Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
Haters will always blame you my brother just because all the enemies of APM can't be happy with your speech. Even the way this woman is interviewing you just shows that she is one of the haters because of this ( I feel bad and hate those ones who are blaming APM for useless things or political reasons and I handle him as my biological father) but no stress brother you're a real and very strong soldier and you're humble man otherwise stupid questions this woman was asking you if it was I, I would just fu....k off from that interview. Your character is a real good courage and discipline soldier and we love you and everything is going to be good
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
Chisale ndimunthu wabwino kwambiri wamanga ma church wachita zambiri Ambuye akudalitsen achisale long live
Big up Norman Chisale ,I love your courage 🔥 Ambuye apitilize kukumenyeran nkhondo ,,,I'm one of your supporters
Ndpo nthawvyamayankho ikubwela big tipanga zobwezera ntoporao
Leah you the best journalist...well done to Me Chisale
The lady was carefully selected to handle this interview am impressed with how she has handled this heavy interview. Professional indeed
😊
Norman ooooye.Please Please please Mr N Chisale keep it up God will help help you, always pray, praise him Amen Amen Amen
Great man Norman Chisale. Oceans of luv to you and your family.
Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Zoonad ol evn Ines zimandiwaw, km Amalawi if nsanje😢
@@AngellahKunsanama amalawi amamukonda munthu akafa, that's why dzikoli lili lobwerera mbuyo,
Titakhala ndi anthu 20 nziko lino ngati Mr Chisale Malawi atha kusintha I proud of you Mr Chisale ndimakunyadilani chifukwa chakulimba ntima kwanu
Komano pa point ya human rights Peter Muthalika he really respects
Gud interview love you questioner and Mr interviewer Norman
Azodiak tamakhalani ndi ma bottle amadzi mukamapanga interview ndi anthu please
Komadi man
I support 😂😂😂good
God bless Mr chisale komano mokupemphani ndithu pepani uyu akufuna kut mumukhululukileyu imvani kulila kwake kut ukulu wayehova ukhalebe pa inuyo yesu anat muwakhululukile chifukwa sakuziwa chimene akuchita
Musaiwale kut munthu payekha alibe vuto koma satana akamulowa amapangisa munthu kuchita zimene choipa chili mwa iyeyo chikufuna please ndikuziwa ndithu ululu ndi ochuluka kwambili koma khululukani ambuye apitilize kukupasani moyo wamphanvu madaliso avumbebe kut wamasiye apeze popumila
Msilikari adzakhare msilikari mpaka kare. Big up bro N. Chisare❤❤
The one who talk the truth doesn't fear and it's really true that the truth pains big up Mr Chisale
Am agree with you 💪
I agree with you.
Ambuyechonde dalitsani achisale, chifukwa siolakwa chonde ambuye❤❤❤
Keep it up umakwana Norman chisale
ulemu wanu bwana mr chisare big pp
Chisale your number 1 well trained soldier
Bravoooo big man chisale i salute you
Mr Chisale isn't my relative but ndawamvesa he is a real soldier, BRAVO CHISALE. BULL Sheet kayun.
Yaaaaaaa ndi nfana wabooooo
Courage muli nayo...komano kusa kululukako kuchita kuoneseratu kuti muli ndi mtima wakupa
😢 or uli iweyo kut munthu akunamizele mulandu wa murder. Uthakumukhululukira?
Sukudziwa chomwe ukunena, sukuona kuti Chisale amuzuza popanda zifukwa?
Ana achepa ulemu wanu bwana chisale 👏👏👏👏👏👏
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Watching from zambia
Zoona zake zake za Norman Chisale.Kunena yekha mwini wake.
great mtolankhani , kip the fire burning girl
Akuzuzika ngati yesu chisare ndi Good Samaritan athu abwino amazuzika
I like sir Norman Chisale he's been good in speech osamaopa pa chilungamo
Chisale usatiuze kuti akhale wo opa mulungu suyo chakwera wo opa mulungu akutizunza
Definition of having readership, fire 🔥 chisale
I like the energy tht u hv Mr chisale as a soldier...big up❤
Mr chisale attitude in this interview shows kuti bambowa ndionama..😂
Ndipo sukunama uku ndiwabodza auze mtundu wa a Malawi kuti ma billions a chuma anawapaeza bwanji osamangobwebweta zopanda phindu, kufuna anthu akumvele chisoni.
