For the love of my country and not any political party i salute you for speaking the truth. What is kungalula? how can someone beneft from kungalula . Tilikonde ziko lanthu osati zipani. In democracy we have to respect someones decision and move forward. Not being an advocate of kungaluta.
Ngakhale anthu ambiri tikulankhula pa nkhani ya Ufulu,mwapadera tikuyenera kudziwa kuti munthu ali ndi ufulu wodziteteza from extenal forces from victims like followers.This is part of defending themselves from being killed according to what people see on the ground.Ndilibe mbali koma ndanena ndimmene zinthu zikuyendera mdziko mwathu muno.This is ufulu wowunikirana.Anthu akuunikirana whether what are the negative impacts or positive impacts.I love you all❤❤❤
Wayankhula bwino kwambiri.Zomwe Dan Lu amayankha ndi zomwe iye amadziwa osati kuyankha zouzidwa ndi wina.Aliyense ali ndi ufulu wopanga chomwe chamkomera iye bola osaphwanya ufulu wa ena.Anthu onse ali mzipani zinawa adali ku MCP ndipo kuyambira 1993 anthu adayamba kulowa zipani zina ndipo palibe omwe ankawaletsa.Enawa sadziwa tanthauzo la democracy.Sizingatheke kuti anthu onse akonde zofanana.
Kunena zoona amene aononga chipani Cha UDF ndi Bingu poyambitsa chipani chake cha DPP panthawi imene ali President wa dziko posankhidwa pa ticket ya UDF
For the first on social media am hearing someone talking sense not being pressurise ndi chigulu kuti angawoneke ofoyira .iweyo umaganiza usanayakhule ndipo umaziwa ku balancer all viewers .and another issue is of Dan Lu, why are we criticising him for his rights ndipo azipani osewa akhala akusitha zipani ena anachoka MCP kulowa UDF ,ena from UDF to DPP , ena from DPP to UTM so let everyone exercise his or her rights and you yourself you will exercise that right thru votes ,that's osamadya ndale ayi gwilani ntchito magaye ,iliyonse bola money
DPP NDIIMENETU INALIMBIKIRA KUTI MCP ISAPITE KU UDF CONVENTION. IWE UKUONEKA NDI WANG`ONO KOMA NDI WANZERU KOMA APAPA UDANA NDIVITSIRU ZONSE ZA PA SOCIAL MEDIA
Akukanawo akuvomerakuti sangakwanitse kupanga run dziko la democracy
Zoona zake ndizimenezozo ndithu @JamesChimera
For the love of my country and not any political party i salute you for speaking the truth. What is kungalula? how can someone beneft from kungalula . Tilikonde ziko lanthu osati zipani. In democracy we have to respect someones decision and move forward. Not being an advocate of kungaluta.
@@TUMISANGBOSILONG Thank you very much for your comment @TUMISANBOSILONG
I support that, you are talking sense
@@francistsutsu4811 Thanks bro @francis
Ndiko kulankhula kumeneko❤
@@BLUR-p6c tathokoza kwambiri @BLUR
@@Explore96736 thanks
MIBAWA IKUTI TO HELL NDI UDANI OPATSIRANA. UDANI WA MCP NDI DPP AKUIPATSIRA UDF
Udani sibwinodi kumapatsirana
Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @yassin
Ngakhale anthu ambiri tikulankhula pa nkhani ya Ufulu,mwapadera tikuyenera kudziwa kuti munthu ali ndi ufulu wodziteteza from extenal forces from victims like followers.This is part of defending themselves from being killed according to what people see on the ground.Ndilibe mbali koma ndanena ndimmene zinthu zikuyendera mdziko mwathu muno.This is ufulu wowunikirana.Anthu akuunikirana whether what are the negative impacts or positive impacts.I love you all❤❤❤
@@Adam-u9x8m Thank you very much @Adam zoona zake ndizimenezozo
Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu
You are welcome
Mwanawe Bingu anali wakuba. Anakanika kupanga kachipani kake ndipo atatoledwa ndi bwana Muluzi tinampangira kampeni ifeyo titamuwinisa anationa ngati zitsiru lero alikuti. Sanazisiye ndalamazo.
