I don't support any idea of making Alliances with Dpp because both Dpp and MCP is ruled by people of same ideology of the one party system. I think the good think UTM can do is to rebuild party with its new ideology but for the coming 10 years. It should have the long term goals by encouraging and promoting new ideas among youths who will be more voters in 2030 while expanding their presence in the parliament.
Ine si mzika ya Malawi, koma ndinkakhala zaka 13 mu dziko, ndipo ndidzahkalanso. Ndinkamuuza anthu poyambira chaka cha dzana kuti njira imodzi yokutithandiza kugonjetsa ndiye ndi yomweyi. UTM atengane ndi DPP, komwe a Chilima anachokera. Maso anga amanyowa ndikamameera zinkhani zikuchitika. Mlengi wathu atitsogolere mu nkhondoyi. Zikamatentha kumenya zitadzakoma kugonjetsa. Without confidence one and ones are twice defeated in this race of life(Marcus Garvey). Moto iyake basi. Kusengezeratu mwa kathithi. Love an peace. Best wishes 11 thousand km away from you my people. Ndimakunyadirani kwambiri❤❤❤
Koma kalindo anakonza ifetinkaona Kuti awa awa analindi cholinga because munthu amalandila malangizo aabwana ke Koma uyu Mmmm anati escariot uyu😂😂😂 aziona next step
Bon Kalindo alibe mbali that's one thing about him I like amangotulutsa mabvuto wambalizonse ndiku ng'alula iye wautali azabweranso ndiina. Mumisala yakeyi mulinso mfundozina zabwino andalenu tolanimo zothandizazo wamisalatu adaona nkhondo the dddd cccc 😂
To be honest Malawian the government is no longer existed there's no government to rule Malawi how is going to be the Parliament without the alliance of the government because that government was formed because of alliance
Tsogolo lathu lowala ili mmanja wathu, Mlengi wathu atitsogolere . Kwacha dzukani, tulo ndi lokama, koma ufulu ndi mtendere ndi zithu za mtengo wa patali.
Ine phee kumastand no more recycled politicians be it UDF, MCP, AFORD, DPP, PP, PDP, UTM. We want achinyamata tilamule tokha. NRC for the prosperous Malawi
Politics is a game that needs proper strategy. In politics there is no permanent enemy. In my personal opinion, it can be wise enough to gang with DPP if DPP can accept it. Otherwise united we stand divided we fall.
The only way for utm is to unite with DPP afford and udf , ldont think among this for partys can make alliance with mcp , most malawians want the alliance of DPP utm afford and udf
Aaa amalawi nsitilalola kuti voti opanda ma ID ansadzalembetse voti PAPO BOLANI IDZALEPHELEKE VOTE TIDZAWONE MENE AWONONGELA ZA ID IDZI OSUTSA WADZELU.ANGALOLE ABOMA KULENGEDZA KUTI OPANDA ID ASALEMBETSE VOTE OTSUSA NDIKUMVUMELA AKUDZIWA KUTI KUMWELA NDI KU POTO ANTHU AMBILI ALIBE MA ID DZIZAPANGA DZIWONETSELO ZA DZIKO LOSE KAYA AKUDALILA MAI YOLAMU TIDZAKOMANA KUTSEWU KOKO MCP IDZACHOKE NASI 2025 za ID ayiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii TAKANA A MALAWI
Ayi koma mcp is too much they failed what development has mcp done, devaluation fertilizer in dpp time was at 25000 now 95000 can't to see the different killing and intimidation. Sankakwanitsa zonse koma awawa angokwanitsa ma speech koma pa ground 0 pa 100

Alimbikitsen a UTM Mr Kalindo... palibeso mavuto amene akumane nawo..bola alliance yathapo...let them keeping forward that's all..✊
more fire DC🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Easy...easy....tawaona kale...ticheza nawo ...zaozo sizitheka!😊😊😊😊😊..anthu ali maso
UTM, Aford, PP should merge their parties to defeat MCP
JB is MCP.
