NKHANI YA NGOZI KUCHIKANGAWA YAVUTA....TAMVANI IZI ABALE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 сен 2024

Комментарии • 96

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Месяц назад +13

    Ndikupusa kwathu ngati amalawi , tasankha kukhala chete pazonse zomwe chakwela akuchita .
    Koma akanakhala maiko ena omwe anthu ake ndiozondikila , chakwela akanatula udindowake by force .
    Chifukwa waonetselatu kuti ndiolepheka pachilichonse

  • @ISHAQADAWDI
    @ISHAQADAWDI Месяц назад +9

    Mvuto kumalawi tidapusa kwambiri maiiko ena pamene paja bwenzi mademo atachitika maliro asadaike

  • @PAULMOSES-y3e
    @PAULMOSES-y3e Месяц назад +16

    Munthu ameneyu anatipweteka heavy kutiphera chiyembekezo chathu eish Malawi

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya Месяц назад +4

    Ambuye kumwambako imvani pempho lathu a Malawi, zifukwa zomwe apule sakufuna kutulutsira report iwo akuona ngati akudziwa okha, akuiwala kuti monse SKC amavutika ku chikangawa kuja inu munali komweko, ifetu a Malawi palibe yemwe angatiuze zoona, koposa posa ife tikupempha kuti mulowerepo apa , kuti yense amene anatenga gawo pa imfa ya kuchikanga inu muchite nawo kotheratu, kulibe komwe tingalirire koposa kupempha kwa inu, sungani mizimu yonse yomwe inalowa mmanda chifukwa cha anthu ena.

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Месяц назад +14

    Chikangawa party chakwela ndiwakupha eishhh koma galu uyu wanzunza amalawi

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke Месяц назад +6

    Ndimamva kuwawa mpaka lero imfa ya anthu amene aja

    • @user-ky4ce9gb6j
      @user-ky4ce9gb6j Месяц назад +1

      Ndipo siwe wekha

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya Месяц назад

      Ineyo misozi imangogwa ndikangokumbukira eish..imfa yopweteka ngati imene ija😢😢😢

  • @user-ri2vi2fd5v
    @user-ri2vi2fd5v Месяц назад +2

    Kuno ku Malawi kulibe chifunga choti chingagwetse NDEGE limeneri ndi bodza lenileni maiko ena ndege zimayenda muchifunga usiku ndi usana komaso chifunga chake osati ngati chakuno ku Malawi, angotiuza zoona basi zidutseko zimatiwawa ndipo zizatiwawabe mpaka kalekale

  • @yusufbakali
    @yusufbakali Месяц назад +3

    A chakwela akuziwapo kathu pankhani ya kuchikangawa

  • @PatrickChisaleJames
    @PatrickChisaleJames 21 день назад

    Aaa osamanga chikangawa bwanji nde okuba ndalama zafetereza ndiomwe amphweka zazilll

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 24 дня назад

    Ndiwakupha chakwera bwanji anabisa malipoti zisilu ndizimene zimuvotere akungotuta ndalama ngati nyerere

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Месяц назад +3

    Mulungu salakwitsa kalikose adziwa pomuyika aliyese wokhudxiwa pa ifa ya chilima

  • @SophieLupiya
    @SophieLupiya 15 дней назад

    Apereke

  • @user-yt5oh8qv5x
    @user-yt5oh8qv5x Месяц назад +1

    Muyaruka simunati tikufuna chilungamo chioneke basi

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад +4

    Yes we need report why akubisa report agalu amenewa tiyeni pa msewu guys ✊💪🔪 we need report

  • @HenryCharles-v6j
    @HenryCharles-v6j 5 дней назад

    Koma tikapanda kuchenjela atitha munthuyu wafika pachigawenga

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa Месяц назад

    Akuziwapo kathu ameneyi

  • @HassanMbayani
    @HassanMbayani Месяц назад +2

    Politics ndi game ya chabe

  • @daviechapweteka4759
    @daviechapweteka4759 Месяц назад +3

    Chule anadabwa madzi muli mwake

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 Месяц назад +3

    Palibe cha Nzelu apa ziko lanthu la Malawi ikuyendesedwa ndi achule okhaokha

  • @carlosZiyadi
    @carlosZiyadi Месяц назад

    🤣🤣🤣🤣🤣wakumpha akusowa choyakha kkkkkkkk zimuonekera sanati😂😂😂😂

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Месяц назад +2

    Kodi ngati anganene chilichonse akudziwapo kanthu sanganene lero ulendo waku Nzuzu akuti kuyima pa njira Bp kushuta akungonjenjemera mzimu wa Chilima udzwasawutsa awa

    • @CathreenKadwala
      @CathreenKadwala Месяц назад

      Ndipo Ambuye amuyendere chikumbu mtima chizimupeza dairy RIP chilima

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад +1

    Ma passport alibe visa anthu akubwezedwa ma border no no this government they must go nyansi za anthu

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE Месяц назад

    😢 chakwera anapha yekha anthuwa ndye sanganene

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa Месяц назад

    Akuziwapo mkathu galu amenei

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 Месяц назад

    Chakwera mfiti yotheratu kwambiri.

