Mole ndi Chifuniro atleast mli boh ndi action zanu cause simuchulusa drama nde zimankhala z boh. Koma pogwila wokubayo Panali ma drama kwambiri nde aaaaa zima bowa , but for the rest actions apart from pogwila wokubayo , guys muli boh just a reminder.
To Be Honest I been flw this episode km zikuoneka kt chinaxhake chasowekera Nanga atonde ndi abale ao anakumana pati adhaa aja banja linantha bwanji Kodi boss ananthamangixidwa nthawi zanji kt agwidwe
Very powerful dramma which gives more lessons,keep the fire burning!!
Achifuniro timakunyadiran sister wathu mu 🇲🇼
😂😂😂😂😂😂 farawo wagwera mnyumba 😂😂😂 big up guys much love you watching it from south Africa 🇿🇦❤❤❤❤
Watching from DRC congo.proud of u guys.
Kkkkkkk eshiii chsokonezo mu tonde wadula. Farao ndchan kkkkkkkkk. Eshiii chifu naenxo mmmh
Ati uyu ndi mbuli okuba haha Farao
Chifuniro angakugwilise bkhala la Moto asa😢. Kkkkk
Zikukoma kwambiri nazisadibwa koma guys Chifunilo ndi Zinveka komanso Gaga muli bho kwambiri watching from Cape Town
farao abwera kuzakhala kwa tonde kkkkkkk
Gaga ndi dolo ❤
😂😂😂 eeh Koma #Mollen amandiwadza
Koma Azimveka mukuthamangitsa Falawo akusangalatu ku nyumba kwanuko.
Mwakunga Episode 33, massive
Naye falawo kkkk😅😅😅😅
Keep it up ❤achina nkhalango..
Watching live from london Uk
😂😂😂😂pharaoh ukumvesela chani,big up guyz watching from durban🇿🇦
😅😊😊😊😊 ati amzako angondikwatila lero ndi lero ai ndithu Danko guys
Koma gyz mwabwela ❤❤❤
End yakeyo km farawo kusuzumira 😂😂😂😂
gagaga ndiwe dolo
awadi adzangosowa akuyitha
😂muthinda zanga bwanji kodi ❤❤
Watching u guys from jonz always proud of you ❤❤❤
Mole ndi Chifuniro atleast mli boh ndi action zanu cause simuchulusa drama nde zimankhala z boh. Koma pogwila wokubayo Panali ma drama kwambiri nde aaaaa zima bowa , but for the rest actions apart from pogwila wokubayo , guys muli boh just a reminder.
😂😂😂 ukali udakalimobe
Nice gusy koma gagayo abwelele kupolice 😂😂😂😂
Eeeee guys ulemu wanu😂😂😂
Chifunilo sopano iwe umatha # yako tiyipeza bwanji timugawile inayaka tsikanayi amatha jelasi dawuni
Bank yavala mpaka ma trouser awiri?😂😂😂
❤❤ tonde is my king tigailen group nangati lilipo la sewelo limeneli pls
Timakunyadilani from mangochi malombe nalikolo ,kawinga , m'baka ndi kaombe vs CHANDE
To Be Honest
I been flw this episode km zikuoneka kt chinaxhake chasowekera
Nanga atonde ndi abale ao anakumana pati adhaa aja banja linantha bwanji
Kodi boss ananthamangixidwa nthawi zanji kt agwidwe
My favourites are Chifuniro and Zimveka, these two😅
yeah, Chifunilo acting so nice ,moti pano I'm planning to send ten pin 🤭🤭for her ,just for appreciation for her character
Gaga zavuta
Bwana munthinda, dziliukuziliuku kugwesa bwato😅😅😅😅😅😅🎉🎉🎉🎉🎉
Mumativesa kukoma❤ I am watching from south Africa ❤❤
Chifunilo wabwera umakwana 😂😂 missng chifunilo 😂
2 weeks know sindinamuone tonde ndie mbora tu koma
😂😂😂achifuniro kuyaka moto kkkkkk
Farao maina aku Egypt😂😂😂😂
Koma plaese mumaxedwa kutulutsatu 😢😢😢😢😢
Koma Chifuniro aziwonekawoneka amabebetsa kwambiri
Dola my favorite
@nkhalango
Penapake flow yativuta....
Farao ndi tonde akumana kutiko?
Gaga wagwidwa motani?
Ndimakunyadilani guys musazafe muzangosowa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chifuniro is back❤
Tonde wadula amsonetsedwa lachingsti ndipo nthaei yanji?
Mmm pachema apa kkkk
Farao 🔥🔥🔥
Wawa, chifunilo
Between episode 32 and 33 there's something missing in between, like something is missing
I also noticed
Dola ndi farao tinvapo dzina 😂😂😂🎉🎉🎉🎉
Bwana Gaga apita tiwasowa🤣🤣🤣
Zilibwino pitilidzani guzy
Koma chifuniro umafunsa mafunso abwino..umakwana
Zilibwino kwambili
Kkkk so nice 🙂🙂
Good work guys
Bt pls try 2 make Fast nyana
Kd tonde ndi farao akumana kale?
gaga 😂😂
Km Amdyangu ija ndi mfumukazi simunayike manambala amapart bwanji?
Makwale kuba😂😂😂😂😂😂
Thanks guys keep gud work ❤❤❤❤❤❤
Favorite Gaga 😂
che muthinda 😅😅😅😅
Wawa makosana ndikudikiratu pano
❤❤
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂 Farao kuno ndi ku Iguputo?
Kd mum'de Ali Kuti guys?
Kkkkk
Chifuniro is back ...mmakwana guys
ISSABEL
Mbambande
I'll follow you guys everywhere u go
Koma chifunilo ❤
Mumakwana guys ❤
❤❤❤
Mole umatha blaz
uyu ndimava mukuna bwanji khope yakeyo ya umbavadi kkkk
Muthidwa zamuonekera
Kkkk