BON KALINDO THE D.C2 JULY 2024

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 97

  • @LameckLubani
    @LameckLubani 3 месяца назад +5

    Keep it up the good work DC ❤❤❤❤❤

  • @SkevaMustapher
    @SkevaMustapher 3 месяца назад +2

    😂😂😂😂😂km kalindo iwe wachipongwe ndithu😅😅😅😅msapato kuyasamula ngati mulamba😅😅😅😅😅😅😅kom uko!!!!!!! Kunyasalandi kuli zithu

  • @KennyTchapo
    @KennyTchapo 3 месяца назад +2

    Ulemu wako DC umakwana

  • @SkevaMustapher
    @SkevaMustapher 3 месяца назад +1

    Kumangidwa kwanu kukupindura ndithu chifukwa mukuonaso mavuto amene Ali m'boma

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 3 месяца назад +1

    Your sense mr kalindo is very powerful like the Kenyans people they don't tolerate nonsense . it's only you the all fucken Malawians you deserve brave enough i like it.

  • @BonfaceMajawa
    @BonfaceMajawa 3 месяца назад +1

    Ngat ife amalawi tilibe mawu action pa 10 July bs the dc Mwana oopse kwambili❤

  • @marthablessings1314
    @marthablessings1314 3 месяца назад +1

    Bwana waanthu osauka..we dilute u🎉🎉🎉🎉🎉

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад +2

    Amalawi anzanga, imvani mawu awa, tikamawona otiyankhulira monga Bon Kalindo, Ntanyiwa pamodzi ndi Limpopo FM, Bakili Muluzi TV, Lwala, ndi ena onse.
    Tikuyenera kumasuntika mumtina mwathu potengapo gawo kumenyera ufulu wathu.
    Dzikoli nde lavunda, chiyenera kuchita tiyeni amalawi chonde pa 10 July pano, tikamuonetse Chakwera kuti eni wake dziko ndiifeyo komanso kuti adziwe zoti tinamuyika pampando ndiifeyo.
    Apolisi komanso asilikali chonde, mudzazipatse ulemu nokha chifukwa pa 10 July, it's a do or die

  • @GiboSunset
    @GiboSunset 3 месяца назад +1

    Chakwera,s brain is divided into two parts.1part is full Of evil & the other part is empty

  • @ZondwayoNyirenda
    @ZondwayoNyirenda 3 месяца назад +1

    Chilungamo chokhachokha

  • @JimmyMzozoma
    @JimmyMzozoma 3 месяца назад +1

    MULUNGU azikumenyera nkhondo osalema pakuchita zabwino the dccccc

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 3 месяца назад +1

    Boooooon kalindooo the DC ,ati msapato zoyasamula😂😂😂😂

  • @NiyonkuruEddy-g6x
    @NiyonkuruEddy-g6x 3 месяца назад +2

    The only man amene akuyankhula zoona zenizeni
    Pa mavuto omwe ali mdziko muno

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 3 месяца назад +1

    The DC ❤❤❤❤❤❤❤ mwana wowopsya kwambiri apolisi ulemu wanu😅😅😂😂😂😂

  • @augustMag
    @augustMag 3 месяца назад +1

    Powerful message the DC Mulungu apitilize kukupasani moyo wautali 🔥♥️

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 месяца назад +1

    Bon kalindo apolice akuvaladi sapato zoyasamula kukamwa yasaa😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 месяца назад +1

    I support The DCs mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi umatiimilira MULUNGU akudaliseni president wa anthu osauka.

  • @MeliaMichael
    @MeliaMichael 3 месяца назад +1

    Sapato kuyasamula ngat mulamba😂😂😂😂

  • @HopesonJailosi-vd6ou
    @HopesonJailosi-vd6ou 3 месяца назад

    Ku South Africa or zimbwete zikupezeka,anthu akuzuzika

  • @kondwaniwhite2871
    @kondwaniwhite2871 3 месяца назад +1

    Good thinking ❤

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande6108 3 месяца назад

    Zipalasilo za nkhuku abale koma Ali ndimaphunzilo awo shame

  • @FrankPhiri-f9w
    @FrankPhiri-f9w 3 месяца назад

    Very Very good Bon Kalindo

  • @ChristopherBwanali-i6b
    @ChristopherBwanali-i6b 3 месяца назад +1

    Bon kalindo the DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @patrickkhomba3446
    @patrickkhomba3446 3 месяца назад

    Are u avice president?

