kwagwanji wa report lomwe achipatala atulutsa lokhudza Imfa ya Dr Chilima 😢

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 июн 2024

Комментарии • 99

  • @frankjolijo
    @frankjolijo 4 дня назад +2

    Chilima sangaphedwe chonchija!!🙆🙆🏽🤦.....we have nothing to lose....we are coming

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 4 дня назад +2

    Agalu abodza ife chilungamu tachidziwa muzinamiza ana osati ife amalawi, mwapha anthu afiti inu

  • @user-zo3bf3ec3g
    @user-zo3bf3ec3g 4 дня назад +1

    Times chichitikileni malilo achilima chinachake pakatipani chachitika ma program anu sakukoma mukuyeneya muzikonze mukuonesa mbali muzochitika zanu
    Kanakonda ndalamazo mulandile ndipo mudye koma muzima pachilungamo ndipo muzitiuza zoona😔😔

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h 3 дня назад +2

    Report lachani umboni ife tilinawo jacket anamumvula ndani?? Nsapato anamumvula ndani?? Osawopa chakwela wapha chilima umboni ife tilinawo

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 4 дня назад +2

    Kumadziwatu kuti Chilima wachita ku phedwa ndi a MCP,paja mwalandira ndalama a wonder

  • @EsnartMartin
    @EsnartMartin 2 дня назад +1

    Atolankhani achinyengo awa tonse tikudziwa kuti ndalama za magazi zilizonse ponse

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 4 дня назад +1

    Kachilungamo aka ena sakondwa nako kuzolowela kunamizidwa times mwapamba kugwila tchito yeniyeni thanks

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 4 дня назад

    thank you for teaching us guys i agree with we must use our brains

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 4 дня назад +2

    Kodi ndege ndiyomweso inamvula chilima dzovala ?chilingamo mukufuna inuso ndiye chiti chionadi mukuchidziwa

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 2 дня назад +1

    Musavutike umboni tinaupeza kale black box ilikuti nanga maphone alikuti anthu wonse anali ndimaphone ndichifukwa chiyani anali wovulidwa zovala

  • @mathewsmakina7845
    @mathewsmakina7845 2 дня назад +1

    Andevu zamwayi zanu munadya kale simunganene zoipa za Mcp ayi

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 3 дня назад +1

    Ine zikundidabwitsa Kuti mchifukwa chani akubanja akuti satulutsa report lonse,akubisa chani????? Apatu zangoonetseratu Kuti zomwe anthu ambiri akulankhula Kuti a Chilima anachita kuphedwa,zomwe akupanga a boma kumamanga anthu chifukwa choti akulankhula molira komaso kufusa mafuso pazodabwitsa zomwe zinachitikaso kutsatira ngozi imeneyi

  • @JiyaWilliam-g8y
    @JiyaWilliam-g8y 3 дня назад +2

    Odziiwa salankhula zambiri amangoti Insha Allah kutanthauza kuti zonse akudziwa ndi mulungu ndipo ndi mwini zonse

    • @user-kt5bq2wg6v
      @user-kt5bq2wg6v 15 часов назад

      Zoona mbale moti anthu wose adakaganiza choncho zikanakhala bwino

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 4 дня назад +2

    Chakwera anapha chilima musatinyase munachita kuwakhapa

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 дня назад

    Nkhan ndyakut chakwera anamupha chilima ndi anzake mcp ndiyakupha kd chakwera chiyambire kulamura kumalawi ndi ngozi zingat,nanga anamuvura zovara chilima ndan samalani mulungu akukanthan nonse muli pambuyo pa chakwera

  • @RabeccaMpunga
    @RabeccaMpunga 4 дня назад +1

    Zoona zeni zeni tizaziziwa MCP ikazachoka pampando ndipo sikale.

  • @HaliJana
    @HaliJana 4 дня назад +1

    MUBISE MUNENE IFE TIKUDZIWA KUTI CHAKWERA,ANACHITA PLAN YOPHA CHILIMA MUKUCHWDWA NAWO UMBONI WANU NDIPO CHAKWERA UFA OSANYELA IWE UWONASO

  • @ZakaliyaAlick
    @ZakaliyaAlick 4 дня назад +1

    Abusa akudziwawonkha kuti kugwa ndzanja la Yehova ndikowopsa akonda chinyengo asiyeni adzaziwona chimwemwe chawo adyelatu.

