TONDE WADULA YATAYA MUNTHU M’MODZI OFUNIKIRA KWAMBIRI - BAMBO CHIBIRITI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 июн 2024
  • TONDE WADULA YATAYA MUNTHU M’MODZI OFUNIKIRA KWAMBIRI - BAMBO CHIBIRITI
  • РазвлеченияРазвлечения

Комментарии • 374

  • @GrantWhisck
    @GrantWhisck 19 дней назад +3

    Ndithudi tinachokera kwa Allah ndipo kwa iye ndikomwe tidzabwerera💔💔

  • @nicechimeza9977
    @nicechimeza9977 18 дней назад +2

    zoyakhula ndetilibe Malawi ndesalibwino tikuluza athu ofunikila siku linalililonse nzimu wawo uuse mumtender makwale asowa owavutisa 😭😭😭😭

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa 19 дней назад +4

    😭😭😭😭 nzimuwawo uwuse muntendere kuchokera kuno ku South Africa johannesburg ine ndimmodzi mwa anthuso amasatira tonde wadula : magawo ambiri omwe amatenga achibiritu pa sewero, adali. Ophuzisa limodzimwa magawowa, ndi ( kutha banja komaso opandakathu nkubwerera kumakakhala pakhomo paazibale ako, umakhala chisiru) (komaso pabanja masiku ano samalimba ukakhalakuti ndiwe lova/opandachochita?
    Achibiritu , ngakhale ife kuno kunja kwa malawi tikukulirani R,I,P 🎉🎉🎉

  • @chimwemwematias6069
    @chimwemwematias6069 19 дней назад +2

    Ndikukanika kumvetsa izi am speechless ndithu aaaa I will miss u Mr chibiliti RIP

  • @chimwemwekaliati4151
    @chimwemwekaliati4151 17 дней назад

    Just to see the video inenso kuyamba kulira. Ndaphunzira zambiri kudzera mwa a Chibiliti. Kudzichepetsa kwawo komwe akufotokoza anthu osiyanasiyana kumaonekera ngakhale mu sewelo. mmene anadzichepetsera kubwelerana ndi anagumbo, mmene amadzichepetsera achina makwale akamawazumza. MZIMU WAWO UUSE MUMTENDERE

  • @blessingsalim3218
    @blessingsalim3218 17 дней назад

    Mmmm mzimu wao uutse ndi mtendele 😢😢😢

  • @Matabwah5
    @Matabwah5 8 дней назад

    Will miss him... He was a man trying to make acting better Mhsrip

  • @SleepyHarmonica-rg4ic
    @SleepyHarmonica-rg4ic 18 дней назад

    Zosayenda bwino nditu taludza munthu ofunikila kwabasi koma tingoti mzimu wawo uwuse mutendele

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 19 дней назад

    RIP MR CHIBILITI,KOMA MWEZI WA JUNE UWU EEE TALUZA ANTHU AMBIRI

  • @BoccatiKaliyati-ky7cv
    @BoccatiKaliyati-ky7cv 18 дней назад

    Tidzakusowani pasi pano ndithu bambo chibilitu RIP

  • @vincentmatemba1659
    @vincentmatemba1659 19 дней назад +1

    Yooh we will going to miss you mr chibiliti 😭😭😭😭 mzimu wanu uuse mumtendere

  • @ChisisiSaynett-nm7uq
    @ChisisiSaynett-nm7uq 17 дней назад

    Zimu wachibiliti uuse muntendele😭😭😭😭😭

  • @owenmagagamsowoya4036
    @owenmagagamsowoya4036 19 дней назад +2

    Deep from my heart am really sorry may his soul rest in peace ine ndili kusouth Africa koma ndimasatira ma comedy ose kuphakizapo tonde wadura achibiliti Asiya gapu ku tonde wadura

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 19 дней назад +3

    Oooh! too bad. a Chibiliti luso lanu tizalisowa, Mzimu wanu uuse mumtendere.

