Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Live from Pretoria ipase moto sis
Ambuye ntengeni ndi osiyana ndi kachaso.....Kumeneko ndi kuba
Mwinatu anamwa asanadye, wanthu ambiritu bizinezi yawo ndiyo mweyo Nanga ndalama wanthu wa akazitenga Kuti, asiyeni
Hanifa keep it up ur doing a grt job
Vuto chakudya chikusowa ndiye adya chiani, kachasu alibe vuto, vuto lina ndi kumwa mwa uchidakwa ndiye akufadi.
hanifa wayamba kuitha tsopano 🔥
Kachaso ndikawawa asamaphwekese game azilonda akumalawiwo
Mwawona nokha amalawi mcp ndiimeneyo muyiziwe mumangomva
Xikugwirizana pat ndi mcp zazii kapena choyankhula ulibe
Kachasuyo akupha anthuyo amaphika ndi a MCP useless
Ambuye dzanditengeni wautsa mavuto 😂😂
Kkkkkkk bas zomangisiya katunduyo iwe kunga'ambikatu😅😂😂😂
Zopusa endani
Ayende maliseche tione zokoka zomwe zinawona Ben longwe zamayi yolamu
Kkkkk kumeneko
Komadi apolice ambili akuphuzilira mukatchatso momwe
Akuletsa kugulitsa mowa koma kulima chamba kkkk km chakwela ndi mbambande ndithu 😅😅😅😅
Ndpo ndiyosagwira bg mn
Ufuludi ukuphwanyidwadi Zedi mmmmm
Muwa mukufuna kt asaguse nde apasenitu ndarama ayambe ma bisness ena
Apasidwa ndalama amenewo.kodi anayamba ayenderapo makampane ama sprit?tikuziwa ife kut akupangila chani ma sprit awa????asiyen azimayi azigulisa mowawo.muwamenye akabweranso apolisiwo asa
Malawi tiyeni tiasiye a police agwile ntchito yawo komaso ndikutha kuona kuti nonse amene mwayankhula pa interview iyiyi palibepo yemwe akukhuzidwa ndi imfa yochitika chifukwa cha magagada police gwilani ntchito yanu zikomo 🤝
Chonchi aziti a malawife ndiosazilimbikira, MCP yabweletsa njala kubwera devaluation, ife tikuyesetsabe kugwiragwira apo ndi apo kuti moyo wathu usinthe akumatilanda nkutimanga opanda chifukwa mmmmm😢😢😢😢😢
Q
Mwina kuwapasa capital ayambe bzness ina
Suga wadulilam kumalanda anthu Katundu wao pali zelu
ayende asiyeni afuna
Mayi auzeni agalu amenewa amcp mbuzi za anthu
Awalakwira anthu atani ndimene zilili zithu panopa koma MCP
Mcp yatani mbuzi iwe
Am the first to comment
kkkkkk kachaso amapha ngati sunadya
Ma because kapena ma problems eeeiiish kma yaaaaa timva zinthu😮😅
Zachisoni kusoweka kwazintchito koseku
😂😂😂😂
Valan tione
This journalist eeeeesh mafutso opanda pake madeya amatani nawo😂😂😂
Malawi Police mmmmmm
Kwinako munva kuti mukhale ndi license muzilipila nsonkho.
Zansonkhozo, dzulo anali ku zomba amalemba mayina aanthu amabisinesi ang'onoang'ono kuti azilipira nsonkho
Akufela ana chifukwa cha manyi amenewo.vuto mimagulisa ndi ana omwe otisakuyenela kumwa kip it up police
Akayenda kuti malichonchowo tikawachingamire koma tsiku nd nthawi
Inuyo ngati mwasakha chisakho chovura ingovurani basi iya.. zauhuleee
I think those people they're selling kachasu the government must give them certificate that's all aboma apatseni zilolenzo zogulitsila
Mcp ndiye imeneyo munyauqona sinus nomwe mumamudukulila chakwelayo inu
Inu zilizonse kuyikamo ndale zina umavera kaye then coment anthù akuti akufa basi muziti mcp ikupha athu
Pitanisoni mukagulise mowa mukathilemo poisonous akakamwa akafendiiwowo
Ayende tione kundata
Akufuna akamwe apolice
MCP ndiyankhanza kuchokera kale siikufuna anthu azichita bwino
Ndipo koopsa bro mmmm
Anthu ena aphunzira school cha mowa wa kachasu Bangamoyo life is hard..