  • @SteveMalata212
    @SteveMalata212 Месяц назад

    Okay 😢

  • @MarthaLuhana
    @MarthaLuhana Месяц назад +1

    Chikangawa coridor yavuta

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Месяц назад

    Kusawulurako ndi umboni oti iwowo ndi omwe anapha chilima

  • @MaryJefry
    @MaryJefry Месяц назад

    Kukana khara ku South Africa kuno atachoka kale galu ameneyu koma amarawi mantha

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v Месяц назад

    Azidandaule yekha chifukwa naye sakudziwa kt azafa imfa yotani ngati anafa atumiki chakwera kachani ngati adapha chilima iyeyoso azaphedwa

  • @emmanuelpiffano259
    @emmanuelpiffano259 Месяц назад

    Eeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee komatu anthu AMULUNGU 😢😢😢😢😢

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Месяц назад

    Zonsezi zikutsimikizira kulephera kwa utsogoleri wadziko
    Tidalakwitsa kupatsa dziko mmanja a anthu opanda ukadaulo wa mayendetsedwe a dziko

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b Месяц назад

    He should not even hide we want the report Mr chakwela

  • @annembepula
    @annembepula Месяц назад

    Zikavutapo asilikali angotiuza basi

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Месяц назад

    We want that report for us to know the truth and its not strange at all

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw Месяц назад

    Palibe chifukwa chomati tikusowa ndalama padakalipano chifukwa tikuona achipani cha MCP akuba ndalama zochuluka,ena kugwida kumene pa airport koma osamangidwa osamangidwa.

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Месяц назад

    Don't force him,,,if he don't know, but our opon and crying we give to God is only one he knows ,,, about the death of our Innocent people and accknownge with excellent

  • @agreementphiri5416
    @agreementphiri5416 Месяц назад

    Mbudzi ndi chakwerayo

  • @AlexChihana-q2i
    @AlexChihana-q2i Месяц назад

    1986

  • @UncleMadaAgro_Dealers
    @UncleMadaAgro_Dealers Месяц назад

    Musiyeni chakwera

  • @LindanSamuel
    @LindanSamuel Месяц назад +4

    Zanziiii

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Месяц назад +2

    Chakwera akudziwapo kanthu pa za ngozi ya ndege. Akubisa chani

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Месяц назад

    Chikangawa Gwenembe anapha mizimu ya anthu 8 aja komanso rsph kasambala

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Месяц назад

    Muotcheleni mu state Lodgimo aluchedwa

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Месяц назад

    Akubisa bwanji anene plz

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya Месяц назад

    Mcp 2025 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤ mufa ndimabodza anuwo shupt

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Месяц назад

    ndipo tizikambabe kuti ndi chikangawadi chimunthu chankhaza wosathokoza pazimene anapanga mramu wathu

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Месяц назад

    Anadandaula chani machende Ake chakwera

  • @MoosahChikwakwa
    @MoosahChikwakwa Месяц назад

    Silent means (yes) wapha, silent that means he killed chilima and 8 others no doubt because he hides the results.😢😢😢

  • @louismagongwa
    @louismagongwa Месяц назад

    awa ndiolephela bas akudziwapo kathu 😢

  • @user-co6sc8om5n
    @user-co6sc8om5n Месяц назад

    Chilima anaphedwa ndi chakwera ndi nduna zake

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 Месяц назад +1

    Report latuluka ukubisa chani ? Ulipampandopo chifukwa Cha vote ya anthu komaso Chilima adakuvotera kuti ikhale pamenepo .. zomwe ukubisa ndizomwe zikutipasa zokamba

