COMRADE LYTON MANGOCHI - OPPOSITION CHENJERANI MUKHALA MUKUMANGIDWA NDITHU

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 38

  • @lyiemax
    @lyiemax 8 часов назад +2

    Powerful talking from our beloved comrade Lyton Mangochi ❤❤❤❤

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 часов назад +6

    Ineyo ndiye chakwera amandinyasilatu .....pa 4 years wakhala ngati president palibe chomwe wapanga chopindulila mmalawi .....this is the worst president since democracy came

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 9 часов назад

      Worst president dziko lonse lapansi abale

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 9 часов назад +7

    Ofunika kuwadziwa khopezawo a police akumangaathuwa ndimaina awo boma tikasitha osewa tchito ikuyenera ithe

    • @spargomw
      @spargomw 9 часов назад

      Ngat sidzawathera ndwkut akawaponye kumamidzi kotheratu. Zitsiru zawanthu. Zimavala nsapato zoti eniake adafa kalekale

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 10 часов назад +3

    Big up our comrade Mr Mangochi

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 9 часов назад +3

    Micheal Usi osazamuvotera chonde madeligates Manganya ndi munthu oyipa zedi ndiyemwe adamupereka Chilima kwa Chakwera kuti aphedwe

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 10 часов назад +3

    More fire big

  • @ADAMSONGONDWE
    @ADAMSONGONDWE 9 часов назад +2

    There is no secret under the sun

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 7 часов назад

    Ulemu wanu brother Mr Mangochi osatisiya kutiimilira ife A Malawi 🇲🇼 MCP ndi anthu okupha

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 9 часов назад +2

    Ndipo apolice amenewa boma ili chakachamawa akatuluka osewa wakundende aziwe zimenezo

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 10 часов назад +1

    Apolisi ambili ndiokuba ndipo sangapange chilungamo ayi ....amalandila ndalama zochepa ndiye amangovomeleza zili zonse

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x 9 часов назад +2

    Mu utm mulid chisikaliyott pochiona chimakhalaa ngat cha misala yake chikdalinayoo

  • @EddahKaunda
    @EddahKaunda 4 часа назад

    Very good father

  • @FlynessWinga
    @FlynessWinga 7 часов назад

    Wow great

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 7 часов назад

    Your right mr Mangochi

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 8 часов назад

    Big up Mr mangochi

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 6 часов назад

    Ukunena zowona chakwela ndi president osazindikila pama president onse mpaka kuposedwa ndi mzimayi Joyce banda

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 10 часов назад +1

    Udasi sikariot ndi Micheal Usi Manganya

  • @ADAMSONGONDWE
    @ADAMSONGONDWE 9 часов назад +1

    Expose the evil one

  • @MariaNyamwera
    @MariaNyamwera 6 часов назад

    Ndipo akwawo kwatha apakire adzipita 😂😂😂

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 9 часов назад +2

    Zakeyu wamanga kaliati

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 7 часов назад

    Ipatse moto Mr mangochi❤❤❤❤

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 9 часов назад +1

    Mphamvu comrade mangochi ❤

  • @AnnahMpamati
    @AnnahMpamati 7 часов назад

    Ndipo mwayakhulatu ma point okhaokha, chakwera is the badest and the worst president in Malawi,apapa zawakanika achakwera no vote at all, 😭😭ndipo tweee

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 7 часов назад

    Power💪

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 6 часов назад

    President ogwila pansi mkumapanga push up aaaaaaaaa sakukwanila kukhala Tate WA dziko lamalawi

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift Час назад

    Usi ndiyemwe akupanga izi

  • @MakeSunshine100
    @MakeSunshine100 6 часов назад

    Tiyeni nazoni a Lyton Mangochi

  • @oswardzenizeni1458
    @oswardzenizeni1458 7 часов назад

    Mcp mumanga bwanji kaliyati osamanga chikagawa

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift Час назад

    A police abili apita ndithu chaka chake ndichin

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 4 часа назад

    Ulemu wanu amangochi

  • @JackMvura
    @JackMvura 7 часов назад

    Zaziiiiii

  • @CourageBanda-d1g
    @CourageBanda-d1g 7 часов назад

    Timve zambiri zikubwera

  • @JangiaChisoka
    @JangiaChisoka 6 часов назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂 ndale xakwa africa

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 5 часов назад

    Kkkkkk yaa

  • @AtonMhango
    @AtonMhango 4 часа назад

    😮😅😮😅😮😅😮😅😅😮.