  • @SleepyAnteater-bh5zo
    @SleepyAnteater-bh5zo 18 дней назад

    R I P mr chimbiliti tikusowani mpaka kale😭😭😭😭

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 19 дней назад +1

    Naneso ine kuno ku south Africa ifa ya a chibiliti yanditulusa misoni, maka maka mene amayamba kulira atonde wadula nane zinandililisa zimu wawo ukause muntendele R.I.P 😭😭😭😭😭😭

  • @KaduniKaripinde
    @KaduniKaripinde 19 дней назад

    Innalilah wainaihu rajiwoon
    Kodi ndichoonadi kuti mkhulu uyu anamwalila .chinachitika ndichani

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 19 дней назад +1

    Nkuluyi analidi wozichepetsa ndipo timusowa eish ayi mzimu wawo ukause mumtendele😭😭😭😭

  • @elizamaster2168
    @elizamaster2168 19 дней назад

    Mmmmmm 😭😭😭 ndazizidwa nd uthengawu,

  • @khumbophiri9006
    @khumbophiri9006 17 дней назад

    Inna lillah wa Inna ilayh rajiun mzimu wawo uwuse mumtendela😭😭😭😭😭💔💔💔

  • @watipasomzungu9911
    @watipasomzungu9911 19 дней назад

    Tood bad! May God rest his soul in eternal peace.

  • @AnabelleBanda-gx9ii
    @AnabelleBanda-gx9ii 19 дней назад

    Ummm rest well Mr chibiriti tikusowani mu tonde wadula ummm 😭😭😭

  • @shamiunamuhammad9081
    @shamiunamuhammad9081 18 дней назад

    Rest in peace Mr Chibiliti imfa za chonchi zimakhudza heavy

  • @zaithwachiwaya8885
    @zaithwachiwaya8885 19 дней назад

    Rest in peace Mr. Chibiliti😭 luso lanu tilisowa

  • @etomansailes4932
    @etomansailes4932 19 дней назад

    Yoo achibiriti tikusowan kwambiri pot kunalembedwa kut tidzafa nzimu wanu uwuse mumtendere 😭😭😭😭

  • @Senifala
    @Senifala 18 дней назад

    Rest in peace madala.....we'll miss you 😢

  • @EdythGloryNamponya
    @EdythGloryNamponya 19 дней назад

    Amadwala mmmh abale...we wl mis you achibiriti😭😭😭

  • @franciscoduartie5762
    @franciscoduartie5762 19 дней назад

    Ause mu mtendere Mr chibiliti.

  • @YusufuAfana
    @YusufuAfana 19 дней назад

    Mzimu wawo uuse muntendele mr chibiliti

  • @estherkamwendo7971
    @estherkamwendo7971 19 дней назад

    Rest in peace my favourite actor, we will miss you

  • @user-zd2ne1ic2v
    @user-zd2ne1ic2v 17 дней назад

    Iiiiii koma zikori zovesa chisoni kwambiri 😭😭😭😭

  • @user-sk1wj9bw6l
    @user-sk1wj9bw6l 18 дней назад

    Tizawasowa kwambiri ndipo amativesa kukoma mzimu wawo uwuse muntendele

  • @EmmReece
    @EmmReece 19 дней назад

    mmmmmmmmmh may his soul rest in peace, tiwasowa kwambili mulungu alandile mzimu wawo

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q 18 дней назад

    GOD KNOWS ALL.
    AMEN

  • @user-qs2tx7wt6g
    @user-qs2tx7wt6g 19 дней назад

    We miss you chibiliti

  • @lillahnmahuzahshabah5883
    @lillahnmahuzahshabah5883 18 дней назад

    We will miss Mr chibiliti😭😭😭

  • @SainanPetro
    @SainanPetro 18 дней назад

    Zosayenda km malawi tikuluza anthu ofunikila ambuye ngati kulikotheka landilani mzimu wawo

  • @bonfacenyalaya2177
    @bonfacenyalaya2177 19 дней назад

    Shaaaaa mzimu wawo uutse mumtendere Napepetsa ku banja lonse la Bambo Lester komanso mudzi wonse wa a Willium

  • @GiiiKatekesa
    @GiiiKatekesa 19 дней назад

    Mmmmmm tataya munthu wofunikila

  • @user-tu2zo3kp3y
    @user-tu2zo3kp3y 19 дней назад

    Zimu wawo use mutelere mr chibiliti tizawasowa 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @gressiabel6850
    @gressiabel6850 19 дней назад

    Mzimu wawo uwuse mu mtendere.

