Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mmmmm 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌
Bola nzimayi ankapanga program iyi uja ankabebetsa.
Mfiti iza fanso kumango khala kuzi vuta kumaloza kapena kupha mzako palibe chosatha pa Dziko Lapansi,kunali koyenera tonse kumalemekeza Yehova, Koma masiku akusa ziwa Mulungu adalekerera mphavu Za satana pa Dziko Lapansi.
Palibe ndatolapo kanthu
Next time dzaesetseni kujambulila malo aboh
Nkhani zopanda mutu zosowa poyambira😂
Komatu nde siinamveke bwino yopandanso poyambira
Aaaaa...basi chinthawi chonsechi yathera pamenepa???.. za ziii
Ndipo kale zimabeba pano I don't understand
Koma mwanao akusokoneza aaa
Mwatisiya m'malere
Hii
Program sili bwino next time zapangen zadongosolo
Alomwe akati awonjezere nkhani. Koma palibe chikumveka
Mmmm
Aaaa chenkope sudziwa kufusa
Koma
Nkhani iyi siikuveka bwino zikuphatikizana mutu weniweni siikuziwika
ufiti uriko muzinamiza anthu kuti ufiti kuribe koma aboma inu ufiti uriko ineyo umboni pankhani naiyiyi yafiti tagwirapo ambiri naine
Mmmm everyone is right according to themselves, koma kwaineyo it doesn't make sense