@@StevenLikukuta Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu
Zoona zake ndizimenezozo
Uthenga wa mphavu kuphunzitsa a Amalawi za democracy
@@DavisKatema tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @DavisKatema
Wayankhula bwino kwambiri.Zomwe Dan Lu amayankha ndi zomwe iye amadziwa osati kuyankha zouzidwa ndi wina.Aliyense ali ndi ufulu wopanga chomwe chamkomera iye bola osaphwanya ufulu wa ena.Anthu onse ali mzipani zinawa adali ku MCP ndipo kuyambira 1993 anthu adayamba kulowa zipani zina ndipo palibe omwe ankawaletsa.Enawa sadziwa tanthauzo la democracy.Sizingatheke kuti anthu onse akonde zofanana.
@@MustafaPemba Tathokoza kwambiri Mustafa
True ❤
@@gomezthera535 Thanks for your comment @gomezthera
Mwayankhula bwino kwambiri anthu akudani chifukwa cha chilungamo paja chilungamo chimamveka ngati mwano
@@NancyNyirenda-v9o Thanks Nancy for your comment
Kunena zoona kuti chipani cha UDF kuti chionongeke mchifukwa cha Bingu amene adaba Boma la UDF mkuyambitsa chipani chake cha DPP
@@ManuelKamba Zoona zake ndizimenezozo ndithu
@@ManuelKamba eya moti inu simudziwa?
Iweyo sukuziwa kuti mcp ndichilombo nde democratic ungapange pamozi ndi chilombo?
@@EmmanuelMphande-f4l Ayi pa umunthu ndiyosagwira koma pa democracy ndiyogwira chifukwa imeneyo ndiyo democracy yo
Mwaiweyo muli nzimu okupha komanso wankhanza ndi idzikonda musatinyanse ndi Dan lu wanuyo nkachainso Dan lu
@@MaryChavula-jz3di Tathokoza kwambiri chifukwa cha comment yanu @MaryChavula
Kunena zoona amene aononga chipani Cha UDF ndi Bingu poyambitsa chipani chake cha DPP panthawi imene ali President wa dziko posankhidwa pa ticket ya UDF
Zosayendatu zinthu zake
Ukuyankhura zopanda zeru iweyo palibe chazeru ukuyankhura apa anthu akufa ndi njara iwe mkumayankhura zopunsazo
@@SanudiMcDonald tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @SanudiMcDonald
Zipani zammabanja zilibe democracy koma maudani
Iwe ndi wabodza kusiyana mcp kunsonkhano sikutanthauza kuti aline femocrase bodza
Ambiri takhutira half sanakhutile
@@thulambale2836 Tathokoza kwambiri @thulambale
Ngati ukuti ambiri, half ukuitenga kuti?😂....ngati wanena kuti theka,mza obvious kuti yatsalanso theka.Equation matters.😂
@@Adam-u9x8m Kkkkkkk koma @Adam
Ndipo ngati UDF yathu ikutha chotchi ndichifukwa cha DPP
@@mayesojameskatete Zoona zake ndizimenezozo @mayeso
For the first on social media am hearing someone talking sense not being pressurise ndi chigulu kuti angawoneke ofoyira .iweyo umaganiza usanayakhule ndipo umaziwa ku balancer all viewers .and another issue is of Dan Lu, why are we criticising him for his rights ndipo azipani osewa akhala akusitha zipani ena anachoka MCP kulowa UDF ,ena from UDF to DPP , ena from DPP to UTM so let everyone exercise his or her rights and you yourself you will exercise that right thru votes ,that's osamadya ndale ayi gwilani ntchito magaye ,iliyonse bola money
@@LawrencePhiri-h3j Thanks Lawrence
Ndimakadeti awa akufuna kusokoneza UDF olo ineyo sgachite zomwe adagazinja aaaaaa DPP ndioipazed adalakwa 2014 musaiwale ai
@@EstherchavulankhomaNkhoma Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @EstherChavula
Apa niwechete chilongamo bro
Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @ AlexKatete
Kma kunena zoona amene aononga chipani chokoma cha UDF ndi Bingu palibenso wina popanda UDF sibwenzi Bingu akanakhala President wa dziko.