  • @GerardFelixDyson-tp1sp
    @GerardFelixDyson-tp1sp 17 дней назад

    May His Beautiful soul Rest in Peace 🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹

  • @EmmaBanda-id4lg
    @EmmaBanda-id4lg 19 дней назад

    Oh zosayenda mzimu wawo uwuse mumtendere

  • @ganizankabango
    @ganizankabango 18 дней назад

    Ine ndili kuno ku South Africa ku Durban anali msangalatsi wanthu nzimu waw uwunse muntendel bambo chibilit

  • @RobertsMchaga-oe1iz
    @RobertsMchaga-oe1iz 19 дней назад

    My condolences to the Family and comedian team. Kwa khalila ife tsono. Tiyeni Tive kuitana kwache Christ Jesus pa khomolo lopapatiza

  • @bonifasthemba9624
    @bonifasthemba9624 19 дней назад +1

    Mmmm abale Taluza ofunika R I P Mr Chibiliti

  • @FelistasChiwanda
    @FelistasChiwanda 18 дней назад

    Mzimu wawo uwuse mumtendere 😭

  • @FumbaniNyirongo-lj6jg
    @FumbaniNyirongo-lj6jg 16 дней назад

    Rest easy Mr chibiliti till we meet again

  • @yesayabongwe4234
    @yesayabongwe4234 19 дней назад

    What a loss, may his soul rest in eternal peace

  • @ROICOTv
    @ROICOTv 18 дней назад

    Mzimu wa achibiliti uwuse mu mtendele tilisowa luso Lani💔😢😢😭

  • @BlessingsBanda-ih4th
    @BlessingsBanda-ih4th 18 дней назад

    Vuto ndi makwale ndi zakhwima amakonda wavutitsa. R.I.P.

  • @user-yp9gn2km5q
    @user-yp9gn2km5q 12 дней назад

    Rest in peace mr chibiliti.wl never forget you.

  • @Munya-vu2md
    @Munya-vu2md 19 дней назад

    My condolence to Tonde wadula member's

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 18 дней назад

    Eish koma life Pena I like tonde wadula chibiliti wapitadi tonde wadula sorry guys

  • @paulinahmanyowa3787
    @paulinahmanyowa3787 16 дней назад

    Ummmm shame bambo chibhiriti nzimuwawo uwuse muntendere from Zimbabwe 🇿🇼

  • @annieaubrey-gx7vg
    @annieaubrey-gx7vg 19 дней назад

    Mmmmmm mzimu wawo utse mtedere Mr chibiliti 😭😭😭

  • @robenmatchilinga604
    @robenmatchilinga604 19 дней назад

    Rip Achibilit tikusowan mu tonde wadura

  • @IbrahimSaid-hu1uf
    @IbrahimSaid-hu1uf 19 дней назад

    Zimu wawoo uwuse mumtendele

  • @vinh509
    @vinh509 18 дней назад

    😢😢😢😢😢😢 zachisoni kwambiri kuno kumozambique

  • @Enjelinatembo-h9m
    @Enjelinatembo-h9m 19 дней назад

    Zachisoni kwambili tinazolowela achibiliti amuna anagumbo tikusowani mwasiya gapu lalikulu mulungu akusungilileni mupaka tizawonaneso kumoyo osatha ngati pena pake simunachite bwino mulungu akukhululukileni

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 19 дней назад

    Ndasweka mtima kwambiri 😢😢

  • @madalomachira7766
    @madalomachira7766 19 дней назад

    Rip,heaven has gained. Tikanaonera momwe zithere ndi mkazi wa new one abale😢😢😢

  • @KelvinEdwin-bn2qv
    @KelvinEdwin-bn2qv 18 дней назад

    Lest in paece mr chibiliti ntchito zanu tizisowa 😭😭😭😭

  • @EmmanuelBenjamin-qy2us
    @EmmanuelBenjamin-qy2us 17 дней назад

    Rest in peace mr chibiliti tilisowa luso lanu mmmmmhh

  • @givenrichard-rz1tg
    @givenrichard-rz1tg 19 дней назад

    I can't believe how ,god why ?chibiliti RIP

  • @BenjaminGondwe-po5dq
    @BenjaminGondwe-po5dq 19 дней назад

    Mmmmm mzimu wawu uwuse mutendele

  • @LinesiKanzota-fw7sj
    @LinesiKanzota-fw7sj 19 дней назад

    Rest well tikusowani ndithu tingoti mulungu afungatire inu nose a tonde wadula

  • @nsanidephiri
    @nsanidephiri 19 дней назад

    😭😭😭😭😭😭 Mmmmm ai zosanda ndipo zandikhudza Kwambili

  • @user-vz8ql9kl8w
    @user-vz8ql9kl8w 19 дней назад

    Rest in peace achibiliti.... apapa sizinayende 😢😢

  • @user-wm7db8zx6g
    @user-wm7db8zx6g 17 дней назад

    Rest in peace mr chibiliti ine kuno ku Johannesburg mulungu ndikuti akulandileni emen

  • @PrinceKangoma-rk7ls
    @PrinceKangoma-rk7ls 16 дней назад

    mmmmm mmmmm so sad Rest in piece mr chimbiriti tikusowani

  • @user-ln1qr7jg6w
    @user-ln1qr7jg6w 19 дней назад

    Sinto muito ,,, vou sentir saudades ! Que deus abençoe voce!

