ACHIPANI CHA UTM ANYASIDWA NDIZOMWE A MICHAEL USI AYANKHULA __2 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 96

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl Час назад +2

    Now you see true colour of usi, he wanted to sell utm ku mcp komanso he knows more about imfa ya chilima

  • @EvanceLumeyo
    @EvanceLumeyo Час назад +2

    Ena anagwiritsa ntchito malupanga ena kudzera kumupereka kwa pirato. RIP SKC tsoka kwa Usi pompano azikhweza monga Judas

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 2 часа назад +4

    Asakupusiseni manganya inu amalawi siinu Ana mukuziona nokha zomwe mbuyomu simunazionepo

  • @GladysBanda-h2w
    @GladysBanda-h2w 3 часа назад +5

    Kuononga mbiri ya mpingo wa SDA galu Usi

  • @FatimaSande-r5v
    @FatimaSande-r5v Час назад +1

    A manganya ndimakhala mbali yanu koma naaa.... Apa eeeee.... Mwandinyasa kobasi

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 2 часа назад +2

    Anagulitsa Chilima chifukwa cha u vice president. Mu plan ake anagwirizana zoti adzakhala vice akadzawina 2025. Munthu oipa Manganya

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi 2 часа назад +3

    Manganya mfiti ndipo ni vundula maji zamukola Soni walutenge Waka ku Chikangawa wakalutizge ntchito yake ya u Yudasi

    • @StiviniMhoni
      @StiviniMhoni 2 часа назад

      😂😂😂😂😂😂😂 wakukhumbika KT nayu wasowe

  • @BlessingsMwale-k4s
    @BlessingsMwale-k4s 3 часа назад +5

    SKC unazungulilidwa ndi mfiti...eeeeee
    Ayi ndithu...

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 3 часа назад +1

      Ndipo inu zoona mwava apande zaonekela

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 2 часа назад

      Mum 120% ndpo moyo uno tidzisamalas ndthu

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 2 часа назад

      Ndamuliranso kachikena SKC lero poona izi mmmmmh ambuye musatinyanyale awawa muwakanthe ndipo musalore kuti ana anu adzingolirabe 😢💔🙌

    • @LawrenceBelson
      @LawrenceBelson 2 часа назад

      Eeeer nyama ikaphedwa eeeesh waziulura yekha manganya chilima akanaziwa eee sakananyoza adad apa nde zaonekeratu kuti ndi wa mcp

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole Час назад

      Michael usi ndi Tony nyelenda ine wa sda ndakwiya nanu😮

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 Час назад

    Omwe analoso mu hulu lokupha chilima ayamba kuziwulura okha Amen

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 3 часа назад +2

    Koma akulu awa ndinkaona ngt ngozindikira koma ah satana amwene ngopsa

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 3 часа назад +2

    Iwe Usi zowona pakat pa athuwa ndi iweyo oyenera kuyamika Mlungu ndi ndani? ☹️ Be careful.

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 3 часа назад +4

    Tianaziwa kale kuti manganya ndimuthilq kuwili amafuna aphe utm ndiye tinamukqna wawona manyazi manganya wasowq chochita

    • @ustintembo
      @ustintembo 2 часа назад

      Ndipo zoona munthuyu ndi mthira kuwiri, amafuna UTM ithe and it was a deal ndi MCP, ndiye wabalalika pano..

  • @charlesmuwanya7845
    @charlesmuwanya7845 3 часа назад +1

    Boma ndi lomweli la Malawi.
    Mike Usi must know better that this is Malawi Government . Voters in 2025 will just change the President. Point blank.

  • @DamianoNombo
    @DamianoNombo 3 часа назад +3

    Unaziwika kale iwe

  • @ShearstonNyirenda
    @ShearstonNyirenda 35 минут назад

    Adpp musanyoze usi musapange kampeni pa imfa ya chilima musapezelepo mwayi opusa kwambili mukusowa mfundo yokamba pa manifesto yanu

