Don't be afraid Ntanyiwa,,,keep on updating truthful,, God is still protecting you all,,,through our prayers,,, this leadership is from satanism but through the power of God they are exposing clearly for any mission.
Comrade ntanyiwa palibe amene angakupheni kumwamba kuli Allah akutetezani mpaka Allah azakutengani osati mcp Allah alipo komaso ambili mwaife timakupempherelani
Malawi Defence Force do your best for the Nation. President osadziwa kanthu kulephera kukaponda pomwe panafera wachiwiri wako eeeeeeeee Koma Man Lazalo inu munaphadi 👹⚒️⛏️🔨⚒️👹
Ili ndi dziko la atsogoleri opusa zedi.Kodi ndimayesa kupereka ndalama mwa njira imeneyi ndi njira ya ziphuphu?Chomwe ndikudabwa ine ndi choti boma la lazalo likupanga za ziphuphu yet akuti akuthetsa zinthu za mtundu umenewu
Ma Israel ndamene anakagwesa ndege ku chikangawa, akayidi ndamene anapita ku airport usiku kupanga service ndege , mwachidure amakachotsa zinazina mundegemo
More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥asilikali
Why Malawians live this shupit presdent like that just see hw poor Malawians suffering no food
Comrade Ntanyiwa Mulungu azikubisani ku Mapiko Ake ndi a Born Kalindo🎉🎉🎉
Ayaluse ntanyiwa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Koma akuzinamiza chakwela ndi ndina zake amalawi mwachidule tingoti tatopa ndi mcp chaka chamawa kwatalika kwambili
Exactly comrade
Komatu comrade mumakwana ngwilanani manja nonse ndi Mr bon kalindo l love u guys
Mcp ingotuluka basi chibwana chachuluka ku mcp tiyen tingomuchosa chikangawa basi ma comrade
Mtanyiwa 🔥🔥🔥🔥
Don't be afraid Ntanyiwa,,,keep on updating truthful,, God is still protecting you all,,,through our prayers,,, this leadership is from satanism but through the power of God they are exposing clearly for any mission.
😂😂😂😂😂
Bwana ntanyiwa tidziweko nkhani ya ma demo ija ili Pati pano
Comrade ntanyiwa palibe amene angakupheni kumwamba kuli Allah akutetezani mpaka Allah azakutengani osati mcp Allah alipo komaso ambili mwaife timakupempherelani
Zisisi zonse timaziwa ndi ntanyiwa ndithu MBAMBANDE Limpopo fm
More fire chachuluka ndichibwana kwambili izi zikhoza kupangitsa dziko lanthu kunkhala pamavuto kma ntchentche nsaitanira pachimbudzi.
Kkkk mitambo mpaka munthu kuthyoka miyendo esh
MANGANYA ASAMULORE KU UTM KUPIKISANA NAWO SI MEMBER WA UTM NDIPO ASAPITEKO KU CONVENTION
Ntanyiwa wathu wathu🎉🎉🎉 ...mor 🔥
Comrade inuyo ndi anzanu awa,the FC and Bakili tv ndinu akatundu
Mosesi kunkuyu ndi munthu olimba mtima kwambiri satana...kunkuyu ndi wakupha pamozi ndi gulu lake ...boma ilili litule phazi udindo ndithu 👹👹
Ayaluke basi Ntanyiwa agalu amenewa atinyasa kwambri ndale zili apo koma kupha Chilima kuja mmmmh anabhowa chakwera
Eekoma zowosha chakwera ndi muthu orengedwa ndi Santana osati murungu udatiphera muthu ofunikira kumarawi chisoni muribe athu 9 kuwasiyitsa ana awo Bora adakadwara anawawo adakarimba mtima koma eeeer zosavetsetseka izi
More fire biggy
Bro Ntanyiwa timakunyadirani, keep it up
Akaidi amenewa siomwe anakapopaso mafuta amundege amenewa esh
Malawi Defence Force do your best for the Nation.
