Welcome Mundelanji, a Chibiliti tamalimbani mtima ngati a Zimveka. Nagumbo wakutani kodi. Mai Phiri game mumaitha. Muthinda samala mwana wako aise I love you welfare ya mwana umadziwa. A Nagumbo musamutaitse nthawi Chibiliti mwayi waupeza koma nayenso kaya ndi kupanda manoko chidodo. Love you guys mmakwana
Welcome Mundelanji, a Chibiliti tamalimbani mtima ngati a Zimveka. Nagumbo wakutani kodi. Mai Phiri game mumaitha. Muthinda samala mwana wako aise I love you welfare ya mwana umadziwa. A Nagumbo musamutaitse nthawi Chibiliti mwayi waupeza koma nayenso kaya ndi kupanda manoko chidodo. Love you guys mmakwana
Ndipo project yomaiyamba iwe mwini wake kulibe amangokudyera...kulakwa kwabasi.
Madala chakuti chakuti kwina kwake kuli 3 kkkkkk❤
Mai o nde ndi owala koma chibiliti yo😃🤣🤣🤣
Kkkkkkkkk mayi phiri muuzeni mkadziyo ine ndilipo
Muthinda anazatenga pangolin wachina zakhwima kkkkk
Zinveka 😂😂😂😂😂😂😂😂 Chibiliti uyigwala wena 😂😂😂😂
Kkkkkkkk koma zakhwima ati ndalama zili umu
Wakuku a zimveka mumakwana!!!!!! Kkkkkkkkkk
Kkkkkkk Amy phiri murindi vuto
Zimveka ulendo wa Chibiriti mayi Phiri
🤣🤣🤣 chibiliti wathawa mkazi okongola
Welcome muderanji❤
Achibiriti amuthawa mkazi😂😂😂😂
Koma Zimveka mumamupatsa nthawi yayikulu bwanji koma samavazanso ayi
Chimphwanya ndiwe galu mpaka mwaswela mwaswela mwaswela bwanji
Mude... Welcome back🎉
Hello
Hahahahah😂😂😂 that's mr zmveka...the guy I like most🎉🎉🎉🎉one wik mah dollah not around ❤❤❤❤
😂😂😂😂koma mayi phiri kkkkkkkk achibiliti yankhulani
Kkkk mwaswera mwaswera mwaswera
Koma Achibiliti ndi one😂😂😂
Komatsu guys mamayitha😂❤
Km ziveka mmmm umakwana unali kt masiku wenawaso timakunyadila ndithu
Chibiliti wathawa 😂😂😂
Zimveka wel explained bruru umakwana aise
Welcome back mudelanji I miss you
I LOVE THE RELATIONSHIP BETWEEN EMMA AND HER FATHER MUTINTA 😊😊😊😊😊😊😊
But they should have picked a better actor for Emma's role. She portrays a chimidzi act. Mwana waku town samayankhula Chichewa cha kwathu Ku Mulanje
@@TheLeezo inde emma di apanga zachimidzi
Bem vindos de volta grupo
Kkkkkk achibitili yabaleka kkkk watch from south Africa JHB
Chibilit kuithawa
Kkkk achibiliti 😂😂
Km ziveka mmmm umakwana unali kt masiku wenaws
Kkkķkkk km2 mai phiri
Kkkkkk achibiliti
Zimveka ndi pangolin. Sakukhumudwisa
Chibiriti wandilakwira wava
Mr Zinveka
😂😂😂😂😂😂 Zakhwima
Watching from mwineriwa vg mulanje
Zimveka, muthinda ma ulemu
😂😂😂😂😂😂😂chibiliti
Mr chbiliti mpaka kuthawa nkadzi kkkkk
Chibiliti ndi chibiliti😅
Zimveka machine amphepo
Azimvekaaa paka kusitha limulocko😂
Azimveka it's true...nnakumanana nawo ku 3 kmaso ndaiwalakut ndiku 23, 43😀😀😀😀
Banja labwereratu
Koma Zimveka amakwanira...😂😂😂😂
Zimveka is really mad
My best actror is Zimveka. Muku zizungu kkk
Koma Zinveka simunthu wamba 😂😂😂 muli nkhanitu
Amai phiri you wa above ❤❤❤
Mai phiri ❤vs mude munasowatu
Ine nde olo muthawire kuno ine ndionerabeee😁😁
Achibiliti yakhulani chilungamo ati bwanji chemwali😂😂😂😂
Achibilit eeee kumuopa mtsikana kumeneko munazolowela tnchembele et
Chibiti kufunsila kutani kkkkkkk
Chibiliti wang'ambika😂😂😂
Welcome Muderanji missing❤❤❤❤
Wathawa chibiliti
Watching
Welcome back mayi molen😂😂😂
A Zimveka mbambandee😂😂😂
Enjoying from Zambia Katete
Kom muthinda kkkkk sazatheka
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Koma zakhwima umandiwaza
Achibiliti kumuthawa nkazi 😂😂😂😂
Iwe muthinda sukufana ndimwanayo ayi😂😂 ukufana ndi Achitsime 😁
😂😂😂😂 mesa alikwamfumu kazi
❤❤❤❤❤
You are best guys, keep it up!
Achibiliti akukanika kutulusa fundo akungo kandakanda
Love u mudelanji
Bwana zimveka mumakwana
❤❤❤❤guys morefire
Chiphwanya💥💥💥
Mulekeni chibiliti pliz kkkkkk
Komatu a Chibiliti zavuta apa😂
Mwaitha
Chibiriti kuthawa mukazi wabwinono bwinoyo chifukwa cha na gumbo yemwe amakudyeraso azanu
Ine ndachedwa bwanji😂😂😂
❤❤
Koma azimvekaaaaaa mumakwana
munasowa mude
Chibilit kuthawa ngat running 🤣🤣🤣🤣
Bola relo am on nomber five tu watch😂😂😂
Achibiliti kuthawa kkkk
I'm first to watch and to comment
Welcome guys
KOMA ZIMVEKA UMAKWANA KKKKKKKK 🎉🎉🎉🎉🎉🎉😅😅😅😅
Let's give them a thumb and like the episode
❤❤ Mai phiri kikik
EMA MY VOTI KKKKKKKK 🎉
Musadzafe
Mudelanji Adasowaaa
Yeeeeeee
Yaleroyi ndi more!!!!
❤
Episode 98 ndi 99 sizikusiyanatu
Ulemu wanu guys