For Presidency Born Kalimdo ☘️🇹🇿🔥🔥
Ine si mzika ya Malawi, koma ndinkakhala zaka 13 mu dziko, ndipo ndidzahkalanso. Ndinkamuuza anthu poyambira chaka cha dzana kuti njira imodzi yokutithandiza kugonjetsa ndiye ndi yomweyi. UTM atengane ndi DPP, komwe a Chilima anachokera. Maso anga amanyowa ndikamameera zinkhani zikuchitika. Mlengi wathu atitsogolere mu nkhondoyi. Zikamatentha kumenya zitadzakoma kugonjetsa. Without confidence one and ones are twice defeated in this race of life(Marcus Garvey). Moto iyake basi. Kusengezeratu mwa kathithi. Love an peace. Best wishes 11 thousand km away from you my people. Ndimakunyadirani kwambiri❤❤❤
@@IyahMohyoh wow that's nice
Where are you from?
@@MalawianCamera I am from Russia
@@IyahMohyoh Oooh okay wow your Chewa is perfect
😂 inuo ndakaz kpn amuna?
@@user-sy5wd3hn9y musanafuse Mafuso ameneo mutumize kaye connection fee ku Malawian Cameras 😂😂😂
Koma kalindo anakonza ifetinkaona Kuti awa awa analindi cholinga because munthu amalandila malangizo aabwana ke Koma uyu Mmmm anati escariot uyu😂😂😂 aziona next step
Bon Kalindo alibe mbali that's one thing about him I like amangotulutsa mabvuto wambalizonse ndiku ng'alula iye wautali azabweranso ndiina. Mumisala yakeyi mulinso mfundozina zabwino andalenu tolanimo zothandizazo wamisalatu adaona nkhondo the dddd cccc 😂
Federal system of government is the only way to go.
Mayine big man kuzatulukila ndikung'alula mwanyooo God bless u Mr kalindo
To be honest Malawian the government is no longer existed there's no government to rule Malawi how is going to be the Parliament without the alliance of the government because that government was formed because of alliance
Tsogolo lathu lowala ili mmanja wathu, Mlengi wathu atitsogolere . Kwacha dzukani, tulo ndi lokama, koma ufulu ndi mtendere ndi zithu za mtengo wa patali.
A UTM ngati akufuna Congress igwe ndiye kuti agwile tchito ndi DPP.
Chifukwa Second term ya MCP idzapanga zokuti UTM ithe.
Ndipo zoonadi kungowamvetsa kuwawa a mcp atuluke
Sunganene kuti DPP igwire ntchito ndi UTM
Honestly speaking from our beloved president, the Dddddd Cccccc!!!! 🔥🔥🔥
Nde mukufuna Dr Usi apange risign iwe ndi Mbuzi Winiko eti
The mouth of the voice less, i@the rest of the followers, we like your updates,
Gwesani MCP please kaloweni ku DPP
Ine phee kumastand no more recycled politicians be it UDF, MCP, AFORD, DPP, PP, PDP, UTM. We want achinyamata tilamule tokha. NRC for the prosperous Malawi
Kalindo azimutsatila ndimbuli zizake
Manganya ndiye yudasi sikailoti
Politics is a game that needs proper strategy. In politics there is no permanent enemy. In my personal opinion, it can be wise enough to gang with DPP if DPP can accept it. Otherwise united we stand divided we fall.