Ndinu mabulutu guys
Koma Chisale uyuyu eeeeeeh 🙌🙌🔥🔥🔥
Matama.ndarama zakuba mbara ziku ikuru mmarawi chisare komaso pitara kabambe mwAnaveka chaponda mutharika bingu ndege supar jet
One thing i like this guy he talk straight
God is great chhisale
Big up bro pitirizan ntchito
Wn am the of them amene ndimamva kuwawa ndikamva kuti mwamangidwa,sinakumane nanu ,sitinayankhulako koma zimkandiwawa koopsa
This was nice chisale seems a good one though ndindale
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
Big up Soldier
Ifee that's straight tolk and being honest kuti a chisale akuyakhula mopanda chigamba ndazikonda kwambiri and please kaimeni bwana chisale
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
Bravo Bravo 👏 😁 Soldier...
Love one chisale
Great man ,i like u
Powerful talking and intelligent, proud of you @Norman Chisale
Intelligent ya ku machende amalawi mapanga support zingawenga bwanji, kupusa
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
Norman chisale iweyo ndi number 1 moto kuti buuuuu!!
Ndamva chisoni pokumva nkhani yanu bambo Chisale 😢 koma chilungamo chilipo ndipo momwe mwadutsa inumo enanso adutsamo ili ndidziko. Abale whyyy a police athu mmatero, olo ndiliineyo ndingaophwezetu ndipo ndikanamizilidwa ndimakwiya kuposanso achisalewo 😂😂
😂😂😂 so in love with his courage 🤦🥰
Ndinu ochenjere nkulu ndinudi nsilikali weniweni osazi njoka luzi tuziona panozi
respect to you both you building Malawi in this interview ..
Your the best Leah
Kkkkkk ayayaya malawi tingogulisa tigawane dollar zo
Soldier never die chisale more 🔥
Mbambande Mr chisale
Dpp yangoyenera kubweler 💓💓🙌🙌
Keep it up Mr chisale
Your such brave boss
Aaa zaxiiiii kod kukhala msilikali ife tiope
Mulungu akhale patsogolo basi Mr chisale Angoni
Komatu chisale ndye akumulakwla
Bwana chisale ineyo ndikuti pepani kwambili pa zomwe munazunzidwa
Ifenso timamvanso kuwawa
Norman akadzalowa muboma yes... Azabwezera
Hahhahahahhahahahah ndipo live azabweza ndithuuu
Mr chisale mulungu akudaliseni posamala Ana masiye ndipo akuonjezere zambili
Big up Mr chisale
Akunama uyu, wakupha komanso wakuba, chitsiru chimangidwa chisiyeni, sakudziwa kuti apita kundende.
Bravo Mr Chisale
Leah , bravo 💪
Haters will always blame you my brother just because all the enemies of APM can't be happy with your speech. Even the way this woman is interviewing you just shows that she is one of the haters because of this ( I feel bad and hate those ones who are blaming APM for useless things or political reasons and I handle him as my biological father) but no stress brother you're a real and very strong soldier and you're humble man otherwise stupid questions this woman was asking you if it was I, I would just fu....k off from that interview. Your character is a real good courage and discipline soldier and we love you and everything is going to be good
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
Amalekano zikomo chifukwa Cha machezedwe anu ndi achisale mkazi odziwa kufusa ngati iwe thanks
Tikukuvesesani mr chisale.
Kma this interview must be repeated even pa wailesi , nice Leah keep on going more fire
Leah malekano powerful katundu omanga ndi mawaya
Chisale oopsya eeeee. Bible mmanja koma Bullshit pakamwa mbweee ashiii
Iwe umati atani? Uzaziona ukadzapeza ndalama
Oh Kodi nsewu uja nza pita etiiii.....lozani zanu ife tione a china Boma ndi lomwelo
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
I have never liked u soldier but i feel your pain.
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
Chisale more fire
The real legend khaaa wauuza ngamo
Koma poti APM ayimezo nde tasephana basi aaaa..mwachidure kumalawi ndare zithe
Iweso khala chete mapazi opotokawo ngati milomo yako ikuyankhula mopotokayo
chisale ndiozipopa mwachamba
Mwana wa njoka iwe kagwere kutali
Mbavaizi aaaaaa awonongachumachamalawikwambili
Steven Kayuni😂😂😂😂
Zoonadi tamakhalani ndimabotolo amadzi ameneyo chisale ndimunthu wabwino
This guy is some how mad
mbuzi chisale ukuona ngati bambowakowo sangawine ameneyo wapha albino wakwa na
Kkkkkkk aaa zoona. Msilikali kiching, amba chilungamo n how he's feeling with de way they r treating him
Chisale💪💪💪🇲🇼🇲🇼
Nice interview
This woman is brave
This was a hot 🔥 one lol 😂
Big up boss
Ee achisale anapsa mtima💪
Yeah azayakha zomwe amamangila Norman chisale
This lady 🙌🙌🙌🙌🙌
😂😂😂😂😂😂😂moto kuti buuuuu L malekano umatimilila koma bwinotu akubandula mbakela bwana ameneyo 😂😂😂😂😂
Adayamba kare kuba amarawi.ndibwino kuba