  • @user-rl1ye8ki2x
    @user-rl1ye8ki2x Месяц назад

    Akuziwa zonse ndi MULUNGU

  • @DaudihFedson
    @DaudihFedson Месяц назад

    Mbudzi yamuthu chakwela okupha

  • @user-il8cn7ko9m
    @user-il8cn7ko9m Месяц назад

    Chakwela mulungu amukatha Pasi pompano

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Месяц назад

    Akudziwa zangozi uyu wakupha, koma kulibe wamuyaya chakwera palibe chinsinsi 😮

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Месяц назад

    Wakupha ndiyeyo ndichifukwa chake akubisa

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa Месяц назад

    Nthawi ikwana timvabe ngakhale atabisa

  • @RowlandChimzimu
    @RowlandChimzimu Месяц назад

    Tikudikila ifeso

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Месяц назад

    Chakwera ndiwamakani ndichifukwa athu samakukonda galu iwe

  • @GaveniShalifu
    @GaveniShalifu Месяц назад

    Agalu away ananama kuti ma passport asika ntengo koma anthu akulipila 300,000

  • @user-un4pm4yt5i
    @user-un4pm4yt5i Месяц назад

    Anthu oyipa awa mulungu awakanthe koma

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Месяц назад

    ndizowona murungu simunthu

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Месяц назад

    Chikangawa chakwela

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j Месяц назад

    La 40 lizakwana ndithu

  • @TonnyB.APhiri
    @TonnyB.APhiri Месяц назад

    A banja la Chilima report ali nalo ......bwanji osawafunsa kuti akupatseni? Kapena reportyi njosiya na ndi imene anapereka ku boma?

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja Месяц назад

    1:50

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Месяц назад

    ndipo kaya tinakhara bwanji vote yathu koma tizifinyika

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Месяц назад

    Chilungamo chidziwike

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Месяц назад

    ifeyo tikudikira ripotiro ndizowona

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x Месяц назад

    Mademo bas achitike chilungamu chiziwike

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya Месяц назад

    Km a nthu enanu ndinu womvetsa chisoni mumalimbikila zinthu zoti zilibe phindu bwanji ? Aaaa mukumakhutitsa eti inu ngati muli ku SA musapusitse anthu ai bp anapangila kt mukuona ngati peter munthalik eti uyutu ndi munthu wamkulu muuzimu ndiye akubanjas anena kt mukuwasokosela ndiye mutseke kuchikamwaa kwanuko

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Месяц назад

    Akudziwa chomwe anachita

  • @Brianchisi
    @Brianchisi Месяц назад

    pangani changu ndinthu

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p Месяц назад

    Ndie mwati awulure report la asilikali ankhondo?.. zikutanthauza chani apa wina atafotokoza bwino bwino...

  • @user-nm5en5ul2k
    @user-nm5en5ul2k Месяц назад

    Wachoke chakwera

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Месяц назад

    Inu a mec mukadanena kuti aliyese adzavote koma ndi umboni ovemelezrka ochokelaso kwa afumu or agroup kapenaso T/A
    Anthu ife tikanati Mwaganizila zika za malawian koma zose zimene mukunena aoazi
    Zaonetselatu kuti muli mbali ya mcp povomeleza kuti anthu adzavote ndi id chosecho pomwe timkavota kuti chakwela. Alowe boma ambilife tinalibe ma id koma tinangwilitsa ntchito umboni wa kwa amfumu mwaona agalu inu amec koma mukachita chibwana mademo apitaso kunyumba kwanu mukapanda kusitha ganizo lanu laka votedwe mupeza nazo vuto or chisakho kulempheleka ndikuikapo wina woyembekezela pa upresidenti wo eeetu chifukwa zomwe akupanga a NRB SATITHANDIZA IFE AMALAWI KOMA AKUZITHANDIZA WOKHA NDI ANA AWO

  • @MrThomas-j9d
    @MrThomas-j9d Месяц назад

    Mitumbo yanu a chewa inu opanda zeru

  • @Edson-sj8vn
    @Edson-sj8vn Месяц назад

    Kod iwe chakwera tulutsa report tione ukuopa chani?

  • @ReginaZande
    @ReginaZande Месяц назад

    Atifotokozere report timve akulephera chifukwa chani?

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b Месяц назад

    It's not kubakakaminza ba president just that after killing his friends today wants to come and say l don't know what happened are you sure Mr chakwela

  • @JonathanMpachika
    @JonathanMpachika Месяц назад

    Apeleke report asanachoke mdziko kupita maiko akunja kuopa kusokoneza report yo

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @user-jn7bt1uy5s
    @user-jn7bt1uy5s Месяц назад

    Chimunthu chakupha

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Месяц назад

    Or aulure asaulure sangauuke kwa akufa, anafa bas remaining is history

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 24 дня назад

    Ndiwakupha chakwera bwanji anabisa malipoti zisilu ndizimene zimuvotere akungotuta ndalama ngati nyerere

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Месяц назад

    Kodi ngati anganene chilichonse akudziwapo kanthu sanganene lero ulendo waku Nzuzu akuti kuyima pa njira Bp kushuta akungonjenjemera mzimu wa Chilima udzwasawutsa awa