Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
God, may you bless this wonderful Malawian honest lady, she's really blessed and she'll be blessed forever!!
Sure
Zaziii
Amalawi musadane nayejen inuyo zkuyendera ukakwera m'mwamba usanene kuti pasi palibe mame?muyeso muyesera azanuo inuso muyesedwa ndiomweo,mayi anasamba mumanja nakusambirani mumanja dxiko ndilimero muzatsi let's appreciate this lady guys
Welcome mai wanga timakunyadira mayi jen asa
Many of the comments are indicating your goodness Mama but they're the same people who insulted you.That's life on earth.
We celebrate you Mai Jane!!!
Munthuwabwino uyu❤❤
Mayi inuyo ndi mbambande and the truth shall set you free❤❤❤
Mom we proud of you God bless you all the time ❤❤❤❤
Mai oyipa uyu munthu oyipa
Mai wa mzelu kwambili uyu ❤
Kutereko Mai uyuyu amaima pa chilungamo koma poti dziko timadana ndi chilungamo🙆
Kodi enanu mukamamunyoza mayiyu muli ndi umunthu?kapena kudzadzidwa ndi uchitsiru,amalakwa chani mayiwa ?khalani chonchi tionana 2025 mudabwa ndi M'busa wanuyu
Nzimayi opanda machimo uyu ❤❤
Apepesa chayani muthu anakuthandizani lero zikukukanikani nokha?❤
Iyi ndiye mfiti yeni yeni, kodi tiziti sopano anthu mwatitora ife amalawi ngati mbuzi? Wina aliyense angoti akasowa zochita basi amvekere "ine ndikuimira a malawi" kwa nonse omwe mukuganiza mopepera mukungotaya nthawi yanu popeza ife a malawi tikuziwa komwe tikurowera.
Amayi awa ana thawa basi
Anauzidwa kuti pakhetsedwa mwazi, koma inu
Komatu mulungu alipo kuyankhula za bodza mulungu sakondwela
Kuno kunalibe ndege mpka kukakwerera ku Zambia
My honest lady Jane Assah my God bless u all the time and am wishing u many more days mama
She already joined a certain party, everyone knows this, don't say she is independent, her party still existing she should not be squeezed
Wakubs uyu woips
Kod mukuyankhula chan kwenikwen mai?
Kaya akufuna ife timve chani kaya
Following
Mai uyu ßiwabwinoaayi😢😢😢kkkkk
Nyini uyu sitikufunazedi wule ameneyu
Munthu wamkulu mama waziko
As a judge, Tippex is not allowed on Govt documents. Wrong is wrong.
Exactly
Mayi ingovemelani munthawa mese munabwezedwapo mutazemba sinaiwale mayi atipex
Uyu alibe chilungamo anakakamizika kulanda a Malawi ma Vote. She needs to be impeached.
Matipex mwabwerako8?
aaaaaa shatapu ifeso tipaka tipex ameneyo mesa mwati alibwino
Pano padzadzadza ma kadeti ndaona,asiye azituwa 😂
Lero tazinsikira kut DPP inawinad kawiri konse
Mukutukwana munthu osalakwa why amalawi
Wolakwa KAPENA olondola sadziwika tiyeni timulemekeze mayiyu.Ngati aMalawi tikuzunzika SI iye.Lets think twice
Koma anthuni mumatiseweretsa a Malawife
Kkkkkkk mmakadya ndalama ku Britain
Don't shout amalawi akubvutika akulamula ndi jen assah tikhoze zithu guys pliz
Chilungamo cheni cheni
Amatuluka bwanji milandu isanathe zoona kunali kuthawa tsono aona Kuti zisankho zilipafupi kubwelano. Don't give her any post wachinyengo
Mbuz iyi
Mbuzi ndi chakwela ozati mayiyu
Ngati Mayi wa ali mbuzi nde chi mfiti chako cho chikhala ndani galu iwe?
Kodi mai awawa kulankhula kumawavuta eti
Chilungamo
Mai Tippex
Choipa savmera
Akudziwa ndi Mulungu basi
Mai wabodza uyu
Pano ndiye taziwa kuti kapeni avuta tipex wambwela zisakho zichema osaopa ndmafana
Anachita bwino kutuluka akanawaphawa
Za zii munthu oipa uyu
Mama mubwelele
Panopa guys sithawi yolozana zala athu just fix maproblems amene tilinao mudziko muno?tikuvitka athufe jen alibe vuto tafufuzani momwe zikuyenderamu guys this is democracy guys don't talk too much days are closer 25
I stil fear thise people to our nation.l even fail to to have a single trust in this person
Kambuku opanda nthito uyu
Arrest her now
😂😂😂😂😂😂 I don't know how to talk
She speaks.too much hence diverting the correct answer to the questions.
mtima umandiwawa ndikaona mai wa akulephera kupepesa kwa mtundu wa A Malawi
Iwe ulibe nzeru Chifukwa dziko silikuyenda bwino .nde wapindula chan pomwe agogo ako akuphedwa ndi njala ndi boma lomweli
😂😂
😖😖😖😖😖
so ur more intelligent than two courts, shutup!! mind u, "rule of law" osadanda.
