Mangochi umakwana koma Harry mkandawire gotani hara ndi Michael Usi ndi Lazro Chakwera osayiwala Valentino phiri ndi omwe anapha Chilima ku chikangawa 😮😮 koma Chakwera achoke anthu akufa ndi chitedze iye kumapita kunja CHIMUNTHU CHA khope yoyipa yankhaza chicchakwera chimwana chake chachamba chija chi Nick Chakwera chimamuna cha Rudo mkukupa ziyanthu zopanda manyazi 😢😢😢😢
last enjoyment Timba kuvina komaliza miyendo nkuthyoka nguluwe inalira msampha utaning'a miyambi yonseyi nja chakwera akudziwa chawo palibe next year ndiye let him use his time, positon /rank without hindrances no roadblocks no traffic no humos no atree kuti angaombe
Komano zisiru Zina zikulowa ku MCP kufuna ndalama basi
KOMA NDASEKA ,ANTHU ATOPA IIIII ATI INET NDIPITA NAWO PASSPORT YANGA IYI IIIIII KKKKKKKK
Awuzeni big ❤
Powerful ❤❤❤❤
Mangochi umakwana kaa
❤❤❤❤Ndipolive
Auzen brother
Oh yes
Kodi paja munati anakuomberani aja sakhalisa pano zili pati?
😂😂😂😂😂😂❤❤
Chakwera akupusisidwa NDI wasatanic
Kkkk eee koma akulu awawa akuvutika kwabasi😂😂😂😂
Mangochi umakwana koma Harry mkandawire gotani hara ndi Michael Usi ndi Lazro Chakwera osayiwala Valentino phiri ndi omwe anapha Chilima ku chikangawa 😮😮 koma Chakwera achoke anthu akufa ndi chitedze iye kumapita kunja CHIMUNTHU CHA khope yoyipa yankhaza chicchakwera chimwana chake chachamba chija chi Nick Chakwera chimamuna cha Rudo mkukupa ziyanthu zopanda manyazi 😢😢😢😢
Tawapasani ka 5 M avutikatu awa
Ndipo live 2025 tipuma ndi mavuto awa sukunama mangochi
Cadet iwe
😂😂😂😂 koma eeee, chikangawa wapita dzulo ndichikaz chake chonyasa nkhope ngati kazizi😮😮😮😮kukanyovwiza misonkho ya amalawi...ndpo kuona ndkomwe kuli chakwerayo abale akusowetsa mtendere amalawi mmmmm😮😮😮😮 mbuzi ya munthu
Kkkkkkk live anthu atopa
Inu olembanu mudzilemba dzowona nanga njira mukudzinena inu ndidzimene wane iye Mangochi dzikugwirizana?MCP ikutulukadi
Ayakhule ave
Apa ndiye mwabwela
mmene imawina MCP nkumatenga mipando kumpoto kuja mmesa iwe unkateroso? iweyo uzilubwalubwa chakwera mpaka 2030
Bwana kabwenzeni zomwe akupasanizo 1/50 kuti MCP idutse mpaka atapha a opposition leaders onsetu
Zowona wina aliyese apite koko
Mcp kwawo kwatha manyaka eni eni
Auze agalu amenewa a Chikangawa amve Ng,'ona party
Auze abwampini awa.
Kodi akulu inu muli mbari itiyo
Adapitilakonji kumsonkhanoko
Pena umakhara mbali yanga Pena ukhare mbali ya mdaniwanga
Awuzeni
The only way to fix chakwera kuti asamyendeyende ,akati akupita muja aliyense passport mmanja kupita kukakwra naye ndege atalipire ndiye ...akafunsa bwanji kumuwuza kuti tatopa kudya chiteze tifuna tikadye nawe masosege ndinkhumba zako ukudyasi nafenso tilawe kukakwerera azimayi athu kumiko azungu mwina zingakome kuposa mmalawi muno am sure sangayendenso mpaka 2025
Kkkkk inu mukuyenera kukhala a pule athu 2025
Kkkkkkkk😂
Azingodya Kilombelo Ku Karonga uko
Zoona abambo
Kom mmalawi muno tusuta kwambr awa ndandani Ot angachotse mcp
Dzoona zimenezo aLyiton apuresident anthu adziko lamalawi akungo tibera misonkho yanthu kumangoyenda yenda Koma dzakuti anthufe Kuti tikufa ayi iyeyo zosankhuza mmalo mwakuti atipase dzimene anatilonjedza ayi ndipamene akutuma anthu Kut awampe anthu akwauza dzoona mmene Lili dziko lanthu ndipamene akutuma agalu adzikuwa anthu apusa olo pamene akukutuman katundu mukugula mudula bolani dzikana nkhala Kuti akakutumani adyozeni azanthu bola mudzimuudza Kuti tikawanyodza pasika katundu tikagula mochipa mudzi wafusa chocho ana afisi
last enjoyment
Timba kuvina komaliza miyendo nkuthyoka
nguluwe inalira msampha utaning'a
miyambi yonseyi nja chakwera
akudziwa chawo palibe next year ndiye let him use his time, positon /rank without hindrances no roadblocks no traffic no humos no atree kuti angaombe