  • @miraclejohnphiri7687
    @miraclejohnphiri7687 2 часа назад +1

    Bambo woyepa iwe ifa SK unasangalala kape

  • @chinomwephiri1183
    @chinomwephiri1183 2 часа назад +1

    Asanyasidwe Kodi samadziwa? Manganya ngwa MCP tu

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 часа назад +2

    Ka short aka:: kakudya misonkho yathu

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin Час назад

    Ine ndinadziwa kuti.manganya akupangila kampeni.mcp ndinadziwa kale

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa 52 минуты назад

    Usi becareful now we know kuti chilima unampeleka ndiwe plz guy tiswe usi

  • @MadalitsoMeyah
    @MadalitsoMeyah 3 часа назад +2

    Wa MCP uyu asatipusiseko

  • @DaudiLesta
    @DaudiLesta 3 часа назад +2

    Mumuuze kt makaka a UTM asazavareso

  • @SALIMASSAN-vr8ld
    @SALIMASSAN-vr8ld 41 минуту назад

    Palib zofuts inus a UTM kungomuchots muchipan pan iyey akubwerelas mphund ranj muchipanich kupatuw kuchiwonong muchosen alibe chinto

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 3 часа назад +1

    Ukawauza ndiweyo okavoterawo kuwaona anthu umbuli??? Zinazi mukuzibaya nokha a Manganya...mukamazaonera muzizazimvera chisoni

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 3 часа назад +2

    Uiwe. galu. mbuzi. enieni palibe chomwe ukuyankhula zimenezo uzikamuza chakwela. iwe maikolo mime. yako. boma wambuyako kodi naweso.paja ndiokupha machendeako maikolo wandinyada iwe galu anthu akufa. ndiye uziti boma ndilomweli iwe galu kwabasi. wava .maikolo. iwe nyani bass. iwe boma. ndilomwel8 iwe utakhuta misinkho yamalawi. iwe galu ndichakwela wakoyo. muxiona

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Час назад

    Pamtumbo pa manganya!! Chitsilu cha munthu

  • @ruthmissi7766
    @ruthmissi7766 3 часа назад +2

    Asintha mawanga aaaaaa

  • @goodwinmtupanyama
    @goodwinmtupanyama 29 минут назад

    Awaso nde sakudziwika chomwe akuchita mdziko muno

  • @cliffndafuwachisale
    @cliffndafuwachisale 2 часа назад

    Amati akakamira ngalawa mpaka kuti, analephera Yona. Asatilepheretse ulendo. Let's go 😢

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Час назад

    Manganya anapha Chilima.

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 часа назад +1

    Manganya satan ooneka ndi maso ndpo iii mukakuman nae Manganya pempherani kosalekeza Mulungu atimenyere nkhondo

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 2 часа назад +1

    Adani amanyi pakhosi ngati chiwala😢

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 2 часа назад

    Kuteroku Manganya ali busy kumenyera ufulu mpando wake wa Vice President,, Koma sizitheka zimenezo akagwere uko Zakeyu ameneyu.

  • @TiyamikeDulamanja
    @TiyamikeDulamanja Час назад

    Ndikape ameneyu akuona ngati mcp ingawinenso? Ukutaya nthawi adah pita ukapange ma sewelo ako aja ife simakape ndpo sitiopa popanga zithu

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 50 минут назад

    Asamfutse metsa okha ndiamene anamkana usi Kuti siwawo? Kkkkkkk UTM yayamba kuzungulila mutu et???

  • @christopherbanda4698
    @christopherbanda4698 Час назад

    Nyani wakupha iwe unanupeleka chilima galu iwe usi

  • @AdamDawood-h7l
    @AdamDawood-h7l 3 часа назад +1

    Mavendeake usi

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale Час назад +1

    Uncle short one😂😂😂

  • @SamsonNyadan
    @SamsonNyadan 38 минут назад

    What is your point bamboo asikono

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 3 часа назад +1

    Tinakhala tikukamba za akulu awa kuti ndi a mcp.Ndiwe chitsilu ase ndipo ulibe nzeru unadziphonya iwe.

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 2 часа назад

      Broh ulemu ndimasata ma comment km lero ndakhulupilira ndpo ngt kuli satan oopsa ndye Manganya

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 часа назад

    Kodi manganya akalakhula basi idzikhala milandu

  • @HowardTchauya
    @HowardTchauya Час назад

    Wamanyii ameneyuu

  • @MebleKalitsilo
    @MebleKalitsilo 3 часа назад +1

    Zachitsiru munthu osayamika

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 2 часа назад +1

    chintchewe iwe

  • @PaulPhiri-w4x
    @PaulPhiri-w4x 22 минуты назад

    Palibe zopanga kafukufuku winanso silent killer waziwulula yekha poyera .Usi only God knows and azakushoka na holysprit together with Chakwera.