God, may you bless this wonderful Malawian honest lady, she's really blessed and she'll be blessed forever!!
Sure
Zaziii
Amalawi musadane nayejen inuyo zkuyendera ukakwera m'mwamba usanene kuti pasi palibe mame?muyeso muyesera azanuo inuso muyesedwa ndiomweo,mayi anasamba mumanja nakusambirani mumanja dxiko ndilimero muzatsi let's appreciate this lady guys
Welcome mai wanga timakunyadira mayi jen asa
Many of the comments are indicating your goodness Mama but they're the same people who insulted you.
That's life on earth.
We celebrate you Mai Jane!!!
Munthuwabwino uyu❤❤
Mayi inuyo ndi mbambande and the truth shall set you free❤❤❤
Mom we proud of you God bless you all the time ❤❤❤❤
Mai oyipa uyu munthu oyipa
Mai wa mzelu kwambili uyu ❤
Kutereko Mai uyuyu amaima pa chilungamo koma poti dziko timadana ndi chilungamo🙆
Kodi enanu mukamamunyoza mayiyu muli ndi umunthu?kapena kudzadzidwa ndi uchitsiru,amalakwa chani mayiwa ?khalani chonchi tionana 2025 mudabwa ndi M'busa wanuyu
Nzimayi opanda machimo uyu ❤❤
Apepesa chayani muthu anakuthandizani lero zikukukanikani nokha?❤
Iyi ndiye mfiti yeni yeni, kodi tiziti sopano anthu mwatitora ife amalawi ngati mbuzi? Wina aliyense angoti akasowa zochita basi amvekere "ine ndikuimira a malawi" kwa nonse omwe mukuganiza mopepera mukungotaya nthawi yanu popeza ife a malawi tikuziwa komwe tikurowera.
Amayi awa ana thawa basi
Anauzidwa kuti pakhetsedwa mwazi, koma inu
Komatu mulungu alipo kuyankhula za bodza mulungu sakondwela
Kuno kunalibe ndege mpka kukakwerera ku Zambia
My honest lady Jane Assah my God bless u all the time and am wishing u many more days mama
She already joined a certain party, everyone knows this, don't say she is independent, her party still existing she should not be squeezed
Wakubs uyu woips
Kod mukuyankhula chan kwenikwen mai?
Kaya akufuna ife timve chani kaya
Following
Mai uyu ßiwabwinoaayi😢😢😢kkkkk
Nyini uyu sitikufunazedi wule ameneyu
Munthu wamkulu mama waziko
As a judge, Tippex is not allowed on Govt documents. Wrong is wrong.
Exactly
Mayi ingovemelani munthawa mese munabwezedwapo mutazemba sinaiwale mayi atipex
Uyu alibe chilungamo anakakamizika kulanda a Malawi ma Vote. She needs to be impeached.
Matipex mwabwerako8?
aaaaaa shatapu ifeso tipaka tipex ameneyo mesa mwati alibwino
Pano padzadzadza ma kadeti ndaona,asiye azituwa 😂
Lero tazinsikira kut DPP inawinad kawiri konse
Mukutukwana munthu osalakwa why amalawi
Wolakwa KAPENA olondola sadziwika tiyeni timulemekeze mayiyu.Ngati aMalawi tikuzunzika SI iye.Lets think twice
Koma anthuni mumatiseweretsa a Malawife
Kkkkkkk mmakadya ndalama ku Britain
Don't shout amalawi akubvutika akulamula ndi jen assah tikhoze zithu guys pliz
Chilungamo cheni cheni
Amatuluka bwanji milandu isanathe zoona kunali kuthawa tsono aona Kuti zisankho zilipafupi kubwelano. Don't give her any post wachinyengo
Mbuz iyi
Mbuzi ndi chakwela ozati mayiyu
Ngati Mayi wa ali mbuzi nde chi mfiti chako cho chikhala ndani galu iwe?
Kodi mai awawa kulankhula kumawavuta eti
Chilungamo
Mai Tippex
Choipa savmera
Akudziwa ndi Mulungu basi
Mai wabodza uyu
Pano ndiye taziwa kuti kapeni avuta tipex wambwela zisakho zichema osaopa ndmafana
Anachita bwino kutuluka akanawaphawa
Za zii munthu oipa uyu
Mama mubwelele
Panopa guys sithawi yolozana zala athu just fix maproblems amene tilinao mudziko muno?tikuvitka athufe jen alibe vuto tafufuzani momwe zikuyenderamu guys this is democracy guys don't talk too much days are closer 25
I stil fear thise people to our nation.l even fail to to have a single trust in this person
Kambuku opanda nthito uyu
Arrest her now
😂😂😂😂😂😂 I don't know how to talk
She speaks.too much hence diverting the correct answer to the questions.
mtima umandiwawa ndikaona mai wa akulephera kupepesa kwa mtundu wa A Malawi
Iwe ulibe nzeru
Chifukwa dziko silikuyenda bwino .nde wapindula chan pomwe agogo ako akuphedwa ndi njala ndi boma lomweli