Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mfumu gaga😂😂Asiyatu walowa mbola 😢...Che mollen ameta
Chaka Chino tikuwina basi kkkkk
Koma a Chiphwanya akangoziwa zoti nkazi wao wayamba zake kuvuta 😂😂😂😂, nayeso Pharaoh wayamba zinatu
Morel waoneka bwinotu wametamo ❤
Farah kubweretsa mkazi pa home aaaaa iwetu wako ulendo ukhala umeneo kkkkkkk😂
Gaga akuyeneradi kudziwa tchito yamutu😅😂Mama Tikudalira Inu Mutikozere Gaga ndi okanika uyu😅😅😅😅
Big up falao wapeza ya nyimbo kale nawe😊😊😊
Aphalawo mwatenga nanu chikwazi chanu hahahaha inutu mupakira sure
Mayi chiphwanta ndi anagumbo palibe kusiyana😂🤣🤣😂🤣
Asiyatu kuchulukidwa kwakoko. ugwidwa
Best comedy
Farao watchetchemula wake kuno 😢😂😂
Gaga sazatheka
Afalawo mwachita bwino kupeza mkazi musamvute chisomo
koma gaga mutumu mulibemo ma gyz mumachulukisa nkhani kwambili
Mwaswela mwaswela mwaswela
Mwafookatu mumachedwa
Madam chipwanya nde sakuziyendesaso bwinotu
With no zimveka mmmmmm mbola
Tonde atenge make dola timuwone ziveka
Inu mukutenga perspective yofanana nane
Farao wapeza wake wake, kodi tsopano Chisomo sayamba naye nsanje? Tikudikira mwatchidwi next episode
Jazila unapala gaga simamuna
Big up my people ❤
Molle bola mmene mwametamo
Asiyatu aphetsa anthu
Kd farau akufuna kubweza ngazi umakwana farau ndimavananu kukoma nose ngaizi zikomo ine BM1 from Namiyango Bangwe BT Malawi
Ndipo amalawi ambili akukukondani ma guys
Asiyatu wawalatu
Falawo wapata omuchosa nkhawa kkk nice one guys
Koma mupwetekana
🤣🤣🤣 at adakamgot Nadine Rand kkkkkkkk gaga
Muli booh anhamata
Chiphwanya ndi more fire
Mwaswera mwaswera😂😂😂Chiphwanya suzatheka
Zabwino zonse farao
Mbambande
Koma kwachemaaaa kunoo
Farao bambo achopeza
Falawo wapata
Kkkk
Jazira vs asiatu
ya Ku stagiyo nde ndikaing'alura Kwa chiphwanya 😂😂😂
Jazira uphunzitse chikhalidwe gaga😂
Mai chiphwanya ndi hure😂😂
Amunao sawakhala kah😂
Koma faraoh
Afarao chisomo wasanduka achemwali anu??😂😂😂😂
😂😂😂😂 Gaga ndiombwambwana😂😂😂❤❤ kungokula mutu koma nzelu mulibe,
Mole ugwidwa
Falao wakwatira xili bho kwambili ndithu 😂😂😂😂😂
Kkkkk Achikwanya thamangani mudzawone akazi anu
So much love guys keep it up
mumakwana
💪
Mukuoneka nyatwa man Moly after kumeta, zilibwino koma muwauze ada mukuwaikila line kwa mkazi wa Chiphwanya asamale
Lets change the name of the comedy from tonde wadula to Gaga saundila😂😂😂😂 😂
Koma farao watola mpini ndinkhasu lomwe😂😂
Mumatimvetsa kukoma kuno ku mozambique tete❤
Achiphwanya ndi akulu Anu a chibilitu, kodi manowa ndi style yanu 😂😂😂 chifukwa ndiye munafananatu nkamwa
Falao ndikutha kuona mimba ya chisomo iliyako moti palibe chance yokwatilawina mkazi cz chisomo wakukubisila chisisi akufuna aone zuluzako
Apa nde mwabwera mwa coming🔥🔥🔥🔥
Matimilila gyz
A chiphwanya m'kazi uja awapweteka kkkk
Kuva kukoma basi from cep town
Faraoh watola khasu ndi mpini womwe 😂
Morel looking handsome ❤🔥
Apa ndiye bolani more wametesa
❤❤❤ zuchita kubeba kwabasi ❤❤❤
Mwaswera mwaswera mwaswera
Super family mumatimvetsa kukoma
Farawo
😂😂😂😂😂👍
Gaga amathaaa
Chiphwanya 😂😂😂
kodi ma part enawa akumabwelezedwa etii special part yagagayi yokuba chimanga ndinayiwonela last week panopaso akuyibwezelesaso 😢
JEZILA IN ARSENAL JERSEY 🇯🇪 WOOOOW MY FELLOW ARSENAL FUNNY ❤❤😊
Choka
Molly mmene wa meta, akuoneka sharp
😂😂😂 zikuchita kubebatu
Khobalilo wameta sisi
😂😂😂😂😂 wafoyilisa gemu.
Koma pharaoh nde amandisangalatsa kwambiri
Iwe mole ukuziwa kuzemba Ku court
Mwaswera mwasweraa
Team falawo 😅😅😅
Ma guys gaga amandiwazaaa
Mai chiphwanya ayamba unyengesatu
Pa gagapo mwebwereza 😢
Chiphwanya amantha achibiliti kuphwekess
Achiphwanya zagwilen kuno wamasuka kuno
Koma ziliko mpakana chibwenz asiyatu wamasukatu
Fadah 🔥🔥🔥
Kodi achina Tonde mudakalipo
Timayamika kwambiri
After a long time
Mumayivetsa kukoma
Munasowatu madolo
Very Long time
Sizikusagalasaso
falawo mwapana kogendagenda 😂😂😂😂😂
Mfumu gaga😂😂
Asiyatu walowa mbola 😢...
Che mollen ameta
Chaka Chino tikuwina basi kkkkk
Koma a Chiphwanya akangoziwa zoti nkazi wao wayamba zake kuvuta 😂😂😂😂, nayeso Pharaoh wayamba zinatu
Morel waoneka bwinotu wametamo ❤
Farah kubweretsa mkazi pa home aaaaa iwetu wako ulendo ukhala umeneo kkkkkkk😂
Gaga akuyeneradi kudziwa tchito yamutu😅😂
Mama Tikudalira Inu Mutikozere Gaga ndi okanika uyu😅😅😅😅