President osadziwa kanthu kulephera kukaponda pomwe panafera wachiwiri wako eeeeeeeee Koma Man Lazalo inu munaphadi 👹⚒️⛏️🔨⚒️👹
True that 😢😢
MDF siili kuimilira dziko ngati
Chitetedzo cha all Malawian's zomvetsa chisoni ili mu nkhwapa mwa Chikangawa coz siikugwira ntchito paokha
Mburi zophunzila esh kk ndipo masapota sangapange Mistake
Asambwadze akugona ngati ndimadolo Nd palibechamsisi pano padzilko zoona zake adzaziona. Kip it up my comrade mtanyiwa.❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Chikangawa ndi Hyena wodya anthu
Asilikali azitero nanga azioneka ngati ose ogona😊❤
Zomvesa chisoni kwambiri esh
Akuyalutsani Ntanyiwa zanu zada basi mabodza onse onena za ngozi za bodzazo mumuze amene angakunveleni ife timanva za Nthanyiwa basi angakunveleni
Live from Tanzania
Kkkk koma inuyo mumatha
Khani ndiyoona asabwazeni ameneyo Moses mkukuyu ndi zake zikhale Ngoma eeeee amenewo ndi athu oipa
Kacheja kkkk
Ulemu wanu Mr mtanyiwa go deepar
Malawi wavuta
and God will not allow these things to go randomly
antanyiwa mulungu azikupatsani moyo wa utali
Ulemo wanu MTANYIWA mumakonda AMALAWI mulungu akusogoleleni nthawi zonse
2025 chakwera life gel
Tizikupephelelani Kuti asakupheni mulungu ndiwabwino
Timadikila Inu
Mademo akhale oti atule pansi u president
More fire ntanyiwa
Koma zimene umalakhula umadzidziwa kapena umangozindikila walakhula
Lero mukut akaid mukupenga et
Koma alibe zochita zina basi kumangopha anthu ndi zomwe akuziwa apite kufambwe amewa
Nkhangaaaaaaaaaaaaaaa zaonaaaaaa🎉
Mumatiyimire broz
Ili ndi dziko la atsogoleri opusa zedi.Kodi ndimayesa kupereka ndalama mwa njira imeneyi ndi njira ya ziphuphu?Chomwe ndikudabwa ine ndi choti boma la lazalo likupanga za ziphuphu yet akuti akuthetsa zinthu za mtundu umenewu
Ngati kwatsala fm yachilungamo ndi Limpopo fm ndi comrade ntanyiwa
Koma chakwera wagwa mwamanyazi kobasi kumpha wanthu zoona zika za AMALAWI chakwera ukhaliketu
Mademo big alpat
Kenyan move. More 🔥 🔥 🔥 🔥
Or ASILIKALIWO angomunyenya mutuwakeo chakwera watikwana kobasi Ku Malawi kuno
Antanyiwa inuyo Mulungu azikubiseni ma phiko ake, awuzeni chilungamo athu oyipa awa
Kodi za mademo aagoni alikoo?
❤❤❤
Yomweyo mtanyiwa
Chakwera zamuvuta
Kodi tizafatsa or kugona mpaka liti Malawi ife
Then these pipo are going to doom times television 📺
Mtanyiwa umandimalizakobas
Chikangawa manyazi bwa
Asilikali osaopa
Munthu wochedwa ntanyiwa ndi chitsiru
Naoso azafa
🔥🔥🔥🔥🔥
Sekelere nkutafune
Mitambo ingachose brack box ndkupitisa ku state House
Eti inu kkkkkkkkkkkk
Etieti just imagine
Mumakwana
Ngati zili tero kulibwino tikafukule mitembo ika yezedwenso ?
Alowa ku kolokolo ukana goti kunyero
Thats my Comrade Commander Mtanyiwa big up Brooo you are the best.
Osaopa,
Osatopa ,
Osafooka.
MCP -- Malawi Chikangawa party killers, 👹⚒️🔨⛏️⚒️👹
ziliko
😂😂😂😂
😂😂
Is your aunt Mbilidzi kapena samiri Muluzi what are the real names because ye you said mbilizi? Bodza limaiwalika
Munkati anali ma Israel lero mukt akayidi mawa munenanso dzina tamatiuxani zowona koma
😢😅
Kkkkkkk
Ma Israel ndamene anakagwesa ndege ku chikangawa, akayidi ndamene anapita ku airport usiku kupanga service ndege , mwachidure amakachotsa zinazina mundegemo
😂😂uyu atipusitsadi
Anthu ena kutsata nkhani kumakuvutani
Mtanyiwa 🔥🔥🔥🔥