Asilikali amakatani kumanda a ku Dzaleka refugee Camp nthawi ya usiku?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024

Комментарии • 172

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Год назад +11

    Thanks bosses stay safe and warm continue with the good analysis of data collection I hope the these videos reaches the president so that they can become a turning point into practical mind set change on actual development
    Continue with these

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +5

    Thank you very much bro 🙏🙏👊👊!! Umakwana ndithu!! Umafufuza kwambiri!!

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Год назад +7

    koma nkhani yolimbana ndi obwelayo sinkhani yabwino,tiyeni tikondane ngati tonse tili ndi red blood cells
    ngati achakwela muli ndi connection yopangila nkhaza obwela from Ruanda please khalidwe limwnwli silothandiza mukanasintha

  • @AbelSakala-n2v
    @AbelSakala-n2v Год назад +7

    Give them citizenship cz they need to stay in peace thank u

  • @DyceMusokhiwa-br1ms
    @DyceMusokhiwa-br1ms Год назад +3

    Ur de 1 👌big boss💥💥

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Год назад +1

    Thank you bg mn respect ndawi zonse appreciate your intelligent sir

  • @samkalua
    @samkalua Год назад +3

    Live live 🔥🔥🔥
    Reality exposure

  • @patricklimiton1023
    @patricklimiton1023 Год назад +4

    Mmatimvetsa kukoma but mumatisiya mmalere....mmangosiya kulakhula osasazika

  • @DavieMafunga-f3f
    @DavieMafunga-f3f Год назад +3

    I need to see you face face brother u r the best guy

  • @JohnMwale-ug1uv
    @JohnMwale-ug1uv 15 дней назад

    Bakili tv u r a legend

  • @mustaffahhemmad
    @mustaffahhemmad Год назад +5

    Ndalama ikuononga dziko lathu

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Год назад +4

    Tiwapemphelere ma refugees

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Год назад +3

    Keep up brother manyazi amugwila chakwela

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Год назад +1

    God provide this channel Aman.

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Год назад +1

    Inu ndiye number one basi kwa history

  • @user-pt1fy3qg4u
    @user-pt1fy3qg4u Год назад +2

    Makwana

  • @alfredbanda886
    @alfredbanda886 Год назад +3

    Chakwela Ndi mbuziiiii yomwa Madzi ometela NDEVU,iye akuti waipeza nzake nkunena Kagame.That's why akumawapatsa ndalama ma Bulutuuuuuuuu ena kuti azisokoneza DPP Bwantasaaaa Nyawu Gule wankulu kwawooooo.Agalu inu muziwanso pa 2025

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Год назад +2

    Musaiwale kut ndi MCP olomutaiwuza mutavula pant singamve ndipo ndiyosamva

  • @StevenFombe-s2c
    @StevenFombe-s2c Год назад +2

    Respect brother man❤❤❤❤

  • @christinemapoko6338
    @christinemapoko6338 Год назад +2

    Ulamuliro umenewu ukapitirira ndiye kuti kuMalawi kudzabwera revolution and Iwill be one of them. We are tired of this nonsense now.

  • @clementmwale9222
    @clementmwale9222 Год назад +2

    Timakunyadilani big man

  • @brasiobrasio2113
    @brasiobrasio2113 Год назад +1

    Kulankhula momveka bwino bro big up keep it up be safe

  • @EsteryChidothe
    @EsteryChidothe Год назад

    Vuto la Malawi timatengeka ndizirizonse zimenezi tikuvutika ndiife osati a president Thanks for your information

  • @khadydiop498
    @khadydiop498 Год назад

    You are doing grt job Mr man, keep it up

  • @Hanisa-zr1jx
    @Hanisa-zr1jx Год назад +2

    Ngakhale Ku South Africa ma foreigners ndi omwe akupanga zitukuko

  • @Allantitas
    @Allantitas Год назад

    You are saying Truth brother 👍👍🇲🇼 🇲🇼

  • @rashidstamburi2705
    @rashidstamburi2705 Год назад +6

    Koma kanyoni analakwanji guys 😢🥺😭

  • @Rafiki-pk7hw
    @Rafiki-pk7hw Год назад

    Chanel No 01 here in Malawi

  • @InnocentPhiri-f2f
    @InnocentPhiri-f2f Год назад

    Salute to our own explorer yool

  • @bwijafidel2809
    @bwijafidel2809 Год назад

    A best analyst

  • @ShyreenKafumbwa-bg2nu
    @ShyreenKafumbwa-bg2nu Год назад +1

    Chakwela mmutu mopanda nzelu south Africa ikupita pa sogolo chifukwa cha anthu obwela muzapite ku bellvell ku capetown amalawi azazako kugulisa tomato kuotcha nyama ndi zina za mbili munangotengela boma msanje mmutu mopanda nzelu

