Chiphwanyatu mkazoyu amuthawa komano munthu akuyenda maiko chokakamira mkaz okut ali pa banja kale ndichani zinaz guys kumakhara serious zikuchitikatu zimenezi ndithu kumalimbana ndi mkaz wa mzako akazi onsewa kumeneko ndie kupusako akaz akukwera mapir kusaka mabanja chonsecho iwe ukulimbana ndi mkaz wa mwini aaaaaaa
Chisulu chilichonse chili ndi mbuyeke kkk gaga kubisidwa
Ajazila atha naye khama Gaga 😂😂😂
Gaga wavuta lero😂😂😂
Ajazila mpaka Gaga kumubisa, chikondi simasewera 🤣🤣🤣🤣
Kkkk gaga nayenso kubweza
Sunday and this Sunday simunatulutse chifukw nchyani please please ife umatisangalas
Nkhani ya chifunilo bola kungoyisiya ine yayamba kundinyasa
Km munthinda samukwatira wantchitoyi😂😂
Mukanazisiya Nanu zaimfazo,AMOLE akupezetsan kale chokudya chabhooo ichi,,wabwezapo pa sister wanuoka
Ajazila kkkk
❤❤❤❤
alipo awili achina gagadiwawo 😆
Gaga watopa sakuopanso
Nice comedy kufulumila kutha motere why
5mins ngat nyimbo eeesh
Shehe wavuta uku
😂😂😂😂😂😂 achina gaga diwa alipo awili
Chiphwanyatu mkazoyu amuthawa komano munthu akuyenda maiko chokakamira mkaz okut ali pa banja kale ndichani zinaz guys kumakhara serious zikuchitikatu zimenezi ndithu kumalimbana ndi mkaz wa mzako akazi onsewa kumeneko ndie kupusako akaz akukwera mapir kusaka mabanja chonsecho iwe ukulimbana ndi mkaz wa mwini aaaaaaa
Ajazira love 😂 kumubisa Gaga 😅😅
Mr. Spider anjele kz wapita bs kz waona makola akhuku plus apasa galimoto aziyendera 😂😂😂😂😂😂😂 kwavuta Mr spider
Ili ndi dziko,
Mwanayo adzawasaka bambo Ako Mumde...
Gaga 😂😂
Ndipo zoonadi
Muthinta waiwonamo 😂😂😂
Ajazira mpaka apo❤
Mole is secret criminal mn
It was a mistake
Kma gaga 😂😂😂😂
Gaga zathawa lero
muthitha sazatheka
Bwana muthinda malamulo amenewo😂😂😂,koma gaga iiiiii
Kiikiki zamalove...Jazira wamuyikira kumbuyo bae wake😂😂😂
Mumatimvesa kukoma ife ngat zizibwera dele 😂❤
Muthinda bwinotu ndiwa mtchito yo
😂😂😂 Gaga naye ATI waluma mgoro😅😅
❤
Kkkkkk gagayo andipezatu ndikhara pompano koma nkaz ndiwachikond ndithu mene akupangira gaga muja mpaka kumubisa eeeee
❤❤❤
Chiphwanya anayika becon
Very amazing keep pushing guys 🎉🎉🎉
Proud of you my Village mates. Kpt up
Kkkkk gaga
Watching from mwineriwa vg mulanje
🎉🎉🎉🎉
Km gaga lelo wayaka moto kkkkkk umakwana ulemu wako
Ati wa dress uja
Eeeh Apa ndye munafatsa ma guys, big up
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥😂😂😂😂😂😂
Gaga lero wayaka moto ndi mowa womwe aljazira sukulakwitsa chimene unachiona mwa gaga umachidziwa wekha achimwene achimwene asakusokonese
Maromours
Gaga 😂😂😂😂😂😂usamale iwe kulalatila pokhala
Gaga my vote😅😅😅😅😅😅 zoseketsatu
Apa mwabwera NGAT khaming'i❤
Kkkkkkk Gaga wumakwana
Muthinda uyang,ana watchito choncho bwanji?
❤❤
Achina Gaga mdiwawo andipeza 😅😅😅
Kungoiponya mwachinsisi 😂 ndaipezabe
Mkuluyi sakumudziwa bwinobwino Chiphwanya
Ayamike kuti wavala machiyani? 😅
Ameneyu AKHALE deya basi
Molle apa wagwidwa 😮😅😅😅😅😅😅
Anambe kolona alipakhos koma osayakha 😂
Nice movies
good video
Gaga yaa umakwana
I love you guys 🎉
Mai phiri ngamabodzatu kk
😂😂😂😂😂
ANdipeza
Kd chifuniroyo sangabwere ngat nzukwa?😂😂😂
Gaga aise mmm
Gaga wapalamula kkkkkk
Anambewe alusiratu😅😅
Jasira kumubisa Gaga mdiwa
Good acting my people
Mole asamale agwidwa pankhan yachifuniro
Guys mmatha keep it up
Koma muthinda mwati zimuthera bwanji? Uyu agwira murder ndithu kkkkkk, naye Gaga ndikatundu amatha uyu
Kkkkkk hehedee uluuuuu
😂😂 koma yaa
Koma Shaikh abwela kkkkk
Watching
Mole serial killer
Ndipo live mn
More fire
koma gaga eeeshiiii
😂😂😂😂😂 ndangoseka
My komede
❤❤❤❤❤
Gaga ndiwa zero
Ajazila munazibaya gaga simamuna
Ndalawilila lero ❤❤
Am first viewer
Mole wagwidwa basi
Chiphwanya mankhwala 😅😅😅😅
Achiswa chan kaya😂
Tafika bas❤
Pa MBC sinayambeyu
Chiphwanya nkzi awasiya basi
Mole asachoke chende chende
Muthinda, wamtchito wakoyo alibhooo ndipatse number yake timvane
But mbiri is beautiful❤
Malawi country 🏆🏆🏆🏅🏅🏅🏅🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ndipo nyumba ya mai Phiri siimatha😂
Cement wadula cc*😂
Km gaga lelo wayaka moto kkkkkk umakwana ulemu wako