  • @augustMag
    @augustMag 2 дня назад

    I am waiting 2025 all Malawian tikazavota amene azawineyo ndikukhala president boma limenero ndi lomwe lizachete kafukufuku wa ifa ya anthu amenewa amene anamwalira pa ngozi ya ndege mizimu ya abalewa iunse mumtendere osatha 😭😭😭😭

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni 4 дня назад +1

    Awanda amzanu munalinawo pa program wa sanati waze asadzabwereso mwamva?

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x 4 дня назад +1

    Ife sitikupanga nawo zinamizanani nokha nokha munamaliza amcp ndi kukhapa

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 4 дня назад +1

    Wander ukungonena chakwela mwina kt alindimamina mumutu

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni 4 дня назад +1

    Tidzingo koment zachina JB zachina ntanyiwa bakili muluzi TV ndi ena akunjawo bas ife sitidzilemba km ma koment kwaolemba akunjawo bas

  • @user-hq8yn8tl1h
    @user-hq8yn8tl1h 4 дня назад +1

    Koma osayiwala Kuti mphekesera ili pawiri;
    Kukhala yoona
    Kapena...
    Kukhala bodza😢😢

  • @Doreen-yl3qm
    @Doreen-yl3qm 4 дня назад +1

    Mboni yayikulu ndi Mulungu amene anali ku chikangawa amene amawona zonse,la 40 likadzakwana zizaulirika

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 4 дня назад +1

    And mukazilowetsa ndale mukulakwisa because muona ngati lamulo ndi loyipa

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 2 дня назад

    Ndege yagwera kutali ndi midzi ya anthu yeti it's not far from villegers ndiye iyeyu sanadziwe kuti amanama zosezi ngati alibe choyankhula akhale chete komanso zonsezo zikanati ndi zabwino zokhuza za zosatira za kuchipatala ko bwedzi abanja sanabwere poyera why delay yeti aziti angonenapo izi zokha zinazo azanenabe, presdent wanuyi has something to do ndi imfa ya chilima period

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 4 дня назад +1

    Anthu kumalawi kuno amasangalala ndimabodza gwelo LA zonsezi ndiumbuli basi

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 4 дня назад +1

    Ndipo ine uyuu wandebvuyi amandiyelamo kobs amazimva nzeru kom ndimbuli yothelatu

  • @user-bl6km6kx7n
    @user-bl6km6kx7n 4 дня назад +1

    mafuso ndiye ambiri choti muziwe vuto mphanvu tilibe bs mthaw yanu

  • @user-cr6if6tz6d
    @user-cr6if6tz6d 4 дня назад +1

    Achitsilu chamunthu a ndevu zatsoka mulungu akulangani inu agalu

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 4 дня назад +1

    Zawusilutu zoti tidzinamizana 😮😮

  • @user-dn6eg1xk7f
    @user-dn6eg1xk7f 4 дня назад +1

    mabodza ayamba osanena moopa ayi anafa ndi mabala ayi

  • @user-hq8yn8tl1h
    @user-hq8yn8tl1h 4 дня назад

    Azanena akazakhumudwisana 😢😢zitapanga xpire😢😢😢😢

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 4 дня назад +1

    Chachikulu akubanja afotokoza okha zilibwino ndiye makape ena azitengela za ndale chilungamo akubanja achiziwa

    • @stevezulu2108
      @stevezulu2108 4 дня назад

      Abanja awophyedwa ndi Boma. Zoona zidzadziwika boma likadza sintha.

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 4 дня назад

      @@stevezulu2108 naweso ofoyilatu mene adaliri chilima uja anthu akwawo angaope boma ali ndi masapota ambili adafotokoza chilungamo palibe amene angachite naye matha chilungamo ndichimenecho Mulungu akuziwa chilichose

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 4 дня назад

    Well come dont forget kuti every accident has acause,car ,motor bike,an aeroplane lets just calm we wiil have good answers dont talk things without umboni because its acrime

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 дня назад

    Anthu aku ena I inu so kuti mwadya buns ya mcp

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb 4 дня назад

    Ineso pang'ono ndayambaso kudanwa nazo mmmmm ndalamatu inapha yesu tisaiwale. Athuwa ...........????????