How is a problem in our nation, the nation of Malawi ? Give me the answer. A police ambiri amamwa kachanso, Amwa umene.
Zikavulani ife zitikhuze ,uhulewo munauyamba kale
😢 kom ofunik a police alawe ambuye mtengen
MAGAGADA OMWEWO
Zivulani nanga mnyelo ndi wanga
Ayende tione zinthu
Km chakwera ndi boma lake mmmm chakwera iweyo ndi mwana wasatana wandimva Kaya satana iwe ufiti wa amai ako
Apiga abomawa
Akumaphikila khonje akuti malo mwa sugar ndpo anthu afadi
Kulankhula moveka bwino ndthu ufulu aziuganizira
Abale kachasu siwabwino ukuwononga life ya youth
Asiyen ayende azimayiwa akafikeso ku stat house koko
Mu ulamuliro wa Kamuzu ankalesanso kachasu. Mcp ndiyankhanza. Everyone knows
Boma la Chakwera limenelo.
Ngakhale sindimwa mowa koma kachasu anayambidwa kalenkale kumwedwa no vuto
Kusauka sizinthu
Mnyamata ngati iwe kumamwa kachasu.sukuona wekha mmene ukuonekela
Ayende tikaonera zimenezo
Kachasu ndi mowa wakale kale wa makolo ulibe vuto ,
Kodi iwe za Boni Kalindo zikuti bwanji?
Akalindo ataniso kodi
Mvulani icho ndi chisankho chanu.. mmene mukuwonekelamu muzivula 😂😂
Asiyeni avule mesa mulungu wayamba ntchito yake mvulani muyaluka nokhatu
😂😂😂 mulibe mabikozi or polebulemu
Nde Lero a police alezeratu😂
Ndiposo eshiii 😂😂😂😂
Wakhuzika chilima 😅😂
Bola kuvulako kkkk
Anthu akuvutika kale koma nkuwaonjezera mavutonso kma boma ilili aaaaa
Ati zipweteko
Business imeneyo ndiyoipa athu healthy wise sizimakhala bwino apeze ma business ena
Mowa wamakolo ulibe vuto ukamwalilanawo umakhala kut sanadye or amazondedwa dangerous bear umapangidwa kuma inderstry ovomelezeka ndi boma chakwera he knows that
Job well done police kapena nkhope ziyambe kuwona bwino
Akulu inuuu hanifa mwaigwila ikuchita kubeba
Walankhula bwino kwambiri mzimayi iwe.ndakukonda banja😂😂😂😂😂.apaseni katundu wawo anthuwo zayambika liti zolesa mowawo?tizelezeka ndichani achinyamatafe???kachaso ndimowa wabwino kwambili mngonena kut akutumani kapena akupasan ndalama zambili amakampani omwe akupanga mowa wama sprit osat kunama kut wapha anthu.zausilu.apolisi nanu galu simchedwa kutengeka
Ayende anthu awone malesawo
Kwachanso yomweyo
chilimadi uyu wavala cha green, akufanana kamwa
Mene wadulila shugamu eeee
Mwaudze.ayende.mbulanda.tiwone.ngati.ali.ndizokokadzo
😂😂😂
😢Km zliko ndthu
Koma ziliko ku boma la tonse Alliance
Mcp 😢😢😢
Akumamwa asanadyele ndie asafe akapanda kudya umapha kumene kumwa osadyela
TAYENDANI TISUKE MASO
This death are because high sugar price, shortage and the lazy affair of government to act on this. Pano instead of acting proper apezela njila yowabela aphawi. At #7 best govern country my black ass
Mwina anthu akufawo akumamwa asanadye nsima nanga kachaso ndi mowa Wakame kale ndithu
Sintchaya😂
Ine sindimwa Koma Ngati mtelo aboma asadalande bwanji azikhala NDI adotolo azipima ndipo akanangotseka mowa ulionse Monga dziko lowopa chauta
Ine ndinaphudzila chifukwa cha kachasu still now mayi anga amaphika kodi apolisi vuto lanu ndichani
Ife timkadziwa kuti mcp mudasankhayi, mapeto ake ndi amenewa.anthu akufa ndinjala,ndiye chilungamo chake.
Uchisilu imeneyo ndi business yodyadirisa koma matha mulibe ndi Mulungu
Tikungodkra ayende athu ndi Maso tione malisechewo
Ndiye akautenga ataninawo akaodwtsa kuti
Tione zokoka zomwedi adazinena sir Ben longwe za mayi yolamu
😂😂😂😂😂