Koma mayi shokoshoko akamamwetulira ndiye akumasangalatsa bwanji 😂
Mwana wamkango my favourite 🔥🔥🥰
Ana amudyangu ose afoira kwa zikazi kkkkk following from south Africa Midrand side
Koma kwa mdyangu😂😂😂😂 ai zikomo
Kkkkk kd Mr Nepaman mwavalawo malipha maphazim kkkkkkk",Ngat wavala chang'az
I love Mai shokoshoko she is beautiful
Beautiful indeed
Nice one
Ya ndimadikilila ine saname mimandimvetsa kukuma 😂😂 e mumandichotsa nkhawa
Francoh wayamba kumuvetsa kuwawa Nepman, kkkkkkkkkk
Kadwafu kkk welcome back mr chokochoko
From Mozambique watching the program
watching from cape town mwana wapa zomba songani man joe tailor nep man umakwana
Nde mwati anyamata amapedzeka munkhalango akufuna atakatile makuwo🤣🤣🤣
Mai shokoshoko can smile 😂😂😂 beautiful smile always
Live from south Africa cape town
Kkkkk koma mwana wa mkango aaaa wabwera kuzakhaladi sungamuthandize chiphwanya moveka bho
Wina akuti first to watch 45 mins ago... winanso first to comment 48mins ago😂😂😂
😂😂😂😂 koma amulelemba, mayi chokochoko ati nda ex anga😂😂😂
Mwana wamkango ndipeleka lobola 😂😂😂😂😂 ndine
Ine ndikule inu muchepe
Kamwanako ndie kakutakatira makuwo ###koma chiphwanya kkk
Kkkk Nepman my guy kuuma kwabwanj uku 🤣 komanso silipasiyo nde eee 😂 mai shokoshoko mmandiwaza hvy 😂 Junior Mdyangu kupasidwa ndalama mkuzatulukanso nd nsima yomwe 🤣🤣🤣
Naye ching'axy angooneka ngat antchona😂😂😂😂
😂😂😂😂 Akazi koma akazi Ashokoshoko momwe muvutira muja koma njara ija anakonza
😂😂😂😂😂😂 shokoshoko ndi half Man
Today is my birthday no one like my comment 🥹
Happy birthday to you
Happy birthday to you 🎉
Happy birthday Dear
Nep man mwaluzatu apa kkk
Mwana watakatira makuwo kunooo🤣🤣🤣🤣
😂😂😂kom mulelemba ubusa muwusiye mwava
Kkkk ashoshoko akuti za size ukuziziwa ndiwe😂😂😂
Mayi shokoshoko she is very beautiful yoooh
Half Muthu kkkk 😂
Am first to watch 🎉
No one is talking about the nepman shoe😂😂😂😂😂
My daughter did ndipo waseka heavy 😂😂😂
Kaya ikupezeka nyanja iti
Bwanji osangomenya ameneyo a shokoshoko kkkkk
Kkkkk inu mukule ine ndichepe yemweyo
Km nyumba imenei ikalipirudwa let kkkkk yamalata,yosawotcha kkkkkk abale ziliko
Kkkkkkk mayi shokoshoko ATI x wanga 🤣🤣🤣🤣🤣
Chipwanya maboza Kaya 4n ndyawodi❤😂😂😂😂😂😂😂😂
Apa bolano yayamba kuveka
Ambuye ndiwabwinooo koma amulelemba
😂😂😂Achphwacha mwana wa mzako half man
Mwati akusintha chani chikombole kkkkk koma guys za size mukudziwa ndinu
Koma ili bwino apa ndikuwobela Ine kuno ikumveka
😂😂😂😂 anapita ku half time a choko,choko koma guys ndaseka kkkk
Akuti kufusira kumandivuta chifukwa chani😂😂😂
Upulofeti wako wabozawo kkkkk
Mlelemba last scene wapha hvy kkkkkk
❤❤❤❤ first to comment
eshi weavzone wa chambo cha fresh😊😅😅
Yaaa yayamba sopano ❤️❤️
i like it
Quuen love you ndwe wabho I hope tizakumana zakuone
Kkkkk kumadwafu😅😅😅
Komaso mwana wa nkango amatha gyz eee ndikatundu
Nepman bwino kumupa francoh kkkk
Mulelemba wati bwanji 😂😂😂😂 APA iliboh heavy nepman Mpakana kukana nsima at nkhawa kkkk
a Junior mwalilowa banja koma shokoshoko akupeze😂😂😂😂
Kkk Nepman mwati kufumsila kumakuvutani mkazi walora kare uyo
Tafika💃💃💃💃🔥🔥🔥🔥
Watching from Westville DBN❤
Km nepman ndimavuto nsaname mpakana canavas wa fish ai zikomo😂😅😊
Nep man game wailuza kkkkk
Kudontha mafilu defiya
Chiphwanya ubashala wakukwana bwelako kkkkkk😅
I'm watching from blantyre ndirande ❤
Km ajunior kulongolola ai zikomo😂😂😂😂
Ashokoshoko musabwere ngt dolo munasiya mkazi ndi njala apa osamtumizira ya chakudya, mumatani atani? Pano ndi mai steve AKA land lady to be😂😂😂
atakatire makuwo kkkk
Kauzeni ankolo akufunsililreni mnakazi oyimbainu hillbrow jouburg
nice
😂😂😂😂 nep man 😂😂😂nkaz olola lola uja 😂😂😂
Nep man imeneyo slipas 😂😂😂
Mule ufuna umpake peanut mmanja mwa Mai Shokoshoko😂😂😂
Nepman adzimangiliratu kuno😂😂😂😂
Ati nzanune ndathodwa..koma chiphwanya ..zankazizo😂
Kma chiphwanya aaaaaa😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤
Agwidwà kuno mayi shokoshoko 😂😂
Mabodza chiphwanya😂😂😂
Mulelemba koma 😂😂😂😂😂😂
Mai shokoshoko mumativesa kukoma ❤❤❤
Ching'aning'ani kanyembete wamkulu😂
❤❤staff ikokedwe🎉
Nepman mutu sukugwira😂😂😂
Mayi stive from mayi shokoshoko aaaa mwina tizolowerabe 🤣🤣🤣🤣
More fire mabomba
Kkkkkk koma sapato ya nepman makina😂
nepman chamba chinamupweteka mfundo zovaila mulibe🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mayi shokoshoko beautiful
😂😂😂😂akudikila wani day di😂😂
Kom Abusa mwata sah watan ???
Kulibe mpira opanda change😅
Zikukhara bwanji volume
Koma nsapato ya Nepman 😅
Kkkkkk koma banja la adyangu silizatheka
Mawu sakuvekatu koma bwanji
Kodi Sindi ( Mai mulemba) mubereka lit?,😂😂😂😤
Inu mukure ine nichepe😂😂😂
Mai shokoshoko kusinthasintha chikombole😂😂😂😂
Amene tinatumizapo transport let's gather😢😢😢😢
No sound bwanji😢😢😢😢
Nanu mayi shokoshoko mpakana shoti ❤❤❤❤❤ kkkkkk

Koma ili bwino apa ndikuwobela
Ine kuno ikumveka