Thanks brother you deserve the best, mutakhala pasi ndikuganiza kuti it's better you must create bakili muluzi tv munali ndi maganizo apamwamba kwambili, much appreciate coz we know lots coz of bk tv thanks munthu wankulu mulungu adzikutetezani😊
Thank you brother. Politics it's a dirty game... Chilima was sold but the seller will face the same fate let's wait and see. God is not doesn't sleep. God bless Malawi ❤
History is the best teacher long live BMTV ♥️
Thanks brother you deserve the best, mutakhala pasi ndikuganiza kuti it's better you must create bakili muluzi tv munali ndi maganizo apamwamba kwambili, much appreciate coz we know lots coz of bk tv thanks munthu wankulu mulungu adzikutetezani😊
Thank you brother.
Politics it's a dirty game...
Chilima was sold but the seller will face the same fate let's wait and see.
God is not doesn't sleep.
God bless Malawi ❤
Inuyo mumaziwa kufotokoza nkhani and may God protect you always wherever you are
Chaka chino kalikonse kobisika tikaona watching from Mozambique never give up big brother
Sure
Nice boss we are watching the bakili MULUZI TV FROM ISRAEL IN THE CITY OF JERUSALEM
Like your voice my kaptain
Thanks we have been waiting for this one boss
Much appreciated
King your really working❤
Zikhare NG. Oma mutu mometeka ngat ponyela pa nyani
Tilipo panopa braza
I like you brother man
That's MCP we knows big up brother aphana okhaokha 😅😅😅
We love you boss
Thanks koma tatifufuziraninso nkhani ya Jimmy uyu akuti barbecue
u r the Best boss I ma proud of u
Aphanako basi ,big up Big Boss
Your number 1 bro.....
This is hw MCP is Malawi is back in the time of Kamuzu
Atsogo mwanisangalatsa ponkhapo mwatchulapo Moçambique zikomo kwambiri,Ana amozambiqui amafunakoso umabvako mbiri.
Mmmmmm ndiye wathibulidwatu
Respect bg mn
The DC anarosera kale kuti campaign ikawandikira ku mcp kuzakhara ndewu zapachibare
Story for chilima ikuti bwanji
Best youtube is bakili muluzi TV kuti. Wawi
🎉🎉Aululeni basi
He got a good voice yes
Mumakwana brother inu
Tamakusatani baba❤❤❤❤❤
You deserve Boss
The bg up ❤
this channel was created ndicholinga tiziva ndikuphuzira zithu zobisika
Never give up ❤
Keep it up kuwayalusa anganya amenewa
Number one Historian
Tiuzen zoona bro
Father mumabweletsa chilungamo pa malawi
❤❤❤❤❤ bro mukwana
❤ bakili muluzi tv
Mpakà kufika pomatolela protection fees? 🙄🙄🙄🤣🤣🤣🤣
Support kwa bakili muluzi TV bas
2025 agalu amenewa akagwere ku gahena
😂😂😂Tambala Stars pa ground pa telera
😂😂😂😂 Koma kumeneko zioneka apana okaoka😅
Asiyeni akwekwesane okhaokha a MCP 😂😂😂
My ❤❤❤ tv
uremu wanu boss man
😂😂😂😂 ndiye mwati mpaka kumutchola nsagwada kkkkk ayi zikomo
Tiwaonela this year aaaa anamiza ndani
Asiyeni aphane ndi banja yawo or atafa tilibe nawo ntchito coz MCP program ilibe
Kkkkkk, komatu anamutupitsa milomo koopsa
Mukwonago boss
Kkkk koma ziliko oooo ata mawo
First comment for me
Watching
❤❤❤❤❤
Imeneyo ndiye mcp imathibula
Wakudzulidwa 😂😂😂😂😂😂😂
ulemu wanu bg
Kwachema kkk apwetekana kk
😂😂😂 achita bwino kutibulana
Akulakulu Tikumvela Nkhaniyi kuchokela ku Rwanda konkho koma eshh ndi Zoopya ndithu
Timakunyadirani abwana abakili tv
Mmmm mwini wake wa kayoyola mwati wathibulidwa?
😂😂😂😂 Koma kumeneko
Zikhale ndimuthu oyipa kwambili zedi
Kumujangilira nzawo mpaka kumusintha nkhope kumawoneka ngati Izeki.
Kkkkk
Vuto ndi lakuti amalawi vinyanga zikhale pofika next week ndi kupha
Kodi zigawenga za Zikhale Ng'oma anazigwila zitathyola shop mu foreigner pa Wakawaka zija zikanali ku Maula?
Ipondeni fadah 😂
Dada man
Maulemu big
limukwanila straight ndipo live mikwiyo ikuyandikira nyimbo yake tonse tikuiziwa by Joseph nkasa
To run the country it's not easy 😂😂😂😂😂 azafa not even to cry
Ati amutikita😂😂😂😂
Chaka Chino kulivintu 😂😂
Anamuphophola ngati munthu wakuba foni ya Nokia 3310 kale
I always loved bakili muluzi tv but am losing interest becoz of more political stories which is breaking my heart.....
Ungotulukapo pa RUclips page,yi,,,usatinyase mbava za MCP
Apwetekana😂
Zigawenga zimenezi hiyaaa
Zilikotu.kumeneko tiuzeni zoona a Bakili tv
Azimenyana kumene
Atikitanadi miyoyo ya mabulundi adawatumiza osalakwa n kukasungidwa kundende Mmmm anthu mzimu wa mulungu tikuusiya Kuti chifukwa cha ndalama
😂😂😂😂😂 Pamalawi tiziona
Mbambande bwana
Koma nde amugwira ntchito kkkkkk
😂😂😂 umwa cha B 📺?
Mcp sizathekaso asatana afiti gulugulgunyinda
Kufufunza nde mmakwana man,palibenso pa Mlw
Koma bakili muluzi tv 😂😂😂😂
Kkkkk atambala awili salilila khola limodzi lelo sidzi ayamba boxing okha okha koma chaka Chino tizinvana ndikuziona
U r the member of dpp? Since then munasiya kuyakhaula za dpp coz like every day kafukufuku ndi wa mcp
I don't understand what is the benefit of Paul kagame? People are suffering in prison what is his plans?
Komatu amutiburad,mpaka kukamwa kusongoka ngati wachiyao kulikutibulidwa
Wachita bwino kukutumulidwa aakucepesera akanangokupha Kkkk ambav A inu ndi ladzaro wanuyo
Yoh
Ufulu wa malawi
Ife koma guys let's reback ku DPP mcp yatizunza
Azipukutana choncho kuchipani kwaoko nde bwino
Ipondeni fada😂😂
Komatu koma