UTM bwererani komwe munachokera zakale zapita zatsala zatsopano, ndipo kutsogoloko mudzautenga mpando waupresident bola kulimba mtima
DPP Must change your bad behavior lets try Aford mix leaders don't forget mr Chihana please
booooon kalindoooooooo❤
Pachibale pawo
Only madness in u kalindo
The only way for utm is to unite with DPP afford and udf , ldont think among this for partys can make alliance with mcp , most malawians want the alliance of DPP utm afford and udf
Ukatelo uziza tukwanaso musogolo muno ndiwe yemwe winiko munthu osaziwika nzochita zomwe uwasiye a utm apange zinthu mwantima pansi wanva winiko wamanyi iwe
Chimene chavuta ku malawi ndi ufiti ndi nsanje, akupaseni inu u president tiwone ngati mungakane
Mr pule Bon kalindo
Ing¹alule basi❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤
I know what is Ndale and how
alliance ai zakamika
Mumalimbana ndi chilima presdent wa utm ali moyo mwamukambila zambili lero wamwalira walowa manganya mwayambanso kodi munakhala bwanji inu
Kuying,alula kweni kwin kkkkkkkk kom
The DC
Koma nzoona kuti abambo amenewa (chakwera) anali m busa ?? Nanga ndi m busa wanji uyu osanva chisoni ndi nkhosa zake zomwe
He was a fake pastor....adakakhqla mbusa weniweni sinmbwezi atajoina ndale
Zimenezo nde ayi ku dpp tinachokako basi iwowo ngati akufuna abwele ku utm basi dpp inati khakaza ife sitiyifuna
Mwerani mayi Mary Chilima analankula dzulo kuti siyani chidani za ku mbuyo.u kuti tigonjetse anthu oyipa. Koma kufunika nkumalungalira mwozama.
Ndipo wandiyankhulila bwino Mary
Now in Malawi it is just dramas
Manganya ndi fiti size anafupika dzose ndi dzelu dzomwe
Wamisala uyu😮😮😮😮
iweyo ndamene uli wamisala
Nyauuu iweee
Trapesi ndi Tambo nde gwelo mavuto akumalawi athu oipa kwambili koma ayi mcp yaonjedza
Zoona autm bwererani ku dpp ndi komwe munacokera
Aaa amalawi nsitilalola kuti voti opanda ma ID ansadzalembetse voti PAPO BOLANI IDZALEPHELEKE VOTE TIDZAWONE MENE AWONONGELA ZA ID IDZI OSUTSA WADZELU.ANGALOLE ABOMA KULENGEDZA KUTI OPANDA ID ASALEMBETSE VOTE OTSUSA NDIKUMVUMELA AKUDZIWA KUTI KUMWELA NDI KU POTO ANTHU AMBILI ALIBE MA ID DZIZAPANGA DZIWONETSELO ZA DZIKO LOSE KAYA AKUDALILA MAI YOLAMU TIDZAKOMANA KUTSEWU KOKO MCP IDZACHOKE NASI 2025 za ID ayiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii TAKANA A MALAWI
@@hanifahmponda8711 Bruto alipo 20 chakuti thousand, anthu 20 chakuti million.ndiye angalimbe mwotani?
😂😂😂
UTM ikhale paokha basi. Masanzi akasanzidwa sadyedwanso. UTM isayang'ane 2025 koma izikonzekeretse za 2030. Migwirizanoyi ndiyakupha. Munthu sakhutitsidwa ndi ma udindo.
Apa nde mwayankhuladi
Zoona ndagwirizana nanu
Iwensotu ndi wabodza pena ndimkakukhulupilira koma apa ndiye ai mwataika kodi siwe umkati DPP siboma labwino umkasogolera mademo iwe lero ukuwaudza anthu kuti abwelere ku dpp uzi sizoona suuja umkanena kuti pita akupha malubino lero ukuti tiyeni ku dpp iwe ndakuona ndiwe nthera kuwiri sopano uyu musamamumvere bola UTM ipange gwilidzano ndi Aford osati dpp zaugalu basi or azaludze palibe vuto
Ayi koma mcp is too much they failed what development has mcp done, devaluation fertilizer in dpp time was at 25000 now 95000 can't to see the different killing and intimidation. Sankakwanitsa zonse koma awawa angokwanitsa ma speech koma pa ground 0 pa 100
Propaganda yanu yoti if a utm tipite ku Dpp zikuvutani.....iwe paja ndiwa Dpp.....we can't go back to egypt
Dpp no no president wake utiyo?
Koma ndiponso inu aaaa
Akeee
Kalindo ndiwe wa Dpp uzachita manyazi 2025 ukunamiza amalawi Dpp sidzalowaso m'boma ndichipani chakupha ulibe zelu kalindo
Wuzachita manyazi ndiweyo bro
@@marryphili5419 zosenzi mukukangalika kunyoza Mcp ndinu alomwe