP ndiwo eni ake eni eni obera dzisankhowo that is why they talk alot about kubera chisankho
Kodi kape iwe ukusowa wokuyankha eti, zoba iwe eti.
Anakuberapo
@EllahChikwatu yes they did, not only me but the whole Malawi remember 'Tippex gate'
Apapa titha kunena kuti zili bho koma sizinati nkhani yagona pa ID basi awonesese kuti ma boma enanso alibhobho pa nkhani ya ma ID
Nde kut a mec yakale onse anali a dpp chifukwa chake anatibera mavoti ana a njokawa
Jokara ku jokara kaya ndiribe lawyer ine
Boma limozi silingawinise chikangawa
Chikangawa sitikumufuna azipita rip SKC
Ali Kuja kwa boma vuto ndilimenero kubela mcp idakozekera kwambiri pakufunika nzelu Mcp idabwela kuzakhala
Inu mukunama Mcp ituluka mufune olo musafune olo Apm atati asayime athufe tatopa
Kuombela m fiti manja zaziii
Kuombera mmanja za ziii Nanunso,,,mwadya ndalama zingat kuchoka ku MCP kod?
Achina chikangawa mfiti za anthu izii
@@EmmanuelNtago Ndiufuluti musaiwale pangani zanu
Mulungu wathu ndi wa mayankho chakwela achoke bas
Mcp yachepa ndipo chakwera azindikila machende alibe
Akubweraso mungot phee dpp yasunga joka
Amwene MCP idzawinira kamba ka ntchito zake zabwino osati kuba komwe mukunenaako ayi 90%vote ✔️
Maina kwinako azizkuvoterani abulu kkkkk
Shame
😂😂😂😂😂😂😂
Azimayi a Dpp ndi ngenge osati jesse kabwila maso ali tudzu mmmmmmmmm
😂😂😂😂malawi wanga😂😂😂
Kkkkk koma
Kabwira ndi wa kachaso.
By the grace of God mcp must go
DPP ndimadolo asukulu zedi Mbambande DPP❤
I love dpp this one my vote
Ndzimene zikufunika kwambili boma la Peter muthalika
Am proud to vote for DPP❤❤ ndikuona kuchedwa
INSHALLAH zizayenda bwino ❤❤❤
Ana achepa awa, chikangawa party yi ikupita ndithu
Ndipo kwambiri
😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤ umatha ase kulibe kunjonja mcp mafada bas
Bola pamenepo DPP woyee atambwali awa atipweteka kwambiri
Big up brother man!!
Ndale ndinyama yovuta Dpp sibeledwa
Nkhani yoti awiriwa anakhalapo ku MEC sizikugwirizana apa cos pano sali ku MEC.
Koma Jane akuziwa Chisinsi chobera
😂😂😂😂 mvuto munthu ukakhala wakuba umawonaso ngati azakosp azapanga umbava wakowo
Exactly
Poti inu ndi agwiro
Kkkkkkkkkkkkk zisankho izi za 2025 zizayenda mwa myaaaa koma dpp sizawina chisankho amene ali ku opposition basi
DPP ndi chipani changa. Mu February ndinali wa MCP. Lero September ndine wa DPP. Chifukwa chakuti Chilima anaphedwa ndi Chakwera.
Akamufuse Joyce Banda 2014 zmene tinapanga tanyenya 2025 a MCP ana achepa💪💪💪
Ndipo kwambiri kkk
zilibe ntchito zimenezo coz kwawo adachita ajeni ansa amachita kuonekeratu kut ndi wa dpp galu uyo
Kalikonse tizakaona.
💙💙💙💙
apa tikapanda ku winner ndiye kuti abera koma tizapanganso ndewu mcp ndi fellow citizens of malawi watikwana anthu mpaka mwafika pomadya chitedze ayi ndithu chakweradi
Kkkkkkk ndiye athu aope azimay amenewo akubawo kkkkkkk
Ngati dipipiyo idzawine chopangila mantha. Kuti azanu dzabela ndichani
Koma zithunzi kumaika za recent osati zakalekale anthu adakali ndi mphamvu. Imeneyo ndi njila imodzi yo bela zitsankho
MCP ili mmadzi
Okumba dzenje amageeramo okhaa lero a MCP asala okhaa tiwona ngati 50+1 chilima ndii ijaa amupha
😂😂😂😂mumakwana brother 😂😂
Kkkkkk mesa ukunena mathanga ndameuja Anatha ndi Anthony Bendulo
Chikangawa sangawine
Ine ndikungofuna DPP NDI MCP Kaya apanga alliance ndindani koma asalowe boma
Azadya makobili ochuluka kumeneku kutero akufuna kupusisa Peter.
Alikunja ameneo
Koma Peter mantha. Mpandowu simukhalaposo.
Wina Aliyense ndale ndale
Ngat ali ndalama osasekula ma kampani bwanji athu apeze ntchito
Kodi amaberaso zisakho? Mutiuza ndinu 😅😅😅
Umbukira ndiye kt namathanga ndi asa amabera zisakho eeee mwatisimikizira lero ok
Tavanawo Kuti amabera
Aàaa 😂 brz ukhoza kukhala dolo koma ngati suli mi system ndizovuta kwambiri kupanga kanthu
Aaah system yanji akulu? Mudanvapo mau woti all eyes on me?
Ukatchali upezeka Big mani
Dpp my ❤
❤❤❤dpp
Following
Xoona gyz chikangawa ndi MCP must go 2025 DPP boma ndizomwe amalawi tikufuna palibe kubela zisankho DPP yawina kale
Abwana nkhani za Nkhondo ku fb mukuti bwanji
Aaaa or alikonko anachoka bwanji alikunja kwa mec akutumikiranso Dpp chapansi akunama amenewo tizangodikira kuthamangitsana
Mapazi ak iwey mmaso ngt chikangawa
❤❤❤❤❤
Zizavuta kwbili akunama mcp
Anthony Bendulo anathana nayo kale Mathanga panopa tilindi new system ku M.E.C
Dpppp woyeeeee
😂😂😂😂😂 we are in democracy
Mukunana tigwiresa new system
DPP inabela chisakho basi
Osatibwatika tipex tipex tipex tipex
Tachokani mbuzi za anthu, ma massage phwi munthu mmodzi zikutanthaudza chani? DPP ndi MCP mbava ndani?
Amwene mwayakhura bwino koma a DPP alimbane Kaye ndi figure omwe a NRB alemba ku central region game ya gona pamene paja
Zonsezo akuzidziwa kale bro ngati tafika pozidziwa anthu wamba ngati ifeyo ase eeeh.
Anthu awawa akuziwa njila zonse za mcp because once anali ndi mcp 2019 ndy akuziwa zomwe akupanga
Ndi m mene mulungu amachitira anasisa ozikweza nakweza ozichepesa choona ndi choona tidalire ambuye mu zonse
Kuchema 2025
Mafiru Dpp
Achakwela ndare ayambalit kut akaziwe kubela ma vote osagwida.
Aaaaaaa big mwatitayatu Ku Facebook what's wrong
Njovu zikumane
Ukakhala wakuba umacheuka cheuka ,that's what DPP is doing
Tiona drama mu 2025😂😂😂
Bolani asamuphenso
Mukuwulurila Mayeso ku Mcp team ya madala
Chisankho ndi funso loti Kodi 5 years anthu mwayuwona bwanji.
Ndiye anthuwo amasankha kuwona amene angathandize kupititsa moyo wabwino KU anthu.
Ndiye ngati chipani chikukonzekera kubela that's bullshit.
That's why Malawi will remain poor chifukwa anthu olephela akukakamira kulamulira