"Anthu Ena A Kwa Nsundwe Anatumidwa Ndi Chipani Cha MCP Kuti Akapange Chiwembu Peter Munthalika"

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 янв 2025

Комментарии • 62

  • @steavejafali
    @steavejafali День назад +4

    Zoona mau ameneyo. Mr lozario mulungu azikudalisani nthawi zonse

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 2 дня назад +3

    Malawi wanga ineeeeee😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @kaungabondera892
    @kaungabondera892 День назад +1

    Where is the clip for those people u talking about

  • @KondwaniGulonyonyo
    @KondwaniGulonyonyo 20 часов назад

    Ntanyiwa ndinzimu sangampeze

  • @laurentbutao4084
    @laurentbutao4084 День назад

    👏👏👏👏👏👏👏👏👏

  • @JohnChitenje-t8o
    @JohnChitenje-t8o День назад +1

    Emen

  • @kantayeniphiri4016
    @kantayeniphiri4016 День назад +1

    Campaign akukuvutani aDpp kwabasi...

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck День назад

    Norman umatha❤

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 2 дня назад +2

    Ameen

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift День назад

    Uyu mumat chakwera okula maso ngat namameyi mm Ali ndi thawi yochepa

  • @MadaChipula
    @MadaChipula День назад +1

    Iwe chisale sana tsogolelepo dziko usamamunyoze ai uyu ndi bod gud osat uziti namiza kut chisale anazuza anthu kod anthu muli ndivut muma bakila zopusa.

  • @tamarajere1624
    @tamarajere1624 День назад +1

    Kupeka

  • @MacpharryMilanzi
    @MacpharryMilanzi День назад +1

    Musamatinanizepo pa aaaa mwasowa zokamba eti
    Mavuto onsewa Malo momatiuza zamavuto awa
    Iweyo ndiwa DPP usatipusise po apa
    Tioneseni anthuwo
    Chisale chigawenga ngati chimenechija muchipasa matama
    Chisale wazuza anthu Malawi muno kooopsa
    Wava ngati suziwa

  • @JulietKapata
    @JulietKapata День назад

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g День назад

    Kkkkkkkk chakwera warephera kupanga maganizo ake oyipa warephera Satana uyo amafuna magazi chakwera iya akufuna kuti azingogwesa vura kuti azipha anthu ndipo chaka chino sizitheka ayi

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i День назад

    Nkhani yabwino kuti mwalankhulana takondwa pomva izi .Timakunyadilani chifukwa munatidziwitsa zomwe sitikudzidziwa god blss

  • @WellodChagunda
    @WellodChagunda День назад +3

    Kumafalitsa zaumboni mbunzi iwe timaona ngati ukamba zazeru

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 дня назад

    May I beg Minister of Unity and Culture, Minister of Home Security, also Minister of State to convene and canvass over lack of national
    Unity,Security , and democratic patriotism in Malawi endangering the nation and backsliding our hard earned freedom.

  • @OstinKwenda-p8p
    @OstinKwenda-p8p День назад +1

    Mumangotithela Madata tapangani zanu kusiyana ndi kumango uwuwa ngati agalu, ndi bodza palibe chipani chomwe chili ndi chilungamo pofuna kuthandiza mtundu wa amalawi

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i День назад +1

      Wa chikangawa samasowa iwe ndi mbuzi ya munthu ngati ulibe chonena udzikhala chete mmesa wati tikukuthela madata? Dza uchikape eti.

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 дня назад +2

    Ndipo ambuye tumizani chitete o chokwanila kwa Peter malo mpha Peter apite chakwera yemwe yo ndipo kudwala kubwera

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 День назад

    Aaaa koma boma la MCP basi akamachita upo zoganiza zao ndi kupha anthu basi ayimani sisiii.