  • @Mercydanie
    @Mercydanie 19 дней назад

    Nzimu wawo ukause mutendele 😭😭😭😭😭

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 19 дней назад

    Muzimu wao utse mumtendere

  • @user-bo8kn2rs4z
    @user-bo8kn2rs4z 19 дней назад

    😢😢😢😢😢zonvetsa chisoni kwabasi 😢😢😢😢

  • @user-dc3bo2ey8t
    @user-dc3bo2ey8t 19 дней назад

    Zimuwao uusemutende Mr chibiriti

  • @YahooYassin-ft8df
    @YahooYassin-ft8df 19 дней назад

    Nzimu wawo onse mumtendere😢😢😢😭😭😭

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi5487 19 дней назад

    Eish koma imfayi

  • @ShabaaniAdam
    @ShabaaniAdam 19 дней назад

    😢😢😢😢😢😢 Zimu wawo uwuze mutendere

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 17 дней назад

    Tikusowani achibiliti ndaliratu eish

  • @user-wm7db8zx6g
    @user-wm7db8zx6g 17 дней назад

    Yo yo yo komano achibiliti dzandikhudza m.zimuwawo use mumtendele mulungu akawalandile

  • @jrculdickson6629
    @jrculdickson6629 17 дней назад

    ndalemba ndafuta ndikulembatso ndikufutso koma ai ifayi

  • @user-nm7mv3wr1s
    @user-nm7mv3wr1s 19 дней назад

    Oooh so sad may his Soul rest in peace,wl miss u bambo Chibiriti

  • @patrickzembani4315
    @patrickzembani4315 19 дней назад

    Continue rest in peace we will miss you

  • @macdonaldchifupa7458
    @macdonaldchifupa7458 19 дней назад

    MHSRIP mr chibiliti tizakusowani

  • @MosesMahowe-vn2tl
    @MosesMahowe-vn2tl 19 дней назад

    Mmmm achibiliti amadwala

  • @elessjia9306
    @elessjia9306 17 дней назад

    Eishhhhh ndalira so bad MHSRP Mr chibiriti

  • @peterbanda3005
    @peterbanda3005 17 дней назад

    Dzimu wawo uwutse muntendele tiwasowa kwambili

  • @sharieffrancis
    @sharieffrancis 4 дня назад +1

    Rest in peace

  • @MiriamPhirip-vr2fi
    @MiriamPhirip-vr2fi 19 дней назад

    Mzimu wawo uwuse muntendele

  • @IsaacKachala-ny9km
    @IsaacKachala-ny9km 19 дней назад +1

    😢😢😢 Rest in peace

  • @user-hj8wr7zb2m
    @user-hj8wr7zb2m 19 дней назад

    Rest in peace Mr chibiliti tidzakusowani mzimu wanu uwuse muntendele 😭😭😭😭

  • @user-bg7lk9sx7n
    @user-bg7lk9sx7n 19 дней назад

    Zosayenda...rip Mr we loved you.... pepan akubanja

  • @user-qq6lw6yo8y
    @user-qq6lw6yo8y 19 дней назад

    Abale pepani kwambili tataya munthu wamkulu wofunika mzimu wawo uwuse mumtendele

  • @kingnavitcha6243
    @kingnavitcha6243 19 дней назад

    MHSRIP unbelievable kmano ndye Zakhwima ndi Makwale amenyanso ndani 😢😢?kma ndye dzosayenda amadwala Kodi ?

  • @fatimaamidu3967
    @fatimaamidu3967 19 дней назад

    Rest in peace Mr chibiriti

  • @superiormoses4802
    @superiormoses4802 19 дней назад

    Eish Rest in peace legend.

  • @marryrobert7092
    @marryrobert7092 19 дней назад

    😭😭😭 RlP mr chibiliti.

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 17 дней назад

    Mzimu wawo uwuse mutendele

  • @MIMIEZenga
    @MIMIEZenga 19 дней назад

    Mmm achibiliti amwalila yoooo dzikoli abale zimu wawo use mutendere