  • @lloydmalinga1198
    @lloydmalinga1198 3 месяца назад +1

    The DC

  • @lloydmalinga1198
    @lloydmalinga1198 3 месяца назад +1

    Big up the SC

  • @kelvindickson
    @kelvindickson 3 месяца назад

    Kkkkkkkk koma DC sapato yayasamula kukamwa ngati mulamba

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 3 месяца назад +1

    💥💥💥💥💥

  • @JanaMussa
    @JanaMussa 3 месяца назад +1

    Mumatiyimila man Dc

  • @ChristinerGoman
    @ChristinerGoman 3 месяца назад +1

    Mumatiimilira keep it up ❤❤❤❤❤

  • @samhussen708
    @samhussen708 3 месяца назад +1

    Ifeyo iiii chakwera Ali shit

  • @moyo77777
    @moyo77777 3 месяца назад

    Very true 🔥🔥🔥

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 3 месяца назад +1

    Kkkkkkkk zosetera mpakana mapepala a ma statement okhaokha 😂😂😂

  • @IrelandKatoleza
    @IrelandKatoleza 3 месяца назад +1

    Mzerutu izi

  • @mosesmakawamalawi
    @mosesmakawamalawi 3 месяца назад +1

    Koma DC sazatheka ata

  • @chrisneySwanepoel-yu5vd
    @chrisneySwanepoel-yu5vd 3 месяца назад +1

    Dc mlungu azikudalisan

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 3 месяца назад

    Fact

  • @BrinoMvula
    @BrinoMvula 3 месяца назад

    Mmmmmm mpaka transfer kumaiko ena

  • @BrinoMvula
    @BrinoMvula 3 месяца назад

    Mmmmmm mpaka transfer kumaiko ena

  • @BrinoMvula
    @BrinoMvula 3 месяца назад

    Mmmmmm mpaka transfer kumaiko ena

  • @PetroMatias
    @PetroMatias 3 месяца назад +1

    Ulemu wanu ADC

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande6108 3 месяца назад

    Pachimake pa chilungamo

  • @IsaacSaine-f1f
    @IsaacSaine-f1f 3 месяца назад

    Ku police eeeeee ayi mazuzo

  • @HopeLuwangakaunda
    @HopeLuwangakaunda 3 месяца назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 bwana Nyoo

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 3 месяца назад +1

    Musamasowe a DC ❤

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Munkafuna kuona zanyuwani lero ndizitu 😂😂😂😂😂😂😂, mcp oyeeee, timkanena anathela mu siizi

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 месяца назад

    Bwana Kalindo mukunena zoona ndipo Boma ili mmmmmmm apolice tili pamavuto bwana ndipo ma uniform omwe akuvalidwa panopa ndi anthawi ya Bingu ndi peter mutharika zomvesa chisoni Bwana, ndikungoona kuchedwa 2025 Chakwera is a destroyer

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 3 месяца назад

    Ndipo Malawi amene a kusangalala ndiomwewo saname dziko lathu ayi saname tithera moyenda momwemu koma na kumalawi adzapita chakwera achoka ndipo eeeeish 😢

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi 3 месяца назад

    DC umatha kucheza iweyo kkkkkkkkk anyamata akugulisa mazila kuno ku south Africa

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад

    Dc machine ❤❤ wi love you

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 3 месяца назад

    Koma abale kkkkkkk mawu achibande simumawadziwa etiiii This is not Thomas chibade.

  • @WinessMatcthuwana
    @WinessMatcthuwana 3 месяца назад

    Umakwana tili pambuyopako. The dccccc!!!!!

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 3 месяца назад

    What u r saying is true DC

  • @chrisneySwanepoel-yu5vd
    @chrisneySwanepoel-yu5vd 3 месяца назад

    Kkkkkk a police akumalawi amangomvera zopoira iwo akuvutikad kumanga munthu akuŵamenyeera ufulu eeee

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 месяца назад

    Tiyeni pa 10 July kumademo ndipo popita tizatenge mauta komanso maregeni sure

  • @ShafieIdrissah
    @ShafieIdrissah 3 месяца назад

    DC ❤❤❤❤exactly kale police imaopya komalele aaaa manyaka😂

  • @RadsonTimoteo
    @RadsonTimoteo 3 месяца назад

    Kkk nsapato yonyamuka ku tsogolo ngati kukamwa kwa nsomba i ❤️ you Bon K umanena chilungamo

