Mnene Zinakhalila Za Norman Chisale Pamene Kunabuka Mpungwepungwe

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 янв 2025

Комментарии • 45

  • @HappyXylophone-hs6gm
    @HappyXylophone-hs6gm День назад +1

    Akanamugwira mmodzi nikumusunga

  • @DollophandmalifaBanda
    @DollophandmalifaBanda День назад

    ❤❤❤❤

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 2 дня назад

    Mr Norman chisale ine ndikufuna ndikuuzeni enough is enough pano tipanga njila yakuti wina aliyese amene angakhale ndi maganizo afuna kukupanganiso chipongwe chipongwe chimenecho akazindikila atapanga family yake kapena Ana ake ifeso ndife anthu timatopa A mcp tayesaniso kumulondola chisale anthu akuyelekelani abelembende inu

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 дня назад +3

    Eeeee ndege imene ija ndiyaukali bwanji kumvula munthu dzomvala, kuba ndalama zakumaliro za chipepeso akasambala ndege yoipa kwambiri.

  • @MadaloMachedwetsa
    @MadaloMachedwetsa 3 дня назад +1

    Ife tonse a Malawi takukanani inu a Mcp,,, chonde musatikakamire ife sitikukufunani anthu oipitsitsa inu

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 дня назад

    Mulungu simunthu chilichonse akumachisiya pa mbalambanda

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 2 дня назад

    Ndipo awa chita bwino kwambili police yanji yolowelela za ndale mesa police imagwila ntchito nda malawi kapena ndinu a mcp zopusa basi kodi ukuwona ngati sitikuwon mukha ulatu inu 2025 tikawona

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 3 дня назад

    Noman big up brother ALLAH is with you

  • @RexElsoni
    @RexElsoni 3 дня назад

    Noman big up god is with you

  • @MzwakhileNjoko
    @MzwakhileNjoko 3 дня назад +1

    zimene akuchita achakwela akundikumbutsa nkhani ya kaini ndi abelo ngakhale kaini anapha mwankhanza abelo chifukwa cha jelasi komabe kaini sanapambane pamaso pa mulungu zimenezi zichitikanso pa a chakwera afune or asafune.

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 3 дня назад +1

    Apolice tiyamba kuwamenya mwayamba zibwana mukunya🎉 simwa

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 2 дня назад

    Mwaputa olakwika Norman mwamuyambayu zikuvutani

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 3 дня назад +2

    Ndipo chipani cha MCP munayambila kupha anthu muja osalapabwanji nthawi yatha

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 3 дня назад

    Ine dikupepha mr chisale mukusowa mboma plz ndiwafuna ndikuuzeni kuti mukoze ndende dzonse dziko muno ramalawi mukazanze ndi member yonse ya mcp onse amene akugwira nchito kumcp mamuna kaya mkazi akamagidwe life sentence bambo munkhito muzagwile nchito mosayanganira nkhope mbamva dzonse chakwera ndi family yake yonse ndi staffu yonse yayemcp kundende akaolele mkonko

    • @EstherChilope
      @EstherChilope 2 дня назад

      MCP ingolapani. Mizimu ikulira munthakatu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дня назад +2

    Not malawi police as such , is mcp police
    But mcp are too much young , this is new generation .

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 2 дня назад

    Kwasala miyezi 7 kuti agalu awa achoke basi

  • @YounusWabullah
    @YounusWabullah 3 дня назад

    Mcp inabwera kudzatidziwitsa a mma 2 pn fe nkhanza zawo nde tawadziwa adzalowaso tikakadzakalamba amma 2 pn fe

  • @Ruthgomonda
    @Ruthgomonda 3 дня назад +1

    asowa zochita ayaluka awona bonawonaaa

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 2 дня назад

    Norman ndikatundu

  • @MathewsMilli
    @MathewsMilli 2 дня назад

    Norman chisale ndi Baracks pa ekha.

  • @salmankhanofficiel.5018
    @salmankhanofficiel.5018 3 дня назад

    Nde wina uva boma ndilomweli 😂😂😂😂

  • @GeofreySaizi-xj6uv
    @GeofreySaizi-xj6uv 3 дня назад

    Inu a MCP a Malawi akayamba kubwenza nkhanza zanuzi muzamva mbebe ndithu

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 3 дня назад +1

    Kungowina adadi ndidzasangalala

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 3 дня назад

    KuNtcheu asationjeze, ndipo asayelekeze maganizo opusawo.akhakhakha, agwinyingwi, agulukunyinda.

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 3 дня назад

    Chikangawa masiku ako ndiowerengeka

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 дня назад

    Mwauze akanganya amenewa
    Agulukunyenda akakaka

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 3 дня назад +1

    Tiana ta police tomwe mukutitumati mutipwereketsa chakwera mboleyake

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 дня назад

    Aaa a MCP awa agalu kwabasi tabwelela kuchipani chimodzi basi

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 3 дня назад

    DPP that's what people are getting better than mcp

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 3 дня назад

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 3 дня назад

    Mapullan amcp satenka mphaka September 16

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 3 дня назад

    Kuzolowela kumwa magazi

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 3 дня назад

    Ife timangomvatu kt mcp ndi yoospa

  • @MaxyMaida
    @MaxyMaida 3 дня назад

    Yatikwana mcp

  • @OdgeNzunga-i1h
    @OdgeNzunga-i1h 3 дня назад

    Zoopsya heavy

  • @DavieDulani
    @DavieDulani 3 дня назад

    2025 Noman comander of inchage

  • @SylvesterSululu
    @SylvesterSululu 3 дня назад

    Koma mcp muwopeni mulungu

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 3 дня назад

    Komanso bottom line pastor shumba kuti tiwafufuze bwino ndithu amenewatu si apolice anangowapatsa ma unform ndi kutheka kuti zigawenga zaku Rwanda zili mdziko mwathu muno komanso musayiwale kuti bushiri analandila alendo osiyana siyana ku church yake moti alendo amenewa ena sanabwere za church dziko lathu lawonongeka

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 3 дня назад

      Akudzinamiza chifukwa Peter simunthu wamba, china chilichonse chachiwembu chomwe akupanga iye amachidziwa. Kumbukirani ndi president opuma.

  • @EDWARDBANDA-x1t
    @EDWARDBANDA-x1t 3 дня назад +1

    Tingodikira September tivote a coke

  • @rosechapita3434
    @rosechapita3434 3 дня назад

    Abusa inu ndinu antopola osokoneza leave utm alone u are not God. Talk about other things. God can do miracles in a second. Ubusa wanu ndiwapanu.

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 3 дня назад

    Machimo mcp