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 Год назад +1

    Kagame walitola dziko lathu ndi boma la chakwela mpaka kulowa asilikali achilendo kumanda malawi inazolowela kupempheza mafano esh amalawi made mistakes to voted congress party chipani chanyazi

  • @victormunthali1924
    @victormunthali1924 Год назад +1

    Thanks bro

  • @user-pt1fy3qg4u
    @user-pt1fy3qg4u Год назад +2

    Never give up bro

  • @user-px9jd9co3v
    @user-px9jd9co3v Год назад

    I learn a lot from you broh.keep it up

  • @irenechirwa9710
    @irenechirwa9710 Год назад +1

    Mulungu azikutetezani brother

  • @Vicky-j5k7s
    @Vicky-j5k7s Год назад

    👏👍2much jzy MW wa2.Brah taday you most am appreciate 2.

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Год назад +1

    BIG 👍

  • @Inzirandende1990
    @Inzirandende1990 Год назад

    You are doing great job

  • @issabwanali29
    @issabwanali29 Год назад +2

    Mulungu achite nawo azikhale ng'oma pamodzi ndi chakwera

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol 2 месяца назад

    Ayi bakili tv palibenso😮😮Ingwileni ntchito bwana

  • @samuwilliam7478
    @samuwilliam7478 Год назад

    Anthuwa ndichimodzi mozi Ife muyisiye free

  • @jamesjealous-p4v
    @jamesjealous-p4v Год назад +3

    Nduna imeneyi ikufunika imangidwe chilungamo chiwoneke ndi chigawenga chachikulu

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck Год назад +3

    Chakwala usatinyatse

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Год назад +2

    Ine ndimafuna anthu angati inuyo muzilowa ndale mukhoza kutithandiza E.g Manganya akugwila ntchito kuposa chilima nd chakwela pano.

  • @Shaabann
    @Shaabann Год назад +1

    Thanks to give us history God bless you

  • @AlexMulinde
    @AlexMulinde Год назад

    Am agree with u y bakili muluzi is quiet ? He is the one who bring democracy but he is quiet y

  • @rickiez
    @rickiez Год назад

    Well articulated sir.

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Год назад +1

    Mumakwana big man !!

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Год назад

    Idi amin criterion all the time, for example raising texes

  • @MaryRasmussen-mr4zo
    @MaryRasmussen-mr4zo Год назад +1

    Chakwera needs God to deliver him from evil spirit

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Год назад

    Our main challenge is Bakili muluzi here .. akungolekelera anamupanga bribe ..tikuvutika freedom that he gave to us akungoyang'anira wina wake akutizuza

  • @EmmanuelThom2-xf6ij
    @EmmanuelThom2-xf6ij Год назад +1

    Following

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib Год назад

    Yonse madala madala keep it up 💕💕💕

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 Год назад +1

    Nkhaniyo ndiyowona bro munthu wakuda kuzuzika mu thaka ya mu Africa

  • @yammiejaymakawa5067
    @yammiejaymakawa5067 Год назад

    Awesome bro

  • @JerryNcube-gt3te
    @JerryNcube-gt3te Год назад

    Ambuye atithandize akanyoni komwe Aliko awoneni Maka chitetezo chamoyo

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Год назад

    Komaso mutiuzereko kwa Chakwerayo kuti kampeni si yopangira ku msikiti

  • @patrickchibwana5895
    @patrickchibwana5895 Год назад

    mumakwana big man from here Dubai

  • @AnordThomson-iw5ny
    @AnordThomson-iw5ny Год назад +1

    Chakwera ndi Zikhale ng'oma ndiwanthu osafunika m'dziko lamalawi anthu achabechabe

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t Год назад +2

    Kkkkm😂 indeed chakwera nd nd young brother of id amin 😂😂

  • @MussahIbrahim-e8o
    @MussahIbrahim-e8o Год назад

    Ndinu mbambande brother

  • @brightbautbright8028
    @brightbautbright8028 Год назад

    Ndunayanu ulibe zeru akupangisa kuti bomayambeso kumatingeira kuno akuwona zimene mukuchita kumeneko

  • @francokaunga2707
    @francokaunga2707 Год назад +1

    Brother don't worry, the spirit of God show me a vision that chakwera and chilima their leadership is over! Dk is coming in next election he will change Malawi for better.