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 4 дня назад +1

    Nde akubitsa chifukwa chani! Or asaneneso zilibe tchito so abitsa bwanji kunena uthenga wenweni 😡😡😡

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 2 дня назад

    Kodi amene akupanga defend chakwelayi amupasa zingati akuona ngati akunamizatu mwana wakwaotu cz zokhuza ngozi zija msagwilise njira yowaseka pakamwa anthu kuti alankhule, komanso funso ndiloti kodi zomwe amapanga a silikali wo zoti tiyeni tikasake ndege uku osati kwinako amawalangiza ndi ndani komanso potumidza anthu nine akasake ndege zimenedzo ukudziona kuti ndi zazeru komanso kusiisidwa kwa kufufuza ndege basi nkhani zonsezo iweyo ndi ukadaulo wakowo sungaone kuti something was off here, let malawian explain there views malingana ndi momwe a presdent anuwo anapelekera uthenga wao unali osagwira.

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 4 дня назад +1

    Olo ingo zisiyani.

  • @user-ec4jo9cu4d
    @user-ec4jo9cu4d 4 дня назад

    Mukundisokosera mukanena zotsatira za kuchipatala mmalo monena zakugwa kwa ndege?!!

  • @wonganichakakanyirenda3299
    @wonganichakakanyirenda3299 4 дня назад +1

    Chilungamo chizaziwika basi

  • @PeterKayuni-n2r
    @PeterKayuni-n2r 4 дня назад

    Yaaaaa

  • @NdamvaScnp
    @NdamvaScnp 4 дня назад +1

    Mcp yakumpha

  • @AufiThera
    @AufiThera 3 дня назад +1

    Mwapha Munthu

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c 4 дня назад

    Akubanja anena chilungamo ndipo tadziwa basi otukwanawa ndimowa ndifodya

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 4 дня назад

    Ndichifukwa chani akumanga wina aliyense woyankhura fir the whyy
    Later kumafufuza

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 4 дня назад

    Palibe chotukwana koma akubanja ndi anzeru siopusa koma wanzeeu sangamasure pano kumbukirani pa bingu anafotokoza chinapha bingu???? anthu amzeru amatero kuti mlungu awamenyere nkhondo popeza zachitika kale

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i 4 дня назад

    Komaso apolisi naonso akuyenera kuphunzitsidwa mokwanira,akuyenera kuti lamulo limeneli alimvetse,asangotumidwa ai

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 4 дня назад

    Koma mwina achita bwino kusanena iwowo akubanja ndimtaya makoko .

  • @ThokozaniSaiti
    @ThokozaniSaiti 4 дня назад

    All of you one day you will pay one by one for what you did to Chilima and others

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 4 дня назад

    Chakwera anampha chilima ndemukukamba chani nkunkuyu zikhare ngoma nose muzaziona analakwanji chilima

  • @user-cr6if6tz6d
    @user-cr6if6tz6d 4 дня назад

    Agalu inu ngati simukuziwa chimene mukupanga kuli bwino mungokhala sibwino kuyiyimira MCP chipani chamagazi

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 4 дня назад

    Inu achina wander dyani ndalamazo ndi chakwera zisiru lnu times palibe chazeru pano

  • @AceelectricalengineeringAEE
    @AceelectricalengineeringAEE 4 дня назад

    Pa... Pako

  • @JTUPHIRI
    @JTUPHIRI 4 дня назад

    Guys Malawi wathapo basi tivomeleze, mpaka wonder kumayankhula moduka mutu
    chonchi! Ndiye amene angatiimile ndindani?

    • @RABSONSIKELO
      @RABSONSIKELO 4 дня назад

      Dziko silinathe vuto lilipo ndilakut mumakonda ma negative

  • @Gautengstanzo
    @Gautengstanzo 4 дня назад

    Akuyankhula apapa panya pawo ndithu

  • @user-sf7sd1hb4g
    @user-sf7sd1hb4g 4 дня назад

    Uyunso wadya ndalama zaboma

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 4 дня назад

    Zoona zidzadziwika MCP ikadza choka Mboma.