  • @DamianoNombo
    @DamianoNombo 3 часа назад +1

    Chilima anakutenga kt

  • @AndyJangiya
    @AndyJangiya Час назад

    Phwala lako mangaaaaa

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 часа назад

    Usi ndamukonda

  • @yopemwanjasi5550
    @yopemwanjasi5550 57 минут назад

    Uyu ndoipa kwambri

  • @ruthmissi7766
    @ruthmissi7766 3 часа назад +1

    Aaaaa kungoona momwe anthu akuyankhila aaaaaaa mfiti iyiiiii

  • @IbrahimIsmael-h2w
    @IbrahimIsmael-h2w 2 часа назад

    Usi munthu oipa kwambiri akukhuzidwa ndi infa ya Chilima

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 Час назад

    Kuti iye akhalebe vice president kkkkkk sizitheka achoka uyo ku mcp kuliso akulu akulu akufuna undindo umenewo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 часа назад

    Tinanena kale kuti kafula uyu ndi wa mcp anthu mumasusa.koma uyu ndinjoka simumakhulupirira manganya zeru alibe ndichifukwa mcp ikumugwirisa ntchito. Amalawi ifa yachilima epengesa atsogoleri kumalawi

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 2 часа назад

    Kumtumbo kwamanganya kapolo wachakwera

  • @emmanuelchokocha
    @emmanuelchokocha 2 часа назад

    Nde mwati nyama ikaphedwa?

  • @BurunoMbewu
    @BurunoMbewu Час назад

    Za Ziii pasana pake

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 2 часа назад

    maikolo. boma. ndilomqeli. kabudula. mwakoma. shuwa iwe. unafupika. ndizeli zomwe iwe. galu kwabass. ukuona ngati madilama

  • @MikeMlanje-m4c
    @MikeMlanje-m4c 2 часа назад

    Asakupusiseni kama drama yi, iyetu akudya nawo za misokho yathu uyu

  • @IreenMwachande
    @IreenMwachande 2 часа назад

    Osamatchula mulungu pazinthu zopusa zanu ndale

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 2 часа назад

    Manganin wafupika ndi mzeru zomwe

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 2 часа назад

    Khani ndiyomweyi vot ndi achakwela bas

  • @FidesChandama
    @FidesChandama 3 часа назад +1

    Mfiti kumatchula mulungu mabuzi ako amako ndi emwe akukutumawo chikangawa wakoyo

  • @AnusaChiwale
    @AnusaChiwale 2 часа назад

    Achisiru kwambiri manganya

  • @dysonchimimba4248
    @dysonchimimba4248 2 часа назад

    True colours yawoneka

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 2 часа назад

    Yusas wabalalika tsopano 😂😂

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 2 часа назад

    Anampanga betray chilima uyu, very bad

  • @isaiahyonasi7629
    @isaiahyonasi7629 Час назад

    kufupikako

  • @JeanBetha
    @JeanBetha 2 часа назад

    Nyamayo nde ndinda

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 часа назад

    Usi more fire

  • @VincentKamwendo-e9t
    @VincentKamwendo-e9t 2 часа назад

    Only GOD knows

  • @MisheckMassa
    @MisheckMassa 2 часа назад

    Chitsilu chamunthu

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe 2 часа назад

    😂😂😂😂Yudas sopano wabalalika uyooooo usova

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v 2 часа назад

    Achitsilu awa

  • @razackibrahim5880
    @razackibrahim5880 2 часа назад

    Mxm

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 2 часа назад

    Ndiwe galu

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 34 минуты назад

    Opusa uyu

  • @GranceChirhwa
    @GranceChirhwa 3 часа назад

    Iwe galu kwambiri boma ndilomweli chisilu chamuthu

  • @DanielaChoguduli
    @DanielaChoguduli 3 часа назад

    Timakunyadilani

  • @AbdulAdin-bt7yd
    @AbdulAdin-bt7yd 2 часа назад

    Kape iwe

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 3 часа назад +1

    A Malawi amawanamizawo manganya akuganiza kuti anthu Sakuona kuti Chakwera ndi boma lake la Mcp Iikulephera

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem Час назад

    musiyeni manganya ndi ufulu wake kupanga zimene akufuna!!!

  • @McfallenHandy
    @McfallenHandy 3 часа назад

    Chakwera my vote

  • @ItigieThawali
    @ItigieThawali 3 часа назад

    Thongu laku Manganya

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 часа назад +1

    Usi ndichisilu Ngati anapeleka chilima amaziwa komwe akulowela