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Год назад

    I like you bro ndipo a Malawi ife nde tili dallow koopsa

  • @thimzymastermind9421
    @thimzymastermind9421 Год назад +1

    First to comment

  • @mdyombamw7659
    @mdyombamw7659 Год назад

    Well spoken, wokuda ndi wokuda ma burundi akuzuzika mu nthaka yawo fukwa cha zoba uyu opembeza azungu he doesn't deserve to be called a brother

  • @hopeskafumbiphiri6011
    @hopeskafumbiphiri6011 Год назад

    azikhale alindivuto ngati zinthu zikutelo nanga anthu athawila kuti sibwino kungopanga zokomela munthu modzi bwanji akanakhala ndi iwo ali kumozambiki ndiye anthu aziwatelo so sad. zipani zinazi ndiye ayi bola dzana lija timadandaula za kudala kwa zinthu ndi mafuta osati zopusa zoika moyo wa anthu ena pachiswe ayi.

  • @blessingnamajagali7118
    @blessingnamajagali7118 Год назад

    Mbale zikhale ngoma, please siyani kudzudza anthu otsalakwa, mwabera ndalama yokwana 6milion, lero mukuwadzudza is it fair, mulungu akuone pamodzi ndi chakwera anthu oipa inu, mulozedwe mudzakapangitse mnsokhano kwa goliati mudzaonanso ndalama zonse zomwe mwaba mudzadzitsandza, chakwera munthu woipa iwe

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Год назад +1

    malawi is now lankin as a 3rd poor country in the world. poor governance, jelousy, oppression are indeed some of the factors that are killling malawi

  • @Lloyd-t8k
    @Lloyd-t8k 26 дней назад

    Bakiri muluzi ndi number one

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Год назад

    Kodi Mr Michael Sauka yemwe anapeka Nyimbo yafukolathu,kwao kudalikuti???..ai ndithu Big timadziwa zambiri kwainu ndi fire!!!!!

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 месяца назад

    Komanso nkhanza (nkhanza ndi katangale)

  • @user-tq2lx3iq7s
    @user-tq2lx3iq7s Год назад +1

    Achakwela alephela kusunga dziko alichaba pa business yakumba ndala za amalawi

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад +1

    Umphawi pamodzi ndi nsanje ndizomwe za manga bomali kotero bomali silikufunikanso term inayo.

  • @frankcholimbirapo262
    @frankcholimbirapo262 Год назад +1

    Only God knows 🙏

  • @princekamfumu8497
    @princekamfumu8497 Год назад +2

    Ati kungopita kunja kukapanga za umasikini😂😂

    • @kondwamlungu8384
      @kondwamlungu8384 Год назад

      Nakha bwanji ndi takhala ine/inuyo mungave bwanji kuti ndinu refugees

    • @gloriaprincessjoseph8313
      @gloriaprincessjoseph8313 Год назад

      Akaka naneso kandiseketsa nde anachita kutsindikiza 🤣🤣🤣🤣

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 6 месяцев назад

    Keep on updating bro mumatiimirira tikuchapika mmutu bro a Malawi these pple they are propagandas the (tonse).

  • @josephmvalo3182
    @josephmvalo3182 Год назад

    Uyu chakwera atipwetekesa

  • @jahiemmusa8796
    @jahiemmusa8796 Год назад +1

    chilungamo ndichimene mukuyqngula ulemu wanu bro

  • @Philemon-dt8il
    @Philemon-dt8il Год назад

    Chilungamo chake

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +2

    Ndikuganiza kut emission imeneyi sichotsedwanso pa youtube. Pali emission yinayake pa nkhaniyi yamalefujizi imene inachotsedwa. Sikupezekanso ndithu!! Fortunately, anthu anaipanga kale download before being removed!!