@@ManuelKamba Zoona zake ndizimenezozo ndithu
Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @ManuelKamba
Kodi mwati ímfa ya chakwela😂 Kodi watisiya
Mcp ilibe chibale ngat wampachilima
@@BensonBwanamili Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @BensonBwanamili
Chitsiru no 1 winiko kupusisa a Malawi 2 ndi a DPP
Kma nanu mfundo zanu mzopangisa mu2 kutukwana asakufuna mwava
@@RAFICKRAHIMUMUSSAH nkhani yako ndiyovuta kwambiri
Nzelu yabwino kwambili
@@VictoriaKumwenda-k6o Tathokoza kwambiri @VictoriaKumwenda
Popanda UDF sibwenzi kuli DPP
@@ManuelKamba Nkhaniyo ndiyoona ndithu
Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @ManuelKamba
Osabisa karindo ndiwa tribalism wauponda ayambeina imeneyo singapambane atukwanapachabe
Ayse anthu akasokonezeka mitu amakhala opanda mfundo zogwirika tiwasiye
Kukachitikenso ngozi ai takana sitilola za manyaka
@@MaryChavula-jz3di Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @MaryChavula
Ineyoso sinaone vuto ai ndiufuluwake bas athuwena anachoka
Zoonadi zenezene ❤kuyakhula ngat wakulu komai ndinyamata wazelu olo banja kumakhalila kutiona ifeyo tivazotukwana bas chikondi chimene chikufunakadi olo atawina dpp adzalamulabe koma kumakhalila kutukwana kukhalangat dan wapita kunja kwadziko.zed ai música ndiufuluwake
Chimodzimodzi chilima anali wa dpp anayambitsa utm ndipo a dpp sanauphe
Enananu muonekatu kut ndinu ziwanda palibe chazeru kuva kumakuvutani zed
@@EstherchavulankhomaNkhoma tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @EstherChavulankhoma
DPP NDIIMENETU INALIMBIKIRA KUTI MCP ISAPITE KU UDF CONVENTION. IWE UKUONEKA NDI WANG`ONO KOMA NDI WANZERU KOMA APAPA UDANA NDIVITSIRU ZONSE ZA PA SOCIAL MEDIA
@@yassinn5634 tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @yassin
Kudya chitedze kuthabeanji boma la anthu akupha ngati amenewa anthu oipa ankhanza
NONSENSE DPP MUNTHU WACHOKA KU DPP NDIYE SANALEMEKEZE CHILIMA BWANJI CHILIMA ANALI WA DPP?. DPP IKUMVA PAIN .
@@yassinn5634 tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @yassin
Iweyo ufuna kut tathandizeso ife ai ndiye bola kukhala patokha bas koma kupitaso ku DPP olotse kakutafune adpp
UDF ndiye make wa democracy not nkhumba zina izo usayiwale nkhumba iwe kuti unachikera mu UDF khala chete unvetse democracy
@@jamesbanda8602 Zoona zake ndizimenezozo
Kodi komamudziwa kut adpp ndamene adachita chipogwe UDF mufunaso akulowetsenitso et mudaona kupusa audf et zomwemunachitazi mwayambaso kwafunaso zooona aaaaa muganize bwino osamaiwale msaga
@@EstherchavulankhomaNkhoma Tathokoza kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu @EstherChavula
A Malawi sitichedwa kuiwala
Galu
@@UmaliIshmael Zosayendatu
Popanda UDF sibwenzi kuli DPP
Zoona zake ndizimenezozo ndithu @ManuelKamba