Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Chemandota ife tilibe nsanje GOD BLESS U
Che Mandota simudzathekanso ngakhale pang'ono.Ndiyetu mukonzekere kukalipira Milandu yonse mwapalamula.Mwadya a Fisi,mwalowa Nyumba yosalipira 😂😂😂😂😂😂.Keep it up Che Mandota.Continue entertaining,educating and Teaching.
🤣🤣🤣🤣 akuti ndizangotenga ndalama zimenezo ndizamulembaso ntchito otupa mutu 🤣🤣🤣🤣
Kkķkkkķ sweet from the beginning up the end ULEMU wanu chemandota 🤣🤣🤣🤣🤣
😅😅😅😅😅😅😅 km akulu awa makani ali ndi awa😂😂😂😂
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
Nice really Appriciete
Yours excellence my best comedy
Koma uzuli mwazinta chivukwa shani🤩This is power💪
Hahaha eeeh chemandotaa akomoka bola sipaja zimathera kunyamulidwa😂😂😂😂
😂😂😂 mandota
Koma amandota mpaka chisaka bag 😂😂😂😂😂 akutiso sisikakwana kkkk
Cosoma must see this😂
Iwe ndikulosan mwangodya mu restaurant mwanga no kulipira km ndalama nd K500 yokha😂😂😂😂😂
Umakwanila aise 🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩
❤❤❤mumakwaka ndinu Dolo Chemandota mumatifesa kukoma❤
My best comedy experience with all
Kkkk koma chemandota mpaka saka bag yotengera ndalama inuyo munafika 😂😂
Chemandota inuyo musadzafe mudzangosowa😁😁😁
Taonani kuda😂😂😂Iwe galu kwabasi.
Ngat ndingoipanga like kawiri lividio iyiyi mwakunga
Welcome again chemandota timadikilati lifidiyo lanyuwanili respect more ❤❤❤❤ I love you to much
You never change 🤓🤓🤓🤓
Mandota ndi 1 keep on burning
Kkkkk uyambire kuwathawa ma board guard akowo bwanawe, cz nde usosoledwatu😂😂
Munthu watenga saka bag kt akanyamulile ndalama eti ili 500 kwcha😂😂😂😂😂
Iwe aaaa misala iyiyi utisunga koma😂
Afisi aja ndadya pa ngongole 😂😂😂😂
Mandota ndiwa 1 paribeso umatha
Koma munalakwitsa kusiya ntchito mwachangu😅😂. Anyway I enjoyed the comedy 🔥🔥👏
😂😂😂😂😂 chemandota mphuma zinthu yooooo n Any way ulemu wako basi❤
Mandota ndi dolo katatu😂😂👏👏👏
Che mandota mpaka adya afisi😂😂
😂😂😂 me lafus you too much
Chemandota kupupuluma kwambiri 😂😂😂ngani yacosoma pakana kuziya njito 🎉ilike your comedy's❤❤
Mandota iweyo unabwela kuzakhala bass
One day muzapanga shulushulu yabwino
You make Malawi Proud lol : I’m Washing you’re video Here in Mauritius 🇲🇺 hahah
Koma ndaseka 🤣🤣🤣u never disappoint 😂😂😂😂😂
Umatitsamwitsa aise ndikuseka❤
Che mandota 🎉🎉🔥😂😂😂😂
Mandota again 😂🙌Stress free 😂😅
Akuti actor wafa😂😂😂😂😂😂😂
It's million or trillion for me 😅😅😅
Eish mandota,iweyo uzafela mmanja mwa anthu iiiiiiiiii✨...😂😂😂😂😂
Utsilu ka munthu umango fikila kuchuluka nzeru
😂😂😂😂😂😂Ndye nyumba ija mukalipila ndchan
Ndemwati afisi right kkkkkk 😂😂
Acta wanga mandota amandivesa kukoma
Che mandota iwe galu ndithu kkkkkkk umatimilira Mali fisi osati mahule
😂 😂 😂 Afisi ndye akudikila zawo uko
Koma ma Mayili alipo muwapatse moni🤣🤣
I love you Chemandota ❤️❤️
😅😅😅😅😂 munalalatatu kwa abwana ndiye zikutherani bwa??