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Год назад

    Zikomo kwambiri big man

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Месяц назад

    Azikhale matama komanso kuipa mtima

  • @BladesBullets-pu5uw
    @BladesBullets-pu5uw Год назад

    Munachita mademo omuchotsa presdent yemwe amapangitsa zinthu kuti zizitchipa. Lero mukulira koma mukulephera kumuchotsa.

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 2 месяца назад

    Akulu inu muyenera kukhala president ndithu

  • @titomethiwa4213
    @titomethiwa4213 Год назад +1

    Mulungu akudaliseni amwene

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Год назад +2

    Koma ku malawi eeeeee ndilibe nako mau

  • @giftsimwaka3971
    @giftsimwaka3971 Год назад

    Only God have mercy on us

  • @HawardZakeyo-fn7bt
    @HawardZakeyo-fn7bt Год назад +1

    Inu ndawakulu ndipo Chanel yanu ndi 1

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Год назад +1

    Kom ziko lanthu ndilomvesa chisoni kwambili, akupanga nsanje ndi ma frica azawo osati anthu a pink wa eshiiii so sad 😏😏😏☺☺

  • @PromiseBarton-em1ll
    @PromiseBarton-em1ll Год назад +2

    Continue kutipatsira nkhani❤

  • @amisichiphiri8227
    @amisichiphiri8227 Год назад

    Boma ili latitopetsa lizipita laononga dziko lathu,tonse alliance boma la nkhaza

  • @khadijailiyasa5315
    @khadijailiyasa5315 Год назад

    Zikomo kwambiri Big,
    Koma titani kuti zithu mukunenazi zitheke kwathu kuno

  • @TrevorChiletso-lo4hk
    @TrevorChiletso-lo4hk 8 месяцев назад

    Pokha pot tili amphawi kamba ka jealous ndi zoona100%

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +1

    Malefujizi anakhana kuaphatsa ndalama makadete aKagame chifukwa ndalamayo ndi imene boma la Kagame limagwilitsa nchito kubwelanso kuzunza malefujizi. Refugees think that by giving money to the government of Rwanda, they are financing themselves actions of destabilizing refugees!! That is why they always refuse these acts!!

  • @lastonkandiyado4526
    @lastonkandiyado4526 Год назад +4

    😭😭😭😭...ife monga a malawi tonsefe ndife athu opusa kwambili ndipo tilibe nzeru or pang'ono athu inu munkampanga mademo ku DPP 2019 mpaka kutseka misewu kuti peter muthalika asaduse kulibwanji mademo omwe aja mutawabwelezaso kuti satano-yo achoke pampandopo kapena tinene kuti ulamuliro wake wa satana-yu ukukusangalasani bwanji mwangoti ziiiii or mademo ayiii tawonani satana-yi mene akumawaphera athu osalakwa sizama refugees okha ayii even a malawi akufu simasewe tawonani njala zithu mene zikukwelera tsiku ndi tsiku koma iyee sizikumukhudza aliduuu basi chimutu thasalala kuma office-ko😢😢😢.. sindikudziwa ngati kuti ma video's Anu ndi ma comment awathu amawafikila koma ngati nkutelo ine ndikuti iwe chakwera panya pako pamodzi ndi nduna zako zonse,,ndipo ine ndine muthu modzi amene sindimakufunira zabwino pa moyo wanga ayiii ndipo sindimafuna even nditava dzina lako likutchulidwa near by me ndipo ndimangolaka laka kuti mulungu atangobwela ngati tsiku la lero kuti adzachitenge chitsilu chukula mutu ngati matako a mayi ake atangochiponyera pakati pa moto kuti chipyi chi nfiti ngati chimenechi fuck you chakwera....😭😭😭😭😭

  • @andrewngowe8836
    @andrewngowe8836 Год назад

    MCP kwawo kapande 2025

  • @yusufbanda4980
    @yusufbanda4980 Год назад

    Kagameyu muzandtsmkzra tsku lina kt azamuukle kagameyu nd asilikali ake omwe. Kunali omar al bashir

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 Год назад

    Koma ine ndikamamva izi mtima kupweteka zedi kodi zimachende zaku mpandozi bwanji nkhaza chonchi ambuye chonde zulani mitima yawo