  • @irenioeugeniosumila6647
    @irenioeugeniosumila6647 3 месяца назад

    A Malawi segulani masso, Izi ndizohona

  • @CharlesKachipanda-jz9jv
    @CharlesKachipanda-jz9jv 3 месяца назад

    The DDDDDDCCCCCCC is machine

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 3 месяца назад

    The DC 😂😂😂😂😂😂

  • @AcksonSimbeye-pm9po
    @AcksonSimbeye-pm9po 3 месяца назад

    Well done mr

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 3 месяца назад

    Good massage

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 3 месяца назад

    DC MARVEL ❤❤❤

  • @FisherAction
    @FisherAction 3 месяца назад

    Mukutiimirira zoonadi go on father

  • @cajozocacheuca8034
    @cajozocacheuca8034 3 месяца назад

    D...,.C

  • @FynessAlfred-j3n
    @FynessAlfred-j3n 3 месяца назад

    Kkkkk 😂😂😂😂

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo 3 месяца назад

    Sapato ngati mlamba😂😂😂😂.

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 3 месяца назад

    Zomvetsa chisoni,

  • @kihiyen3100
    @kihiyen3100 3 месяца назад

    😂

  • @RuthNanthando
    @RuthNanthando 3 месяца назад

    😭😭😭😭

  • @RuthNanthando
    @RuthNanthando 3 месяца назад

    😭😭😭😭

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 3 месяца назад

    ❤❤❤

  • @OwenJambo
    @OwenJambo 3 месяца назад

    Akumangatu dala

  • @EliasWotch
    @EliasWotch 3 месяца назад

    DC ulemu wanu

  • @RonaldodalitigerSpencerDaliRic
    @RonaldodalitigerSpencerDaliRic 3 месяца назад +1

    The DC....kugazakugaza,kuswa kuswa....😅

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 месяца назад

    I feel sorry for the people in malawi,now we have just seen they have devalued money silently,check on exchange rate,very sad

  • @Eliza-h6o
    @Eliza-h6o 3 месяца назад

    Kalondo ndiyekhayo Oyankhul chilungamo koma azipan zotsusa Ali chete

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 3 месяца назад

    Mmm galu iwe anthu anayamba kupita kunja kalekale it’s nothing to do with boma….uwafunse ayao ndi atonga!

    • @kihiyen3100
      @kihiyen3100 3 месяца назад

      Galu? Mphapsya mtima tu😂😂😂 kabaya?

    • @ziyamporoma377
      @ziyamporoma377 3 месяца назад

      @@kihiyen3100 mmm malume palibe zopsyera mtima apa. Tikungofuna ma activist apa social media asamaname

    • @kihiyen3100
      @kihiyen3100 3 месяца назад

      ​@@ziyamporoma377I thought ndinu a MCP

    • @BensonChilundu
      @BensonChilundu 3 месяца назад

      Gulu la agalu ngati awa odana ndi Bon Kalindo ndi agalu osakonda dziko lawo.Kodi ndiwe waku Kasiya omwe mukulandila ma 750,000 malawi kwacha.Mulungu akukanthe ndithu.Momwe anthu akuvutikila muno mkumasangalala nazo

    • @marryphili5419
      @marryphili5419 3 месяца назад

      Galu ndiwe wodana ndi bon kalindo chisiru panopa winawake angamasapote MCP stupid

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd 3 месяца назад

    Sapato...ngati Mulamba? Kkkkkk

  • @godfreyalberto7425
    @godfreyalberto7425 3 месяца назад

    Bon kalindo umandinyasa chifukwa ulemu kwa akulu akulu ukamachula kunenakuti mfumu iwe ndikunyoza kwambiri . Iweyo ulibe mwambo sulemekeza akuluakulu sungalitsike choncho ndiwe mwana chosalemekeza akulu nditsoka

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 3 месяца назад

      Kape khala chete iwe, mfumuyo ndimulungu

    • @CharlesmakveliNyirenda
      @CharlesmakveliNyirenda 3 месяца назад

      Uyu panya pake msiye boni kalindo akulakwila chan mungiba basi

    • @AnnaPhiri-b8t
      @AnnaPhiri-b8t 3 месяца назад +1

      Apolice akumvetsadi chisoni komanso zochititsa manyazi angokhala akapolo aanthu andale

    • @lucianojames7555
      @lucianojames7555 3 месяца назад

      Mbuzi

    • @kelvindickson
      @kelvindickson 3 месяца назад

      Galu