kkkkk komatuuu or mukomoke koma kunjaku akudikira malipirooo 😂😂😂😂 koma mandota aiseee kkkk
😂😂😂😂
She mandota phuma😅😅😅iwe Andu akupani
Mumakwana Mr Che mandota 💯🔥🔥💯
Always stand with mandota ❤
😂😂phuma ndi ndalama Che Mandota
😂😂😂😂 koma cosoma ahhh 500 kwacha
Fire.... ambasada, Wachiyao
Bwanawe Mandota 😂😂Wawoo wa puma
Akut billion or trillion 😂😂
Title yanyimbo mu back ground 🙏🏿
Lero m'mbazada wangokomokeratu
Nde driver akudikila 50 pin yake😂😂😂😂
Koma nde ndaseka 😂😂mandota iweyo ndi dolo bas
Koma mbasada Umakwana 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nde mwat mahule nda afisi 🤣💔
She mandotatu safuna wakomoka pokumbukila ma bill a anyamata ndi wa galimoto
Kkkkkkk wagwa ndi bp akakata kukozekel uy kkkk
Akut afisi ndadya pangongole😂
Komatu masowa pokuikani inuyo aah makwana
Nice Dr mandota
Nkhotakota love you ❤❤❤
😂 Unabwera ngat comming😂
Ana anzanu mpaka afisi😅😅
Ndiye safutatu 😂😂😂 big up
Bag yonseyo 😂Mandota iweyo nd 1😂😂😂
Iyi aione waxy k 🤣🤣🤣
Number 1❤
😂😂😂😂 chema dota ndakomoka kuseka😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂 mk500 kudyera ma afisi😂
Kkkkk Koma adaah 🙌🙌🤣 Koma pa
😂😂😂 kkkkkkk Yafela M'Gear
munasowatuuuu bwanji 🎉🎉🎉🎉🎉
😂😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka
Good video
Mr mandota😂😂😂😂😂
Fire chemandota🔥🔥
Am first today give me my like now ❤❤❤❤❤❤ always proud of you bro man
Kkkkkkkkk iwey ase umaganix bwanj ????
❤❤❤❤ iweyo ndi 1 ase kkkkk
Inutu nda chitsilu😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 che mandota 🔥🔥🔥🔥
Pa msasa samaipita 😅 Che mandota, my guy 😅😅
Koma ndaseka che mandota😆😆
😂😂😂 Thought 500 thousand
siinathe bho mandota 😂😂😂 mumakwana
😂😂😂😂koma iwe ndi G.O.A.T aaaaaaa
Chemandota ife tilibe nsanje GOD BLESS U
Che Mandota simudzathekanso ngakhale pang'ono.
Ndiyetu mukonzekere kukalipira Milandu yonse mwapalamula.
Mwadya a Fisi,mwalowa Nyumba yosalipira 😂😂😂😂😂😂.
Keep it up Che Mandota.
Continue entertaining,educating and Teaching.
🤣🤣🤣🤣 akuti ndizangotenga ndalama zimenezo ndizamulembaso ntchito otupa mutu 🤣🤣🤣🤣
Kkķkkkķ sweet from the beginning up the end ULEMU wanu chemandota 🤣🤣🤣🤣🤣
😅😅😅😅😅😅😅 km akulu awa makani ali ndi awa😂😂😂😂
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
Nice really Appriciete
Yours excellence my best comedy
Koma uzuli mwazinta chivukwa shani🤩
This is power💪
Hahaha eeeh chemandotaa akomoka bola sipaja zimathera kunyamulidwa😂😂😂😂
😂😂😂 mandota
Koma amandota mpaka chisaka bag 😂😂😂😂😂 akutiso sisikakwana kkkk
Cosoma must see this😂
Iwe ndikulosan mwangodya mu restaurant mwanga no kulipira km ndalama nd K500 yokha😂😂😂😂😂
Umakwanila aise 🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩🤩
❤❤❤mumakwaka ndinu Dolo Chemandota mumatifesa kukoma❤
My best comedy experience with all
Kkkk koma chemandota mpaka saka bag yotengera ndalama inuyo munafika 😂😂
Chemandota inuyo musadzafe mudzangosowa😁😁😁
Taonani kuda😂😂😂
Iwe galu kwabasi.
Ngat ndingoipanga like kawiri lividio iyiyi mwakunga
Welcome again chemandota timadikilati lifidiyo lanyuwanili respect more ❤❤❤❤ I love you to much
You never change 🤓🤓🤓🤓
Mandota ndi 1 keep on burning
Kkkkk uyambire kuwathawa ma board guard akowo bwanawe, cz nde usosoledwatu😂😂
Munthu watenga saka bag kt akanyamulile ndalama eti ili 500 kwcha😂😂😂😂😂
Iwe aaaa misala iyiyi utisunga koma😂
Afisi aja ndadya pa ngongole 😂😂😂😂
Mandota ndiwa 1 paribeso umatha
Koma munalakwitsa kusiya ntchito mwachangu😅😂. Anyway I enjoyed the comedy 🔥🔥👏
😂😂😂😂😂 chemandota mphuma zinthu yooooo n Any way ulemu wako basi❤
Mandota ndi dolo katatu😂😂👏👏👏
Che mandota mpaka adya afisi😂😂
😂😂😂 me lafus you too much
Chemandota kupupuluma kwambiri 😂😂😂ngani yacosoma pakana kuziya njito 🎉ilike your comedy's❤❤
Mandota iweyo unabwela kuzakhala bass
One day muzapanga shulushulu yabwino
You make Malawi Proud lol : I’m Washing you’re video Here in Mauritius 🇲🇺 hahah
Koma ndaseka 🤣🤣🤣u never disappoint 😂😂😂😂😂
Umatitsamwitsa aise ndikuseka❤
Che mandota 🎉🎉🔥😂😂😂😂
Mandota again 😂🙌
Stress free 😂😅