ZENI ZENI ZA KALIATI KOMA IZI - BOLA ASAMUSOWETSE MNYAMATAYU

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 25

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 12 часов назад +4

    Yes be strong 💪 mr man 👨 💪 this government is nonsense government 🙄 we don't need 💯 this government again

  • @BlessingsMarley-l2x
    @BlessingsMarley-l2x 7 часов назад +1

    MCP yawonjeza zedi ndipo tatopa nayo this government no sens is very bady government and is very rude sitikuyifunaso ndipo tasikimizadi kuti boma la MCP ndi yankhaza

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 6 часов назад

    ❤❤❤❤❤❤❤

  • @CourageBanda-d1g
    @CourageBanda-d1g 10 часов назад +1

    I'm sure mulungu atengapo gawo pazonse zomwe zikuchitikazi anthu atopa

  • @ADAMSONGONDWE
    @ADAMSONGONDWE 12 часов назад +2

    The truth shall set you free

  • @ErnestJohn-gp1ub
    @ErnestJohn-gp1ub 12 часов назад +1

    💪💪💪💪💪💪💪

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 7 часов назад

    osawopa osafowokaaaaa

  • @ChipiriroDumba
    @ChipiriroDumba 7 часов назад

    Asatuluke ameneyo

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 10 часов назад

    Kaliati kapirikoni buzi kd Mesa Inu Antanyiwa mumati akariati amayakhula ndi achimwendo ndiye bwezi atawamanga inusomumanama ndiye chani kd mene mukunyozera Apure inuyo Ali abambo anu mungave bwanji .
    Mwina Apure saziwa km nduna zinakhala bwanji nthawi ya dpp achisare ankanamizira kt ndi Apm guys tione zithuzi

  • @EmmanuelWhite-h7e
    @EmmanuelWhite-h7e 9 часов назад

    Nfanayu akunena zoona ,nthawi ykwanad

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 10 часов назад

    Koma Atuluseni...mai Kaliyati.... eeeish

  • @spargomw
    @spargomw 12 часов назад

    Koma ndie kuli kunenelera ngat Mpira😂😂😂

  • @Mobilot2android
    @Mobilot2android 10 часов назад

    Komatu anthu amatopa😂

  • @TinoCharamba-hr9el
    @TinoCharamba-hr9el 12 часов назад +1

    Kod sanati kulowa bwalo lamilandu

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 11 часов назад

    Ngati UTM yatha, boma iopa chani galu iwe

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 11 часов назад

    Tikufuna anyamata monga awa,ndipo l which I was there,ife tinamenyana ndi apolice akamuzuyo, ndiye talowa mu democracy atibvutetso?ine ndinganalowa momo.anyamata,ogona kukhomo kosatseka mcp yagwa pazokhazi,ndipo palibe akuwafunatso.

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 11 часов назад

    Kodi a police muteteza boma la nkhanza amai anu kumuzi akusangalala ndi boma ili ?

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 12 часов назад +1

    Kaliati anthu samukonda, taonani kumeneko kkkkk, kulibe wanthu omutsatila, kkkkk koma

    • @shadreckphiri1799
      @shadreckphiri1799 12 часов назад +2

      Kulibe fuel

    • @TracyBanda-i2g
      @TracyBanda-i2g 10 часов назад

      @@shadreckphiri1799
      Wamuudza bwino kuti mafuta kulibeko athu akadakhamukirako

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 11 часов назад

    Mcp tasiyan zomanga athu plz manyadzi bwanji

  • @JeremiahThaulofromMalawi
    @JeremiahThaulofromMalawi 9 часов назад

    MCP ur decampaing ur self can't u advice each other guys kaliati has been campaigned tu take the readership mantle wat a shame

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 12 часов назад

    Utm yatha mayo ineeee!!!!! Kkkkk