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z День назад

    Mupitilize tizi

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 2 дня назад +1

    MCP 💔 MKSPITILIZA ZOPUSAZO MUDZAPEZEKA KUTI MWAWUMA

  • @FrankPatrick-p1t
    @FrankPatrick-p1t 23 часа назад

    Zangoyamba

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 2 дня назад

    Iweso ndiyewuti wuti MCP 💔 😭 anthu akubadwa dairy dairy wonderful ma activitis

  • @NkhomaFungo
    @NkhomaFungo День назад

    Following

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 2 дня назад +2

    Chakwela sakwanisa maganizo akewo walephela ngo'ooooo

  • @samueljere4997
    @samueljere4997 День назад

    All lies

  • @HennockMpumulo
    @HennockMpumulo 2 дня назад +1

    Mulungu akusungen ndimoyo wawutali nthandizan malawi

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie День назад

    Kodi a mcp magazi a anthu omwe mwamwa sanakukwanedi kodi

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf День назад

    Tipatseni chithuzi cha a mpayawo

  • @RabeccaPhiri-y1q
    @RabeccaPhiri-y1q День назад

    Koma athu chipani simukugona nacho tulu. Every day. Nkhani zopanda tsogolo

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o День назад

    Map yata palibe chao

  • @LimbikaniTambala-z1y
    @LimbikaniTambala-z1y День назад

    Iwenso ndiwe omvuta kukumvetsa bwanji mmalo unene kuti Mulungu akumuteteza, chinsale ndi ndani?

  • @SlowbutsureManagerposition
    @SlowbutsureManagerposition 2 дня назад

    ATHU INU PLEASE ZIWANI YESU DAILY KHANI DAILY KHANI MMMM MALO KUTI TIPEPHELELE ZIKO LATHU LIKHALE LAMTENDELE, BASI AMALAMI TIYENI TIKONDANE WINA NDIMZACHE PLEASE PLEASE

  • @LameckNgwangwa-g3p
    @LameckNgwangwa-g3p 2 дня назад

    Chisale bravoo🦾🦾🦾🦾🦾

  • @ElijahTheprophet-y9m
    @ElijahTheprophet-y9m 2 дня назад

    Tipatseni chithuz chake mpaya yo Ife ju south Africa kuno

  • @DenesceFredericks
    @DenesceFredericks 2 дня назад

    White kwathu sangawina olo zitavuta motani ndi namusankha muchaka cha 2020 koma sanapanga chitukuko kwathu palibe anga votele olo pang,ono olo kuli iye akudziwa kuti sawina

  • @LafickDickson
    @LafickDickson 2 дня назад +1

    Mcp yata futo apanga ubale ndi masatana

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga День назад

    galu lwe kanyere uko

  • @PembaStamps-f8m
    @PembaStamps-f8m 2 дня назад

    Ayelekeze aphe winanso awone omwe anawachita chipogwe aja anakwana

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 2 дня назад

    Koma chakwela mwayambila kuwononga ndalama ati kumu saka Ntanyiwa koma mu kulephera osango vomeleza bwanji

  • @blessjare
    @blessjare 2 дня назад

    Kodi a chakwera ukuopa chani masankho osangosiya kuti mupilikisane bwanji mupha anthu angati Inu achakwera sumudzafa

  • @RoseLibamba
    @RoseLibamba День назад

    Iwe ukukamba za ntanyiwa sukumukonda zako

  • @GraceNdamuwa
    @GraceNdamuwa День назад

    Mumatha bwana

  • @McfallenKayuni
    @McfallenKayuni 2 дня назад

    Nafetso tikupemphera Chakwera.

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda День назад

    Tamuuzeni abwele kuno timuombera kuno tikudikila iyeyo Charles paya bwera utipeza chakwera akuphesa

    • @FaroukSaliem
      @FaroukSaliem День назад

      Ayelekeze kupita ku south African. Akakumana nayo polo polo

  • @FannyChimombo
    @FannyChimombo День назад

    😂😂

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y 2 дня назад

    AKUTUMA ZIMENEZO PAMTUMBO PAWO

  • @EdsonChiwereChieere
    @EdsonChiwereChieere 2 дня назад

    Wabodza iwe tiuzen zoona osati zimenezii

    • @manualrapheal6048
      @manualrapheal6048 День назад

      Iweyo watchulidwamo?😂😂😂😂kodi kumakhala kupusa kapena kumbwambwana?
      😢😢😢😢😢talongosola iweyo zoonazo data alipo

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 День назад

    Achakwela anakangotiphamo tose

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z День назад

    Mupitilize tizi

  • @LafickDickson
    @LafickDickson 2 дня назад +1

    Mcp yata futo apanga ubale ndi masatana

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z День назад

    Mupitilize tizi