  • @user-dg5pc6rz1b
    @user-dg5pc6rz1b 4 дня назад

    Zao izo or cent sidadyepo nde worries what bisani

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly 4 дня назад

    NDALAMA MDANI WA CHILUNGAMO

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
    @MadalitsoTamayenda-ez5pj 4 дня назад

    Zitsiru Inu mwadya ndarama zochuruka thus why mukuyakhurah zopusaaa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 4 дня назад

    Paja madolowatu adya za MCP sizodabwisa

  • @Sophisticate230
    @Sophisticate230 4 дня назад

    Izizi nde ndizopoila kuti tizinamizana

  • @DafterChitema
    @DafterChitema 4 дня назад

    Kodi anthu Inu atakhara mbale kapena mwana wanu mukhoza kuyankhula zokhuta choncho

  • @phillipmphanda2163
    @phillipmphanda2163 4 дня назад

    Tizakumana pakachele bola chilungamo tuchidziwa

  • @JacobTMarko
    @JacobTMarko 4 дня назад

    Umbuli ndikufa nanga kumafika pomagenda m'mdipiti wa galimoto zonyamula maliro pali umunthu pamenepo .

    • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
      @MadalitsoTamayenda-ez5pj 4 дня назад

      Imeneyoo timayintcha aggressive ndizinthu zopusa mafunaaa tizisekererah inunso umbuli mulinawo cozi mukufusa funso lopusa kwambiri

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 4 дня назад

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @BerthThomas-v9l
    @BerthThomas-v9l 4 дня назад

    Munagulidwa Ndi mcp agalu inu

  • @AshlafHakimi
    @AshlafHakimi 4 дня назад

    Chinyengo ichi agalu inu

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 4 дня назад

    Zitsiru izi zinadya ndalama

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 4 дня назад

    koma eee msova a dpp

  • @wonganichakakanyirenda3299
    @wonganichakakanyirenda3299 4 дня назад

    Pano akutiuza zina kusongolokuso azatiuza zina akubanjayoo

    • @ChikondiLikapa
      @ChikondiLikapa 4 дня назад

      Man akubanjawo apasidwa chiseka pakamwa apapa zaoneselatu chifukwa palibe chobisila choona choti chimasule amalawi tathandiza kulila lelo akatibisile alibe chisoni nafe ata ine basi ndazituluka akubanjawo mwina alandila ma banzi

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo 4 дня назад

    Eee

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
    @MadalitsoTamayenda-ez5pj 4 дня назад

    Taziyayakhurani zanzeruuu ngati ma citizens amalawi bax bzy talking foolish thing yr stupt you tow gys mukuwona ngati mwawinaaa time yovata ikubwerah muzarirah ng,weee😂😂😂😂

  • @JimsonChisi
    @JimsonChisi 4 дня назад

    Mwaononga kawailesi kanu takasika

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 4 дня назад

      Indeeee awonongadi Wailesi yawo pano sitikumvetseranso tasiya kuwadalira

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 4 дня назад

    Define assassination

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 4 дня назад +1

    Zopusa chakwera ndiwakupha basi olo Mbiri yake ndinyasa wapha Mia, busa wake reason kufuna mpando

  • @courageouslondon586
    @courageouslondon586 4 дня назад

    Don't post this .who a u.

  • @user-hq8yn8tl1h
    @user-hq8yn8tl1h 4 дня назад

    Chibanzi😂😂😂😂😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 4 дня назад +1

    MCP ndi yakupha

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 4 дня назад

    leave chakwera alone put the matter in the hand of God

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 4 дня назад

    Zachamba ngozi lmavura zovara lnuso madya mabanzi

  • @ModicaiChirwa
    @ModicaiChirwa 4 дня назад

    Zitsiru inu mwadya zakukuyu eti,anthu Ali kunja akulankhula chilungamo ndiye mukuti abwere kumalawi mufuna president wanu wazawaphe kumalawi kuli ufulu panopa pathako panu achina wonder

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w 4 дня назад

    Ndipo mukanangosiya osatiuzanso chifukwa chilungamo chili pa Limpopo fm, Bakili tv n Booooon Kalindoooo bas ena nonse mbuzi za anthu zopusa sitikufuna ife

  • @chrismando224
    @chrismando224 4 дня назад

    Anthu akakhara ogudwa sasowa kulira kwathu ngati amalawi misonzi yathu ikhare pamutu panu